kangaude

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 24. 06. 2023

Komentáře • 113

  • @user-ze9gy1fp6y
    @user-ze9gy1fp6y Před 5 měsíci +1

    Mwana osalakwa ambuye muchite nayo mwana mu phavu yamuzimu wanu ambuye muyendelen mwana munamupasa mphatso ndinu tikumupelekaso kwa yinu oipa azachite manyazi amen

  • @user-xk6lb5hy4u
    @user-xk6lb5hy4u Před 3 měsíci +1

    Mulungu wazatheka bwanji ndinu nokha amene muli ndi thandizo kwamwana ameneyi muchite zodabwisa

  • @kedibonesegametsi2493
    @kedibonesegametsi2493 Před 3 měsíci

    Eish

  • @duncanafunsaniduncan7651
    @duncanafunsaniduncan7651 Před 11 měsíci +1

    police yaku ku malawi mmmm mbola chinyengo ...i wish ndingathandizepo ..
    ambuye akhuze ndikuthangatilapo

  • @steviemikechimenya2628
    @steviemikechimenya2628 Před rokem +1

    Ambuye mkhuzen mwanayo ndi dzanja lanu la machiliso.mwana akuvutika uyu chitan chodzidzwisa pamoyo wake.
    Mai a mwana musatope kusamalira mwanayo.
    Azibambo kwenikweni ndi chani zoona kuzunzisa mwana chifukwa cha ndalama? Mulungu akupasen mtima wa umunthu komanso zomwe akuona mwanayo taganizirani muli inuyo.
    Apolice aku Malawi simukudziwa ntchto yanu maka maka inuyo amene mwatenga gawo lalikulu kudya ndalama kuti Norman oipayo asamangidwe Mulungu akuyenderen ndithu.
    Mabungwe pls loweleraponi mwanayo apeze thandizo loyenera.

  • @Marialongwe-nzlib
    @Marialongwe-nzlib Před rokem +3

    Nanu Police Muziona Nkhani Zodyapo Ndalama aaah Kungokhala ndimtima Wautsamunda basi, Inu Nkhani yozikamba yokha iyi Mboni ndimwanayo koma Mpaka kudyapo Ufiti chani

    • @husseinnicks4042
      @husseinnicks4042 Před rokem

      😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 please tiyen tikondane

  • @NiclyKasambala-rg2ep
    @NiclyKasambala-rg2ep Před rokem

    Nkhaniyi saname yandimvesa chisoni mulungu oziwa kulanga alanhidwe chemwali wamwamunayo pamodzi ndi mwamunayo mmene amapwetekela mwana mwana wokongola oooh ambuye aoneni

  • @brightkaunda920
    @brightkaunda920 Před rokem +1

    Ambuye simunalephelepo ndinu wamphavu zonse tikukupemphani kuti ndimphavu zanu zonse mumuchilitse mwanayo kuti oipayo azindikile zaukulu wanu

  • @samsamuel9280
    @samsamuel9280 Před rokem +2

    Bwanji mwanayo osakamusiyila mfitiyo kt angomumaluzapo.Anthu ena ngoipa mtima kuposa chinyama chakuthengo.

  • @banetmatanje2336
    @banetmatanje2336 Před rokem +4

    😢😢😢😢 chiuta akatiranga koma police officer wuzinganizire kukhala iwe uka natani ????

  • @EsnatNkomaGine
    @EsnatNkomaGine Před rokem

    Sing'anga mkulu ndiye YESU, amukhuze mwanayo akhale bwino

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 Před rokem +1

    Mwana ali pa ululu uyu 😭😭 ambuye ndinu dokotala oposa ma dokolata mumaika njila popanda njila ambuye chitani mwakufuna kwanu

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Před rokem +1

    Zomvetsa Chinsoni 😭😭..moyo wa Mwana Gracian ukudzuzika chifukwa chabambo ake oipa mtima kufuna kulemera...koma chikumbutima chimusowese mtendere ndithu

