BON KALINDO PA 2 JULY 2024 |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 1. 07. 2024

Komentáře • 52

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 2 dny +3

    Bonnnn! Kalindoooooo! The DC😅😅😅😅 mwana oopsya kwambiriiiiiiiiiii😅😅😅 We love you forever asanje atembenuke azilume kunsana😅 😅 more 🔥 🔥 Dr DC

  • @smartjohn4684
    @smartjohn4684 Před 2 dny

    I like bon kalindo amatiimilira kwambiri zed

  • @mecanhelaseomundo915
    @mecanhelaseomundo915 Před 2 dny

    The DC umakwana. From Mozambique.

  • @frankiechasokoneza5802

    Our own opposition the DC

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e Před 2 dny

    Ndakulira konko ku police nthawi ya Kamuzu ,Ndipo M'sandikumbutse inu zokoma ndi nzabwino zomwe zinali nthawi imeneyo Sir❤❤❤

  • @AzaniaSibuqashe
    @AzaniaSibuqashe Před 2 dny +2

    Bon kalindo the dc sanama ❤❤❤❤

  • @user-eh6xz1vx8p
    @user-eh6xz1vx8p Před 2 dny

    chabwino born kalindo akupanga ndale komano fact zomwe akunena zikuchtika en ambiri tikuona koma mantha kuyakhula hahah salute to yuh the DC born kalindo

  • @dysonmasiye5736
    @dysonmasiye5736 Před 2 dny

    Nkhani zonse zamveka ndipo Ambuye azikusungani ndi moyo wautali. Dzikoli likuonongeka ndi anthu ophunzira komanso opembedza osaiwala amaudindo.
    Anthu ochuluka ali mu umphawi wa nyoooo koma sangalankhule chifukwa alibenso ufulu wolankhulawo.
    This is why Christ is to come adzapereke makofi ndi mateche plus mambama kwa anthu tonse oipa, ozunza, ankhanza.
    Akubweratu ndipo si kale owowo

  • @chiletsobisweck5007
    @chiletsobisweck5007 Před 2 dny +1

    Alindinkhaza chifukwa cha mkwiyo wamalipiro ochepa 😂😂😂
    Kalumo kobunthwa🤸🤸🤸

    • @WiskMaulana-ky6nf
      @WiskMaulana-ky6nf Před 2 dny

      😂😂😂😂😂😂 ameneyo ndiye booni kalindo aka winiko

  • @FrederickFyson
    @FrederickFyson Před 2 dny

    Exactly ❤❤❤❤❤ Mr DC

  • @crosbeygondwe5403
    @crosbeygondwe5403 Před 2 dny

    Bonnnn!!!!!! Kalindoooooo!!!!!

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 2 dny

    I salute you 😅😅😅 muzibwera everyday,chilungamochoooo tizimva

  • @BillyMhone-jp3kn
    @BillyMhone-jp3kn Před dnem

    TAPANGISANI MA DEMO UTHENGA UMVEKE IZI ZOMANGUYANKHULA SAAKUMVA ABOMAWA

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 2 dny

    Mmatiuza zoona , izi ndi zeni- zeni maka za ku mapasipoti mukutiuza chilunga. Komatu Chakwela nda agulu anzakewo azafera kutulo , boma lankhaza ndi kuba, Chakwela must gooooo!

    • @user-se7wf4ei5b
      @user-se7wf4ei5b Před 2 dny

      Zovuta kwambiri kuma passport tikuguba ngati tikulonjelela ngongole koma amene anatikhalilayo anatikakwila kwambiri

  • @LeooTungama
    @LeooTungama Před dnem

    The Dc moto kuti buuuuuu🎉🎉🎉

  • @user-xc1gk6bw6m
    @user-xc1gk6bw6m Před 2 dny

    We are love you always fadah

  • @BillyMhone-jp3kn
    @BillyMhone-jp3kn Před dnem

    Director wa Migration yo akugwira ntchito yanji??? ma passport sakupangidwa ..

  • @AngozoMalunga
    @AngozoMalunga Před 2 dny

    Keep it up Mr born kalindo

  • @PasadiKatole
    @PasadiKatole Před 2 dny

    Kuswa kuswa basi akunjoya ndi a mcp okhaokha mdziko muno ngakhale akufonyika alibe problem

  • @LovenessNdlovu-w1p
    @LovenessNdlovu-w1p Před 2 dny

    Born kalindo mr nyooooo !! Umatha❤

  • @user-yi2fg1lh8x
    @user-yi2fg1lh8x Před 2 dny

    Mpaka kusilila usilikali chifukwa cha Nido..

