Velikost videa: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Zobrazit ovladače přehrávání
Automatické přehrávání
Přehrát
Apapa chemandota uyembekezere kubetsa 50pin kwachiphwanya😂😂😂😂 paja udamukanika atabwera kwanu kkkkkkk wakupezera plan aise😂😂😂😂😂
I love your comedy All the way from Ethiopia even i don't listen your language
I will be teaching you 🎉
Kkkķkk mandota umakwana komano achiphwanya pena palipose aaaaaaaaaaaaa inuyo umngakwatileko😂😂😂😂😂
Am the first to view 😘😘
These two ndi ma best comedians in Malawi🤣
Kkkkkkkkk
Kungokhala ngati ma asikono ndimanganya kkkkkkkk
😂 😂 😂 😂 Ka elisabefi kadyatu basi mudya.
Chiphwanya wasewera plan B kuti apeze 50 k ija 😂😂,wangopangana ndi ma chick wo🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣🤣🤣apa 50pin ipitadi Basi,,, wakupezera plan chiphwanya🤣🤣🤣🤣
I am the first person to view 🥳🥳
I like your comedy che mandota❤
Your number 1we like your comedy
Komatu amayili simukutionesa ngati a Sikono bwanji kkkkkkkkk.Kungoti a Mayili akiya nyumba Basi osaona mmene abwelela Aaaaaaa sinthu zake.But u are the best
Like this comedy
Sending loves ❤️❤️
Number ya Ma maili taponyani che mandota amandiwaza😋😋😋😋😅😅😅
Chiphwanya ndi matchini mandota kupeleka mosavuta chuma kkkkkkkkkkkk
Nice
Keep the fire burning.... Che Mandota timakunyadirani .
Chemandota please upole moto wati nkatimu mumaoneka ngati chiyani ? Kkkkkkkk ayi dzikomo mandota muuze chipwanya andipase nkadzi mmoziyo maka uyo akupita kwa aunt kkkkkkkk nankha awiri yekha aaaa
Mtunduka🙈.....bwelani musatenge mkasi
Amwene mandota inuo mumatha much love from this side machinga T/A nyambi makwana
Ndipo ma mayili muzangokwatirana ndi Chelindotawo basi kkkkkkk mukumaitha you two are best
Mkatimu ndiye mumawoneka mtumbuka mtumbuka 😂😂😂
😂😂😂😂😂mwadzaaa
You never disappoint
🙌🗣️🤣🤣🤣Chemandota fire
Umakwana kwambiri brother
Kutengeka akulu inu kkkkkkk km mwammanatu nzanu 50pin zikutsalira kuteleku
musapeleke 50 pin mubeledwa. keep it up guys
Fire ndox
A che mandota you always makes my day
Akupusisa ase....dollar ija upereka usakuziwa kuti akuponda😂😂😂😂😂🙌
Good combination
ukutha aise....u will go far
Iyiyi mwapha guys eiish kkkkk
Kkkk mumativesa kukoma pakhani zama drama
Chemandota ndi chiphwanya kkkk, koma akangodziwa ma Maili akupha kkkk, mandota ndi maMaili munachokera patali, timakunyadirani
I like you guys 😅😅😅
Kkkkk koma very impressive
Amayi amayiliiiiii🙄🙄🙄🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 We want to see mayiri please 😂😂😂😂😂😆
Me 2 wooooo
50 pin ija mukafupatu kwa anthu oti anagwilizana zochita awa kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkk chiphwanya kupeza dollar mosavutatu uku
Guys ndafwa ndi mpwetee😍 😘 🦋 😍 😘 🦋
I like your composure in this one.
