BON KALINDO PA 19 JULY 2024 | MINISTER YAGWIDWA NDI NDALAMA KU AIRPORT |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 5. 09. 2024

Komentáře • 117

  • @user-wq9ex2sf3b
    @user-wq9ex2sf3b Před měsícem +5

    Kalindo I love you the DC ❤

  • @DanChirwa
    @DanChirwa Před měsícem

    Thanks so much mr DC Bon kalindo for everything you done for malawias🙏🙏

  • @ChimmsRichardOrden
    @ChimmsRichardOrden Před měsícem +1

    God bless you Hon Bon Kalindo, that's so very powerful MASSAGE

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm Před měsícem +4

    Thanks so much for your help Malawias

  • @CosterMustafa
    @CosterMustafa Před měsícem +5

    The DC Iweyo umakwana Kom vuto ulipo wekha zimafunika gulu izi 🌄💥💥

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Před měsícem +6

    Kodi Utsi,akupereka ndalama Kwa mavenda, bwanji ndalama zimenezo bwanji akana ngo gula Chimanga NKU gawira wina Ali yense kumalawiko ngati m'mene tina landirira ife mu 1993,timalandira thumba la 50kg mwana wina Ali yense pa classroom, komanso Wanthu aku muzi, Ndiye Lero akupereka Kwa mavenda basi?koma Amalawi ngopusadi koma kunja Kuno Wanthu adapenya Kale kumeneko nso mupenye muthatu njala psyiti bolani ife tidathawa zanu izo

    • @user-vm7iz6oz6r
      @user-vm7iz6oz6r Před měsícem

      Pali uchisilu wa MCP ndipamenepo saziwa chomwe akuchita

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před měsícem

    The DC Mulungu anasankha inuyo kuti muyimilire amalawi ndipo tikupenpha Mulungu yemweyo apitirize kukutetezerani kwina kuli konse kumene mudzapite❤

  • @GodfreyMpate
    @GodfreyMpate Před měsícem

    Yes we go for it mr bon

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx Před měsícem +1

    Komanso ndalama zomwe zapezeka ku Zambia boma likuyenera lifotokoze. We are ready for demonstrations Mr Bon Kalindo

  • @blessingcharo7669
    @blessingcharo7669 Před měsícem +2

    Timakunyadirani bwana keep it up

  • @BrandonThomas-le8eb
    @BrandonThomas-le8eb Před měsícem +2

    Boni umakwana Allah akudalise

  • @Innocentmagido
    @Innocentmagido Před měsícem

    Ine ndiwa kalindo❤❤❤❤❤

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před měsícem +1

    The Dc bon kalindo number one ❤

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 Před měsícem

    Timakunyadilani Big man Kalindo

  • @user-gz9en9jf6m
    @user-gz9en9jf6m Před měsícem +1

    Number 1 boni kslindo

  • @temwarachaelkhonje3733
    @temwarachaelkhonje3733 Před měsícem +1

    Mr Booooooon Kalindoooooo for president basi

  • @ednakachangaule9985
    @ednakachangaule9985 Před měsícem

    Tiyeni tidzuke Malawi Bon Kalindo amatikonda amakonda dziko lathu.

  • @AliajoeAliajoe-vv1wo
    @AliajoeAliajoe-vv1wo Před měsícem

    Thanks Mr DC u helping us alot

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e Před měsícem

    Kalindo nd mbambande kma tioloka masiku amatha nd kugona😊

  • @PatrickTchuma
    @PatrickTchuma Před měsícem +3

    Dziko Lankaka ndi uchi, uchi unaola nkaka unayamba kutuluka mphutsi

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw Před měsícem +1

    Đc boooooorn kalindo the president,,mumati imilila kwambili timathokoza koma a Malawi kufatsa kwambili

  • @user-yq7dq2dk2i
    @user-yq7dq2dk2i Před měsícem +1

    Ife sitiwasekelera Agaluwa

  • @ChimwemweChinjoka
    @ChimwemweChinjoka Před měsícem +1

    🎉😅 Umakwana the DC

  • @AubreymedsonMbewe
    @AubreymedsonMbewe Před měsícem +1

    Nthawi yakwana amalawi tidzuke kunali cash gate tinawasiya lero Boma ili kuba kopanda manyazi oponde fada tipite kunseu very soon

