Hilco and Ching'axy - Provoke Provoke ( Plan B Season 1 Episode 2 )
Vložit
- čas přidán 7. 03. 2024
- Get Wakuba Audio 👇
open.spotify.com/album/6Nopi5...
Get Wakuba From A store Of your choice 👇
fanlink.tv/vz6z
Watch Pemphero ft Sangie 👇
• Hilco feat Sangie - Pe...
Get My E.P Maluwa 👇 open.spotify.com/album/7Dpfql...
---------------------------------
Follow Hilco
TikTok : / hildaulolo
Instagram : / hilcomw
Facebook : / hilcomw
#hilco #ching'axy #wakuba #ponit #malawi #trending #maluwa #hilco #ching'axy #planB #malawi #comedy #trending - Hudba
😂😂😂😂 Fanz yaching'axy ibwele pano tipatse moto🔥🔥🔥👍
provoca basi
😢❤😮😮😮@@vincentngulube2300
Nice 👍👍 well done 👍👍✅
Wow that's awesome 👍
Fans ya Hillco bwelan pano tiipatse moto pa modzi ❤🎉
Ife ai😂😂
Tilipo tiyipasa moto
mkazi winayo ..amanga hilco kumutu she is too emotional ...akufunika traning yabwino ...
Eeeh komano ching'axy amatha ma guy eeeh 😂😂 🔥 🔥
Next plz
Ndipo ndi dolo kwambili
Ine ngat ndingalembedwe ntchito tuu kumeneko ndiyonkhala ndi Hilco yooo 😂😂😂😂😂 ching'axy fire 🔥🔥🔥🔥
🙌🙌😂
😂😂😂😂😂
Ching'axy ma award onse mpaseni 😂😂😂
Ndi a usiku omwe😂😂😂
Hahahahahahaha kofunsira banja kuja akufunsirakonso ntchito ,mpaka kulira.
Ndpo kufusila kuja osazapwekesa ndi ntchito yapadera.
Zili bwino keep it up chings
The prove mode.😅😅🔥
Was everything
Ati " look at Mr spider 🕸 " koma @ching'aning'an you are the best Comedian in Malawi 🇲🇼.
Ati look at Mr Spider 🤣🤣🤣
😂😂😂
😂
Ching'axy n Hilco mumatha inuyo 😊😍
Paliponse pakungosekesa ndiye nkuyambila pati kusekako 😂😂😂 ching'axy anaza 😂😂😂😂
Koma Ng'axy😂😂😂😂😂😂😂 Hilco keep the fire burning, I have laughed today lol😅😅😅😅😅😅😅😅
Kufunsira kuja ndikovutaa😂😂😂😂Ine umbon ndili nawoooo😂😂😂
😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂
Agwilisa
Makhwala
Fire 🔥 🔥 🔥 mabomba ching'axy n Hilco
Hiluco ndimokonda❤
Umakwana ching'axy ati muzipempha appointment 😂😂😂
Kkkkkkk Mmmm chinga`aning`ani unapitililila pokwana I can't wait for episode 3 Guys chonde pasamatenge nyengo yaitsli musanatuluse kena mix mukutisiyila nmalere anyway more fire
@@AungunKadzinja-wv2uc kod part 3 sibwela
If you see this comment in 2063 know that I was watching this in 2024 while smiling 😀
Am gonkoko😂
2063 youtube kuzakhala kulibe aise
kkkkkkk guys
😂😂@@mlimolubanda6348
Ndipo it was fun
Ching'axy matama onse aja mwafunsilako ntchito 😂😂 zoti akulolani zikukaikitsa
I love this...mayi ching'axy
Thanks for the feedback
Zabhob
Hello
Wow this is so great guys😂 Km Ching'axy😂😂😂
Ndungoseka ine kuno iiih. Ching'aning'ani ndi dolo eeeesh 😂😂😂🙌🙌🙌🙌
Adha awowo operekeza ching'axy, a very good actor
Wangoyamba kulira chingaxy po mmene ndasekera ine😂😂😂😂komatu mwaikometsa musachedwe ina changu❤❤
Makina pa macheza ❤😂😂😅😅
Ching'aning'an nikatundu pa plan b😂😂😂😂😂
Provoke provoke 🤣🤣🤣🤣🤣 kma yeah 🙌
😂😂😂Ayi ndithu. Zoti kufunsila kumavuta Ndaonela pa ching'axy😂🤣 Ayi ndithu. May God be with you and Gate be with me😂😅🤣
Mukafika pamalo muzifika bwino guyz
God be with you & Hilco be with me... koma ching'axy 😀😀😀
Koma ching'axy osa give 😂😂😂😂😂
Kuyipasa moto chinga'axy😂😂😂😂
Yomweyo 😂😂😂
😅😅😅😅 bwana ching'axy ati mkazi uja ndagwira.... My me
Wow! I've enjoyed it. Can't wait for the next episode. 🥳😋
Ndi Ambuye indeed 🔥 from the song in the background.
