ZAKU NTCHEU/ ZOMWE A KALIATI AYANKHULA KWA A MALAWI 🙌🙌🙌

SdĂ­let
VloĆŸit
  • čas pƙidĂĄn 15. 06. 2024

Komentáƙe • 155

  • @BernadettaGhambi
    @BernadettaGhambi Pƙed 26 dny +3

    I'm not a politician but this death has affected the whole nation since our VP was so humble in all areas
    Tiwalila mpaka kale kale, MHSRIP

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Pƙed 27 dny +17

    Mai Patricia Kaliati ndimakulondani inu ndinudi mai wathu ndiodziwa ndale ndiutsogoleri, mulungu akudalitseni RIP SKC 😱

    • @CEDRICJIKA
      @CEDRICJIKA Pƙed 26 dny

      How can Usi talk he had more time to talk in the past. But while he is in this sanking boat we saw him being silent for sure. A silent baby on journey dies with hungry but the crying baby always finish the journey with full belly. Shame for him.

    • @ireenzulukamanga9099
      @ireenzulukamanga9099 Pƙed 26 dny

      I totally agree with you. She is indeed a Super Woman. Infact, I admire her courage đŸ’Ș.....

  • @williskabambe7811
    @williskabambe7811 Pƙed 27 dny +5

    AKWENI SHOULD RISE UP AND BE BRAVE ENOUGH TO FILL SKC POSITION.

  • @user-nr4mi7pt8g
    @user-nr4mi7pt8g Pƙed 27 dny +12

    Mcp has lost it, no matter whether they did it or not but God had chosen this way to bring them down . Paja Mulungu anaumisa mtima wa pharaoh mwadala

  • @CEDRICJIKA
    @CEDRICJIKA Pƙed 26 dny +2

    Kaliati is wise and crever enough keep it up

  • @shuraimuwamama2349
    @shuraimuwamama2349 Pƙed 27 dny +8

    Mpungwe sinjira yokodzera zinthu inde Komano ngati chilungamo chikusowa zimakhala zomvuta,aboma akanakhala kuti kafukufuku wapangidwa nkuziwapo chilungamo sibwenzi zili choncho,komanso akadawamvetsa zoti anyamula okha osapanga nkhanza padipiti bwenzi ili nkhani ina,anyani amvumbwawo mukadawaudza kuti asabwere kumeneko anthu akanadekha koma mukumanyanya kumachita kuwapatsa pepani zopusa

    • @Okalekale
      @Okalekale Pƙed 27 dny

      Kafukufuka si 1+1.Sizingatheke tsiku limodzi

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Pƙed 26 dny +2

    Zonsez zikuchitila chifukwa chakusowa chilungamo kwa boma kwasalaku ndi by fire by force

  • @chikaonekarh
    @chikaonekarh Pƙed 27 dny +2

    RIP SKC ,as a Ngoni from Ntcheu ndalira kupita kwanu a Chilima, mpaka ndakhetsa msozi.

  • @FloraNtakwile
    @FloraNtakwile Pƙed 26 dny +1

    Imfa iyi nde yawawa💔💔💔, koma ndadandaula ndi aMalawi anzathu amene atayaso miyoyo usikuwu😭😭😭, mizimu yawo iwuse mu mtendere wa AMBUYE🙏

  • @AlexanderYovatiKhumalo
    @AlexanderYovatiKhumalo Pƙed 26 dny +1

    Respect the burial ceremony of the late VP Chilima no matter where you are please avoid misbehave.