  • @StewardKapoto-u7k
    @StewardKapoto-u7k Před měsícem +1

    🔥🔥🔥🔥 The DC

  • @patccholapitsahillary2340
    @patccholapitsahillary2340 Před měsícem

    The Almighty God will continue to protect you The DC continue sharing the truth

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Před měsícem

    Go konko I love you Mr kalindo ❤❤❤❤

  • @user-uf4go7fg2h
    @user-uf4go7fg2h Před měsícem

    Love you bon kalindo
    Osafoka kuti menyera khondo athu osauka tiku lephera ku bwera ku malawi😢 abusa awa 2025 waku muzi wako aka pume mwina aka seguleso mpingo wina

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo Před měsícem

    The DC

  • @iamandypandy
    @iamandypandy Před měsícem

    Zoonadi Mr President

  • @carlosprecious
    @carlosprecious Před měsícem

    Malawi first wathu

  • @JunaKananji
    @JunaKananji Před měsícem

    ❤❤❤❤❤karido

  • @AlliYussuf-j7n
    @AlliYussuf-j7n Před měsícem

    The DC umakwanila tili pambuyo pako. Chakwera watikwana

  • @LamieTiger
    @LamieTiger Před měsícem +2

    Olimba ntima amasowa

  • @collennyadile8179
    @collennyadile8179 Před měsícem +1

    chakwera anabwera kuzawononga dziko la Malawi chifukwa ntchito za satana zitatu kuba kuwononga ndi kupha basi ndizomwe akupanga chakwera

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Před měsícem

    Kalindo 🔥🔥🔥🔥.. tili konko❤❤❤❤

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Před měsícem

    Osewo akuyeneleka kupangidwa 🔥 pakuti osewa Ali limodzi kukadakhala Kuti Sali limodzi ndi president sakanayimba fone Kwa apolice Kuti amusiye Ayi ,,, pakuti Lero chakwela ndi wapolice apolice sanduka ayikhata asilikali asanduka apolice wamba ma department wosewa sakudziwa ntchito yawo ,, ndimava Kuti asilikali amatha kumuwukila president Ngati sakupanga bwino ndikulanda Boma ,kapena tiziti asilikali akuona Kuti chakwela akupanga zabwino?

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Před měsícem

    Tiyen pa nsewu bas afitiwa atikwana heavy

  • @MariamChipoka
    @MariamChipoka Před měsícem

    I believe you

  • @PreciousMwalwimbah-t4q
    @PreciousMwalwimbah-t4q Před měsícem

    Bon umakwanira pomenyera amphawiyife ufulu kmaso kusegura mumaso anthu mulungu a
    Zikudalisani

  • @EvanceKapondeni
    @EvanceKapondeni Před měsícem

    Mr dc keep it up

  • @user-xy5bm7sz8o
    @user-xy5bm7sz8o Před měsícem

    🙌🏾

  • @user-rz8qp8tj8e
    @user-rz8qp8tj8e Před měsícem

    Munthu wa mcp apa ai please boma la chikangawa we are sick and tired nonsense pano tinapenya fire to fire

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 Před měsícem

    Ndye wina akuti timupemphelele chakwera kkkkkk wanena izi mutu wake sugwira ntchito ndthu mcp must follow

  • @PaulKalambo
    @PaulKalambo Před měsícem

    Inu akalindo kumwalira ku Malawi kuno tizakhala mu msautso ngat nyengo ya nowa. Koz sipazakhala otiyankhulira wa bakili muluzi tv akazapanda kuikapo mphavu

