AMENE WAULURA ZA CHINSISI CHA JOYCE BANDA NDI LAZARUS CHAKWERA LIVE LIVE PA NSOKHANO WA PP UJA UYU

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024

Komentáře • 113

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr Před 29 dny +25

    Sangasiyane ngwilizana wawo ndi wamaganzi kuteloko mayi Joyce Bandah ,,ngankhale muli akulu Anga Koma lmfa yachilima mudziwapo kanthu inuyo ,,

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere Před 29 dny +2

      Mutu wanu ndiobonga amai Inu, mgwilizano wa DPP ndi UDF siwamagazi?

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d Před 29 dny +3

      @@PhillspicJerechokani inu mulibe mzeru palibe chomwe mudziwa mmutu mwanu mwangodzadza manyi umuuzeso chakwera kuti machende ake anapha chilima

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere Před 29 dny

      @@Musa1828-l5d Ndiwe mwana phone ndiyako koma uziona Zotukwana komaso owatukwana

    • @chippakaribafox2865
      @chippakaribafox2865 Před 28 dny +1

      Obvious....she can do anything for money shame

    • @ThokoLungu-tq6pw
      @ThokoLungu-tq6pw Před 10 dny

      Akuziwadi kwambili mmayi oipa uyuuuuu alape

  • @charlesnankumba9991
    @charlesnankumba9991 Před 8 dny

    Those that think that Dr. Joyce Banda is a spent force in Malawian politics are cheating themselves and at the same time misleading others. Dr.Joyce Banda is and will still continue to be a highly respectable force in Malawian politics. There are so many good and great things Dr. Joyce Banda has done for Malawians and continues to do which Malawians of good will and sound reasoning will never forget. Long Live Amayi!

  • @EvanceLumeyo
    @EvanceLumeyo Před 29 dny +8

    Asatanic okhaokha ndi Mr chikangawa iyah..

  • @AustinBornface
    @AustinBornface Před 29 dny +9

    Ndiye china nkumati Mutharika wakula? ifetu tikungofuna fertilizer tizidya nthalo yambiri

  • @SophiaKalonga
    @SophiaKalonga Před 29 dny +3

    I love this man eeshhh

  • @WisemanMunthali
    @WisemanMunthali Před 17 hodinami

    Titamakhala ndi anthu ngati awa mziko olankhula chilungamo bwedzi ziko likuyenda bwino

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr Před 29 dny +2

    Komatu zomatenga amalawi ngati nyape zanuzo ife timadya nawo musatitole osaukafe musamale,,,,kulankhula kwabwanji uku? Timve ziti? Muona ngati ndi nthawi zopusitsana panoso?

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope Před 29 dny +1

    Joyce Banda osavotera ndikape ndi munthu mmodzi safunira amalawi zabwino mutayeni

  • @andrewchiyembekezadimba7173

    Akuluwa nzeru mulibemo. Iye akuti mgwirizano sunathe pamene amai ananena kuti anauzidwa MCP ikalowa ku convention ndiye kuti mgwirizano watha

  • @ShaidaJackson
    @ShaidaJackson Před 7 dny

    Agalu inu asatanic okhha okha,tikumana 2025

  • @ClementsKamanga
    @ClementsKamanga Před 9 dny

    Chokhacho achimwene mwauponda mcp ndimbola

  • @ElizaLabson
    @ElizaLabson Před 8 dny

    Adadiiii moto buuu!!¡

  • @user-qv4yu2ir2k
    @user-qv4yu2ir2k Před 29 dny +2

    Cashgeti people's paty

  • @Kamwachale
    @Kamwachale Před 29 dny

    Politics at its best. PP is still with MCP. This is a strategy of dividing votes in the south. Amalawi akupenya masiku ano sangapusitsidwe

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Před 29 dny

    Moonse NDinu amane mukuzunza Malawi ,vote Kwa Dadie basi

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před 21 dnem

    Inu palibe chanu chipani cha satanic chakwela palibe za vote

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama Před 29 dny +1

    Gashiketi yokhayokha kulibetu ndege yogulitsa kumalawi anagwetsa chakwela ndiye akadzawina maiwa

  • @EmanuelFundudwa
    @EmanuelFundudwa Před 3 dny

    Nkhani yabwino hvy

  • @innocentlipita3630
    @innocentlipita3630 Před 29 dny +1

    Anthu ngati pa msonkhano wa fumu wa macopoun

  • @user-ld8gb9xm7v
    @user-ld8gb9xm7v Před 29 dny +1

    Mmphuno mwako

  • @user-ld8gb9xm7v
    @user-ld8gb9xm7v Před 29 dny +1

    Ndimwe wa tonse alliance mavwele yinu

  • @stewart.mwamughunda
    @stewart.mwamughunda Před 21 dnem

    Kondwani Nakhumwa chikapeta Chakwera bwana mkonzeke kukalowa Ku state house 2025

  • @amoschisisi2070
    @amoschisisi2070 Před 29 dny

    It only happens in a federal government

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Před 29 dny +1

    😂😂😂😂😂😂 Inu munaziyipisila mu trauser chifukwa cha tonse alliance simuzawinanso agalu inu😂😂😂😂😂