  • @towerankhoma1380
    @towerankhoma1380 Před rokem +1

    Koma officer in charge Mulungu akuyendere mwapaderadera, ndiwe oyipa

  • @AgnessChimwaza-dy9oz
    @AgnessChimwaza-dy9oz Před rokem

    Maganizo anga,mwanayo mupite naye kumapemphelo chifukwa anamuika ziwanda Bambo akewo

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Před rokem

    Mpaka kulolera kuzunza mwana mzimu osadziwa kanthu cjifukwa chandalama ,m,bambo ameneyu

  • @Watson-q4d
    @Watson-q4d Před 11 dny

    Mulungu muchitepo kanthu PA moyo WA mwanayu komanso langizo Kwa apolisi athu mmalawi muno mwachulusa kwambiri chinyengo mukuyenera kugwira ntchito yanu moopa mulungu

  • @AgnessGuta
    @AgnessGuta Před 3 měsíci

    Ndipemphelo lokha limene lingamumasule mwanayuu

  • @user-xk6lb5hy4u
    @user-xk6lb5hy4u Před 3 měsíci

    Tizalangidwa chifukwa chachimo lalingono pollice yamalani ndintchito yanu chifukwa mulungu azaweluza and nthawi yasala pangono mwana akuonekelamu kumalimba ntima ndikumusekela opanda chisoni

  • @muhadusuman
    @muhadusuman Před rokem +2

    Malawi wabwino uja ali kuti? Izi ndiye ziti guys 😢😢😢

  • @violetwanja9592
    @violetwanja9592 Před rokem

    Mulungu awakhululukile apolice onse amene akupondeleza nkhani iyi komanso amukhuze Gracious ndi dzanja lamachilitso

  • @MemoryLungu-sp8eq
    @MemoryLungu-sp8eq Před 3 měsíci

    Mulungu mumuyendele mwana uyu pamodzi ndi mayi uyu mzina ndi mphanvu Zanu poti inu simulephera

  • @jamesngalande4345
    @jamesngalande4345 Před rokem +1

    Apolice ziphuphu mpaka kuzunzisa mwana osalakwa Aboma zonsezi mukuwona komanso mukuziwa

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Před rokem

    Tieni abale tithandize Gracious..sister wathuyu akuvutika nae...mwana...

  • @StevenSteveni-xr3bf
    @StevenSteveni-xr3bf Před rokem

    Banja la Moyo osadandaula, Mulungu salakwitsa as Iam talking God is in control ndipo kuzuza kokha komwe akuchita pa mwanayi Mulungu akuona

  • @collennyirendah5768
    @collennyirendah5768 Před rokem

    😢😢😢 Zomvetsa Chisoni kwambiri,
    Koma agalu osakawa akuthandizira kuchotsa moyo wamwana, 😭😭😭 Ambuye akuoneni

  • @rooseveltmtemula2643
    @rooseveltmtemula2643 Před rokem

    Koma anthu tikuziwa kukwatibwa ndi afiti😢Lord have mercy iiiiiiiiiiiii ambuye amukhuze Greycious oipa wo achite manyazi

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Před rokem +1

    Mmm koma kunjaku kuli anthu oyipa mitima koma ndithu kufuna kupha mwana cholinga mukhwimire damu iweyo mamunawe ukumva bwanji komwe uliko ukamazunza magazi ako ? Kodi nanu apolice mukuvutika chintundu chani mpaka nkumadya ndalama kuzera nkhani zomvesa chisoni nkhati izi ? Inu chemwali eni a mwana ziyikeni mwamulungu odziwa kulanga awalange anthu amenewa inuyo limbikirani posaka chithandizo chamwana china chilichonse chomwe mwalandidwa chisiyeni. Ambuye mwainu nokha ndimomwe muli machiliso mupaseni mwanayu kuchira nsanga ndikupempha kuzera mwa mitukiki yanu yonse ameni

