Video není dostupné.
Omlouváme se.
KOLANDIRA NDALAMA - Episode 150
Komentáře • 334
Další v pořadí
Automatické přehrávání
CHUMA CHOLANDA - Episode 147CHE MANDOTA COMEDIES
zhlédnutí 138K
OYIMBA A KU MALAWI AKUPEZA NDALAMA ZINGATI PA YOUTUBE? - TILI NDI TOP 10Factory265 Media
zhlédnutí 67K
NGONGOLE - Episode 105CHE MANDOTA COMEDIES
zhlédnutí 256K
Ženu pronásleduje vrah #horrorshorts #shorthorrorstory #shorthorrorstoriesPrézovy noční můry
zhlédnutí 225K
Box jumping challenge, who stepped on the trap? #FunnyFamily #PartyGamesFamily Games Media
zhlédnutí 31M
V MÉ HLAVĚ…Attack
zhlédnutí 558K
WHO CAN RUN FASTER?Zhong
zhlédnutí 40M
UKU NDIYE YALAKWA, ANTHU AKUCHILIMBA BLANTYRE ZOMWE ACHITA🙌🙌🙌HOT 265
zhlédnutí 179K
Kunte Jekete Full HQ VideoKunte Komedy
zhlédnutí 22K
USAUVER S06E07 MASAMUPiksy TV
zhlédnutí 158K
Ching'aning'ani Comedy and Giring’ande Entertain Inmates on Prison Health Day at Chichiri PrisonAmuna Misso Tv
zhlédnutí 128K
GOtv Malawi Izeki ndi Jakobo Safunsa anadya phulaBaby rilyn123
zhlédnutí 473K
Honey Snake Girl 😱 (Full HD) | Mark Angel Comedy | Yawa Skits | OGB Recent | Mr MacaroniFunnyBoys Comedy Tv
zhlédnutí 8M
NDONDOCHA ft Atoht Manje- Episode 64CHE MANDOTA COMEDIES
zhlédnutí 252K
MU LIMBE - Episode 158CHE MANDOTA COMEDIES
zhlédnutí 75K
Pick a Color, I'll Buy 🟪🟨Brianna
zhlédnutí 38M
Cool barbie shoes! #shoes #makeover #diy #upcycling #handmadeLa La Laugh! Shorts
zhlédnutí 7M
Get 10 Mega Boxes OR 60 Starr Drops!!Brawl Stars
zhlédnutí 15M
Co divného umíš ty? 😝Tary
zhlédnutí 429K
Koupím Barče Cokoliv Co Trefí Šipkou!DodoCZ
zhlédnutí 154K
The Real Process of Harvesting Honey 🐝🍯 #funnycats #funnyvideo #reaction #honeyMeowtropolis
zhlédnutí 5M
ОСКАР СБИЛ ЛЕРУ С НОГ 🥴HOOOTDOGS
zhlédnutí 4,9M
GAME OF O.U.T. vs MINI CELINE 🙈⚽️Celine Dept
zhlédnutí 30M
Phuma ndi ndalama che Mandota😂😂😅iiih ndafa ndi phwete...keep up the good work😊
Chikuchitika Pano mukuchidziwa? Eya kulandira ndalama😂😂😂
Wow I lavuzi you Che Mandota,inu ndi dolo basi💪 Lesson learnt,more love and respect for you from Lusaka Zambia 🇿🇲
There's a good lesson for those who are interested in looking for benefits while ignoring the effects
Ndota APA nde ukala opanda siwalotu😂😂
Mundu wamkulu mwandizangalaza kulimba mtima 😂😂😂😂😊
🤣🤣🤣🤣🤣 always hillarious. I like the ending
Koma ndanseka 😂😂 mandota iweyo ndi galu kwabasi
😂😂😂😂😂😂 upongwe waiting next part ,but am worriying that ur ambassadorship with Inno build its over but i wish u all the best till u find another one still u support here from SALIMA Town
Chemandota kukonda ndalama ndye ndizimenezotu 🤣🤣🤣
😢😢sikuti siku lithe uyu asanapepere ayi ndithu,as a Matala of fact
Kumafunsa kaye a Mandota🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mandonda kukonda ndlama wakumana nazo😂😂😂😂😂😂
Akadule basi 😂😂😅mandota wasala dzina lokha
😂😂😂 are mandota uxandipha ndi kusekha kkkkkkkk
Mene tilili kudikira 😂😂😂😂😂
First to watch and comment 😂🔥🔥
Tiwona zina zache kuzogolo ku😅
eeeehhh koma iyi katundu wapha😃😃😃🔥🔥🔥
Nthawi zonse umafa mandota😂
Chemandota kumafusa kaye 😂😂😂😂
Ache mandota kumafunsa kaye mmmm apa nde Akita wafa 🤣😁😁😁
Kupupuluma akulu, nde akukakuchosanitu😂😂😂😂😂
Koma iwe wakulila kumangamba❤❤❤❤😂😂😂
Nyambalo kukaiotcha😂😂😂😂
Mologeni adzakupweteketsani 😂😂😂
u don't want peace you want problems always
mumatha Inu I loves you indeed😂😂
We've been waiting timaona kuchedwa
Sipatsalapo kanthu Ata 😂😂😂
Iwe ndi one❤
Inu a chemandota kulandira ndalama osafunsa kuti ndizachiyani mudzathetsa ana samalani.