  • @SUFIAANJAZEEMMSUSAHASSADU
    @SUFIAANJAZEEMMSUSAHASSADU Před měsícem

    Good speech

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Před měsícem

    Malawi I don't know where in Africa can this happen very disappointing

  • @MoosaChirwa
    @MoosaChirwa Před měsícem

    ❤❤❤❤❤Izi ndiye timati nzeru

  • @EliasIdrissaPoster
    @EliasIdrissaPoster Před měsícem

    🔥🔥🔥💪Mr DC

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali Před měsícem

    ❤❤ndizoona DC

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s Před měsícem

    Ndipo abale dziko lathu lilikumka kt iiiiii

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 Před měsícem

    Zovuta zed Anthu akuvutika ndi njala

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před měsícem

    Achisilu awa daily kumangoleza umphawi ngati mpila zazii

  • @solobertkamunga2826
    @solobertkamunga2826 Před měsícem

    Ya MUBAS tafufuzan bwinobwino bwana DC kut ziveke

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo Před měsícem

    Ndalama zambiri mbiri zomwe zapezeka ku Zambia zo koma boma la chakwera likuleohera kupeleka ndalama za anthu omwe anapuma pantchito za ka ziwiri zapitazo what is happening in chakwera administration nyansi zenizeni

  • @Ndexyfunny
    @Ndexyfunny Před měsícem

    ❤❤❤❤

  • @user-ml2yi3zk5x
    @user-ml2yi3zk5x Před měsícem

    The Dc❤❤

  • @AcksonSimbeye-pm9po
    @AcksonSimbeye-pm9po Před měsícem

    Tiini naoni bwana tisawalekelele

  • @MphatsoChafala
    @MphatsoChafala Před měsícem

    Atikwana amenewa achoke bas

  • @user-dy4gc2hr5e
    @user-dy4gc2hr5e Před měsícem

    More fireeee bon kalindo

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 Před měsícem

    Dc ❤

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn Před měsícem

    Ankhulukunyinda kkkkk😂😂😂😂😂

  • @johnnytheyounger7505
    @johnnytheyounger7505 Před měsícem

    kuswa kuswa

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p Před měsícem

    True talking

  • @FrancisChimberenga
    @FrancisChimberenga Před měsícem

    May God bless Malawi

  • @user-he5ol5or7f
    @user-he5ol5or7f Před měsícem

    Bwana DC 🔥🔥🔥

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l Před měsícem

    Sikufasa amalawi koma dyela

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Před měsícem

    The DC boooon kalindoooooo

  • @AaronByson
    @AaronByson Před měsícem

    Eeee km akuru Inu munasamba potan km aaa km inuyo a DC nd 1

  • @user-km8vl6tw2c
    @user-km8vl6tw2c Před měsícem

    DC

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko Před měsícem

    Timakunyadira bon kalindo

  • @HamiltonwaNamuwah
    @HamiltonwaNamuwah Před měsícem

    Kkkkk owoo , mpaka afisi

  • @ChrisEnos-to5uv
    @ChrisEnos-to5uv Před měsícem

    The DC🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @SinsaKachale
    @SinsaKachale Před měsícem

    Vuto anthu olimba mtima ali moyenda anafunika akanaona za Donald trump wamlayi

  • @JonesohmsMmanga
    @JonesohmsMmanga Před měsícem

    Dc ndi one 2 kuopa kupindika

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r Před měsícem

    Chakwela satana wohipa aziwa kupha anthu

  • @johnman4619
    @johnman4619 Před měsícem

    Baibulo sanalembe yesu ayi adangolemba anthu wamba

  • @innocenttasiziyo-rj3wr
    @innocenttasiziyo-rj3wr Před měsícem

    Osafooka💪💪💪🔥🔥

  • @user-zw8ns7bk7s
    @user-zw8ns7bk7s Před měsícem

    Kalindo ndi bakha

  • @SteviePatrick-g2p
    @SteviePatrick-g2p Před měsícem

    Zikoli lafika pot munthu utha kuyankhula udyo tithokoze inu chifukwa mumatiziwisa ndikutisegula mmaso pitilizan awawa tionana nao 2025

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt Před měsícem

    Komalawi ndife opoyila ndinthu nthu kumatipusisa nditimachenje akupromisa manganyayo basi kumaombela manja osamuwuza zanjala bwanji ndi kudula kwa zinthu koma ife ndiye aii ife sitibwelako kumeneko pitilizani kukhala atulo zanu izoo ife kunu nkhuku zikuthipha tilipheee osagwira ntchito kuno amamwa tea adyaso nkhuku sugar aliko R1 kuno 😂😂😂😂

