Limpopo vuuu! phaaa! wafikatu Ntanyiwa madzulo omwe ano timve zimene wasokola lero muja achitila

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 3. 07. 2024

Komentáře • 103

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před 3 dny +5

    Ntanyiwa iweyo ndiwe mtunda 😂😂😂😂😂😂😂 khomboledi ntanyiwa timakunyadila kwambili
    Anthu amenewo akawaponye munyanja yang'ona muja sitikuwafunaso ayi 😂😂😂😂

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c Před 3 dny +3

    Good comrade zawo izo ifeee amalawi tooonse ambiri tiri pambuyo pa DPP and APM 2025 BOMA ZINAZO AI AKAGWERE

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi Před 3 dny +2

    Akulamulira dziko koma mozuzika...no peace 😅😅😅😅

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma Před 3 dny +3

    Aaa serious comrade,big amen Mulungu akutimva ma pemphero athu sangatiphere Chilima ulerei

  • @janemvubu7750
    @janemvubu7750 Před 3 dny +3

    Mulungu simunthu achiziwe chimenecho alangidwe amenewo

  • @LunnahMtambo
    @LunnahMtambo Před 3 dny +2

    Comred agwa nayo amenewo,mulungu Ali mbali Yako ,ambuye akutetezereni kuli kose komwe muli ,mumatiyimilira

  • @MoffatChiwaya-i5k
    @MoffatChiwaya-i5k Před 2 dny

    Good job continue informing the nation,we are proud of you

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona Před 3 dny +1

    Next will be Zikhale Ng'oma followed by Kumkuyu 😂😂😂 evil men,auzeni Mr. Mtanyiwa.

  • @user-zm9nl8zn2b
    @user-zm9nl8zn2b Před 3 dny +1

    Love you all comrade Ntanyiwa n Bakili Muluzi tv watching frm vanderbijl park

  • @AlaniWaludza
    @AlaniWaludza Před 3 dny +1

    Nice job, god bless you mtanyiwa

  • @NizigiyimanaChantal-c2p
    @NizigiyimanaChantal-c2p Před 3 dny +1

    May God continue bless you mtanyiwa

  • @YusuJames
    @YusuJames Před 3 dny +1

    Amangidwe bac osawasekeleratso naye chakwera atule udindo bans sitikufuna kmatso sindimamuopa

  • @CaptainNyenga
    @CaptainNyenga Před 2 dny

    What a wonderful job mtanyiwa 😂

  • @AliKaukutu-bo7cx
    @AliKaukutu-bo7cx Před 3 dny +1

    All the way from balak but am in cape town mumatha amtanyiwa

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Před 3 dny +1

    Zonse ziwoneka. Mulungu simunthu.

  • @user-ks3uw8gj8h
    @user-ks3uw8gj8h Před 2 dny

    Akatero Mulungu wanthu wayamba kuvumbulutsa poyera, koma wina ayaluka sumungamawononge ma tax anthu ndi za Zii, tingopita ku nkhalango ya ku state house komweko

  • @CharlesKachipanda-jz9jv
    @CharlesKachipanda-jz9jv Před 3 dny +1

    GOD IS GOOD ALL THE TIME

  • @InnocentPotani-lv1on
    @InnocentPotani-lv1on Před 3 dny +7

    following from blantyre chilobwe,proud of you comrade

  • @user-oy6dl1pv9e
    @user-oy6dl1pv9e Před 2 dny

    Mmankhwana inuyoooo❤ MULUNGU adzikudalitsani ndikukutetezelani
    Emeeeniii

  • @lottiempata2487
    @lottiempata2487 Před 3 dny +1

    😂😂😂😂 , there's no secret under the earth 🌎

  • @SeephyMfaume
    @SeephyMfaume Před 3 dny +2

    Mr zikhale ng'oma Mboli yawo mozesi kunkuyu pamtumbo Pake 🖕

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Před 2 dny

    Watching from Blantyre God bless you bwana mtanyiwa

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa Před 3 dny

    ❤❤❤❤ from johannesburg

  • @fedson2050
    @fedson2050 Před 3 dny

    Mbambande Mtanyiwa inuso pitilizani kutivetsa kukoma, mpaka chirungamo chitapezeka chirungamo mini Mmalawi

  • @MphatsoMkanda-1616
    @MphatsoMkanda-1616 Před 3 dny

    All the way from Pretoria South Africa 😂😂😂😂😂😂 Zomba boy

  • @ThokozaniMaulana-oi5hz
    @ThokozaniMaulana-oi5hz Před 3 dny +1

    Iphani onsewon

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Před 2 dny

    Proud of you comrade 🔥🔥🔥🔥

  • @IgnatiusMbewe-z2f
    @IgnatiusMbewe-z2f Před dnem

    One comred nice job pa limpopo fm

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge Před 2 dny

    Mmmmmmmh 🙌🙌🙌 😢😢😢😢😢 Malawi R.I.P SKC 💔😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @FrankHaruni
    @FrankHaruni Před 2 dny