Ndaseka paka misozi
Kikkkk,, ati mukhala pa pay slit 😂😂😂 Ching'axy 🔥🔥🔥🔥
Kkkk for those watching in 2080 remember that I shall be in the grave then
Alimi ndasiya kucheza nawo 😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂 km yaaa
💥💥💥💥💥 Umakwana m'dara wazimagwelu 😂😂👏😂😂
Kkkkk ching'axy @ wasiya kucheza ndi alimi
🤣🤣🤣🤣 aaa nde amabwera kuzagwila ndi wina iwe ukulepheera choncho
😂😂😂😂 more fire mr chi ng'ax
Ching'axy anabwela kudzakhala😂😂😂😂
Kali bho😂😂😂 can't wait next ep
Nyc nyc nyc ili mwala hvy
Hahaha koma iwe
Kofusira banja mpaka kulira mwati muloredwa inu😂😂😂😂🙌
Komatu umatha hilco
Vuto la ching'ax ndilimenelo osangopita pa mfundo bwanji😅😅😅😅😅😅😅
🔥🔥🔥🎉🎉🎉🎉
God be with you Hiloc be with me 😂😂😂🔥🔥🔥😊
😂😂😂😂😂Atii muzibukatu ma pointment 😂😂😂 ndie dzakeyo atii ndikukupatsatu 10 minutes ndikuonera😂😂😂😂😂
Akuti kusakhulupilira ngati Thomas didimu kuti misomali inayenda bwanji 😂😂😂😂
bwana ching''axy kkkkkk nice one
Wow that's great 🎉
Ching'axey tsopano
😂😂😂 can't wait another part
Kufunsira mkovuta😂😂😂
Kofusira hilco chibwez wakafusira tchito 😂😂😂😂Kom ching'ax
Ching'asy aise 🔥
More fire 🔥 keep it up guys 🥇
Provoke, provoke😂😂
Ching'axy nd GOAT 🐐🔥🔥🔥
ching_axy his always make crazy....... big up to hilco and them
Satana amatha kukhara Nanu pafupi Koma inu simudziwa😂😂😂
Koma guys eeeeeh....mwabweratu, big up.
Ching'axy unaza ndiwe G.O.AT🤣🤣🤣🤣🤣
umakwana ching'axy
😂😂😂 koma provoke provoke unabwela 🙌
Uyu kukhomelela 😂😂😂😂more 🔥🔥💯♥️♥️
Ching'ani ng'ani 😂😂😂❤❤
Mbambande
😂😂😂😂😂Ching'axy wasiya kucheza ndi alimi 😅😊
Kkkkkk mwagwila ntchito mwina ntchito ching'axy kkkkk😅😅
Tomasi didimu😅😅😅😂🎉😂
😂😂Koma a ching'axy kumuwalira mzanu choncho ngt wagwiraditu🙌
Kkkk zina umangoona waziyamba❤❤😅😅
😂😂😂😂😂😂 Ching'axy ndi one
I can't wait, next 🤣😂🤣
😂😂😂😂😂😂😂 walira Mwana wamwamuna
God be with you, hilco be with me 🤣🤣🤣🤣
Kod inu mukuyakhula bwanji 😂😂😂
kkkkkkkkkkk koma yeeeeeeeh apa wabwera hilco ndi nzako ching'axy
😂😂😂😂😂 Koma mfundo kubakalika hahaha
Kkkkk nice
Ching'azy tsopano wabwera ndi fire 🔥🔥🔥💚 ipitilize mission ilibwino hvy
I love seriousness in all the actors 😂
Mabwera ngati coming
😂😂😂😂😂 ayaaaa
Fanzi ya hilco bwelani tiyibongese🔥🔥🔥🔥😄🤣😂
Amayi anga❤
Zikooomo chingang'axy potisekesa 😫😅😅😅
Zina umangoona waziyambadi 😂😂😂😂
ching'anxy kkkkkk ugalu wako manthano🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂Ching'axy anabwera💥💥💥✌
Aweso boza
This is great
Opemphappha😂