Bakili Muluzi ndi munthu oopsa, wakuba komanso wakupha.

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 2. 06. 2023

Komentáře • 194

  • @goodwellchanunkha1971
    @goodwellchanunkha1971 Před 10 měsíci +5

    Mwa chilima ndinkaona material ngati Julius malema koma mmmm mikozo yeni yeni. Malawi wanga ine

    • @SameKaposa
      @SameKaposa Před 9 měsíci

      😂😂😂😂😂😂 Koma ndaseka

  • @Seche204
    @Seche204 Před rokem +7

    Chakwera failed us, but Chilima can not be a solution 🚮🚮

  • @kamwendoderek6567
    @kamwendoderek6567 Před 11 měsíci +2

    kodi athu amenewa akuyakhulawa ndi akuti,,, koma pano ali kutiko pano anthu amenewa?????????????????????? may almighty true living GOD FORGIVE THEM JUST BECAUSE OF THEIR SPEECH

  • @sesfikileshop7344
    @sesfikileshop7344 Před rokem +2

    Lero Nanu muli ndi milandutu mumkanena anzanu kumadziona ngati ndinu ochenjera
    Nawenso mbava yachabechabe

  • @SagonjaWadc-tk1ey
    @SagonjaWadc-tk1ey Před rokem +4

    Bolanitso bakili zinthu zimayenda bwino

  • @nditumenichagunda4192
    @nditumenichagunda4192 Před rokem +4

    Osamatchula yesu pa zopepela zanuzo

  • @kassimjummah9489
    @kassimjummah9489 Před 11 měsíci +3

    Chilima boza limenero

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga Před 9 dny

    mtambo ndi m'bulundi...😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂akagwele

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Před rokem +2

    Mbava za Tonse Alliance ndiye bolanso mmbuyomu,

  • @leonardmchiela6533
    @leonardmchiela6533 Před 9 měsíci +2

    Kodi achilima siwaja adapanda akazi awo aja ?

  • @williamdaisithom5913
    @williamdaisithom5913 Před rokem +1

    Happy and good speech today but remember tomorrow your not a leader someone will Judge you
    🕊📖.........✍

  • @user-lf6qf2tw5o
    @user-lf6qf2tw5o Před 13 dny

    Mwaziona amutambo chakwera ankafuna mmuchose mmatope lero ndi izi aliyese amene adamuolosa akufuna atamupha

  • @user-fr6bf4ne2d
    @user-fr6bf4ne2d Před 3 dny

    Kupatula zot zomwe mwakambazo but nthawi ya UDF aaa guys ndalama imapedzeka...mboni ndi mavenda..
    Chilima for the first time ndinkamufila but nnangowona kut nayenso zinali nkhobwe zen zen nnamutuluka

  • @emmanuelchimela4656
    @emmanuelchimela4656 Před rokem

    Bakili ndimunthu wabwino ❤ mukamati ndiwakuba osaona manyazi iii akudyeselani ?

  • @AlexKaunda-ir6rz
    @AlexKaunda-ir6rz Před rokem +2

    Atupele ndi mbuzi ngati bambo ake😂😂

  • @olivechikwindi9126
    @olivechikwindi9126 Před rokem +1

    Anyamata ndie akugwira ntchito momasuka,😂😂😂😂ntchito sizikusowa chilima ndi chakwera eishhhh😮😮😮😮😮

  • @TONYJUSTIN-cx7yt
    @TONYJUSTIN-cx7yt Před rokem +4

    Adale nose wakumoto basi palibeso zokambilana iyayi fire 🔥

  • @user-dv2it6co1i
    @user-dv2it6co1i Před 8 měsíci +1

    Were still waiting jobs 1million

  • @ReamogetsiMaredi-dn9sm
    @ReamogetsiMaredi-dn9sm Před rokem +1

    Kkkkkkkkkk mamuna mzako mpachuludi nanga mesa ndi awaa zawakanikawa
    Fetlizer lero 90 pin fuel 2pin

