Hanifa Mw
Hanifa Mw
  • 326
  • 7 757 500
KUKHALA CHETE KWA A CHILIMA PA A CHAKWERA
A CHILIMA ASANKHA KUKHALA CHETE PAKULENGEZA KWA A CHAKWERA KUTI AYIMANSO
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima asankha kukhala chete pakulengeza kwa a Lazarus Chakwera amene ndi mtsogoleri wa dziko lino kuti adzayimanso pa masankho a chaka cha mawa kumachita kuti mgwirizano wawo wa Tonse umakamba kuti amene akuyenera kudzayimira pa masankhowo ndi a Chilima. Atafunisdwa lachisanu lapitali kudzera pa makina a mchezo a Whatsapp, a Chilima anangoyankha kuti palibe chimene angayankhule. Izi zikudza a Lazarus Chakwera pa 30 May 2024 atayankhula pa msonkhano wa chitukuko umene anachititsa m’boma la Lilongwe kuti adzayimira chipani cha Malawi Congress (MCP) ngati mtsogoleri wake pa masanh akubwera chaka cha mawa cha 2025.. Msonkhanowo kunali kukhazikitsa gawo lachiwiri la ntchito zachitukuko za Millennium Challenge Corporation (MCC).
zhlédnutí: 23 086

Video

AMUPHERANJI CHILIMA ? IMFA YOWAWA YA SAULOS CHILIMA
zhlédnutí 39KPřed 21 dnem
A CHILIMA AMWALIRA PA NGOZI YA NDEGE Dziko la Malawi lili pa chisoni chachikulu pamene nzika zake zikulira kwambiri kamba ka ngozi ya ndege imene yatenga miyoyo ya anthu asanu ndi anayi (9) amene ndikuphatikizapo wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Klaus Chilima. Ndegeyi imene inanyamula anthuwa inagwa dzulo pa 10 June 2024 ku dera lotchedwa Nthungwa mu nkhalango ya Chikangawa m’boma...
KWABVUTA IMFA YA SAULOS CHILIMA IFUFUZIDWE
zhlédnutí 48KPřed 21 dnem
KWABVUTA IMFA YA SAULOS CHILIMA IFUFUZIDWE
'AMANDIYAMWISA MALISECHE DAILY '- MMWENYE AWUZA WA NTCHITO ADZIMUYAMWA MALISECHE
zhlédnutí 52KPřed 28 dny
MMWENYE AWUMIRIZA WA NTCHITO KUTI AZIMUSEWERETSA MALISECHE Kupeza ntchito ndi chinthu chokoma kwambiri kwa munthu aliyense makamaka uyo amene wakhala nthawi yayitali akuyisakasaka ndipo ali ndi anthu amene amadalira iyeyo monga makolo, ana komanso mkazi. Pamene munthu wapeza ntchito ndiye kuti amakhala ali ndi chiyembekezo chachikulu kuti zinthu zake zisintha ndipo amene amamudalirawa ayamba na...
Nkhani Yomvetsa chisoni Nyamata waphedwa Chifukwa Cholowa m'munda
zhlédnutí 23KPřed měsícem
Nkhani Yomvetsa chisoni Nyamata waphedwa Chifukwa Cholowa m'munda
zionetsero Za Polisi Ku Blantyre
zhlédnutí 12KPřed měsícem
lero Kunali zionetsero Za Polisi Ku Blantyre
Mabvuto Kokhwima
zhlédnutí 6KPřed měsícem
Mabvuto Kokhwima
MOYO WOMVETSA CHISONI WA GEOFFREY KAPUSA MR SPLASH
zhlédnutí 7KPřed měsícem
MOYO WA GEOFFREY KAPUSA MR SPLASH Mu chaka cha 1998, dziko la Malawi linayamba kukhala ndi television yake yoyamba imene inali ya boma. Television inatchedwa kuti Television Malawi kapena kuti TVM mwachidule ndipo inayamba ngati project imene mkulu woyambilira anasankhidwa kukhala a Benson Tembo. Ngakhale kasanjidwe kama programme komanso awulutsi ake anali ngati ongoyesera, mu gulu la anthu og...
Mutharika Ndi DPP Anaimitsa Dziko | Umu ndi m'mene zinalili
zhlédnutí 15KPřed měsícem
Mutharika Ndi DPP Anaimitsa Dziko dzulo | Umu ndi m'mene zinalili Blantyre