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh Pƙed 27 dny +4

    Palibe munthu amene adalengedwa kuti sadzafa ndipo kuti adzafa bwanji uchitsiru chabe ukuonekawu

    • @user-fp1qg1uy7g
      @user-fp1qg1uy7g Pƙed 27 dny +1

      Chilikwanzako Chima phweka a braz. Chikakhala nyumba mwako it feels different

  • @user-fi2by2ui9o
    @user-fi2by2ui9o Pƙed 27 dny +5

    Chilungamo chioneka chifukwa MULUNGU alowelerapo ndipo aliyense amĂšne akuweruza anthu ena chikhalireni alibe umboni achita manyazi posachedwa

  • @BlessingsKalonga
    @BlessingsKalonga Pƙed 26 dny +1

    God Knows everything May your soul Rest internal peace tonse tikudikira komko

  • @RajanaBaluwesi
    @RajanaBaluwesi Pƙed 27 dny +2

    Malawi wachita chiwewe. Amene akuchita zinthu Ali phee kumene Ali kufuna kuyipitsa mbili ya anthu ena. We belong to the Lord Almighty and one day we shall retain. Usiyeni nzimu wa Saulosi uwuse mu mtendere.

    • @user-ty1vq9lq6w
      @user-ty1vq9lq6w Pƙed 27 dny

      Chitipa chimaziipitsa mbiri chokha ndipo mbiri yake yaipadi

    • @user-ty1vq9lq6w
      @user-ty1vq9lq6w Pƙed 27 dny

      Chaziipitsa mbiri chokha

    • @EllinaMasimo
      @EllinaMasimo Pƙed 26 dny +1

      Indeed good people die young and l quote mmmm the pain is hard to bear😂😂😂😂

  • @jamesphiri-ob6br
    @jamesphiri-ob6br Pƙed 27 dny +2

    Malawi suzasintha tilibe moyo wausamunda omweuja😭😭😭😭😭

  • @PriscahMkandawire
    @PriscahMkandawire Pƙed 26 dny +2

    Ussi amudyesa chibaziii ambuye akamakatha a agyptu akathira limodzi ndi usssi

    • @SamJalie
      @SamJalie Pƙed 26 dny

      Oh! Wajoina ma Lacoste mwachinsisi?

  • @user-xo5ll6se3e
    @user-xo5ll6se3e Pƙed 27 dny +2

    Respecting the burial ceremony of the late leader will be of more importance. Malawi is one and very small

  • @GeraldMkandawire-bl8po
    @GeraldMkandawire-bl8po Pƙed 27 dny +2

    Michael usi has chosen to be silent at this mourning time of our beloved vice president why????? Michael usi mwakhala chete bwanji

    • @SamJalie
      @SamJalie Pƙed 26 dny

      Ma Lacoste anamuseka pakamwa

  • @user-xo5ll6se3e
    @user-xo5ll6se3e Pƙed 27 dny +2

    Mwambo woyika SKC umafunika utazayamba nsanga Kuti udzathenso nsanga Kuti mwina anthu obwerera adzayende kukadali koyera. Enafe timabisalira pochita zoyipa chifukwa tawona mdima.

  • @JamesSimbeye-qw6dz
    @JamesSimbeye-qw6dz Pƙed 27 dny

    Skc !unali, uli ndipo uzakhalabe hero wanga. Rest in forever peace.

  • @augustMag
    @augustMag Pƙed 26 dny

    Tiyeni monga mwini wake analiri honorable Chilima pamene moyo wake unali olandila chipongwe koma sanabwezere monga anali ofasa ndi ondekha tiyeni tichite Chimodzi modzi kuti mzimu wao uunse mumtendere osatha kuti mwini wake kumene akupita apitilize kukondwerera 🙏🙏

  • @user-sh6gi5uq3l
    @user-sh6gi5uq3l Pƙed 27 dny +1

    Sizipangisa kupereka moyo kwa otisiyawa chofunika ndikulira maliro ndi mtima osweka komanso olorerana kuti munthuyu alowe mmanda mwamtendere

  • @VeronicaGalileya
    @VeronicaGalileya Pƙed 27 dny +2

    Warm heart of Africa ija yaonongeka 😭😭😭😭😭😭💔

    • @Okalekale
      @Okalekale Pƙed 27 dny

      Democracy ndi nyasitu,Kamuzu anatiuza kale

  • @AlieKamoto
    @AlieKamoto Pƙed 25 dny

    Mr akuopa kulankhulapo coz iyeyo nd part of tchile ndpo moto uli behind his back 😂😂😂😂