You know how best to make us laugh 😄
Waberedwa iwe basi
Ineso ndiseke ki ki ki ki ki
Kkkkk ai nditu umatha iweyo
🤣🤣🤣🤣🤣🤣Your super star my brother
Nkhan ndi tiktok tili pano kudikila part 2 MANDOTA 🔥🔥🤣🤣🤣🤣
I know kumapeto kwake wina apusa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
she mandota inuyo mumatatu💥💥
AMaili zitumbuwa zawo asungileni kkkkk
Komatu Melosi Kumpanje 🤣🤣🤣🤣asaaah
Very nice
Chipwanya ndi dolo 🔥🔥🔥Mukuipasa fire guys
K50 000 ingopita basi mesa mwati ayi mulibe ndalama
More fire 🔥
Your the best mandota
Komatu chemandota bwino kwa asing'angako 😂🤣🤣🤣🤣
😂😂😂Koma makosana ndinu madolo
Inuyo ndi Therapy 😂😂😂 adha
Koma chiphwanya naye mpaka akaz awili 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🙌
50pin ija mmakaniza ija mperekatu inu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Awawa Ndma best
Mmakwana
Fire mandota
mbambande 😀😀 waiting for part 2
dope
Hahaha chiphwanya ndiwe wakubatu iwe
Guys u are best comedian tikudikila part 2
Apa ndewakometsatu Dr ulemu wako🤣🤣🤣🤣👨🍳
Masha Allah
mwati mkati mumaoneka chani?🤣🤣🤣🤣🤣
Mumakwana Mr, koma part 2 akita saafa😅😅
Anthu awili awa😂💀🔥🔥ehhh mumakwana kwambili guys Mandota plz next vidz mayeleyo awonekeko mwanayo man😂😂🔥
The best comedian in Malawi
Chiphwanya kufewa😂😂Kip up the good work
Wayitha chiphwanya umudyera mandota ndi mfana 😂😂😂😂😂😂😂😂
Chemandota n Chiphwanya ulemu wanu!!!!!🧔🧔
🤔🤣🤣🤣🤣🤣 koma madolo iiii Patiently waiting for part 2
😂😂😂😂 akubera aise
Mmmm 😂😂🤣ai zikomo, waiting for part 2 🥰
Akubela chiphwanya uona shomwe shina meta pala khanka
Kkkkkk mandota kkkkk akumpasan minyama
Kkkkkkk mbambande Amuna😂😂Achiphwanya mpaka amkazi awiri
Mumatha guyz ....ulemu wanu
You guys are just amazing 🤣🤣🤣 Chipwanya wandiwasa
Amamaili munakapita kukamuitana maili timuoneko asachite kukhala ngat sikono
Eee ayi zikomo 50 pin ija
Umatha iweyo madota
Ipase moto mandota
Mumatha A mwene timakufilani
Wow Nyc comedy chemandota 😂
Chiphwanya simuthu wamba,Mandota abeledwa 50pin ndithu kkk
Hi
Ulem wanu ma fumu 🍻one love
I can't wait for part 2
Nice one ❤️
Kkkk Chiphwanya adakonzatu , keep it up
Chiphwanya apa nde waipeza fifty thousand munamukanisa ija baasiiii😂😂😂😂😂
Hy broz mandota pitirizan kutipatsa ma comedy anu muli boh man
Ma mayili mmakwana Mandota anakukondan
Apapa chemandota uyembekezere kubetsa 50pin kwachiphwanya😂😂😂😂 paja udamukanika atabwera kwanu kkkkkkk wakupezera plan aise😂😂😂😂😂
I love your comedy All the way from Ethiopia even i don't listen your language
I will be teaching you 🎉
Kkkķkk mandota umakwana komano achiphwanya pena palipose aaaaaaaaaaaaa inuyo umngakwatileko😂😂😂😂😂
Am the first to view 😘😘
These two ndi ma best comedians in Malawi🤣
Kkkkkkkkk
Kungokhala ngati ma asikono ndimanganya kkkkkkkk
😂 😂 😂 😂 Ka elisabefi kadyatu basi mudya.
Chiphwanya wasewera plan B kuti apeze 50 k ija 😂😂,wangopangana ndi ma chick wo🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣🤣🤣apa 50pin ipitadi Basi,,, wakupezera plan chiphwanya🤣🤣🤣🤣
I am the first person to view 🥳🥳
I like your comedy che mandota❤
Your number 1we like your comedy
Komatu amayili simukutionesa ngati a Sikono bwanji kkkkkkkkk.Kungoti a Mayili akiya nyumba Basi osaona mmene abwelela Aaaaaaa sinthu zake.But u are the best
Like this comedy
Sending loves ❤️❤️
Number ya Ma maili taponyani che mandota amandiwaza😋😋😋😋😅😅😅
Chiphwanya ndi matchini mandota kupeleka mosavuta chuma kkkkkkkkkkkk
Nice
Keep the fire burning.... Che Mandota timakunyadirani .