  • @folamitowing238
    @folamitowing238 Před rokem +1

    Anthu awa ndiye ndi abodza enieni komanso abodza Eni Eni.Abakili munkawanyoza aja ndi amene anatimvetsa kukoma kukoma dziko lathu la Malawi.inu agalu mukupanga chani chiyambireni cha boma lanu

  • @stainmilanzi5293
    @stainmilanzi5293 Před rokem +1

    guyz chilima nda azizake omwewo mavuzi awo ndithu anyapapi setezawo

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga Před 9 dny

    chakwera NFUNDO ALIBE😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @rabsterkamoto8953
    @rabsterkamoto8953 Před rokem

    Atupele Ali ndi experience than them u can see they're destroying our country instead of kuli kwedza dzikoli. Atupele anali Nduna Koma sanabe what if atakhala president obvious sangabe

  • @daudsagona1952
    @daudsagona1952 Před rokem +1

    Bwanji Kodi tizimulemekeza bakili muluz coz anasiya ndale

  • @IdrisaJetu
    @IdrisaJetu Před 2 měsíci

    Chilima ndamuda sangandinyozere atupele

  • @homeremedys3748
    @homeremedys3748 Před rokem

    Aliyense Ndimbava, inunso mukumvera izi ndinu akubanso, Don't judge anyone.
    That's why jesus anati amene sanachimwepo atenge mwala amugende

  • @issahkagansamussah
    @issahkagansamussah Před rokem +1

    Ndichifukwa chake mukufuna kumalimbana ndi atupele ndichani anakulakwilani Inu ili ndi chimo la bambo and not him

    • @giftdulamkalenga7344
      @giftdulamkalenga7344 Před rokem

      NDIPOSO MWINI WAKE WA TV IYI NGWAWUSILU ..AMAKONDA KUNYOZA BAKILI MULUZI KOMA NDIMAZIFUSA WHY DOES HE USE HIS NAME

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py Před měsícem

    Lero zakudera galu bakili umalimba naye uja lero wakutembenuza wangopusa wasocheresa amalawi galu iwe

  • @user-zp6eq4br7t
    @user-zp6eq4br7t Před 7 měsíci

    bakili akaba, ma chenje osala amagawa moti umphawi kunalibe pomwe anyani inu mukaba mungoziunjikila nokha achule inu

  • @christinemapoko6338
    @christinemapoko6338 Před rokem

    Amalawi timangoombera mmanja zopanda pace. Achinyamatafe tatopa kenako tizalowa mchire n'kuyamba kupulitsa mizinga

  • @Kasawalah
    @Kasawalah Před 3 měsíci

    Iwe ndi mbuzi yamunthu iwe ndiwabodz iwe sukunamiza anthu apa!!

  • @alicehananiya
    @alicehananiya Před 5 měsíci

    Atupele mulidzi Vs Peter muthalika 2025 Boma UTM anthu asatanic inu

  • @SindiweAllhajih
    @SindiweAllhajih Před rokem +1

    Chakwla ndichilim ndagalu opanda man kobas wallah......pano achewa ndamene akusangalala mh mulingu awakathe ndithu

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y Před 5 měsíci

    Mtambo alibe nzeru, kulakwa kwa abambo ake Atupere chikumukhunza nchayani?

  • @noahtsamdoka1172
    @noahtsamdoka1172 Před 10 měsíci

    sindikudziwa apumbwawa azalowanso ndi it it 🤔🤔🤔 Linda madzi aduse uziti Wadala ukanama sikuchedwa kucha

  • @drlifa1588
    @drlifa1588 Před rokem +2

    Koma agalu atonse 😂😂

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 Před rokem

    Malonjozo aanthu andale paradise yanu ndi padziko lino lapnsi basi kwa Mulungu jahena fire waiting for u .Quran said dziko lapnsi lakwanila kukhala jana kwa anthu osaopa Mulungu mmodzi mwa iwo ndi atonse alliance aboma la Malawi ndaona lero after Malonjozo awo

  • @BilaliIshu
    @BilaliIshu Před rokem

    Agalu a anthu awa. afiti awawa ndamene akuononga dziko lathuli. Kubako kukupitilila Bola khale