  • @MphatsoBandah-bl9jl
    @MphatsoBandah-bl9jl Pƙed 26 dny

    Mulungu akudalitseni mai kaliyati chifukwa chamau achilimbikitso😂😂😂😂😂😂

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju Pƙed 26 dny

    Great speak anakhoma

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju Pƙed 26 dny

    Mr usi umkakulatu mtima pamene APM inali m'boma ...lero uli chete ngati bubu onetsatu u master akowo ...

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Pƙed 27 dny

    Zikumveka ndithu zimenezi koma, young generation tingoti tiyeni tiike maliro chifukwa tataya mbadwa ya ife 😭😭😭😭😭😭

  • @MwaleMussa
    @MwaleMussa Pƙed 27 dny +3

    Zikuwawa koma😭😭😭

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Pƙed 26 dny

    Action pasogolo osafooka guys zibonga zituluke zochuluka kumeneko ntcheu morefire

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl Pƙed 27 dny +2

    Maico utsi amuchose muchipani ndifiti arindi chakwera

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 Pƙed 27 dny

    My fellow Malawians let's bury our hero peacefully other than causing havoc

  • @MphatsoJuniorLimbanga
    @MphatsoJuniorLimbanga Pƙed 27 dny

    Kulira kwanga nkosatonthozeka,,

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Pƙed 26 dny

    Bvuto ndiumbuli ndiumphawi kubvetsa kumakhala kobvuta koma ndikuyamika bambo njawala komaso mai kaliat ambuye akudalitseni

  • @anoldluke-rl6pe
    @anoldluke-rl6pe Pƙed 27 dny +1

    Mr usi tiyankhuleni koma

  • @MussaWinfred
    @MussaWinfred Pƙed 27 dny +3

    Titsalila kosaiwali malawi dot for geet vice president history

  • @MphatsoKachere-rs3bf
    @MphatsoKachere-rs3bf Pƙed 27 dny

    Zovuta kuvesa kmabe RIP DR SKC

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu Pƙed 26 dny

    MCP yanyika it will b difficult for them kukapanga campaign ku ntchewu.

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v Pƙed 27 dny

    Sa utm nda amalawi osweka mtima

  • @user-zq3uf5bc8v
    @user-zq3uf5bc8v Pƙed 26 dny

    Glorify to almighty God for this lost of chilima life

  • @user-qf4lq2mo6n
    @user-qf4lq2mo6n Pƙed 27 dny

    Koma mwambo uthe nsanga chonde muyende usana osati utsiku ngati momwe umayendera dzulu

  • @anarfmveluwa332
    @anarfmveluwa332 Pƙed 20 dny

    he s pro mcp

  • @NastonVickta
    @NastonVickta Pƙed 26 dny

    We never keep silent till chakwera atamusata chilima

  • @FrankChizenga
    @FrankChizenga Pƙed 27 dny

    Zooonadi kuti ndife okhudzika funso ndi loti boma lidatenga nthawi pokayafuna ndege ija lero mukuona ngati achinyamatafe ndife okondwa nanu?

  • @kenmadan5350
    @kenmadan5350 Pƙed 27 dny +3

    Zochitisa manyazi kwa atsogoleri a utm ,bad example

  • @RaphaelGwaza
    @RaphaelGwaza Pƙed 27 dny +1

    Mwina munakapepha achakwela

  • @user-vg5so7mz3s
    @user-vg5so7mz3s Pƙed 27 dny

    A president achakwera chimene amachita amachiziwa and ndi muthu oipa wapha Mr chilima