  • @costerrobert1519
    @costerrobert1519 Před rokem +1

    Mwana akudzudzika chifukwa cha apolice kamba kadyela landalama

  • @user-pd2jq9rx3s
    @user-pd2jq9rx3s Před rokem

    Kulakwa mwana osalakwa kuzuzika mulungu muyendeleni😢😢 zibambo otani ameneyo mwana wake yemwe ufiti otani umenewo ndalira😢

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd Před rokem

    Ambuye mukhuzen mwanayo ndi zanja la machiliso.... mwanayo ali pa ululu kwambiri chitan kufuna kwanu mbuye wanga😢😢😢😢

  • @user-vv7ub7no1j
    @user-vv7ub7no1j Před rokem +5

    We were watching this program while taking our dinner but upon following it, the whole appetite vanished comrades there are some people who are evil than Pharaoh of Moses' time😭😭😭😭

    • @edwintshepang5108
      @edwintshepang5108 Před 9 měsíci

      This guy is very wicked, evil scarem
      This is unfair treatment 😡😡

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Před 4 měsíci

    Panopa ineyo nnazipanga kuti munthu kundibela, kundilakwila kulibwino ndithane naye ndekha bola mtamudziwa. Ndilibe mawu zomwe a police anandipangila pankhani yoti ndikukadandaula ineyo kunditenganso ngati ineyo ndiye olakwitsa ndipo a police achizimayinso ngati awo ondipanga zoophyazo 🙌🙌 ndipo mulungu adzikukanthani ndipo muliko ndimakutembelerani ndikukupemphelerani pamodzi ndiokubayo. Mulungu wazifundo awathandizepo

  • @user-pw1kl3vo5d
    @user-pw1kl3vo5d Před 7 měsíci

    Wapolici ameneyu akuyenera kuchotsedwa tchito akalime nandolo

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 Před rokem

    Chilungamo chimamasula osadandaula mulungu ndi wakuntha..ndipo tsiku lina udzakhala umboni wanu..nkhulupilirani..

  • @johnsong7236
    @johnsong7236 Před rokem +1

    osapitako kumene akuitaniko apolice apo biii tipange ma demo

  • @costerrobert1519
    @costerrobert1519 Před rokem +1

    Koma apolice amenewo kunali kuwamangisa ndithu

  • @user-kq7ht6ic1i
    @user-kq7ht6ic1i Před rokem +1

    😭😭😭zokhuza kwambir

  • @tshepangmatebele7822
    @tshepangmatebele7822 Před rokem +1

    Nkhani yomvetsa chisoni 😢😢😢😢😢😢

  • @user-pw1kl3vo5d
    @user-pw1kl3vo5d Před 7 měsíci

    Apólice opusa osapola panchombo komaso amina mmutu mwao akuononga mbili zabwinoza za azao

  • @johnsong7236
    @johnsong7236 Před rokem

    ndipaseni map a aunt akewo ndikawasiyile chipolopolo chimodzi chakumutu ndi mbuzi

  • @hopembendela
    @hopembendela Před rokem +2

    Mulungu wayakobo mulungu wa davite mulungu wa eliya ndikupempha kut muonesele ukulu wanu pa mwana uyu ndikumulandisa manja mwa mikango iyi amen

  • @matomachika
    @matomachika Před 9 měsíci

    Eeeee ayi izi zaonjeza ambuye 😢😢😢chitanipon kathu ambuye

  • @user-od6ek3tx6m
    @user-od6ek3tx6m Před rokem +1

    Mudzina layesu achilitsidwa

  • @user-ne3ui4op9m
    @user-ne3ui4op9m Před rokem +1

    😢😢😢msaname ndalira

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před rokem +1

    A police sakuchita bwino olo pang, ono

  • @FosterCement-yn4cj
    @FosterCement-yn4cj Před rokem

    Dziko la Malawi Mulungu atikhululukire chifukwa amphawi tili pamavuto akulu kwambiri Koma Mulungu kumwamba kulibe Sankho apolice mukamakonda ndalama kusiya chilungamo dziwani Kuti kumwamba kulibe mphawi kulibe ndalama chepesani zimenezo

  • @thokochilimba-bs2mm
    @thokochilimba-bs2mm Před rokem

    Kulakwa abale mwana akuzimzika😢😢

  • @frankkamwendo4950
    @frankkamwendo4950 Před rokem

    A court nawonso akugona pa ntchito yao, munthu kufika pomatukwana ma officer kumangomusiya? Mesa mumakamutenga by force kuti akakhe madzi kae ku prison?

