Koma ma decision makers particularly politicians amamva zimenezi? Uthenga nde ndikwabwino and straight forward. Vuto aliyense angofuna iye ndi abale ake akamachoka, zawo zikhale ziyenda. ie alibe chikondi kwa a malawi koma kuzikonda
😂😂😂😂😂😂😂..ati sitidya kwaaaanu eishhhh anyamata anakalowa mu studio ndi mkwiyoo awa...Iman moona mtima ndimopanda mantha ngat Mikaya wa mu Bible yemwe anasutsana ndi mafumu ochuluka pozindikila kut zoyankhula zake ndizo zinali zoona
Malawi has suffered leaders who kept us in the dark for years. Without water. Leaders that store n cut all rail lines to replace it with mangochi based vehicles. The nation suffered from leaders without teeth who paralized universities for almost a year. If asked, they would go on holiday in the USA. Now, are we promoting such leaders to come back? This is an opposition forum. Not a program that talks reality. None bias reporting is what this nation needs.
Sometimes it's good to understand the message properly,who is celebrating here? If someone is failing to run the affairs of the country,how does that concern me?,he has 23 advisors,What is their job?what are all the advisors doing, this is high level filth,Justice hurts.
That's why they assassinated malemu mnyamata woganiza boo Adamupha KS and they think we have mastered the crime and they will not be able to be caught and arrested.
❤❤❤iyiyi mwanena zogwila mtima lero mwaonetsa u independent wa times keep it up
Ulamuliro wa nkhanza inde pano school fees anthu tikulephera kulipira ndiye Ana aphunzire motan mmmm ambuye atithandize
Zoonadi
For the first time Malawi can see great roads not just miyala ya madziko.
I pray that Malawi wakes up.
We should wake up n balance our forums
Kuyakhula mopanda mantha. Komaso mwaphawi zofunikira kwaose amalawi pabwino mkuyamikirana. Poipapo dzuzurani, rangizani akapanda kumva arekeni!!!!🎉
Iyiyi nde yandifikapo ndithu big up Hot current 💪💪
Tisinthe flag yanthu ilindi mintundu yoyipa ntunduwake mmm ndiwachabe mutundu ya bendera yanthu imagwilitsidwa nthawizabili ndizinthu zakumidima panayenela kuyisintha bas
Koma ndipo Simukunama. Taonani flag ya Kenya 🇰🇪 ndi ya malawi 🇲🇼 sizisiyana kwenikweni koma mmene zinthu zilili ku Kenya ndi kuno nzonvetsa chisoni
Massive analysis this is good idea and solution zoonad katangale akhoza kutha zkufunika azitsogoleri odana ndizopusa that's right guys.
Tidakhala ndi atsogoleri ophunzira angapo koma sitidatukike pa cbuma ndi zitukuko ndiye tidzayese mtsogoleri wa form 4
Mumapanga ma demo abwino not like born kalindo, thanx TTV
Apa ponkhapa mwawalakhulila amalawi🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Koma ma decision makers particularly politicians amamva zimenezi? Uthenga nde ndikwabwino and straight forward.
Vuto aliyense angofuna iye ndi abale ake akamachoka, zawo zikhale ziyenda. ie alibe chikondi kwa a malawi koma kuzikonda
Apankunku ndi ndevi zamwayi mwayamba bho next time muzapose apa apa ndakayika kuti mudadya chikondamoyo we love you lots ❤
Suzumilani mu MRA muwone zomwe zikuchitika especially in a hot activities eg boarders kkkk
U guys u talking the really truth
Anyamata inu get ready in 2025 boma lina likubwerari tikonze malawi you are good indeed.
😂😂😂😂😂😂😂..ati sitidya kwaaaanu eishhhh anyamata anakalowa mu studio ndi mkwiyoo awa...Iman moona mtima ndimopanda mantha ngat Mikaya wa mu Bible yemwe anasutsana ndi mafumu ochuluka pozindikila kut zoyankhula zake ndizo zinali zoona
Mwauzeso kuti akugulileni track trauser kuti yikhale top and down
😢 Apa palibezoti bola baja bandani ni same thing those bantu
Mmoziyi ndamene amalakwisa program amakonda kuwatchinga azinzakewo kuti asamasuke
Amati mwanapiye anawonera make kunyera munyumba nde tiphe mayi wakeyooooo
Tikadali njira, sindazione munthu wa zaka 60 akukakamira kuyamwa bere la amache. Mkakawo udakoma chotani.
impressive guys Ndevu za mwai umaitha ndi nzako yo 🤞
Bravo guys mumakwana
MWALANKHULATU MWAMPHAMVU RELO NDIYAMIKE KWAMBIRI.
