Video není dostupné.
Omlouváme se.
Report lomwe lapezeka kugwa ndege. imfa ya Chilima yamukhuza Chakwera
Komentáře • 192
Další v pořadí
Automatické přehrávání
MDYANGU COMEDY SERIES..12/07/24..Flora Suya's👉+265883106798 strictly for business purposes only.LIKI-LIKI Ladies
zhlédnutí 45K
Box jumping challenge, who stepped on the trap? #FunnyFamily #PartyGamesFamily Games Media
zhlédnutí 31M
Gyms in 2024☠️Noel Deyzel
zhlédnutí 19M
How I Did The SELF BENDING Spoon 😱🥄 #shortsWian
zhlédnutí 35M
FIZI DRINK VS. COCA COLA? Co je zdravější? #shorts #marcel #cocacola #fizistyleMARCEL
zhlédnutí 183K
Zomwe Zinachitika Kut Ndege IsoweSam Malvitha
zhlédnutí 229K
Shocking News! Anthu 6 from DRC amene anabwera ndi Chakwera amwalira.Bakili Muluzi TV
zhlédnutí 67K
HOW TO MAKE AVOCADO OIL AT HOME. HOMEMADE AVOCADO OIL FROM SCRATCH. #avocado #oil //Village life ugVillage Life UG
zhlédnutí 953K
#BBC HAUSA LABARAN YAU NA RANA 19-08-2024 labaran niger na juyin mulki #bbchausa #labaran duniyaHGN Hausa Global News
zhlédnutí 3,5K
Nkhanga zaona. Chakwera ngati sanaphe Chilima akubisilanji? Report, sakupita ku Italy koma GermanyJay Kawere Mw
zhlédnutí 13K
BON KALINDO PA 19 JULY 2024 | MINISTER YAGWIDWA NDI NDALAMA KU AIRPORT |DZIWE TV
zhlédnutí 26K
What is going on? 😂 (via haechii_br/IG) #shortsSportsNation
zhlédnutí 16M
STEP CHALLENGE🦶Celine & Michiel
zhlédnutí 9M
CO TVOJE TĚLO NEDOKÁŽE UDĚLAT (ALE MĚLO BY TO UMĚT) 😅🤣Stejk
zhlédnutí 291K
Koupím Barče Cokoliv Co Trefí Šipkou!DodoCZ
zhlédnutí 157K
SPILLED CHOCKY MILK PRANK ON BROTHER 😂 #shortsSavage Vlogs
zhlédnutí 45M
Gli occhiali da sole non mi hanno coperto! 😎Senza Limiti
zhlédnutí 13M
Ženu pronásleduje vrah #horrorshorts #shorthorrorstory #shorthorrorstoriesPrézovy noční můry
zhlédnutí 226K
My Bed On Different Days #ShortsLuke Davidson
zhlédnutí 17M
Chakwera Ambuye amuone ndionse omwe anatengapo mbali
My president suffered with others on that day,oooh God u r the God who never sleeps, THE WICKED WILL NEVER REST
Yehova amava aliyese apukute misonzi yathu ndi chilungamo
Zinsinsi ndzayehova, zombvumbuluka ndi za ife ndi ana athu, Mulungu ambvumbulutsa China chilichonse chikhala poyera
Chakwera unapedzeka bwanji ndi black box asilikari amalawi ndi manyi chakwera nyini yamako 😢😢😢😢
Mutu sugwela iwe
Sitingamangoyasa candle for nothing
Mzimu wa chilima sunagone
Uzagona chilungamo chikapezeka. Mukazangophaso a nyamata awiriwa, Mizimu ikupengesani misala baba kuvula kulipo chaka chino
Koma chonde chonde izizi ngati zili chotcho sizabwino .komaso azungu awa atiwuze mwachangu mistake its mistake asibisepo munthu chonde timakukondani koma payizi fulumizitsani chonde ngati zinatelo kungo vomekeza mbili siyiphamunthu panalakwika koma zovotela dpp ayi tizavutika amalawi tisakhe chipani china kupatula ziwilizi ngati ndizowona izi koma ngati ndibodza mcp yomweyo.