  • @HarryKazumbu
    @HarryKazumbu Pƙed 27 dny

    Zoon osationongel mbir

  • @RasheedMaster-md2vz
    @RasheedMaster-md2vz Pƙed 27 dny +1

    Ifa ndi thawi Muthu wina aliyese azalawa ifa and paliponse pomwe angakhale ifa ikupezani olo mutakhala malinga otani. Muthu wina aliyense alinayo thawi yofera ndipo thawiyo ikakwana sangayichedwere kapena kuyifulumikisitsa ai ndipo dzikoo lapansi ili ndi chabe ndinchitsangalalo chonyenga basi

  • @IsaacKulongwe-ol5mx
    @IsaacKulongwe-ol5mx Pƙed 26 dny

    Usi pajatu pazokambilana zilizose za UTM akumuthamangitsa nde mutakhala inu mungatani

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Pƙed 27 dny +1

    OSAONETSA NKWIYO ANYANI AWAWA AZOLOWELA AND AZINGOPITILIDZA KUCHOTSA MIYOYO YA ANTHU ENA.KOMA NGATI MUKUFUNA BATA .MWAUDZE A BOMA ASATENGE MBALI MAKAMAKA POLANKHULA PAMALILO .AND MWAMBO UYAMBE NTHAWI YABWINO MALILE AYIKE NTHAWI YABWINO.POKHAPO ZITHEKA .KOMA KUNGOPELEKA MPATA KWA NDUNA KULANKHULA ZINTHU ZIKAIPA

  • @user-zv3cy2xj5p
    @user-zv3cy2xj5p Pƙed 27 dny

    Kaliat wayankhula ngat wanzeru

  • @CashmoneyMillionaire-rc1hf

    I don't even think that chilima will go like that R I P

  • @emmanuelmukondia3568
    @emmanuelmukondia3568 Pƙed 27 dny

    Mr.Usi has been sidelined just because he was not politicking as others have been ding

  • @HannockMesiwni
    @HannockMesiwni Pƙed 26 dny

    Apa nkhondo yapa chiweni ndimene umayambira mumaiko ena ngati simkuziwa

  • @chifundochiwaula998
    @chifundochiwaula998 Pƙed 27 dny +1

    Chilungamo chikuoneka kale maganizo amalawi ndamodzi palibe kusintha kulikonse sitikusowekela maumboni ena

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon Pƙed 26 dny

      Ndipo iwe ndikugwirizana nawe anthu ena sizikuwawawa chifukwa abale awo ndi a mcp komaso afawo sabaleawo palibenso kufuna umboni wachani zinthu zikulankhuka zokha,zomwe zachitika achita kupha anthu awa pano simungawanamize amalawi kulibe chakwera amaonangati wabisala osadziwakuti wabisalamumbatata nsana ukuoneka nyekwe asowa nayo mtendere,

  • @AndrinaBanda-bo4pd
    @AndrinaBanda-bo4pd Pƙed 27 dny

    zosayenda

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y Pƙed 26 dny

    We so disappointed with this government

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos Pƙed 26 dny

    Koma ife amalawi tisayembekezere kuti boma lingabwerese chungamo poyera MMM ayi

  • @Jaydee-mw4
    @Jaydee-mw4 Pƙed 26 dny

    Votolake inuyo chilingamo chikukusowan agalu inu

  • @user-zc1mg5lj7p
    @user-zc1mg5lj7p Pƙed 27 dny

    Malawi ana uzidwa ndi malemu kuti tisaope tisagonje tisaope komanso ma demo pa malawi anayamba kale

  • @ackimChiumia
    @ackimChiumia Pƙed 27 dny

    Zadabwisadi,olo speech yake sindinayimvepo but he could stand up and say something,let's wait n see

  • @EdwinMabviko
    @EdwinMabviko Pƙed 27 dny

    Ku UTM munthu amene ali mtsogoleli wawonetsa kulila kwenikweni ndi Dr Usi!!!!