  • @BdhfbHdhe-pd7nh
    @BdhfbHdhe-pd7nh Před rokem

    Mwana wamwezi angasuke mmimba.mmmmmm anthu ndioipa Mulungu ateteze mwanayu

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Před rokem

    Adzakukantha mulungu ulibe masiku galu wabambo iwe

  • @victoriawilliam4490
    @victoriawilliam4490 Před rokem

    A police amenewo Mulungu awayendere ndithu
    Kulakwa mmmmm ndalamazo zakoma bwanji kuyerekeza ndi moyo wamwana mmmmmm

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 Před rokem

    Mulungu alowelele pazosezi mwana akunzunzika uyu ngati bambo ake alibe eish koma azibambo enawa ndiyafiti kwambili

  • @user-tr1rh4xn1w
    @user-tr1rh4xn1w Před rokem

    Tangognizani Ali chemwli wanu mungave bwanji khzatu idzi

  • @lytonmaseko4534
    @lytonmaseko4534 Před rokem

    Malawi nkhalani wachifundo komatso achisoni ku malawiko ineyo ndikanakhala ndili ndi ndalama ndikanapanga zinthu zina
    Komatso please amabungwe tenganipo gawo
    Agalu onse awo apolice muwamange
    Zandikhudza kwambiri😭😭

  • @AnaniasRathwakga
    @AnaniasRathwakga Před rokem

    😢😢😢 alibe

  • @lovebinta6863
    @lovebinta6863 Před rokem

    Mmmmmm kma abale inu mwana adalakwa chiyani kut akalandile ululu umenewo mmmmmm Ambuye mukhudzen mwanayi Ambuye

  • @mayesochitedze2513
    @mayesochitedze2513 Před rokem

    Zandikhudza abare anthuwa athandizidwe

  • @user-xf1gb5gu3z
    @user-xf1gb5gu3z Před 4 měsíci

    In this case, my opinion is to arrest both the husband and his sister. They are all wrong, Anti-Corruption bureau has to take a stand together with the social welfare with people of disability.
    The court has to help in judging righteously, that child needs a great and total support especially from his dad. The love from your parents brings joy to yourself.
    That bail has to be null and void, apolisi nawo azitha kumvetsetsa what is going on before coming up with judgements, malo mokonza zinthu they'll end up spoiling. Don't take sides, do what is right.

  • @jrculdickson6629
    @jrculdickson6629 Před rokem

    Ndisaname zandiwawa kuchokera poyambilira mpakana kumapeto nkhani iyi yandivesa chisoni yanditulutsa misonzi koma chifukwa chani mwamuna uyu aliolimba mtima chonchi ........apolice akumalawi vuto siinuyo vuto ndi boma la malawi momwe zikuyendera koma china ndi china chilungamo pa nkhani iyi tingopempha mulungu alowelelepo .........chisomo walankhula mwachikulu😢😢 ....chisomo mulungu akuthandizani pepani kwambiri .......agogo ake amwana ndizoonadi simungakhale ndi mtendere pa zomwe zililimo pepani kwambiri mayi anga mulingu alimbali yanu mabungwe oona za ufulu chonde chonde lowelelanipo hapa komaso apolice omwe muli ndi khalidwe ngati mwachita apa mulungu akulangeni ......

