Brian Banda Chikuvuta Mdziko Muno Kwenikweni Ndi Chiyani

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 27. 04. 2024
  • Bian Banda Chikuvuta Mdziko Muno Kwenikweni Ndi Chiyani

Komentáře • 40

  • @mussahkachere2332
    @mussahkachere2332 Před 2 měsíci +5

    Program iyi ilibwino kwambil 100%, pitilizan ndthu kutisangalasako🎉🎉

    • @mussahkachere2332
      @mussahkachere2332 Před 2 měsíci +2

      Ithink mutamupangaso include Mr bon kalindo ma program ngat awa zitha kukhala bwino

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l Před 2 měsíci

    Asogoleri bakili kuba, peter kuba, joyce banda kuba and Chakwera kuba... Vuto ndi kuba basi

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 2 měsíci

    Mr Banda number one

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson Před 2 měsíci +1

    Kuyakhula ❤❤kwabwino

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b Před 2 měsíci +1

    Komanso maakitivisiti akutengapo mbali poononga dziko monga anthu awa ntambo Ben longwe munlo layitoni akumabwera ndi zina loti oyimira wanthu koma lero onse akubakira boma chifukwa chadyera maakitivisitinso nkhati awa akutengapo mbali poononga dziko .

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 2 měsíci

    Kuyankhula kwa bwino ❤

  • @ThokohKalonga-je9rx
    @ThokohKalonga-je9rx Před 2 měsíci

    Ilibwino program Mr pitilidzani

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b Před 2 měsíci

    Umoyo wamunthu simasewera zimafunika kulimbikira paiye yekha koma idzi zoti boma aziyenda ndi matisheti ndi kaufa nkamagawa ndizosathandizika chomwe chikufunika kusegula makhomo omwe asekeka andalama ziseguke mabizinesi awanthu aziyenda aliyense azitha kuzipangira paiye yekha

  • @BrianMasiyakurima
    @BrianMasiyakurima Před 2 měsíci +1

    Yohane kuchokela Ku thyolo Maganizo anga ndi oti ziko la Malawi silizatheka chifukwa andalewa ukungopanga za mimba zawo osakhala kutumikila anthu plus dyela yawachulukila

  • @charleskunjawa6999
    @charleskunjawa6999 Před 2 měsíci

    Where was this

  • @PromiseMankhwa-cr5mw
    @PromiseMankhwa-cr5mw Před 2 měsíci

    Kod ku Lilongwe tipanga liti program iyi ndi 100% ndithu

  • @TrinityManeya
    @TrinityManeya Před 2 měsíci

    Brain your a great dada

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 Před 2 měsíci

    University graduates you’re looking for other people to employ you instead of you to be the change that you need by creating those opportunities

  • @yusufrasheed3646
    @yusufrasheed3646 Před 2 měsíci +2

    Kom yah

  • @user-qw4pk7wj8i
    @user-qw4pk7wj8i Před 2 měsíci

    Kom Mumbai's inayi kkkk ndaiposa kkkkkk kuchita represent kkkk

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw Před 2 měsíci

    ing`ambeni bg

  • @user-bl6km6kx7n
    @user-bl6km6kx7n Před 2 měsíci

    mzofunika mwayambazi zikanakhala bwino kupanga madela ambiri ndi mchimidzi

  • @user-sb6by9sq5n
    @user-sb6by9sq5n Před 2 měsíci

    Programu ili shrp

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw Před 2 měsíci

    Takuthokozani kuti mukufufuza maganizo awanthu mupitiĺize

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d Před 2 měsíci

    Koma molaro omangopanga paliposewo ndie kusokonezako ngati program ili ya for good izi ofundika muziunikilepo

  • @Yamikaniwalasi
    @Yamikaniwalasi Před 2 měsíci

    Shaya

  • @lusolawo73
    @lusolawo73 Před 2 měsíci

    Best TV

  • @user-ce6hy6tp7e
    @user-ce6hy6tp7e Před 2 měsíci

    Kunena zoona chakwera uyu sakufunikira, komaso ngati iyeyo ali ndi nzeru akanangosiya osaimaso watizuza mokwanira ife amalawi apite uko mwana wa satana mbusa waboza,ine Doreen kuchokera kuno ku South Africa krugersdrop

  • @user-nw6ie3xx8b
    @user-nw6ie3xx8b Před 2 měsíci

    Koma a brayn mwayamba ndale?

  • @lawrencewyson8229
    @lawrencewyson8229 Před 2 měsíci

    Ash

  • @UsumanLuwayo
    @UsumanLuwayo Před 2 měsíci

    Ku poly chidzungu chikuwadzungulira eti eish

    • @ChifuniroKapinama
      @ChifuniroKapinama Před měsícem

      Not ku poly but some anali maperi amangonama kut ndi akupoly

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089 Před 2 měsíci

    Koma kulemba ntchito anthu opuma kale koma chakwela

  • @ibrahimkazembe4363
    @ibrahimkazembe4363 Před 2 měsíci

    So sad that the student from university could not express herself in English. What example are we giving to those who aspire that one day they can go to the place of high education in Malawi.

    • @chesterphiri7523
      @chesterphiri7523 Před 2 měsíci

      I observed that and I was just scared to mention it.

  • @RCFAKI-mx4dv
    @RCFAKI-mx4dv Před 2 měsíci

    Hy

  • @estherkambewa7791
    @estherkambewa7791 Před 2 měsíci

    Gonjetsani adani athu, njala,nthenda, nsanje

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Před 2 měsíci

    Program ipitilire ilibho kwambili

  • @MustafaLikaomba
    @MustafaLikaomba Před 2 měsíci

    Muuzene chakwela yo wamamina mmutuyo choopanda mzeru choongolamulidwa ndimwanawakwe

    • @Pangolinimw
      @Pangolinimw Před 2 měsíci

      😂😂😂😂😂

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td Před 2 měsíci

      Akulu inu ndinu oipa mtima msanje sipindula yeserani Zanu tikuoneni Malawi is open for everyone chakwera anayesa zake zidayenda kwatsala iwe wa msanje we Moyo kuwawa tisatero tichedwa adaaaa voterani adad musiyeni chakwera zake zinayera kale

  • @user-ss9sr7bi6f
    @user-ss9sr7bi6f Před 2 měsíci

    Kuti uku

  • @BrianMasiyakurima
    @BrianMasiyakurima Před 2 měsíci +2

    Ine yohane bobo kuchokela zinda uno wa Durban maganizo anga ndioti bwana brayan zinthu sizikuyenda pa Malawi vuto ndi usogoleli womwe tili nawo kmaso chondidabwisa kuti avomeleze kuti zinthu zawavuta ndipanene akufunaso kuti ayime dye zosatila zake mavuto azipitililabe