Mulungu saozela ❤❤❤
Azimangilila ameneyi chikangawai
GPS global positioning system.
Anamva akuthama ali Geographical mmalo mwa global
😄😄 CHakwera manyazi bwaaa, amalawi kuwamenyanitsa mitu mmaganinzo Pa ifa ya chilima iwe ukudziwa, apa ndy waonetsa machendeee manyazi bwaaaa
Ndipo inu esh
Mmmhh ayayi imfwa yowawa iyi
Chilima ause mumtendele
Shaaaaa kutamba masana mcp😊
GPS stands for Global Positioning System
Auzenidini amenewa hahaha
Anaminyero ose amatumbwa kumapakira chakweraaja arikut Sono nthawi yakwana DC karindo nkhan ndiimeneyo mmawa kofunika kuilengeza zenizen bakiki muluz osaiwara nkhan ndiimeneyo
GPS means Global positioning system
Galu kamupeni akapangire kwa make,osati a Malawi ndindaniso angamuvotere
Ayi koma mumatha kitumikila satana inu munakachipeza bwanji kumeneko 😅😅 eeeeeeeee kuli ntchito a Malawi amalawi kodi yesu atakupezani mukunena zopanda umboni mungatani osamvako mu mtima kuti ndikunenazi ndili ndi umboni? 😅😅 manyazi mulibe anthu inu work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die
Global positioning system is very accurate
MCP chomwe yinapanga siyikuchiziwa kom chomwe aziwe misozi yaathu ambiri singapite pachabe muwona mulungu ava kulila kwa malawi
Chilima wanga 😭💔
Ayaluka wakupha Chakwera satanic yamuyalusa kwambiri chisilu chamunthu ichi
Ngati sazipha yekha azangosowa ziii chekwera wakupha oipa koma ndi chintima chomwe😢
Wina nkumat nkavotera chakwera. Mulungu akukanthen ndithu
MCP yayambitsa yokha nkhondo komwe azikapangila kampeniko kuzikhala nkhondo sindikukayika ndipo a Malawi tilimbe nazo team imeneyi isadzayende ayi
Ofufuza amaona ngati sapeza chilichose km achakwera mtima wa nkhandwetu mulinawowo muyaluka simunati ndi ndale zopanga usiku ngati afiti akuti tayedzeka wamkulu maso ngati kadzidzi uja 😢😢
Chidzimangilire chabe chimunthu chakupha ichi tilibe nacho ntchito
Mulungu wanthu atithandize mmmmmhu Amalawi tikupita kuti ifeeeeee nkhondo kunoo mizimu Yao iuunse mutendere 😭😭😭😭😭😭
KOMA CHAKWERA NDIWE OLIMBA MTIMA ANTHU 9 UMAGANIZA BWANJI KOMA MIZIMU 9 KUPHA CHAKWERA ULIBE UMUNTHU PANYELA PAKO
Mtanyiwa adzanena kuti mafon black box zili ku state house 🔥🔥🔥kuyalukatu uku abusa🙌🙌
Cakwera mmmm cakwera upedzeka bwanji ndi blackbox unaitenga.nthawi yanji cakwera okupha
Yomweyo Chikangawa 😂😂😂
Mulungu amapanga njira popanda njira
Zikomo big, vuto anapha ndi anthu wosalakwa
Ndipo kwambiri mm
Kumkuyu mneneri waboma yakhula suumayerekedwa ndikuyakhula zopanda nzeru blackbox ipedzek ndi cakwera bwanji anthu opanda nzeru mumaona ngati amalawi ndi oogona zisiru inu kwabasi takudziwani asatanic inu chipani ca magazi mbusa wakumidima kuno ku fatima chikwawa sitingakuvotereni asatana inu kumkuyu wasala pangono ukayakhe mlandu wA.allan witika iwe udzakwililidwa wamoyo
There is no secret under the sun .