  • @Martinmkapangakapanga
    @Martinmkapangakapanga Před 29 dny +1

    koma ambuliwu amalawi changamukani

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Před 29 dny

    Zinawakanika awa analamulira dzaka za Bingu ziwiri basi koma Bambo uyu wakhura za nzeru Koma mai athuwa akuba

  • @PatienceHarry-z7h
    @PatienceHarry-z7h Před 15 dny

    Mcp zake zada basi

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y Před 29 dny

    Mabindi (masanje) APM my vote

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 Před 29 dny

      Kutaya vote my friend kumeneko think nicely

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga Před 29 dny

      Kagwere uko mufuna muphe tonse ndi chifunga tikakuviterani ​@@damianokachingwe3531

    • @tamalangoma2765
      @tamalangoma2765 Před 29 dny +1

      Eti munthu wanzeru zoona angavotele Peter kkkkkkkkk

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d Před 29 dny

    Zamanyi basi mesa Joyce Banda yo ndi mfiti anatigulisa kwa chakwela yo hiyaaaa

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Před 29 dny

    Kuonekerathu kuti muri pamodzi ndi Mcp mkufuna kunamiza amalawi muona pa 2025

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 Před 29 dny +1

    Kodi mukadali ku mcp eeeti?? Ayi tamva

  • @KensonMsiska
    @KensonMsiska Před 29 dny +1

    😂,,,😂😂 palibepo Cha nzeru apa

  • @user-ku3gk4fz5i
    @user-ku3gk4fz5i Před 29 dny +1

    Ingotulukani ku mcp inu

  • @kondwanichirambo7797
    @kondwanichirambo7797 Před 29 dny +3

    Bakili muluzi TV yokha nde ya nzeru zinazi zimakhala ngat mwa chiphwilikiti

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 29 dny

    Inu muli ku Mcp musatiputsitse kuteroko nde kuti kutsogoloko chachiziwikire midzapanga mgwirizano ndi mcp

  • @FlywellThengo
    @FlywellThengo Před 29 dny

    Kunena zoona mulamuliro wanu amayi zinthu zimaenda km ife tili pambuyo panu mai 2024 moto kt buuuuuuuuuuiiiiiiiii

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma Před 29 dny +1

    Mfundo za ziii

  • @happynyirenda8790
    @happynyirenda8790 Před 29 dny

    Kanyamata aka boza ngati katsikana ka 15 yrs old

  • @MangaDamiano
    @MangaDamiano Před 29 dny +1

    Mwasowa chochita Kodi ?

  • @PatienceHarry-z7h
    @PatienceHarry-z7h Před 15 dny

    Koma ndiye mutimatiza

  • @faidaceciliaYekha
    @faidaceciliaYekha Před 29 dny +1

    Kkkkkk kuiyang'alura😂

  • @EddenKamanga
    @EddenKamanga Před 19 dny

    Chasowa chochita inu

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 18 dny

    AGALU kwabasi inu mbavu satanic nokha nokha simungawinenso afiti inu ndi chikangawa wanuyo

  • @user-rv7tk8cv2q
    @user-rv7tk8cv2q Před 29 dny +4

    Your Back ground music ndibwino kuyichosa zizimveka boh boh

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před 29 dny +1

    kodí zílimótero et

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Před 29 dny

    Zilombo za chakwera

  • @ednanamboyachilambe6901

    Hahaha koma ndale kkk

  • @tobiousmtenje139
    @tobiousmtenje139 Před 29 dny

    Ubwino wake mwavomereza kuti mafumu akuvutika.Mavutowo ndye akuta wina aliyense

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 29 dny +1

    Kod chilipo chipan ichi et

  • @LovelyAntenna-jh8yh
    @LovelyAntenna-jh8yh Před 29 dny +1

    Kuyankhula kwamanyi uku nkotani

  • @user-lc3sw8iz2g
    @user-lc3sw8iz2g Před 29 dny

    ATUMIDWA KUTAPA MA VOTE A KUMMWERA A DPP.

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 Před 16 dny

    Salu zikugawidwa koma sakuvala mudzifuse

  • @henrymwale8994
    @henrymwale8994 Před 29 dny

    Koma timvereni ma followers anu background sound yo muchotse ikumatisokoneza

  • @MabvutoMichaelPanagona

    Mai Joice banda imfa ya chilima akuidziwa

  • @godrickmapepu2754
    @godrickmapepu2754 Před 29 dny

    A Joice Banda tazisiyani izi. That time you had that opportunity because of death and you can't win your dreams.

