Zifukwa zimene A tupele Muluzi wasiyila ndale

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 06. 2022
  • if you like my content and would like to support me further, please
    PayPal
    ➡️To Donate please use PayPal www.paypal.me/hanifamalawi
    Business/Sponsor Inquiries //hanifamw.suggestions@gmail.com
    ATUPELE WASIYA NDALE
    Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) Atupele Muluzi, lachisanu pa 28 May 2022 analengeza kuti Wasiya kuchita ndale mdziko muno. Mu kalata yomwe iwowa analembera mlembi wamkulu wa chipanichi, a Kandie Padambo, a Muluzi aanati aganiza zosiya kuchita ndale ndikukhala mtsogoleriwa chipanichi pofuna kuchilimika pa ganizo lawo lofuna kuchita za malonda zomwe, malingana ndi kulankhula kwawo, ndi zothandiza dziko lino kupita pa tsogolo ndi chitukuko. Anthu ambiri mdziko muno anadabwa ndi ganizoli popeza iwowa anapanga kale dzina mu ndale ndipo anthu amayembekezera kuti adzapikisana nawo pa masankho amchaka cha 2025. Kudzera pa tsamba lawo la pa Facebook, pa 30 May 2022, a Muluzi anatsimikizanso pazakusiya kwawo kwa ndale ponena kuti iwo ndi amzawo ena ochoka mmaiko osiyanasiyana pa dziko lonse, aganiza zoyamba kupanga kampani zomwe zithandize dziko lino kuti litukuke pa chuma.

Komentáře • 23

  • @harrisonmwanga9812
    @harrisonmwanga9812 Před 2 lety +2

    Apa ndiye mwaitha osati kumangobva mau.sanataike ali moyo'waona kuti sadzawinatso mu UDF.zidzingomutaitsa nthawi.

  • @trymoo8479
    @trymoo8479 Před 2 lety +1

    voice sounds like HANIFU

  • @theone7558
    @theone7558 Před 2 lety +1

    How was you balancing your voice? anyway I like your information keep it up

  • @luciuschigoga2607
    @luciuschigoga2607 Před 2 lety

    I like your analysis
    Atupele sold his father's party cheaply
    He really don't know what he wants

  • @hamzysamusoni6655
    @hamzysamusoni6655 Před 2 lety

    Tinakusowani hanif

  • @brendadumisan2526
    @brendadumisan2526 Před 2 lety

    Wachita bwino nanga u President ngati ndiufumu kuti azichita kusiyilana

  • @user-qs3oj7kb5s
    @user-qs3oj7kb5s Před 5 měsíci

    Nahant ikumveka bwino

  • @dytonsaidi9444
    @dytonsaidi9444 Před 2 lety

    Bose mukusowatu bwanji mumangoti ziiiiiii ife timakusatilanitu

  • @binwellchunga4986
    @binwellchunga4986 Před 2 lety

    kodi munthu amayankhula mau yakulu chonchiwa ndimwana oteleyu???

  • @jermahkell8538
    @jermahkell8538 Před 2 lety

    Timamukondabeeeeeeee

  • @daudsagona1952
    @daudsagona1952 Před 2 lety

    Kod chifukwa Chenchn simunatiuze

  • @Andy-mw2on
    @Andy-mw2on Před 2 lety

    Wachitabwino kusiya zankutu basi sakanawinaso amalawi sitingapusisidweso

  • @lucymawindo9283
    @lucymawindo9283 Před 2 lety

    kani hanifa ndiweyo

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Před 4 měsíci

      😂😂😂😂😂😂Pola moto iwe😂😂

  • @meesailikeyougirlmoosa9801

    Wachita bwino kutula pans Atupele saamathandza Mdera lake lomwe ndye upresdent anga wukwanise?? Ndipo iyyeyo amachigwetsera pans chipanicho. Nthawi zonse campaign amapanga nthawi yakutha itha

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 Před 2 lety +1

    Ndi wafodya ngati Bambo ake

  • @waynenyamudo6710
    @waynenyamudo6710 Před 2 lety

    Km ndiye 🤪

  • @brucewarchild2156
    @brucewarchild2156 Před 2 lety +4

    Most boring channel, umaika mutu wina and you talk something else,

  • @sidickbadat1086
    @sidickbadat1086 Před rokem

    Be boring really topical of Malawi 🇲🇼 they make their reporting very long and boring and repeats the same thing over and over.