  • @user-cx7ep1dt8z
    @user-cx7ep1dt8z Pƙed 26 dny

    Ngakhale one ndikanagenda athu achakwela athu oipa kwabasi

  • @jomochirwa
    @jomochirwa Pƙed 27 dny

    Mama a kaliyati ambuye azikutsogolelani pa tchito yayikulu imene mukuyigwila.koma dziwani ichi amayi chipani cha utm panopa chidzakhala ndi mphavu komanso sapoti yayikulu kuposa kale.inu ndinu atsogoleli chabe koma chipani chili ndife anthu wokwiya chifukwa ndi amene timavota.

    • @SamJalie
      @SamJalie Pƙed 26 dny

      She'll rise this woman

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu Pƙed 27 dny

    Tinayenera kupanga action kuti adziwe zatinyasa coz malilowa akayika sindikuwona nkhani imeneyi ikupitilila, anthu a ndale ndiwoyipa tinayenera kuti tingowagenda kumene

  • @NastonVickta
    @NastonVickta Pƙed 26 dny

    Mtumbo wako kaliati, naweso ukuziwapo kanthu usatinamize,, mesa unaimbilidwa foni kukuuza kuti umuuze DR SKC kuti asapite ulendoo, chomwe unalepherera kumuuza ndi chiyani, mapiruod ako

  • @julietbanda5203
    @julietbanda5203 Pƙed 26 dny

    Ussi is a betrayer,Mai kaliat congratulations,MHSRIP,Mr chilima 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭,chakwera why why why you killed chilima

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od Pƙed 26 dny

    Iweso Patricia kaliati utisamale tikufuna iweyo

  • @LindaChithumba
    @LindaChithumba Pƙed 27 dny

    Anthu angat amwalirawo?? 😭😭😭😭😭😭 Omg

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq Pƙed 27 dny

    Congratulations ntchewu fans,stone chakwera with his team.mugendeni chakwera palibenso chabwino apa amada,amada arise,atiphera athu athu akumwera ameneyu.chipolowechi osawone ngati ntchitha .Rest in peace all.

  • @user-xd1cm7tm7t
    @user-xd1cm7tm7t Pƙed 27 dny +3

    Tiyen nawo osaopa chakwera asamazitenge ngat mlungu

    • @Allan-bk1
      @Allan-bk1 Pƙed 26 dny

      Kkkkkkk eeeesh tiyeni tikhale abata ngati chilima

  • @GoodluckChristopher-og9wi

    Koma tiyeni tipereke bata president wathu timuperekeze mwa ulemu

  • @FrankFrancis-ch3xv
    @FrankFrancis-ch3xv Pƙed 27 dny +1

    So painful end unforgettable in history of malawi at large

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l Pƙed 27 dny

    Ali kumeneko ndi akutundu osat achipan

  • @LucrenciaNambuzi
    @LucrenciaNambuzi Pƙed 26 dny

    Dr salous klaus Chilima is died soul rest of peace

  • @user-oj5ym5uy7s
    @user-oj5ym5uy7s Pƙed 27 dny

    Ussi ndi mbuzi kwambiri,

  • @Cuddy-ol5wq
    @Cuddy-ol5wq Pƙed 27 dny +2

    Aboma asatenge mbali pozolankhula kuti kukhale Bata ngati akufuna mtendele

  • @user-iw5gg8ng3p
    @user-iw5gg8ng3p Pƙed 26 dny

    Big loss to the Malawi Nation indeed

  • @SusanPilingu
    @SusanPilingu Pƙed 27 dny +1

    Si aUTM amene akupagisa ziwawa koma a malawi ndiwokhumudwa koma tisamulole Santana Kutenga mbali chifukwa a Chilima anali wokonda Mulungu

  • @FatimaMsusa
    @FatimaMsusa Pƙed 26 dny

    Chipani chakupha inu ichi..... Mcp... Kwao ndikupha anthu.... No more vote for mcp.... Period.

  • @EvanceLumeyo
    @EvanceLumeyo Pƙed 27 dny

    We should thank for the Woman Patricia Kaliati to stand strongly. I think God uses her for he is not scares God he connectes to even the one whose heart is flaming up.