Center yapita 😂😂you😂
Chemandota, safunsa anadya phula😂😂😂
Akita opanda ziwalo 😂😂😂😂
Mmakwana big
Chemandota changu mpaka kudumphila nzere 😂
𝐒𝐢𝐭𝐢𝐦𝐚𝐟𝐮𝐬𝐚 𝐤𝐚𝐞 𝐢𝐧𝐮 𝐚𝐚𝐚𝐚😂😂😂😂
Mukufunikadi award koma apanda ziwalo 😂😂
Akulu inu kugundika uku Mayili asatengere😂😂
❤❤❤love from USA
😂😂Mduleni ameney
😂😂😂😂😂😂 Che Mandota inuyo ndi number one.
Ili ndi phunziro labwino kwambiri osamangolandira ziri zonse musanafufuze za zolinga zake.
Keep it up Che Mandota ❤
❤From RSA
Koma aise Mandota dzuwali munthu kjmagogawa ndalama za ulere umaganiza bwanj?😂😂😂😂😂😂😂😂😂 eeee ndaseka and is good lesson to us.
Kkkkkk much appreciated to madota
🤣😂😂🤣🤣🤣 big up
😂😂😂😂 aaa iwe nd dolo aseee.
Big up bro
Kumafunsa pa malo ukafika mdyomba 😅😅😅😅
Usadzamwalire ase. we lafvs yu tu mach again😅😂😂
Kkkkkkkkk thanks mandota
Koma mandota panka kulowerela ndilama zaena kkkkkkk I love you
Mandota puma
kumafusa kaye mmm m😂😂😂😂😂
Nice movie
Kodi nindalama zanji zoti muzifusanaso kuti mwalimba mtima 😢😢😢
Mandota I'm warning you tsiku lina suzasala mkathu sure coz ukuoneka kut ndalama umazikonda heavy kkkkkkkkk
Zina wumango wona waziyamba 🤣🤣🤣🤣🤣
Kkkkkk ndaseka kwambil mpaka kutsamwa.kkkkk kumangolandil ndalam osadzwa it zikuchok kt kkkkkk k km mandota
Koma mandota 😅😅😅soo much love ❣️
😂😂😂 mandota sazatheka
Koma mandota uzathera mmanja🤣🤣🤣
Iweyo. Umakwannila ❤ayilafiyu tumachi
Umakwana ❤❤❤
Top fan!
Ilove mandota umativesa kukoma
😂😂😂😂Koma Ka Dokotala akaka
Mandota suzatheka kkkkkk
😂😂😂 ukali wanu ma boys mumatha inuyo palibeso
Nice
My best
Inu kukonda ndalama ,lero mwadulisa naso ziwiya kkkkk
Ndakomoka mkuseka 😂😂😂😂chemandota kunoooooo
Okonda zinthu wakumana Nazi dulen matako😂😂
Much love ❤❤❤❤
wathawisa center mandota😅😅😅😂
Midfielder yapita😂😂😂😂😂
Mandota ndidolo
Safusa adadya phula akulu🤣🤣🤣🤣
Koma kumeneko 😂😂😂 che Mendota iweyo 🤣🤣🤣🤣 usazafe uzangosowa
Haha uyo apa nde Akita wafadi basi wagulitsa centre 😂😂😂
Asibambo tayiman kaye 😃😃😃😃
Chemandota ndi number one
Muli uthenga wa bwino kwabasi.... Umakwana chemandota😂😂😂🙏🙏🙏🙏
Koma msanga wanga iwe muthu iwe mundimpha
Kkkkk bwana mandota kwere kusokonasya kapena kusigalila
Wawojo adolo
Koma ndaseka mpaka misozi kutuluka, Chemandota ndi massive
Wow a good lesson
always first to watch and comment
Akuti poti mabele mulibe tidula chani? 😂😂😂😂
Kmatu che mandota phuma lidzakupha sure!
Eeeeee🔥🔥🔥🔥🔥🔥 iyiyi yabweraaa ili bho heavy ✊✊
Ife timakufilaa braza
Koma tsono Mandota umaganiza bwanji kwenikweni 😂👏👏👏
Akita wafa😂😂
Mandota phuma ndindalama
Dr. Mudzafa osadwala kamba kokonda ndalama,ili mwala 🎉🎉
❤❤❤ mandota umaganiza mwa thinking iweyo
Moto unandi 🔥🔥🔥
Matako amadota kkkkk abale koma akagulitdidwa zingati 😅😅
Ndinu akamuna mesa I love you
Mumakwana guys 😍