MCP Kumangochi Yayaka Moto
zhlédnutí 6KPřed měsícem
MCP Kumangochi Yayaka Moto
EXCLUSIVE: Interview With Zacc Kawalala
zhlédnutí 7KPřed měsícem
EXCLUSIVE: Azibutsa Ayamba Kutisambira Manja za Chakwera Ndi Tonse
Fredokiss Ndi Felix Njawala Speech ''UTM SiYaPa Facebook Mulira Nayo"'
zhlédnutí 8KPřed měsícem
Fredokiss Ndi Felix NjawalaPa Msokhano wautm
UTM Yasambwaza Peter Mutharika Ndi Mayi Joyce Banda
zhlédnutí 9KPřed měsícem
UTM Yasambwaza Peter Mutharika Ndi Mayi Joyce Banda
Milandu Yakuba Ya Saulos Chilima Yatha
zhlédnutí 6KPřed měsícem
CHILIMA ALIBE MLANDU POTI BOMA LATHETSA MLANDU WAKE Malamulo oyendetsera dziko lino a Constitution, Section 99 (2) imamanena kuti, mkulu woyimira boma pa milandu kapena kuti Director of Public Prosecutions (DPP) ali ndi mphanvu pa mlandu uliwonse umene ukuzengedwa ku mabwalo amdziko muno kuti akhoza kuwuthetsa kapena kuwuyimitsa mmene akufunira, chigamulo chisanaperekedwe. Section 77 (1) yakaye...
Milandu Ya chilima Yatha | Kaliati Ndi khwimbi La UTM kusangalala ''Athyola dance''
zhlédnutí 14KPřed měsícem
Patricia Kaliati Ndi khwimbi La UTM kusangalala ''Athyola dance''
Nawo Osatira Chipani Cha UTM Akulira
zhlédnutí 6KPřed měsícem
Nawo Osatira Chipani Cha UTM Akulira
Akulu Akulu Achipani Cha UTM Kuyankha Mafunso Pa Hanifa tv
zhlédnutí 12KPřed měsícem
Akulu Akulu Achipani Cha UTM Kuyankha Mafunso Pa Hanifa tv
Zomwe Wayankhura Patricia Kaliati Zadabwitsa Anthu
zhlédnutí 43KPřed měsícem
Zomwe Wayankhura Patricia Kaliati Zadabwitsa Anthu
Nawo Achinyamata A MCP Akulira
zhlédnutí 9KPřed 2 měsíci
Nawo Achinyamata A MCP Akulira
Tamvani Zomwe A kuyankhula Za Kondwani Nakhumwa
zhlédnutí 20KPřed 2 měsíci
Tamvani Zomwe A kuyankhula Za Kondwani Nakhumwa
Zinthu Zikungokwera Monga Mwa Dzina Lawo
zhlédnutí 7KPřed 2 měsíci
Zinthu Zikungokwera Monga Mwa Dzina Lawo
Part Two: Dr Cassim Chilumpha | Kung'alula Chilima Ndi Lazarus chakwera
zhlédnutí 33KPřed 2 měsíci
Part Two: Dr Cassim Chilumpha | Kung'alula Chilima Ndi Lazarus chakwera
Tamvani Zomwe MCP ikubweletsa Ndi Kukhazikitsa
zhlédnutí 4,6KPřed 2 měsíci
Tamvani Zomwe MCP ikubweletsa Ndi Kukhazikitsa
Zomwe Wayankhula Fredokiss Zakwiyitsa Andale Mdziko Muno
zhlédnutí 18KPřed 2 měsíci
Zomwe Wayankhula Fredokiss Zakwiyitsa Andale Mdziko Muno
Akuti MCP iwinaso 2025 Zifukwa Zake Nazi
zhlédnutí 2,8KPřed 2 měsíci
Akuti MCP iwinaso 2025 Zifukwa Zake Nazi
Brian Banda Chikuvuta Mdziko Muno Kwenikweni Ndi Chiyani
zhlédnutí 12KPřed 2 měsíci
Brian Banda Chikuvuta Mdziko Muno Kwenikweni Ndi Chiyani
Mavuto Achuluka, Mdziko Muno Zinthu Sizikuyenda
zhlédnutí 4,2KPřed 2 měsíci
Mavuto Achuluka, Mdziko Muno Zinthu Sizikuyenda
Fredokiss-Andale Akunamiza Achinyamata
zhlédnutí 2,5KPřed 2 měsíci
Fredokiss-Andale Akunamiza Achinyamata
Chipani cha ADD chakonzeka kugwetsa Lazarus Chakwera
zhlédnutí 5KPřed 2 měsíci
Chipani cha ADD chakonzeka kugwetsa Lazarus Chakwera
Zodabwitsa Zimayi Uyu Watutumusa Gulu -''AKUMASHANTAH''
zhlédnutí 9KPřed 2 měsíci
Zodabwitsa Zimayi Uyu Watutumusa Gulu -''AKUMASHANTAH''

