Mbiri ya Bakili Muluzi PART 3

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 25. 01. 2021
  • Anyamata a pa Town PART 1

Komentáře • 39

  • @thembelanithandanani9001
    @thembelanithandanani9001 Před 2 lety +3

    Nice. Big

  • @ericbishopjere4494
    @ericbishopjere4494 Před 3 lety +4

    It's only we poor people who are arrested for small things. My country Malawi mmmmmm

  • @georgemsangu
    @georgemsangu Před rokem +1

    Malawi lizakhala Dziko lochitisa manyazi mpaka Ambuye yesu azabwere.Silixatukuka

  • @hassanj1014
    @hassanj1014 Před 3 lety +3

    Palibe azalowe boma nde osaba ...never ever onse ndi okuba amene analipo alipowa onse mbava

  • @laddinshaibu6932
    @laddinshaibu6932 Před 11 měsíci

    Nice 1

  • @idreeshasheem1518
    @idreeshasheem1518 Před 3 lety

    Where do you get all these

  • @aselomisheck638
    @aselomisheck638 Před 3 lety

    Malawi sadzathekanso basi kudachuluka anthu ozindikira akuba osaukafe tizingolira ndithu ndikumamva mbiri ngati imeneyi😭😭😭😭

  • @umaliisah6920
    @umaliisah6920 Před 3 lety

    We follow u

  • @collengoma6542
    @collengoma6542 Před 3 lety

    Malawi sazatheka chifukwa atsogoleri ndima big crooks

  • @piperharder7436
    @piperharder7436 Před 3 lety

    Ineyo ndikufuna history yanunso ndiyinve ikhoza kukoma kwabasi.

  • @imulandunkeni1226
    @imulandunkeni1226 Před 3 lety

    Next chilima please

  • @aliiizani1260
    @aliiizani1260 Před 3 lety

    Kkkkk zandare dzizidziwa chirimayo ridari bodza aribe umboni akusowa poyambira

  • @paulnkhama3621
    @paulnkhama3621 Před 2 lety

    Pano akudyana ndi chakwera kkkkkkk

  • @charlesmuyaya8839
    @charlesmuyaya8839 Před 3 lety

    Bingu anangommanga Muluzi pa zifukwa za ndale ndi chifukwa chake anasowa umboni

  • @user-rl5zq1qr4d
    @user-rl5zq1qr4d Před 4 měsíci

    😅😂😅😅😅😂

  • @user-rl5zq1qr4d
    @user-rl5zq1qr4d Před 4 měsíci

    😅😅❤😅❤😅❤❤

  • @manfredhillchidomba5090

    Mumakwana bwana pongofufuza tiziva

  • @aubreywallo1987
    @aubreywallo1987 Před 3 lety

    Malawi sazatheka kuba kumayambira kumpando kumwambako mpaka pansi

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 Před 3 lety

    Amene ankapanga zakatangare ndi bakili muluzi ndi nduna zake

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 Před 3 lety

      Olo bingu anali so wakuba moipa kuposa Bakili Muluzi. Kuteroko munthuyu poyamba paja amanena za Kamuzu. Pano umuone wasintha ma video ake akunena kwambiri za Bakili. Tsiku Lina umvera akukamba za bingu. Ungoti pheee udzazimvera wekha mmene bingu anabera ndalama za boma

  • @user-rl5zq1qr4d
    @user-rl5zq1qr4d Před 4 měsíci

    😅❤😅😂😅😂😅😂❤

  • @atusayekamanga3807
    @atusayekamanga3807 Před rokem

    Info mumaigoba kuti biggy🤣

  • @memoryfrancisco6558
    @memoryfrancisco6558 Před 3 lety

    Komanso bingu ankaganiza mwauchitsiru. Anatsegula mlandu wa k1.7 billion alibe umboni okwanira. Akanationetsa ku khothi mapepala enieni oonetsadi kuti ndalamazo zinachokera kwa ma donors.

  • @maryannhuxter1376
    @maryannhuxter1376 Před 2 lety

    zostsapindulitsa izi zinapita pa nthawi yake . munali kuti panthawi yomwe mumaona pamene amaba ? onse adalamulira monga mwa plan yawo

  • @mouricesaidi5348
    @mouricesaidi5348 Před 3 lety

    kodi nkhani Ya George Chaponda ilipati?

  • @francismtawayatv5336
    @francismtawayatv5336 Před 3 lety +1

    I can see kuti muikila kumbuyo bakili muluzi. But still anthu andalewa they are all the same in stealing. Bakili is not a fool kulanda dictator kamuzu boma nde muganiza angamutulukile just as easy as that ataba ka ndalama ka kwacha? He knows how to play the dice well.ma pepala onsewo anawakonza akanali m'boma cos he knew this wil happen

    • @memoryfrancisco6558
      @memoryfrancisco6558 Před 3 lety

      Komanso tiyeni tiyione nkhaniyi posatengera ndale. Kodi a boma akamanena kuti bakili muluzi anaba k1.7 billion umboni wao unali kutiko? Olo atakhala kuti muluziyi anabadi koma chofunikira apa unali umboni kapena mapepala oonetsa kuti ndalamazo zinachokeradi kwa ma donors. Koma to say the truth this case was politically motivated

    • @lastonekaponya7675
      @lastonekaponya7675 Před 3 lety

      Tsongoleri akakhala wakuba anthu akeso amakhala akuba komaso timadziwa kuti achikulirewa ndamene akugubira ku court

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 Před 3 lety

      @@lastonekaponya7675 koma olo amagubira Ku khothi koma a boma analibe umboni. Chifukwa a DPP akanationetsa ma cheque kapena ma list a Ku Bank oonetsa kuti ndalamazo zinachokeradi kwa ma donors. Koma bingu inali mbalame ya munthu ndi chifukwa chake mlandu umenewu ukungoononga ndalama za boma. A boma akulephera kuthetsa mlandu umenewu chifukwa akuopa kuti Muluzi akhoza kukawasumira kuti amulipire ndalama zambiri chifukwa chomuyipitsira mbiri

  • @georgephiri4181
    @georgephiri4181 Před 2 lety

    Chair munthu wamkulu

  • @talimilejosephmakawa4967

    Ndiiwe mbuzi kwambiri umachita kuonetseratu mbali yomwe uli

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 Před 3 lety

      Munthuyu poyamba ndinkamuona ngati wa udf, koma ukamumvetsera bwinobwino udzaona kuti alibe mbali. Zomwe akufotokoza zili ndi ma facts enieni. Za mlandu wa a Muluzi aliyense akudziwa kuti a boma analephera kutulutsa umboni ku court.

    • @kassimjummah3018
      @kassimjummah3018 Před 2 lety +1

      Mbuzi ndiweyo bola ifeyo akutisegula m'maso

  • @francismtawayatv5336
    @francismtawayatv5336 Před 3 lety

    Zinachita kuvuta mwantundu wanj mpaka air malawi kugulisa 4million nyumba?...

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 Před 3 lety

      Mu 2000 k4 million inali ndalama yambiri. 1 dollar inali 100 kwacha, pano 1 dollar ili pa 800

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 Před 3 lety +1

    Biased analysis