    • @sharfalie3943
      @sharfalie3943 Před rokem

      Apolice opondeleza onse mulungu achitenanu mai uyu akumusogolela nchimwene wake wakuphayu mawa nayeso azapeza vuto kuposa limeneli ndipo ndikupempha mulungu achite back to sender

  • @YankhoJuma
    @YankhoJuma Před 9 měsíci

    Mmmh 😢

  • @user-nk7gn3lz3f
    @user-nk7gn3lz3f Před rokem

    Koma apolec wankulu wazengeleza khani Malo mwa cilungamo

  • @faithmtika6121
    @faithmtika6121 Před rokem

    So sad

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk Před rokem +3

    Very bad, one who so called wachitetezo akuthandizila kupha mwana kamba ka ndalama.
    Mulungu azakulangani.
    Kangawude program nkhaniyi musasiyile pomwepa follow it till end.
    Inunso amabungwe ntchito koma iyi athandizeni mayi moyo ndi banja lawo.
    Apolice Maka apa lucheza very soon mulungu akulangani choyipa chisata mwini pitani mukabweze ndalama mwadyayo.
    Iwenso munthu wanambo ufiti uwu ziwa kuti uzafa uchonsenso ziwanda wayika mwa mwanayo. Mulungu akulanga kunjaku kuli mulungu.

    • @billymhoni9527
      @billymhoni9527 Před rokem

      A police akuyenera afufuzudwe mwana samalowesedwa mu cell...

  • @user-qr2fx7eb3y
    @user-qr2fx7eb3y Před 9 měsíci

    😢😢😢

  • @user-gn6yl2kv2c
    @user-gn6yl2kv2c Před 4 měsíci

    Guys mwana akuchita kumvesa chisoni shame this world is so cruel

  • @piliranichikwapata349

    Why kuzunza mzimu osalakwa like that God have mercy upon the child 😅

  • @user-dp2dg8oe6p
    @user-dp2dg8oe6p Před rokem

    😢😢so sad

  • @user-tu8yx2on1r
    @user-tu8yx2on1r Před 3 měsíci

    Lord have mercy

  • @chenonoissah4540
    @chenonoissah4540 Před rokem

    3:35 pm Malamulo aku Malawi amakomera anthu andalama, apolice athu chilungamo alibe

  • @egreymkumba-tj5ji
    @egreymkumba-tj5ji Před rokem

    😢😢😢😢😢😢😢

  • @BrynMakaika-eb3ue
    @BrynMakaika-eb3ue Před rokem

    Ngakhale Police yathu itagwira bwino ntchito chotani, a police ngati awqva Luchenzacndi Thyolo akuonetseratu kuti analowa upolice kutu adzibera anthu mu njira ya ziphuphu

  • @user-hx2vy5ys1j
    @user-hx2vy5ys1j Před rokem

    Sister munakwati ndi mfiti munayenela kuzisiya mmanja mwa chauta ndamene akudziwa mawa la muthu

  • @herbartkaphamthengo9978

    Chifukwa chiyani apolice amazuza anthu osauka palibe chabwino chomwe munthu osauka amalandila thandizo kwa police koma malawi

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Před rokem

    Lord have mercy 🙏

  • @abdulkatopola3612
    @abdulkatopola3612 Před 9 měsíci

    Nkhani iyi ili pati tilowelelepo pls link us

  • @user-hx2vy5ys1j
    @user-hx2vy5ys1j Před rokem

    A police Aku thyolo chilungamo chimawamvuta

  • @HappyKalagho-ky7lh
    @HappyKalagho-ky7lh Před rokem +1

    Let the plan of devil fail in Jesus name

  • @robertchitsulo8006
    @robertchitsulo8006 Před rokem

    Zosakhala bwino ai ikani ma number anu .

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 Před rokem

    Mwana wabwino ngati uyu ..so bad ...

  • @faithleon653
    @faithleon653 Před rokem

    Zovetsa chisoni eeeee

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 Před rokem

    Boma lilowelelepo there has been Child abuse apa..