Koma a Brown mpinganjira mpaka liti osavomeleza kuti Mulungu sanafune kuti akhale president iiiii
Nelson Nelson 🤣🤣ukumaika ma flash et
Zoti inali times television yooneledwa ndi anthu ambiri pano ndi history chabe hahaha ndaonela ma viewers ndi kuchuluka kwa ndemanga
Ambiri amaonela but they reserve their comments but ndawakonda ma guys
❤😂😢 nkhani yagona pa utsogoleli, kwa anthu amene ukuvoteledwao, tinawavotela pachifukwa chiani?😢 Kd tinawavotela chifukwa choti mwaiwo tikuonamo muzimu wa utsogoleli? Kapena chifukwa choti tikumadyanawo? Apa tiwonepo apa, kwa Ife ngati ovota. Kwa iwo amene akhalapo atsogoleli, ndi iwo amene ali atsogoleli, Asanapange chiganizo chofuna kukhala mtsogoleli anayamba azifufuza okha kuti mwaiwo yilimo mphatso ya utsogoleli kapena ayi? Akulu akulu tisaname apa onse amene tawavotela awa ndi amene tikuwavotela awa akungogweramo chifukwa chokakamizidwa ndi anthu ane amene ali atidyenawo, chifukwa cha mzimu uwu uwu, woti tikamuona munthu ndikumuwuza kuti km inuyo kuti mukhale mtsogoleli anthu akhoza kukuvotelani zaziiii, mawa olira ndifetomwe, muMalawi alimo anthu anzelu ophunzira aliso ndi utsogoleli mkatimwao km chifukwa choti ndi osauka palibe munthu amene angawa votele, pano ndi izi zaka 60+ chifukwa chokonda kusankha bakawalala aba tilindicha zero chosangalasa ndichani kumuvotela munthu maba akukufiya pahoroh 😂 kpn kukumanga ndikukakusekera inside kirikiri😮
Ine nde kumalawi kwandikwana😭😭😭😭😭😭 thupi lonse likumachita kuwawa ndikuganiza
Dear bwelani mbalikuno bas
@@user-ec3xh4pc6t kutiko kumeneko saka bag yanga ndapakililatu
I like the conversation
Guys mwasiya kugawa ma sweet ulemu wanu. Timayesa nanuso akudyesani chibansi
Mmmm Zikhale Ng'oma nawoso akufuna u Vice President ku MCP? Mmmm awa ai body structure
Kkkkkkk 🔥🔥
Hahahaha koma iyiyi nde ndiyong'alura kuyipatu kkkkkkk
Hahahaha akuti 👇
"Sitidya kwanu!" 😅😅😅😅
Eeeeee anyamata relo mwatokota kkkkkk muli bho kwambiri mwaveka ❤❤❤
Malawi has suffered leaders who kept us in the dark for years. Without water. Leaders that store n cut all rail lines to replace it with mangochi based vehicles.
The nation suffered from leaders without teeth who paralized universities for almost a year. If asked, they would go on holiday in the USA. Now, are we promoting such leaders to come back?
This is an opposition forum. Not a program that talks reality.
None bias reporting is what this nation needs.
Zoonadi my brothers osaopa osapepesa zaka 4 palibe chanzeru olo chimodzi chimene achita awa a Tonse
Keep it up times musalore akupatseni ma banz mudzitiimilira chonchi
Za katangalezi tinaluza munthu wofunikira kwambiri amene anali ndi masomphenya pa nkhani iyi....SKC 😢 tidzamlila mpaka kale...koma adaferanji?
Brian alikuti Kodi? Amabebetsa
To say the fact ma guys awawa amayankhula zoona koma kumtunda ku mmm
Iyi koma mwang,alulandi makosana abwana kutundako azizifusa makamaka achekwela ndimbava ndifukwa akopa ACB
Iyi ndye hot current yen yen 🔥🔥🔥
Koma ndiye mwanena mosanyengeleratu
Nice message
Ife timamva nanu kukoma chifukwa mumayankhula chilungamo ,ndipo nthawi ya program yanuyo muionjezele mabwana
Musogoleri akawoneka wa good future kumapha basi
Yeah! This is hot for sure.
The curtain in the temple is about to be torn, we are waiting eagerly
The problem of you and us as Malawians we always celebrate when someone fail, this is very bad and ugly kkkkkk
Sometimes it's good to understand the message properly,who is celebrating here? If someone is failing to run the affairs of the country,how does that concern me?,he has 23 advisors,What is their job?what are all the advisors doing, this is high level filth,Justice hurts.