Komentáře

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 4 hodinami

    Chinali chiwanda

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 4 hodinami

    Eh

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 4 hodinami

    Iweyo easy come ndonwe imakupwwteka kusavera lamulo la Mlungu loti udzadya thukuta lako umafuna kudya mofewa motsatulutsa thukuta (ulesi)apo waiwala Mlungu size yako

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 4 hodinami

    Ku mpoto nde kuli ufiti wa serious akapha akapha anthu aphabasi tsamauka ku manda pamene kumwela amauka kumpoto kuli ufiti oyipa!anthu ambiri kumwera akumauka ku mpoto zero🙄

  • @AndyGama-m3u
    @AndyGama-m3u Před 11 hodinami

    Ayi wachitola chikwama Nanga ma million onsewo pajatu ndalama zilimunyasi

  • @IshmaelSaidi-f8l
    @IshmaelSaidi-f8l Před 22 hodinami

    Chiwanda chimenecho

  • @AngelaMhango-c2i
    @AngelaMhango-c2i Před 23 hodinami

    Izooo

  • @eliaskachali-xn2ve

    Chakwera ndiwe wakuba pa thako pako, niwezgere ndalama Zane nkhuyiwona ya passport yane

  • @Aisha-db6ds
    @Aisha-db6ds Před dnem

    Atsogoleli ake opanda mfundo

  • @YONA-v5o
    @YONA-v5o Před 2 dny

    Nde inuyo aku banja munthu woti mmakhalanaye simnamu fananitse ndamene anamwalilayo

  • @YONA-v5o
    @YONA-v5o Před 2 dny

    Nde inuyo aku banja munthu woti mmakhalanaye simnamu fananitse ndamene anamwalilayo

  • @tiwongehojaney5873
    @tiwongehojaney5873 Před 2 dny

    Tangomugululabi mpezi ameneyo

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx Před 3 dny

    koma dzikoli ndi lanthu olemeradi et? mpaka munthu kuba chinthu cha office ya boma mpaka kurephera kumulanda???? mukutiseweretsatu makosana😂😂😂😂😂

  • @MatumeMkhondo
    @MatumeMkhondo Před 4 dny

    Mzimu wawo ukawuse mutendele

  • @HassanCharle
    @HassanCharle Před 5 dny

    Mbambande amalawi mumakwana

  • @HassanCharle
    @HassanCharle Před 5 dny

    Km sili bwino Pamenepo galu ameneyo achijapulapo chifukwa chakwera ndi mbuzi galu yachabechabe

  • @LovenessLester
    @LovenessLester Před 5 dny

    That's a great city for many Malawians let's learn how to appreciate this our man of God 🙏

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 5 dny

    Lazy people lovers of miracle money will always have negative minds against trueth👹👺👿

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 5 dny

    ,,,😂😂mzimaiyo akunama amafunanso nae amagwilidzana naeso akufuna chipepetso eti 😂😂😂😂🤸🤸🤸🤸🤸

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 6 dny

    Inuso asilikari musati bowe manyi anu mulibe chisoni ndi Amalawi

  • @KimamboPk
    @KimamboPk Před 6 dny

    Zam'Zam'masiku omaliza no wonder

  • @JosèFelixsailessFelixsailess

    Zoipatu zimenesi

  • @JosèFelixsailessFelixsailess

    Zoipatu zimenesi

  • @BarnabeMacuane
    @BarnabeMacuane Před 6 dny

    Ndikupemba mamba ya profit ine Kuno ku mozambiaue

  • @ChadichadinjanjeNjanje

    Zohona anaphedwa ndi nzake amene Ana mukongola mavoti yake

  • @DorrahBanda
    @DorrahBanda Před 7 dny

    Osauka tilipamavuto mabwana ndimfulu olo atalakwa chotani samamangidwa km mulungu nfiye mwini zonse