  • @ForsterThawan
    @ForsterThawan Před 2 dny +1

    Sukunama aise iweyo umatha kuyankhula Bon kalindo

  • @JonathanTambwali
    @JonathanTambwali Před dnem

    DC tsopano 🎉🎉🎉🎉

  • @RamseyWasi
    @RamseyWasi Před 2 dny

    Apempheni apuulewo kuti
    Mulamuliileko inuyo miez isanu.tione kenakake kamene kangasiinthe.
    Please abeg

  • @user-so7wg6ii5m
    @user-so7wg6ii5m Před 2 dny

    The DC mwana ooooooopsa kwambili ❤

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 Před 2 dny

    Tiyeni tonse tikavote mwanzeru 2025 awa akapume chifukwa ndiye sasiya kukhesa mwazi mmalawi

  • @smartjohn4684
    @smartjohn4684 Před 2 dny

    Km a malawi tilibe gwirizano tiyen tizuke malawi

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Před 2 dny

    Inu aboni yambisani chipani tizakuvotereni ndipo mzawina

  • @user-ph6yr3fh8w
    @user-ph6yr3fh8w Před 2 dny

    The DC mwana ovuta kwambiri

  • @JamesMwayi-ct3wv
    @JamesMwayi-ct3wv Před 2 dny

    Nde maganizo amneoo mudachedwa nawo coz pakatipa pa dutsa anthu awiri peter nd ndi mzake nde mukalakhula lero chifukwa Cha chakwera aaaaa muzikhla nd umunthu osangoti kukhla nd Kwa ulere ai

    • @franklameck5700
      @franklameck5700 Před 2 dny +1

      Inu munali kuti osayankhula ???
      Mzanu wadzuka mkuyankhula walakwa ?
      Inu osayambitsa zanu bwanji, mukudikila wina ayankhule inu mkumampanga let down ?

  • @John-v7p
    @John-v7p Před dnem

    Keep on fire

  • @user-vw4vc9xd5z
    @user-vw4vc9xd5z Před 2 dny

    malawi Pena tiziganiza asamangoyika anthu pampando anthu opanda dzelu alipoyi Bola kazizi amaganiza koma uyu aaaaa ayi

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo Před 2 dny

    Zoonadi tikuvutika kuno chifukwa kumalawi ntchito kulibe

  • @user-dk6yc8pl2m
    @user-dk6yc8pl2m Před 2 dny

    The DC ❤❤❤❤❤

  • @Catheymtimuni
    @Catheymtimuni Před 2 dny +2

    Mavuto aonjezadi

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 2 dny

    Bon Kalindo number one

  • @andrewmtendere3167
    @andrewmtendere3167 Před 2 dny

    The dc❤

  • @ImraanKaletso
    @ImraanKaletso Před 2 dny

    Zoona the DC that's true

  • @getbusy7173
    @getbusy7173 Před 2 dny

    mwaaaaaaaaaaaaana oooooooooooooopsaaaaaaaaaaaaaaa kwambiriiiiiiiiiiii

  • @JamesMwayi-ct3wv
    @JamesMwayi-ct3wv Před 2 dny

    Km ngati ku Malawi kuno kuili chitsilu kwbri nde nd iweo kd umafuna kutchuka kpn udindo aaaaa machende ako bwji umandipsetsa mtim kwbri

    • @user-qn9vc8em6z
      @user-qn9vc8em6z Před 2 dny

      Inu ingokhalan chete ....monga mmene akuendela malawiyu zikukukomeran ......

  • @mwayimmbanga4011
    @mwayimmbanga4011 Před 2 dny

    Machine

  • @chrisgremu740
    @chrisgremu740 Před 2 dny

    Mukunya inuuu

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 2 dny +1

    I trust you mr DC

  • @JhdaLifi-vu9sd
    @JhdaLifi-vu9sd Před 2 dny

    Ddddddddddddddddccccccccccccccccccccc

  • @SellahBanda-cg9kh
    @SellahBanda-cg9kh Před 2 dny

    The Dccccccccccccc

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Před 2 dny

    Tili pambuyo panu DC born kalindo more fire 🙏🙏🙏🙏🙏🙏