Mvuto ndiloto panopa anthu sakuopaso sinanga tikudziwa kuti chakwera akugwirisa ntchito kupha nde atipha ambili anyapala amenewa chakwera zeru alibe gay's
Yes that's true ndipo akunena zoona koma afufuza bwanji popanda black box
Chakwela wapha anthu akayenela kumangidwa agalu amenewa
Zamanyanzi kwambili athawa dziko lokhala lawo
Koma mutuluke amalawi tiziwe chowona Chakwera ndi wakupha iiiiií
Zimenezo nde inu mwazitenga kuti,mu Black box, kapena zabodza zanuzo
Koma mbuz imenei osangoimika manja bwnj coz zonsetu zingofika poyera
Zomvetsa chisoni zachitikikazi man made disaster
Mizimu ipitirize kukukantha woipa wakupha satani chakwera mbuzi
GPS is global positioning satellite! Don’t get it twisted.
Ndiolotse nkakutafune ,, koma abusa awa 🤔 hmm
Chitsilu chamunthu kumakhalila kupeka mabodza basi mupitanazo pati zimenezi
Obakila tiuzeni ndinu zoona uyu ndiwabodzadi, uzani dziko zoona lija ndikale
Obakila aja alikuti apa sindikuwawona?
Geographical position system
GPS stands for Global Positioning System
Chakwera your days are numbered
Mizimu ndi yambiri zedi kuwapha anthu osalakwa zoona mmmmmmm koma mcp ayi ndithu
Paline chinsinsi pa dziko la pansi aziona Mulungu amalanga
Masiku ano kuli technology asatengere nthawi ya kamuzu anthu chilungamo amachibisa ndimatha
Wina afa ndi chikumbumtima sure
Mzosatheka ukunenazo ase iwe Chimphuno chako
Ose paulendo omwe anatengapo gao koma ziliko
Ambuye zikomo
Inuyo patali brother
Chakwera wapa chilima 😭😭😭😭
Wayaluka chakwera
😂😂😂😂😂 yehova yekha ndye akudzwa
Amalawi tikufuna chilungamo
Globe Positioning System 🤔
Chakwela kuyalukatu kumeneko
Koma chophera anthu ndi chiyani satana iwe wandiliza
Ambuye aika chilichonse pambalambanda
Powerful 👊
Chakwera pamtumbo pako galu iwe
Tanyiwa ndi garu
Yakwiya ndi mizimu...
Dziko alinva kuwawa nayeso iyaaa
Anyanduka uyu chakwera
Koma Dziko...mmmmmmm.Lovuta
Komano kodi amalawi tizingoyang'anira anthu akuphedwa?
Did chilima uses a car the time they were going to Mzuzu? We are waiting for results ,not what are talking
Ine sangandipeze😮😮
Mr nkhangatu ananenadi kuti black box yasungidwa ku state house limodxi ndi mafoni. Wopha ndi lipanga, ndi lipanga lomwelo lizamuphe.
Tikutsatila mwachidwi osafooka
Chakwera akanakhara wina akanango pitaso ku church Kuti akalape ndikuyambaso wubusa wakewo shame
Rip SCK
Ungotipha tose bas usare ndi akazi akowo bs
Athakati awa koma ndi abusa assemblies fake
Chipulezidenti chakupha
It's too hard mmmmm
Eeee koma sure ndithu
Ukuyankhulawe ndi wa MCP. Apa ukufuna kusokoneza kafukufuku wa German. Chonde khala chete tose tiyang'anile chimene a German atanene, mukachulusa zokambakamba choona chenicheni chisokonekela chifukwa oganilizidwawo alibe pa ulamuliro wa ziko lino
Bakili muluzi tv tisikimizireso timadalira iweyo tikudikira iweyo ing, alure bas
Sapanga kampeni awa akapangira kuti? Nyumba mwaotu
Zili kuoneka tsogolo
Km akuchepa amenewo cz military kunoko kulibeko km zisilu zokha zokhazo
KKK apa nde madzi achita katondo
Baliki muluz ali ku tete ntanyiwa ali ku tazaniya
Zochititsa SHAME
Kusayamika,Chauta sagona tulo.
❤❤❤
Chakwela ndi mufiti
Amen mulungu wathu ndiwamoyo ndipo amayankha ndipo ndiwowopsa plibe angafane nan
Amen 👏
Malawi wavunda, anthu kungolimbirana maudindo mpaka kuphana
This is sad 😔