Velikost videa: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Zobrazit ovladače přehrávání
Automatické přehrávání
Přehrát
I ve followed the story am from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Mmmmmmm Malawi, too bad watching from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲
All very wonderful Malawi what's going on?
Kukhwima kwake kopusapusa nanga kulemela kwake kulipati nyumba yadothi lokhalokha
Eishhhh God have mercy upon Malawi😢
I pray for my brother sisters and my dad kuti mwina naonso angabwele coz sitikhutila nazo imfa zao
I pray my husband to come back five years now Koma still sindikhutisidwa mpakana pano
Malawi nkhanza
Sonawonepo zolemela kungozizuzapo ndiza ziii
I have followed the whole story of Mr sato and the omighty Lord should drop more miracles to this village so that people there have to live without fear.
Ambuye sizingachitikileko ine izi adad kungotulukila mmmmm😭😭😭😭
Amalawi nzoopsa.
Koma kulemela kuli pati apa umfiti si zithu sure
mukufanana mphuno komanso nkhope..zomvetsa chisoni
Eyaa
amalawi muzipenpela kwambili🇿🇲🇿🇲🇿🇲😭😭🙏
Ambuye asala pang,one kubwera tiyyeni tirape a abare anga chance nthaw yantha
Wakufa sadziwa kanthu bii
Att Ng'ombe 5🤣🤣🤣🤣
Amalimatu mesa amalimisa mizukwa anawachita bwino bambo akowo afit inu agalu mukuzuza amzanu kwambir
Mr sato where are you now too bad from chama zambia
Amalawi kodi mwatani kodi mulungu alimumalawi
Amalawi azanga moyo wopepetula abale anu pofuna kulemera simoyo wabwino ndithu
🙆🤷
Abale ndiluti sindikuvesesa momwe wamwalila mwana wanga yekha yekha ndinabeleka , Pano Ali ndi mwezi pasi, koma chomwe chikundidabwisa Amati apopano beseni lomwe amasambikira mtembo anangoliyika kusi Kwa bed kwawo , kuwauza andipase akukanilila abale ndithandizeni ndithu
Anthu Ali ndi nsambi ndinthu mmmmm
Kma anthu mumalakwa ufit ilipo ndthu
Ndiye aziti ufiti kulibe
Koma anthu amaipatu
Tili masiku otsiriza nde zobisika zose zayanera kukhara pamtunda
Achewa muli ndi ntchito choncho dziko lingatukuke sham
😂😂😂😂😂
Zosatheka ndi anthu zimatheka ndi ambuye ,,,may God reveal all the secrets in this world
Zaziiizo ng'ombe 5 zophela athuzo zaziiizo mxweuuuuuuuuuuu
Lord have mercy on us. May you deliver your people.
Komatu agogowo akufunika thandizo lakuchipatara
Palibeso kulemela apa munthuyu anangokhala chabe mfiti
Eeeh Koma munthu !!!
Much respect boss ❤️
Chofunika kuima pa maso pa mulungu
Oh my God!.. miracle working God please bring back his senses 🙏🙏
How are you ❤❤❤❤❤
Ufiti malawi
Koma mlungu. S mthu
Zaka zadusapo zochepa kakumben manda mukawonemo mafupa
Lunch time
Kodi bwanji kukumba mmandamo ndikutsimikiza ndithu
Akakakumba akampeza, it's spiritual thing u know
😢
Shame
Ufiti ulipodi a Malawi mmmmmm
That family needs a breakthrough and deliverance, God have mercy on this family.
A chewa koma
Nanuso ndachewa amenewa?
People are bad wichchruft is real
Kom uphawi sizinthu kusowa zochita chifukwa cha uphawi
L
Ufit ulipod mmmmm
Ai ndimasiku yotsiliza,,