  • @abdulsalammkwepu3321
    @abdulsalammkwepu3321 Před 5 měsíci

    Nonsenu ndinu mazoba akamazi okhaokha ndipo kwanu kwatha akabawi inu

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 Před rokem

    Iwe galu kwabasi chilima wamva bakili tsungafane naye unambitsa kuba kwakoko umaona kwadzako galu iwe...lero iwe bell yako tsukuyenda mtumba galu iwe chilima ndemvu zoyerazi galu

  • @user-bm8kh9rw6u
    @user-bm8kh9rw6u Před 10 měsíci

    Chonde mukapeza mpata mundipelekele moni kwa chakwela ndi saulosi kuti mboli zawo

  • @chitimbethegreat-pc1bp

    Iwe unena mzako za bello Yako pano ili mthumba chakwera chilima agalu anthu utakhala mowa ndiye wamatokoso kunama kumeneko hell is waiting for you

  • @user-ix4yp5lp8m
    @user-ix4yp5lp8m Před rokem

    Agalu nose mbava inu ndiyeno panopano bwanji?? Komaso Amalawi kutengeka mwachangu

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Před rokem

    Iweyo chilima fertilizer wa k 4 .495 akupezekera kuti ? Nankha iweyo chakwera job 1 miliyoni ziri kuti ? Nankha iweyo chimutu chachikulu chimwendo katangale ukunkanayo katangale wake uti kodi za kubutchary zija katangale apose pamenepo ? Nankha iweyo okuda nkhati kumatako kwakoko ntambo ukundiudza kuti upresidernt ulipowu siwa famiry?

  • @chekiamaabdul5083
    @chekiamaabdul5083 Před 5 měsíci

    mbolo zosadulazo Agalu

  • @user-ri6ed1yk1g
    @user-ri6ed1yk1g Před rokem

    Km chilimayu bwanji osakamnba zoyendesela ziko lino bwanji km busy kunyoza ena yoo km Malawi

  • @benbanda453
    @benbanda453 Před 10 měsíci

    Inu 2025 muzaluza ngati ana oti akufuna kuyamba kukwawa kumene

  • @shideshidex5679
    @shideshidex5679 Před rokem +1

    Listening

  • @chimbamukuka722
    @chimbamukuka722 Před 10 měsíci

    which alliance is coming from God....if I may ask you as MCP -UTM did you give people a cheaper fertilizer and food,,,, All politicians are just the same.

  • @fansciodancun6036
    @fansciodancun6036 Před rokem +1

    Bola muluzi zinthu zimayenda

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v Před 9 měsíci

    Chamba sichabwino, Mtambo & Chilima, Munasutilanji taonani sono mwayamba kuonekera.

  • @gomzmoyo2253
    @gomzmoyo2253 Před rokem

    Koma anagamula mulandu tawakhululukila unatha ali mfulu tsopano tiwone enawa kuti ma belo mthumba azatuluka liti

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw

    Achilima zakusi zanu ...ngati muli ndi umboni okwanira bwanji boma likusowa umboni wa mlandu wa Atcheya inu mulinawo....lero udziwe ichi.Zenje lomwe umakumbira zako umagweramo wekha ..lero ndiwe uli pa bail

  • @user-ol3wb2rd5w
    @user-ol3wb2rd5w Před 9 měsíci

    Devil kuchita quote Bible kkkkkkkkk

  • @derekkolopo1300
    @derekkolopo1300 Před 9 měsíci

    Muzafa ngati gwanda chakwamba opanda kanthu nonse

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 Před 10 měsíci

    Galu wamuthu the whole world ndi chilima kuyankhula ngati waduka muthu lero nayoso akuyakhamilandu yakatangale komaso maboza iyeyo one million jobs yilikuti?? Kudya katatu kulikuti so waboza ndani apo??

