ABITI WILLIAM DAWOOD kusosombetsa NEC ya UTM...zimvere mtolo kachilungamo kalimo umu👐👐👐

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 28. 08. 2024

Komentáře • 82

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před měsícem +5

    Chilima was a threat, that's why panopa MCP yayamba kumasuka, u can even see kusankhidwa kwa Micheal Usi akusangalala kwambiri.

  • @matiasncalaila4003
    @matiasncalaila4003 Před měsícem +4

    Watching from Mozambique, ln fact Our SADC countries are in chaotic. Presidentes and ministers in SADC are different in coulors but are the one pessonal. Hospitals and Schools in their own countries always become useless when they are on top they tataly forget their background. My dear Sister , You are speaking and talking about the things that also is happening in my country. We need prayers for SADC leadership.

    • @NthambiInvestment
      @NthambiInvestment Před měsícem

      Amati nkhondo ndi anasi judas sikaliyoti anapeleka Yesu,, chilima anapelekedwa ndi omuzungulila koma ambuye salakwisa amalola zowawa zichitike kuti ukulu wake uonekele may his soul of skc Rsst in Peace

  • @williamdaka79
    @williamdaka79 Před měsícem +2

    Thanks good message,watching from Jeneva Switzerland 🇨🇭

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 Před měsícem +6

    Ya mantha ndi yowona. Amalawi tapusadi kugoyakhula uva uli ndi roya. Aaaa zowona tiwope kufa Ngati alipo wamuyaya bwanji

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před měsícem +5

    Ine ndiye sindiopa waudindo aliyense Chakwera anapha CHILIMA

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Před měsícem

      Chakwera.Zikhale Ng'oma ndi Kunkuyu anapha Chilima.

  • @vivianmkwate8536
    @vivianmkwate8536 Před měsícem

    keep it up Abiti 👏🏾👏🏾👏🏾

  • @user-gd2kl1fx1q
    @user-gd2kl1fx1q Před měsícem +1

    Aunt God be with you, with ur wise words I wish ku chipan chathuchi ku takhala anthu 10 ngat inu please let's accomplish what our president started for his soul to continue resting in peace though the pain still exist bt God is all over tsogolo lowala lija litheka in jesus name

  • @MilikaKilion-tn1bn
    @MilikaKilion-tn1bn Před měsícem +3

    Ifa ya chilima usi alimomo asamatinamize kufupika ngati ntchimba wa nkhoswe

  • @nafejonga972
    @nafejonga972 Před měsícem +3

    My fellow nurse wowww😂😂😂

  • @nafejonga972
    @nafejonga972 Před měsícem +2

    I love you mama😢😢

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Před měsícem +1

    Mwayankhula mama ambuye akudalitseni..

  • @nafejonga972
    @nafejonga972 Před měsícem +1

    I have started loving you too, am a utm member too

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před měsícem +2

    It's so sad ndege kugwa mpaka the whole Day no results,

  • @HameedahMasambuka
    @HameedahMasambuka Před měsícem

    Mukhalike mama l love you ❤

  • @coastersRob
    @coastersRob Před měsícem +2

    Ayi muziti kudambwe airport

  • @AlbertDuke-of9nn
    @AlbertDuke-of9nn Před měsícem +2

    kuyakhura kwabwanji uku😂😂😂😂😂😂

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Před měsícem +2

    Ccta ulindizeru zoveka ❤

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 Před měsícem +3

    Powerful speech

  • @ManyambaInnocent-x8i
    @ManyambaInnocent-x8i Před měsícem +2

    Chilungamo sichipotsa apa mkadzi wayankhula moveka

  • @user-ui4ux5kc8d
    @user-ui4ux5kc8d Před měsícem +3

    Chilungamo mchoti amalawi. Tiri ndimantha ndipo mantha amenewa ali ngakhale ku tsogolo komweku mmalo modzimenyera mkhondo tokha timadzifinya tokha ndithu ndiye Mai viuseni kwambiri

  • @peterjoshua2595
    @peterjoshua2595 Před měsícem +1

    What a emotional ending malawi sad

  • @wonganikaunda
    @wonganikaunda Před měsícem

    More fire mum

  • @tarkuesamson8838
    @tarkuesamson8838 Před měsícem

    Amayiwa ndiosokoneza zedi ndakhala ndikwapangako follow, inu ndiena mumanyoza kwambiri kunyoza Author Mutharika munapangitsa astray Amalawi kuvotela Mcp lero ndiizi!palibe chanzeru mungatiuze inu.