  • @berthakambwiri6288
    @berthakambwiri6288 Před 10 měsíci

    Wow😮 this is very sad and it is a criminal offence arresting a child that committed no crime, this should be followed up and if possible these girls can sue the officers who did such

  • @moseschizyibwa4463
    @moseschizyibwa4463 Před 11 měsíci

    What a beautiful baby. God will punish the father of that baby, and he will never see peace in his life. Mr. Zulanga continue with the good works.

  • @MercySaiti-et1ty
    @MercySaiti-et1ty Před rokem

    Ndiye kut opanda ndalama ku police kulibe nthandizo lake et, muthokoze kut anthuwa angokhala ndi umunthu mkadakhala ine mbambadi mkadafufuza komwe wapolice adalandira ndalamayu amakhala mkadakamuonetsa kut ena atengerepo phuxilo, apo bii mkadasaka petrol mkukabusa office ya police coz palibe phindu kwa anthu osauka, ndamva ululu kwabasi

  • @chikonjiwe007
    @chikonjiwe007 Před měsícem

    Koma a Police .aku Malawi hmmmm you are very wicked

  • @user-nl7xv8om5e
    @user-nl7xv8om5e Před rokem

    Yehova. Munkhwaskani mwana uyu na zanja linu lakuchizga

  • @PatriotSatheka-ws7kn
    @PatriotSatheka-ws7kn Před rokem

    Zoopsatu

  • @user-tr1rh4xn1w
    @user-tr1rh4xn1w Před rokem

    Inetu ndalila kwambili ndipo zandikhuza koma mulungu khuzeni mwana ndikono wamadalitso amen

  • @chifunirosaka9077
    @chifunirosaka9077 Před rokem

    Mudzina la Yesu matsoka komaso matembelo apite kwa aliyese amene watengapo gawo lozuza komaso kusautsa banja limeneli akumane ndi zilango mulungu awonetsa ukulu wake in Jesus name

  • @stevezulu2108
    @stevezulu2108 Před rokem

    Iiiiiii koma abaleeee?😢😢😢😢

  • @johnsong7236
    @johnsong7236 Před rokem

    pray for me Malawi,when i get rich all the corrupted police will be fired
    fokoffffff

  • @collennyirendah5768
    @collennyirendah5768 Před rokem

    nkhani ya straight ngati iyi akulu achitetezo ndikupanga chinyengo mpaka kudzudzitsa moyo wa Gracious 😢😢😢😢😢

  • @chifundomhango3324
    @chifundomhango3324 Před rokem

    So bad 😢😢😢

  • @johnsong7236
    @johnsong7236 Před rokem

    ndadaula kwambiri koma and zandipangisa kulira

  • @hopekamanja5407
    @hopekamanja5407 Před rokem

    Very bad

  • @luciarashid1961
    @luciarashid1961 Před rokem

    So bad😢

  • @mafia_noel7220
    @mafia_noel7220 Před rokem +1

    Bad

  • @steviemikechimenya2628
    @steviemikechimenya2628 Před rokem +1

    Ambuye mkhuzen mwanayo ndi dzanja lanu la machiliso.mwana akuvutika uyu chitan chodzidzwisa pamoyo wake.
    Mai a mwana musatope kusamalira mwanayo.
    Azibambo kwenikweni ndi chani zoona kuzunzisa mwana chifukwa cha ndalama? Mulungu akupasen mtima wa umunthu komanso zomwe akuona mwanayo taganizirani muli inuyo.
    Apolice aku Malawi simukudziwa ntchto yanu maka maka inuyo amene mwatenga gawo lalikulu kudya ndalama kuti Norman oipayo asamangidwe Mulungu akuyenderen ndithu.
    Mabungwe pls loweleraponi mwanayo apeze thandizo loyenera.

  • @FrankMitochi
    @FrankMitochi Před 11 měsíci

    Ndalila kwambili ambuye amukhudze grecious NDI mkono wamadalitso kut oipayo achite Manyaz zibambo oipa ofuna kupha mwana wake 😢😢