  • @mickyhassan3178
    @mickyhassan3178 Před rokem

    Kkkkkkk 😂😂😂🤣🤣🤣koma chilima

  • @user-lp7hw9cs5n
    @user-lp7hw9cs5n Před rokem

    Mpaka lit
    Kodi adadi apanga lit nsonkhano si sizizi ai

  • @HamzaAyame-ch3et
    @HamzaAyame-ch3et Před 4 měsíci

    Yiwe machende ako

  • @laitonkamanga7679
    @laitonkamanga7679 Před rokem

    Pano 2023, azimayi 1million analandira capital kodi, nanga achinyamata

  • @user-et3yo6re6v
    @user-et3yo6re6v Před 5 měsíci

    Kape iwe choka ukuti nyadza pita ukachape kamwa

  • @umaliishumaeli9637
    @umaliishumaeli9637 Před 7 měsíci

    Panyapako lwe galu wa muthu

  • @felixntaika6201
    @felixntaika6201 Před rokem

    Nde lero mbuzi ndindan 🤣🤣🤣 atambo kuda kulibiiiih ndi mtima omwe

  • @Kasawalah
    @Kasawalah Před 3 měsíci

    Apa Malawi wadzadza ndi atsogoleri onama akuba abodza mbuzi za anthu zitsilu agalu

    • @ShabaniKuswere
      @ShabaniKuswere Před 2 měsíci

      Ndipo mbuzi zake osangoti mbuzi Koma mbuzi zamano kunsi

  • @henryibrahimsailes4638

    Osalira munka vota nokha lero ndiizi tinkakuuzani kuti mcp ndiyakupha yankhanza pano kusintha kumene amanenaku ndikuphanaku ndiye pano mukulira kufananso adadi mumawanyoza aja bwa mumawombera mmanja zigawenga inu muluzi anakutsegulani mmasoyo kuti mudzikhala ndi ufulu olankhura munamunyoza ngakhale amakuuzani kuti osazavotera mcp kuyipa kwake amakudziwa anthu osanva inu lero ndiizi ndipo uku ndikuyamba chabe ankakugulitsani fertilizer ndi pakamwa mk4500 koma pano mukugula mk100 + zauzand thumba limodzi ,atupele ndi bambo ake mumawanyoza aja ndiawo sanakwiye nanu anamuperekeza chilimawa ndipo adad wo akuchita bwno kusalankhura msanga pazimene anthu mukukumana nazozo chifukwa ndiinu anthu osanva muphunzire kuti nthawi zina ndibwino kumanva makolo akamakulangizani look now this is just the beginning for mcp izi ndinjoka izi

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před rokem +1

    Anthu Inu Mulungu azakuotchani sure

  • @professorsafuta3936
    @professorsafuta3936 Před rokem

    Mmmm indedi mbudzi ikakodwa amalonda ali pafupi ndithu.eeeeish anthuwa mngodzuwa kunama ndithu.

  • @user-yi8jb2xg7o
    @user-yi8jb2xg7o Před 2 měsíci

    Burundi ngat iwe, ungotiombanitsa mitu bas

  • @user-mb1ly4dv5l
    @user-mb1ly4dv5l Před rokem

    Kupepela amalawi tawonani pano mwaja mwala waukulu olepela kuuswa ndi amala ya yikulu

  • @user-wd7lk7nx7m
    @user-wd7lk7nx7m Před 9 měsíci

    galu iwe osantchula yesu pazopusa zakozo

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 Před rokem

    Chokani apa ana njoka Inu anthu akuba tionana 2025 ino muona nyoooomphamba za kuba

  • @user-uk8sj2vd2v
    @user-uk8sj2vd2v Před 3 měsíci

    Panyapanu agalu inu pano mukupanga cani? Iwenso chilima macende ako

  • @InnocentKapesi-gx7yf
    @InnocentKapesi-gx7yf Před 6 měsíci

    Awa ndi achitsiru chilima

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Před rokem

    Mamvuto okha okha dziko lathu lamalawi palibe wabwino zed pandale angokhala ngati ayao bodza lokha lokha basi

  • @user-ik7fq4ok2r
    @user-ik7fq4ok2r Před 8 měsíci

    Uzipusisa achewa ndi atumbuka zot inu mukuba saakudziwa

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Před rokem

    Chakwera ndi satana mpaka kusiya ubusa ndikuyamba usatanic eeee koma satana akugwiradi ntchito yake