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před měsícem +1

    Mama.uyu amadziwa kubeleka nkowawa ndithu akudziwa kumwalira koti amadwala ndi kwina koma kumwalira kwa Chilima kunawaw

  • @WanangwaTauzie
    @WanangwaTauzie Před měsícem

    Ndakumvani mama

  • @Leonilde-wn4le
    @Leonilde-wn4le Před měsícem

    Fazem a escolha certa,no dia das eleições

  • @MaeCuinhane-gq7ub
    @MaeCuinhane-gq7ub Před měsícem

    mom ulemu wanu, mkazi olimba mtima komanso wachilungamo ambuye azikudalitsa komanso apitilize kukupatsani mzeru

  • @isaacchipatala1618
    @isaacchipatala1618 Před měsícem +1

    Very truly sisi

  • @mwaiwaobanda2691
    @mwaiwaobanda2691 Před měsícem +1

    Ine nde ndinalidi supporter wa skc ....osati wa utm...mama mwandigwira mtima ndi mau awa....ngati kuli kopuma pumani mwa Ambuye bwana skc..😭😭

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 Před měsícem +1

    Chilima kusamva ,nanunso mungobwerera ku dpp otherwise mutha ngati makatani

  • @user-ee8og2mb5r
    @user-ee8og2mb5r Před měsícem +2

    Wacthing from zambia madam

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Před měsícem

    Chakwela the killer 💔

  • @noliachelewani2208
    @noliachelewani2208 Před měsícem +1

    Kodi mamawa Ali Kuti Apapa Ali NDI nzelu kwabasi yooh

  • @user-zp8hv7bq3o
    @user-zp8hv7bq3o Před měsícem +1

    A chemwa muku bandula bwino, a Malawi ndife a Tulo, Mantha ndi uchitsiru. Pitirizani kutilankhulira, zikomo mayi athu.

  • @jameshuwanzulu
    @jameshuwanzulu Před měsícem +2

    Akunene zoona ka

  • @BandaSpeak-bg3ev
    @BandaSpeak-bg3ev Před měsícem +2

    Listening madam

  • @CorneliousKaliat-od3un
    @CorneliousKaliat-od3un Před měsícem +1

    Khani ndiyoona mama

  • @lame8
    @lame8 Před měsícem +1

    Komatu mavutowa anachokela iye mwini alimoyo. Ndikumatha kuona zinazake zimamjchiyikila amaopsezedwa munthu uja 😢 koma zambiri akuzidziwa miniwake. Kalindo anayesetsa kumuuza chokako chokako zinakanika. Anayankhula za mngwilizano anamuyankha popo popo a mcp kuti sakuzidziwa 😢 nanga manganya ndindani kuti asaopsezedwe muzitionela patali guys.

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před měsícem +1

    Nthawi yakwana yokha anthu a dyera muaone ku UTM omwe akufuna kugulitsa chipani chanu walira mwana mkazi kuchililira chipani chake cha UTM zili kwa aKaliat, Fredox a Jawala ndi ena kulandira ndalama kuchokera kwa YUDASI MANGANYA

  • @isaacchipatala1618
    @isaacchipatala1618 Před měsícem +2

    MCP blood

  • @user-ky2fs3zr8y
    @user-ky2fs3zr8y Před měsícem

    Manese chitedze mdala mwakongolako ku USA.ubwera liti kwaSafarao kkkkkk

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před měsícem

    Ulemu wanu mama

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 Před měsícem +2

    Yomweyo

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Před měsícem

    Anapha Sadik Mia kunamira covid

  • @user-zm9nl8zn2b
    @user-zm9nl8zn2b Před měsícem +1

    Komatu iwe nabanda iwe yaaaa

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Před měsícem

    Anthu amvere interview ya Brian Banda ndi Manganya

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Před měsícem +1

    Zowonadi matha kutenga za chipani cha uku kupiti nazo uku. Mulungu awaranga onse.

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Před měsícem +1

    Eeee koma or a Patricia kaliyati akanangoganiza or kulingalira ngat iweyo mama,mmm anthu ndiye anawakonda ndipo akanaima popanda opikisana nawo,koma akuoneka kut ayamba kale kudya bans.koma nzomvesa chison anthu anali ndi hope pa mai wa,now amalawi ndiamasiye pano.ngatbndikunama tamverani speach yao yapamaliro a Lucius Banda.nokha muziyankha popanda fuso.