@@user-si7po9sd5iexactly tell this person the truth
@@EdwinMakwangwalait’s not celebrating them. It’s celebration that the truth about them will be coming out
Mmmmm tiyeni ticheze bwino
Number one brothers
Well spoken
Kma iyiyi mwang'alula🥳
Chanzelu apha chilima+anthu 8 kumphatizapo kasambala
Why big people wear tinted sun glasses
Ku painter eti?
That's why they assassinated malemu mnyamata woganiza boo Adamupha KS and they think we have mastered the crime and they will not be able to be caught and arrested.
Mwalakhulako zazerutu, mukamadya ma bazi guys times izakhala Ngati MBC yoonera achakwera okha
Ati sitidya kwanu kmatu Mr wonder
Watopera akanganya amenewa.
Vuto lolandililatu zanu tinkhope tanuto nditamanyaziii😢
Guys mumatha keep it up
Nde mwati amagwila pati anyamata aja
Koma zikhale ng'omayo nde ayi aaaaa
China chake kuseliku nkumati ndikupeleza 7 kwa ten mfiti 😢
If yuo steal with sorrounded one day all will 😂😂
Aaah koma ma boys inuyo mumakwana 😅
Komadi ma junior police akuvutika ,srs
😂😂😂😂😂 apa mwatha manthatu
Lelotu anyamata mwawalankhulila amalawi pitilizani
Every day kusokesa uniform ya police zovuta zedi
Ayi palibe chabwino kulibwino undindo asiyile wena
Brilliant idea 💡
Mukamatero tililimodzi pamenepo
anyamata musamale muphedwatu mcp sifuna anthu oyankhula chilungamo
Ndakutayilani kamtengo guys
Mmakwana uzo ndi mzao
Iyayi bomali linaziyipisila kale
Koma kumeneko
Abodza awa sanena zoona komaso oopa kwabasi bwanji analephela kutuuza zoona nthawi ya maliro anyamata wanthu skc timakubukila zbs isakudziwa ndalama pa imfa ya bingu atolankhani amakwela mu tengo kuti anene zoona Koma pano mmmmmmmmmma radio ake cabbage oneka oliba koma mkati madzi okhaokha
Ulemu
Mtsogoleri yekhayo adali ndi kuthekera koteroko adali Akamuna a Bingu seconded by Akamuna Dr Saulosi
Exactly!
Thanks you 2 guys there,Komano kod mmesa achakwera anatiuza Kut adzamanga aliyense ochita katangale m'boma lawo? Ndy chilowele amenebanamuona mkumanga ndi achilima okha? Plz plz t mkwabwino kusangalatsa Mulungu than munthu mzako
😂😂😂😂
Zofunika osambisala munda wa mtedza timadabwatu koma apa mwabwera
Mumakwana gayez
Hello Guys. Please continue hitting the nail on the head.
More fire gentlemen, Malawi wathu ndiyemweyu,Osaopa kuzilangiza nkhutukumve ndi mbala zimenezi
Chakwera must go before September pls God is looking for us
bora bingu ndi ng'ono wake pta osati uyuyu chakwerayu ndimbzi
Chilungamo chimamasula, azibambo inuyo mulungu azikudalisani ndikutetezani mukugwila tchito, from cape town
😂😂😂😂😂😂😂😂 ndemvu zamwayi apolice akumadula zikhadabo atavala nsapato kkkkkkkkkk
😂😂😂😂😂😂😂 uyu ndiwamwano ati kuwenga zikhadabo autavala nsapato
@@CalvinThomson-ys5zf kkkkkkkkk akutero kuli kutha kwa nsapato kkkk
Apapa ndiye mwabwera madolo ulemu wanu that is democracy
Pitilizani kumatiyakhulira chilungamo pa hot current
Pamene apolisi akusowa nsapato nawo ma pensioners sakulandira ndalama zawo ena mpaka zaka panopa katangale mbona wa chulukadi
Mumapanga ma demo abwino not like born kalindo, thanx TTV❤
Mumapanga ma demo abwino not like born kalindo, thanx TTV
U guys u talking the really truth
Matha
Koma kumeneko
Mumapanga ma demo abwino not like born kalindo, thanx TTV
Vuto lanu lopanga compare anthu awiri osiya, zolinga zosiya, koma kulephela kusiyanitsa.
Mumapanga ma demo abwino not like born kalindo, thanx TTV