  • @rickiez
    @rickiez Před rokem +1

    Let's we forget

  • @georgemsangu
    @georgemsangu Před rokem

    Koma Dziko la Malawi kaya ndi umbili ndiye Kuti ndichifukwa Chake tizikhumbila anzathu akutukuka

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e Před 6 měsíci

    INU A ALLIES NU NDIYE MWACHITA KUPOSA MBAVA ZONSE ZOMWE ZAKHALA ZIKULAMULIRA MALAWI.😢INE KUKUDABWANI KUSIYA KUTUMIKIRA MULUNGU, NKUKALOWA SATANIC...! God forbid. Koma ku ubusako zimandako bwino bwino? Kapena ndi aja okhalira Kuba cha khumi aja...! Charlatans😢

  • @user-hq3hv5nu5n
    @user-hq3hv5nu5n Před 3 měsíci

    Siku lotenga minyama 😢😢😢😢

  • @mussafrank-ev6zx
    @mussafrank-ev6zx Před 4 měsíci

    Muzayankha kwamulingu time is coming

  • @SharfHanf-pg5wk
    @SharfHanf-pg5wk Před 2 měsíci

    Mwana opanda ulemu iwe, iwe si wakuba?

  • @nellikkmwenda7087
    @nellikkmwenda7087 Před rokem

    Mbuzi iyi

  • @tiwongehojaney5873
    @tiwongehojaney5873 Před 7 měsíci

    kd afolenawa akuti chani ?kutereko ukuwona ngati ungati lamulire kuno kumalawi kuno aiiiii

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před rokem +1

    Lakulemphelani Boma , lamutondani Boma ,Anyamata inu

  • @user-ik7fq4ok2r
    @user-ik7fq4ok2r Před 8 měsíci

    Chilima uzipusisa achawa omwewo

  • @user-nq1pe9ng9m
    @user-nq1pe9ng9m Před 9 měsíci

    Iwe ofoira waononga chilima

  • @user-sq5ms1ne9g
    @user-sq5ms1ne9g Před rokem

    Mukhalila yomweyo anzanu akuchita bwino

  • @ritchardchakuma5725
    @ritchardchakuma5725 Před 5 měsíci

    Masendako wedoda sunanyoko

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw

    Kodi campaign yanu inali against muluzi kapena Atupere kkkkk

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 Před rokem

    THEY GOVERN OUR GRANDFATHER'S GRANDMOTHERS FATHERS AND MOTHERS WE WILL TAKE OUR DESTINY OURSELVES AM GOING TO GOVERN THEIR CHILDREN SO HELP ME GOD

  • @user-rk4ch1ly3z
    @user-rk4ch1ly3z Před 5 měsíci

    Tikumalizani a tonse alliance

  • @wysonwyson7251
    @wysonwyson7251 Před rokem

    Izizi nde zausilu a malawi nafeso ndiopepela kwambili lelo ndi zimenezo agalu achabe chabe

  • @user-vj6mo6qp7r
    @user-vj6mo6qp7r Před rokem

    Galu wamunthu chakwera ndi chilima mbava za anthu mulungu adzakulangan

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363

    Zitsilu izi mmene mukubera agalu inu

  • @MaidakaisiNkota-oo5tz

    Mtambo garu kwabas

  • @ibrahimbamusi109
    @ibrahimbamusi109 Před měsícem

    Mundichimwisa chonde

  • @user-nx2tz8vs5q
    @user-nx2tz8vs5q Před rokem

    Onsewa NDl mbava amalawiwa kaya ndiu mphawi kaya umbuli amaombela mmanja nzopusA zomwe

  • @user-dp3fo7tl8c
    @user-dp3fo7tl8c Před 7 měsíci

    Nanga iwe milanduyo ulibe

  • @professorsafuta3936
    @professorsafuta3936 Před rokem

    Chilima kutha mawu kwambili mmmmm lero si izi hiyaaa