    Omwe amakaikila kuti tanyiwa amayakhula dzongofuna kutchuka akhulupililano nde yes wadzathekabwanji😅😅😅😅😅

  • @zaitwazaitwa941
    @zaitwazaitwa941 Před 3 dny

    Umakwana iweyo mtanyuwa❤❤❤❤❤😂😂😂😂😂😂😂

  • @amonkaunda1930
    @amonkaunda1930 Před 2 dny

    Unless evidence is provided I don't believe anything on social media

  • @HameedSaleem-o4v
    @HameedSaleem-o4v Před dnem

    All the best comred

  • @Jamesmwale-iz4ri
    @Jamesmwale-iz4ri Před 3 dny

    Proud you comrade

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 Před 3 dny

    Koma guys comrad ntanyiwa ndi ndi galu ndithu kuwagwira yekha? kkkkkk limpopo fm i ❤ limpopo fm with bon kalindo

  • @janemanyamba7201
    @janemanyamba7201 Před 2 dny

    Following from ndilande pa boma ❤❤❤❤

  • @user-re9cu5tb3y
    @user-re9cu5tb3y Před 2 dny

    A ntanyiwa pamenepa mupha mbalame ziwiri ndi mwala umodzi,ngati agwidwadi pezani njira yoti aulule nzonse tatopa ndikudikira chilungamo cha chilima

  • @AndrewMagombo
    @AndrewMagombo Před 2 dny

    Mesa ife tudalira inu n TV bakili❤❤❤

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi Před 3 dny

    ❤❤❤❤

  • @DanielTwiscombewe
    @DanielTwiscombewe Před 2 dny

    Makwana boss

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Před 3 dny

    🔥🔥🔥🔥🔥

  • @KENETHMAJASA-ud5ee
    @KENETHMAJASA-ud5ee Před 2 dny

    Amen!

  • @GeorgeSmart-wp9qp
    @GeorgeSmart-wp9qp Před 3 dny

    Thanks God

  • @GanizaniManyamba-i6q
    @GanizaniManyamba-i6q Před 3 dny

    Ntanyiwa iweyo ndikatundu 😢😢

  • @Macnovas-dp7pj
    @Macnovas-dp7pj Před 2 dny

    More 🔥 comrade 😅😂

  • @henrynsiku2108
    @henrynsiku2108 Před 3 dny

    Comrade remember my yesterday 's comment.

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před dnem

    MUWAUZE KUTI A POLICE ASAWASIYE AWAMANGE MPAKA 2030

  • @MecyMalothi
    @MecyMalothi Před 3 dny

    Comrade Ntanyiwa umakwana

  • @charlesmataka1700
    @charlesmataka1700 Před 2 dny

    Umakwana mtanyiwa 😂😂😂😂

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 2 dny

    Chakwera ndi dzakumwa mazila😢

  • @AlliSaiti
    @AlliSaiti Před 3 dny

    Koma MCP guys aaah

  • @SymonYohane-i5q
    @SymonYohane-i5q Před 2 dny

    ❤🎉🎉🎉

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r Před 2 dny

    Kkkkk awa chita bwino zina umango wona waziyamba umayamba yoti sunga imarize azithaima amenewo

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo Před 2 dny

    Well done

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Před 2 dny

    Mai yolamu mavuzi anu sure 😢

  • @PatrickKennith
    @PatrickKennith Před 3 dny

    Mulungu amasamala anthu ake komanso amalanga muchisisi mulungu sazakhala Chete pachilungamo.

  • @user-qd8cu3sl4w
    @user-qd8cu3sl4w Před 2 dny

    Zaboza ayi man,we need some proof of your stories,anthu anapenya pano

  • @Bonisiwentamo
    @Bonisiwentamo Před 3 dny

    😂Aphedwe amenewo kapena omwe atuma wo ayimbidwe milandu pompano

  • @wilsonali7890
    @wilsonali7890 Před 2 dny

    😂😂😂😂Kodi maRwandis sachedwa kuwulula kkkk

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Před 2 dny

    Azituma anawawo mwina ndipanene aziva kuwawa

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge Před 2 dny

    Live 🇰🇪🇰🇪💪💪💪💪💪💪

  • @arnoldkamoto2968
    @arnoldkamoto2968 Před 3 dny

    Afaileni poison waoyo amuyese ngati amagwira ntchito

  • @ZexGabadson
    @ZexGabadson Před 2 dny

    Yah ney

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg Před 2 dny

    😂😂😂😂😂 Yomweyo chingawa Chakweraaaa
    Awatu ndi ma introduction chabeeee ifika turn yakooooo wina azinkhweza yekha mwazi ukufuula nchipululu ndipo nonse you will follow Chilima one by one kkkkkkkkkk
    Pemphero osazaliphweketsa and we still praying until mwini film awonekere poyeraaaaa
    Zikutiwawa tisamakhare mwa mantha dziko lomwe mulungu anatipatsa 😂😂😂😂😂😂
    Anthanyiwa God is with you