  • @MoosaQasssim
    @MoosaQasssim Pƙed 27 dny +1

    Guys lm not politician but why president Lazarus chakwera said in his speech that, i know your anger is beyond limit but don't fight back the wrong, now which wrong? Silent of manganya bring many questions all the part of world.

  • @LexaShaba-sc3iq
    @LexaShaba-sc3iq Pƙed 26 dny

    😊L0

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe Pƙed 27 dny

    Anthu agenda magalimoto amalilo kulibwanji adaniwo akabwera nde kuzakhala zotani

    • @SamJalie
      @SamJalie Pƙed 26 dny

      Maka-maka Zikhale Ng'oma, Harry Nkandawire

  • @ramseygamah
    @ramseygamah Pƙed 27 dny

    Tonse ngati a Malawi tikulira pomuluza wachiwiri kwa mtsogoleri choncho ndizabwinodi kuti tilire mwamtendere komanso ife ma commenter tiyeni tisatukwane koma mumuikiza mmapemphero veep kuti Mulungu amukhululukire zofooka zimene anali nako popeza njira yokalandilira zabwino kwa Mulungu ndi imfa

  • @WhatsongreyDuncan
    @WhatsongreyDuncan Pƙed 27 dny

    😂😂😂😂😂

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge Pƙed 27 dny +27

    I wonder why vice president of UTM,Dr Ussi has chosen to be so silent at this crucial time..is he pro utm or pro mcp??

    • @champianchampian2148
      @champianchampian2148 Pƙed 27 dny +4

      Man has been mcp for long

    • @billykhonje1433
      @billykhonje1433 Pƙed 27 dny +6

      I heard that chakwera promise him to be VP but he is stupid if he will accept it he saporsed to say something in this matter see kaliati she is very strong woman

    • @asahelmachila3026
      @asahelmachila3026 Pƙed 27 dny

      Usi has been greased by Chakwera. He is a traitor, the modern day Judas Iscariot

    • @SurprisedDriftwood-ef3lc
      @SurprisedDriftwood-ef3lc Pƙed 27 dny +1

      Mumati azitukwana ngati munthu opanda zeru

    • @user-rl5zq1qr4d
      @user-rl5zq1qr4d Pƙed 27 dny +3

      Not kuti azitukwana ai palibe member wa UTM amene akutukwana koma him as a vice president of the party anayenera iyenso kutenga mbali yokhazikisa Bata kumamvesa zimene zikukambidwa osamayankha zoti anthu akukayikireni as if munayamba mwapengapo

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 Pƙed 27 dny

    😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @HannockMesiwni
    @HannockMesiwni Pƙed 26 dny

    Why u fear people UTM while they kill chilima like chicken this not gud it will be end up fight

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh Pƙed 27 dny +2

    Akaliat ngakhale atayankhula any how she was the one amafuchita influence ziolowe koma God's plan with not change because chilima is dead

  • @user-nu9dp3gm1p
    @user-nu9dp3gm1p Pƙed 27 dny +1

    Zinthu zalakwakwika fukwa chainu kaliati

    • @anniekanyenda3016
      @anniekanyenda3016 Pƙed 27 dny +1

      Straight amayiwa sanachite bwino.

    • @BrunoMbewe-xj1yy
      @BrunoMbewe-xj1yy Pƙed 27 dny

      Mayo kaliyati takuthokozani.Koma a VP a utm alikuti sakuoneka Komaso sakuveka Mr Michael usi alikuti?

  • @kelvingremphiri565
    @kelvingremphiri565 Pƙed 26 dny

    Michael usi ndiwopepela, ma program ake a Tikuferanji am not going to follow

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs Pƙed 27 dny

    Dikila aikeye malilo aveno madzi achina chimwendo banda Koma apule sidzikuwakhudza Koma ndunadzaodzi