  • @FatimaRehemah-gi4mp

    ma gay achimwenye🤨🤨🤨

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 8 dny

    Kupusa bwanji samakadandaula ku ma bungwe ndi opepera

  • @GeraldJairos
    @GeraldJairos Před 9 dny

    Zochitika m'masiku otsiriza machenjera amdyerekezi Osakhulupira kwa tonse owerenga tiyeni tikhale mmaso,wakufa sadziwa kanthu bii

    • @GeraldJairos
      @GeraldJairos Před 9 dny

      Kodi inu bambo osapeza mkazi wina,ndikupemphera ,ngati mutachita bwino nkudzakumana ku ulemerero wa mulungu

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Před 9 dny

    Ndipo chitukuko chikuwakanika akurimbana nikupha anthu

  • @user-rc8ze8do7e
    @user-rc8ze8do7e Před 9 dny

    Kkkkkkkkkkk sister laz ndwe kangenge

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x Před 9 dny

    Kkkkkķkk km ku malawi kokoma😂😂

  • @HamzahBandah
    @HamzahBandah Před 9 dny

    Mundipaseko nambala ya aprophert akulilongwe ndikuwafuna aprophert andithandoze

  • @IdrissahSadick
    @IdrissahSadick Před 9 dny

    That's just jiin

  • @user-kk5br9vm9u
    @user-kk5br9vm9u Před 10 dny

    Nyimboyi ikunena zoona ndipo munthuyo sakunama koma nkhani ndiyakuti billy ponena bakili anaikapo nkhope yake naeso ngati amafuna kunena achakwela akanaikaso nkhope yake

  • @OjesYahaya-zl4rx
    @OjesYahaya-zl4rx Před 10 dny

    Athu akumwalila zimpatalamu kamba kosowa Panado ndiye Muthu mozi ndalama zosezo kusonyeza kuti miyo yanuyo ndiye yofunikila mumwalilabe mutisiya aphawife mulungu sowona chuma

  • @fredlemani
    @fredlemani Před 10 dny

    Anali yemweyo kapena ayi? Nkhope imasiyana bwanji? Mprothet ameneyo anamutumiza Mulungu kapena ndani? You and your prothets are fools and you don't know God.

  • @EthelLimited-bo5ey
    @EthelLimited-bo5ey Před 10 dny

    😂😂😂😂😂😂

  • @HellenGondwe-d1g
    @HellenGondwe-d1g Před 10 dny

    Mpaka Chaka kumalorera zimenezo mavuto ake amtundu wanji

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Před 10 dny

    .musiyen waimbayu Ali ndi luso.nyadilan bro billy

  • @user-qb2lt6qj1p
    @user-qb2lt6qj1p Před 11 dny

    Palibe chomwe chikuveka

  • @user-ot6jv1gj9w
    @user-ot6jv1gj9w Před 11 dny

    Nkhani sikunvekatu ife timaona ngat muli ndi umboni kuti anayenda bwanji.

  • @FinishB
    @FinishB Před 11 dny

    Zonse aziwa ndi mulungu siyeni muthu

  • @IqrahSikweya-wm5mn
    @IqrahSikweya-wm5mn Před 11 dny

    Bodza.... Mzosatheka munthu kufa mkuukanso...... Anali asanafe ameneo

  • @LisaMwemba
    @LisaMwemba Před 11 dny

    We need to see her face why don't you show her face?

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Před 11 dny

    Bushiri uzangokhara president

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Před 11 dny

    Akurephera chakwera kutukura ziko.rino angoononga ndarama chakwera chito zamanja ako zikuchitire umboni bushiri

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika Před 12 dny

    Ukalemera ndiwe wa satanic ukasauka mphawi iwe amalawi amafuna chani

  • @mercynamangale98
    @mercynamangale98 Před 12 dny

    Aaaaaa zauchitsiru basi,amangidwe ameneyo basi

  • @WhiskyMiti
    @WhiskyMiti Před 12 dny

    God is greater than all,