  • @user-mx7oj1vx3l
    @user-mx7oj1vx3l Před měsícem

    Every face tells a story mukawawona anthu powapatsa ma udindo,ngati wothandiza pomwe bolanso mfiti nthawi Zina ingakuwuze Kuti ndikuloza koma yawa ankawoneka ngakhale interview yawo inali pa dziwe TV two weeks back ,lilime lawo lidawonetsa Kuti mhu! ngogulitsana yawa😢😞

  • @wonganimoyoh2535
    @wonganimoyoh2535 Před měsícem

    wise saying sister

  • @user-rm2xv8ys1i
    @user-rm2xv8ys1i Před měsícem +1

    ❤❤❤❤❤

  • @RobertMvina
    @RobertMvina Před měsícem

    Tiuzeni titani

  • @MakandeMpambalika
    @MakandeMpambalika Před měsícem

    Ndikumasulani yes go deeper mum

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon Před měsícem

    Mau amphamvu mama

  • @clocksigns9755
    @clocksigns9755 Před měsícem

    Nambo niwakutakata

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 Před měsícem +1

    Wasowa chokamba uyu. Ngati anthu akufalitsa zabodza aziwaombera mmanja? Undunawo akanapatsa iwe ungakane?

  • @MakandeMpambalika
    @MakandeMpambalika Před měsícem

    Mmm ndiwe mzimayi wochenjera ka bandle kanga kathela pompo

  • @user-yk5qd6sk8e
    @user-yk5qd6sk8e Před měsícem

    usi akuymila kabula

  • @GraciamChopih
    @GraciamChopih Před měsícem

    Chemwali mwalankhuladi zoona zeni zeni,zonse mwalankhulazo palibe chomwe mwalakwitsapo bt chilungamo basi😂😂😂

  • @ritchardchakuma5725
    @ritchardchakuma5725 Před měsícem

    Mama Uyo gwenembe Uyu mumusiye timuwonela 2025 tasanduka zisilu Koma mufufuze kuafilika kose ndife zisilu uphawi njala kukwala kwazithu gwenembe chakwera maikousi mutayeni ndiwamisala bambo asikono mutunjasiugwila

  • @Leonilde-wn4le
    @Leonilde-wn4le Před měsícem

    Amalawi mantha achuluka kwambili,chilima wafera dziko😢

  • @AndrewInnocent-he8gs
    @AndrewInnocent-he8gs Před měsícem +1

    Fasefase yomweyo

  • @user-be1zt6xl3f
    @user-be1zt6xl3f Před měsícem

    Mayakhura mau abwino kwambiri sister

  • @TonyOkoibedi
    @TonyOkoibedi Před měsícem +1

    Mama ukukambazo ndizoona ndikukutsatila kuno Ku South Africa

  • @AmaliYahaya
    @AmaliYahaya Před měsícem +1

    😢😢😢😢😢

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před měsícem +2

    A ccta inu muli ndi zeru kwabasi mwina pa akazi akumalawi azeru inu muli panambala yabwino. Ndege ija si imafunika anthu ena ochokera kunja kuzafufuza ayi. Even mwana wa standard one kuti afufuze za ndege ija atha kupeza kuti boma ndilolakwa vuto Malawi mantha komaso kutenga atsogoleri ngati ndi Mulungu. Pazina kumalawi tinakula molakwika.
    Manganya tinanena kale kuti si wa utm.
    Manganya ali mu cabinet ya president chilima bwana wake wasowa 10 o'clock analola bwanji kuti president awuze mutundu wa Malawi 11 o'clock usiku. Pali zimasache zina za utm zopanda zeru ife sitikufuna banja limozi kulemera ayi tikufuna Malawi aliyese aziva kukoma ccta inu mukufunika mukhale president wamalawi

  • @WeziKamanga
    @WeziKamanga Před měsícem +1

    Talking

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb Před měsícem

    Zonsezi nchifukwa chakusanva kwa kwanu tinakuuzani ku MCP mukafako anthu aja ndi afisi .

  • @user-gd7xm7xr9v
    @user-gd7xm7xr9v Před měsícem

    Ungokhala president wa UTM ndiwe

  • @RobertMvina
    @RobertMvina Před měsícem

    Too much examples

  • @user-un8yq1gg2i
    @user-un8yq1gg2i Před měsícem

    Kamkazi kokongolatu, koma eti kakuyankhuranso chichawa eti akuti fasafase Kaya ndiyekuti chiyani? Kkkkkkkkk pachilungamo chake ukunena zoona mchemwari.

  • @user-lg2ws2ki3d
    @user-lg2ws2ki3d Před měsícem

    Zaziii

  • @lewisdicksonmlozi130
    @lewisdicksonmlozi130 Před měsícem

    Powerful speech

  • @SteveTebulo
    @SteveTebulo Před měsícem

    Tikufuna anthu olimba mtina choncho usi siwa utm limbikani mayi kulankhula tchaya tchaya