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g Před 29 dny

    ❤❤❤❤❤ 50 +1

  • @SpiweJambo
    @SpiweJambo Před 29 dny

    Zee one films

  • @RoseChiphiri-ts8jx
    @RoseChiphiri-ts8jx Před 29 dny

    Moni kwa mr Chikaonda ku chipani kwanuko 😂😂😂

  • @voicedumathindwa
    @voicedumathindwa Před 20 dny

    Joyce chipani chako ndi chakwanu konko ndi zisilu zakozo

  • @user-nj4pn8gx7y
    @user-nj4pn8gx7y Před 29 dny

    50+1🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @MaggieCement
    @MaggieCement Před 29 dny

    Za ziiiiiiiiii kwanu kunatha Inu limbani mtima

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka Před 29 dny

    Zaziiiiiiii tixivaso za mcp pano

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m Před 27 dny

    Musapepelese anthu Mai inu

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 Před 29 dny +1

    Aimed basi

  • @SmilingFishingRod-zc4wx

    Kkkkk koma anthu akafuna kum'bera wankulu eeeee amanama koopsya. M'bereni Ali ndi ndalama zomwe anaba kuzera mu Caschgate tuyeni naoni musamukhumudwise m'beleni

  • @IgnatiousFote
    @IgnatiousFote Před 29 dny

    chivunde ali nd mfundo mbambande koma chipanichi chamuchepela kwmbr

  • @PrinceTaibuBanda
    @PrinceTaibuBanda Před 29 dny

    Good

  • @grantkangombe6804
    @grantkangombe6804 Před 29 dny

    Ndiye ngati akukayikirana kuba chitenje what more ndalama za boma?

  • @IgnatiousFote
    @IgnatiousFote Před 29 dny

    Kod chivunde first name ndindan

  • @Martinmkapangakapanga
    @Martinmkapangakapanga Před 29 dny

    mukuwapusisa amalawi awuzeni Zoona

  • @MoreenHussein
    @MoreenHussein Před 22 dny

    Tinadzidzukadi zoona Ng,alulula basi ,tachika nacho kutali

  • @esaumtambo-d3h
    @esaumtambo-d3h Před 22 dny

    Anthuwa atiwonjeza ife ovota atifuna pompano

  • @WisilamuSaid
    @WisilamuSaid Před 29 dny

    Musezeseni katundu muzakana kumutura pasogolo

  • @ShaibuAmeck-z5w
    @ShaibuAmeck-z5w Před 29 dny

    Aaaaa awa ndi anthu okuba

  • @user-yq1mc3nm1f
    @user-yq1mc3nm1f Před 29 dny

    Kkkkk Joyce banda amakhala mu fernbrook estate muno pa Stage wood street apa ife tinali kumuona tsiku ndi tsiku and olo amufunse anena kuti zoona. Ku America Joyce adakhalako liti ? Joyce amakhala mu fourways/ Johannesburg Fernbrook estate - kenako anasamukila ku Dainfern ndikomwe anamumangila kuti abwelere ku Malawi zaku America mukuzitenga kuti agalu inu

  • @frankiechasokoneza5802

    Awa angomasuka basi atulukamo mu gwilizano wa Tonse alliance

  • @aliemohammed5853
    @aliemohammed5853 Před 25 dny

    Achakwela mundu jwamatama

  • @BEATRICE-t7k
    @BEATRICE-t7k Před 11 dny

    Mhuu!!!

  • @CatheySichari
    @CatheySichari Před 29 dny

    Tikuvoteran may tavutika mokwana

  • @AlihAmdulillah
    @AlihAmdulillah Před 29 dny

    Zaazii kuti ziveke bwanji inuyo

  • @user-hx6jd4yy4u
    @user-hx6jd4yy4u Před 29 dny

    Hi

  • @kearabetswemashego3084

    Hhhh kom inu mupangisa kuti chakwira awine hhhh

  • @YobuMbawa
    @YobuMbawa Před 26 dny

    Kkkkk kwachema ku pp

  • @JosephKandapako
    @JosephKandapako Před 29 dny

    Ulemuwanu amai ine ndichisanzo chabwino ulamulilowanu unatisithadi achinyamata mmalawimuno munasitha dziko lamalawi masiku owelengeka amalawi tiwakumbukile anapangazabwino❤

  • @JusticeKalemba
    @JusticeKalemba Před 29 dny

    Vinyo watha

  • @BridgetZingani-gb8yf
    @BridgetZingani-gb8yf Před 29 dny

    Kutereku zolinga zao nzimenezi? Mwayaluka. That's why speech ya mai sikumveka mutu wake kkkkkk

  • @StainMlamba-x5e
    @StainMlamba-x5e Před 25 dny

    Amapocholol

  • @KaungaYawaka
    @KaungaYawaka Před 29 dny +1

    😂😂😂😂

  • @TimothyKabumbuKendrix
    @TimothyKabumbuKendrix Před 29 dny +1

    😅😅😅😅

  • @esaumtambo-d3h
    @esaumtambo-d3h Před 22 dny

    Chaka cha mawa chakwera no vot

  • @GrealishMulimah-y5i
    @GrealishMulimah-y5i Před 29 dny

    Ine vote yanga ilikwa may

  • @MaggieMuhone-r7m
    @MaggieMuhone-r7m Před 29 dny

    Kkkkkkk Kkkkkkk Kkkkkkk