Mkangano Wa Azikazi Asidik Mia Fatra Ndi Abida Mia

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 07. 2022
  • #SUBSCRIBE #LIKE #HANIFAMW
    FATRA
    Pa 4 February mchaka cha 2021, banja la a Mia kudzera mwa ma lawyer awo Sacranie, Gow and Company analengeza mu newspaper za mdziko muno kunena kuti, potsatira imfa ya a Mohamad Sidik Mia omwe anamwalira kamba ka Covid-19 muchaka chomwecho cha 2021, akupempha aliyense yemwe anali ndi ngongole ya mtundu uliwonse ndi malemuwa, anene ndi cholinga chakuti abweze kapena kubwezeredwa.
    Izi zinachitika pambuyo pakuti a bwalo la milandu amayenera awerenge chuma chonse chomwe malemuwa anasiya. Izi zinapangitsa mkazi wina, Fatra, kubwera poyera mkukasuma ku bwalo la milandu kuti banjali likuyenera kumuwerengera iye kukhala olandira nawo chuma cha a Mia popeza iye anali mkazi wawo wachiwiri.

Komentáře • 14