  • @ShakilahMbwanaa
    @ShakilahMbwanaa Před 3 dny

    Ntanyiwa inuyo ndi one

  • @AndileyaMkandawire-x8r

    Akowapha oseo ndi zomwe anyamulazo

  • @kelvindickson
    @kelvindickson Před 2 dny

    Mtanyiwa iwe ndi amuna

  • @TawongaGSMwale-cc2vm
    @TawongaGSMwale-cc2vm Před 2 dny

    😂😂😂😂😂 eti Kut muzayese mwayi 😂😂😂😂

  • @NumbDee
    @NumbDee Před 3 dny

    Kodi mmesa mwati mmodzi ndi mmalawi.ndiye Ambbassy ikayakhula ndi iyeyo 3stop

  • @DanielTwiscombewe
    @DanielTwiscombewe Před 2 dny

    Nde yake ntanyiwa

  • @user-yn6vf2ci3h
    @user-yn6vf2ci3h Před 2 dny

    Tipulumuseni,chauta alipasogolo panu.

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Před 2 dny

    Komaso chakwera utikwana

  • @MustapherLino
    @MustapherLino Před 3 dny

    Chakwera ndi galu wachabe chabe

  • @user-up8dr9jr8b
    @user-up8dr9jr8b Před 2 dny

    Viva tanyiwa

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 3 dny

    Kkkkkkk Mulungu alipo kunja kuno chitani manyazi boma la mcp

  • @user-vu4cz1mt4f
    @user-vu4cz1mt4f Před 3 dny

    Kod mwadzi sunawakwane anthuwa et

  • @giftsululu4274
    @giftsululu4274 Před 2 dny

    NKhamba kamwa zatitopetsa antchuren maina

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga Před 3 dny

    zabodza lzi uzinamiza ana kumakhara kusowa zochitatu mmalo mogwira ma ganyu uko bize ndi ndare

  • @TheolianBanda
    @TheolianBanda Před 2 dny

    Tikudikilabe ma report a imfa ya chilima

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w Před 2 dny

    Nonsense

  • @DanielLekitala
    @DanielLekitala Před 2 dny

    Antanhiwa Mili boooooo

  • @mkandawirem610
    @mkandawirem610 Před 2 dny

    Mbambande

  • @MaggieKaufa
    @MaggieKaufa Před 3 dny

    Mumatha inuyo

  • @AndrewEphraim-cs5es
    @AndrewEphraim-cs5es Před 3 dny +2

    What goes around comes around listening from kzn umakhwana mtanyiwa

  • @WilliamKapungu
    @WilliamKapungu Před 3 dny +2

    Luv you comrade ntanyiwa ❤❤❤❤❤❤❤
    FROM Durban

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona Před 3 dny

    Tchimo limazunza .
    Yense Woyipayo akusowatu Mtendere. Kulephera kugona Koma ziliko liko.
    Muli ngati abwino Anthu Adyera. Evil men.

  • @SeephyMfaume
    @SeephyMfaume Před 3 dny +1

    Mr zikhale ng'oma Mboli yawo mozesi kunkuyu pamtumbo Pake 🖕

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před dnem

    MUWAUZE KUTI A POLICE ASAWASIYE AWAMANGE MPAKA 2030

  • @arnoldkamoto2968
    @arnoldkamoto2968 Před 3 dny

    Afaileni poison waoyo amuyese ngati amagwira ntchito

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga Před 3 dny

    botswana yake lti matha okhaokhawo dziko la luwandalake litilo anthu akakhare bize kusaka lweyo aaaaha

  • @SeephyMfaume
    @SeephyMfaume Před 3 dny

    Mr zikhale ng'oma Mboli yawo mozesi kunkuyu pamtumbo Pake 🖕

  • @SeephyMfaume
    @SeephyMfaume Před 3 dny

    Mr zikhale ng'oma Mboli yawo mozesi kunkuyu pamtumbo Pake 🖕

  • @SeephyMfaume
    @SeephyMfaume Před 3 dny

    Mr zikhale ng'oma Mboli yawo mozesi kunkuyu pamtumbo Pake 🖕

  • @SeephyMfaume
    @SeephyMfaume Před 3 dny

    Mr zikhale ng'oma Mboli yawo mozesi kunkuyu pamtumbo Pake 🖕