Chemandota please upole moto wati nkatimu mumaoneka ngati chiyani ? Kkkkkkkk ayi dzikomo mandota muuze chipwanya andipase nkadzi mmoziyo maka uyo akupita kwa aunt kkkkkkkk nankha awiri yekha aaaa
Mtunduka🙈.....bwelani musatenge mkasi
Amwene mandota inuo mumatha much love from this side machinga T/A nyambi makwana
Ndipo ma mayili muzangokwatirana ndi Chelindotawo basi kkkkkkk mukumaitha you two are best
Mkatimu ndiye mumawoneka mtumbuka mtumbuka 😂😂😂
😂😂😂😂😂mwadzaaa
You never disappoint
🙌🗣️🤣🤣🤣Chemandota fire
Umakwana kwambiri brother
Kutengeka akulu inu kkkkkkk km mwammanatu nzanu 50pin zikutsalira kuteleku
musapeleke 50 pin mubeledwa. keep it up guys
Fire ndox
A che mandota you always makes my day
Akupusisa ase....dollar ija upereka usakuziwa kuti akuponda😂😂😂😂😂🙌
Good combination
ukutha aise....u will go far
Iyiyi mwapha guys eiish kkkkk
Kkkk mumativesa kukoma pakhani zama drama
Chemandota ndi chiphwanya kkkk, koma akangodziwa ma Maili akupha kkkk, mandota ndi maMaili munachokera patali, timakunyadirani
I like you guys 😅😅😅
Kkkkk koma very impressive
Amayi amayiliiiiii🙄🙄🙄🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 We want to see mayiri please 😂😂😂😂😂😆
Me 2 wooooo
50 pin ija mukafupatu kwa anthu oti anagwilizana zochita awa kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkk chiphwanya kupeza dollar mosavutatu uku
Guys ndafwa ndi mpwetee😍 😘 🦋 😍 😘 🦋
I like your composure in this one.
You know how best to make us laugh 😄
Waberedwa iwe basi
Ineso ndiseke ki ki ki ki ki
Kkkkk ai nditu umatha iweyo
🤣🤣🤣🤣🤣🤣Your super star my brother
Nkhan ndi tiktok tili pano kudikila part 2 MANDOTA 🔥🔥
🤣🤣🤣🤣
I know kumapeto kwake wina apusa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
she mandota inuyo mumatatu💥💥
AMaili zitumbuwa zawo asungileni kkkkk
Komatu Melosi Kumpanje 🤣🤣🤣🤣asaaah
Very nice
Chipwanya ndi dolo 🔥🔥🔥
Mukuipasa fire guys
K50 000 ingopita basi mesa mwati ayi mulibe ndalama
More fire 🔥
Your the best mandota
Komatu chemandota bwino kwa asing'angako 😂🤣🤣🤣🤣
😂😂😂Koma makosana ndinu madolo
Inuyo ndi Therapy 😂😂😂 adha
Koma chiphwanya naye mpaka akaz awili 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🙌
50pin ija mmakaniza ija mperekatu inu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Awawa Ndma best
Mmakwana
Fire mandota
mbambande 😀😀 waiting for part 2
dope
Hahaha chiphwanya ndiwe wakubatu iwe
Guys u are best comedian tikudikila part 2
Apa ndewakometsatu Dr ulemu wako🤣🤣🤣🤣👨🍳
Masha Allah
mwati mkati mumaoneka chani?🤣🤣🤣🤣🤣
Mumakwana Mr, koma part 2 akita saafa😅😅
Anthu awili awa😂💀🔥🔥ehhh mumakwana kwambili guys
Mandota plz next vidz mayeleyo awonekeko mwanayo man😂😂🔥
The best comedian in Malawi
Chiphwanya kufewa😂😂
Kip up the good work
Wayitha chiphwanya umudyera mandota ndi mfana 😂😂😂😂😂😂😂😂
Chemandota n Chiphwanya ulemu wanu!!!!!🧔🧔
🤔🤣🤣🤣🤣🤣 koma madolo iiii
Patiently waiting for part 2
😂😂😂😂 akubera aise
Mmmm 😂😂🤣ai zikomo, waiting for part 2 🥰
Akubela chiphwanya uona shomwe shina meta pala khanka
Kkkkkk mandota kkkkk akumpasan minyama
Kkkkkkk mbambande Amuna😂😂
Achiphwanya mpaka amkazi awiri
Mumatha guyz ....ulemu wanu
You guys are just amazing 🤣🤣🤣 Chipwanya wandiwasa
Amamaili munakapita kukamuitana maili timuoneko asachite kukhala ngat sikono
Eee ayi zikomo 50 pin ija
Umatha iweyo madota
Ipase moto mandota
Mumatha A mwene timakufilani
Wow Nyc comedy chemandota 😂
Chiphwanya simuthu wamba,
Mandota abeledwa 50pin ndithu kkk