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před měsícem

    Cakwera sanabwere kudzasogolera amalawi koma kupha kuba ndi kuononga ndipo iye anayenera kuudza apolice kuti amumanga galu wapedzeka ndi ndalama koma akutetedza mbava imatetedza mbava idzake ndiye kumkuyu ali kuti atiudze kuti achimwene akewo ndalama adzitenga kuti poti amayerekedwa kuti odziwa kuyakhula okupha Allan witika boma loipitsitsa mbiri yadziko lamalawi

  • @SusanDickson-e1n
    @SusanDickson-e1n Před měsícem

    Mmatimilira

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Před měsícem

    Anthu Ife umphawi unatitseka nzeru , zonse zimene akunena MR DC ,ndizowona ,aMALAWI ,mmene tadzadzila Kuno Ku MAYIKO AKUNJA , mm zomvetsa chisoni kwàmbiri. Anthu tikanakhala Ngati MR DC kulimba mtima tikanamuchosa pa mpampando Chakwera

  • @PreciousHenderson-qc1hq
    @PreciousHenderson-qc1hq Před měsícem

    Ndipo malawi wake up ndalama akugawana kuno Zandinyasa kwambiri tikuyatsa Moto basi mademo tikuwayambaso Mr DC tiyeni go konko

  • @bysongeorge3243
    @bysongeorge3243 Před měsícem

    Otsutsa Boma nawo adakagona ati kudikira chisankho Chaka cha mawa pamene a Malawi tikuvutika kosaneneka..Bon umatiimiliraaa....

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před měsícem +2

    Mr DC president

  • @InnocentKavalo
    @InnocentKavalo Před měsícem

    Umatha aise the dc

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Před měsícem

    IWE UDATIKWANA NDITHU

    • @Dysonkhofi
      @Dysonkhofi Před měsícem

      Philip usiye kusegula VN ya winiko.
      Ndiwe kape
      Sungaone kut Chakwer waononga dziko lathu!
      Basop!

    • @chekiamaabdul5083
      @chekiamaabdul5083 Před měsícem

      Kumaa nini ? Wewe mbwa msenge

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson Před měsícem

    🎉🎉

  • @EliasIdrissaPoster
    @EliasIdrissaPoster Před měsícem

    🔥🔥🔥💪

  • @user-wg7bw7py3z
    @user-wg7bw7py3z Před měsícem

    Musamaphatikize ndi video yomwe Kalindo amaoneka PA khoti zikubalalitsa mudziyikapo audio basi

  • @DistanceChirombo265
    @DistanceChirombo265 Před měsícem

    Stop using bakili muluzi tv ase ma broadcast ako siobeba

  • @user-nv3rf7bl7r
    @user-nv3rf7bl7r Před měsícem

    Pepani a bon kalindo sinamalizise audio yanuyi koma ndufuna ndiyankhe pankhani yotuluka mumalawi musanamizile chakwela enafe sitinatuluke nthawi yachakwela or 2 inuyo musayankhule za mulungu pankhani zopepelazi chifukwa mulungu amakonda ntendere mukawona nzanu akulakwitsa mupempheleleni koma musamupemphelele zoipa chifukwa inuyo simulungu ndipo oweluza ndi mulungu mpando uja ndiwomvuta or kukhala inu anthu azakudandaulani chifukwa simungasangalatse aliyese koma za mademo anuwo palibe chomwe muzapindule chchikulu ndikugwada pasi ndikupemphela kuti ambuye tithandidzeni dziko lathu layipa tipaseni musogoleli oti angasinthe moyo wathu kaya ndiyemweyo chakwela kuyikizamupemphero kuti ambuye apatseni dzeru asogoleli athu ambuye amva ndipo palibe chowakanika mvuto ku Malawi yachuluka ndi nsanje komaso kufuna maudindo koma dziwani mulungu amadalisa yemwe wasankha kukhala chete kutukwana or mutani sizikupindulilani amalawi anzanga ambuye atithandize kuti tiziwe chowonadi

  • @SusanDickson-e1n
    @SusanDickson-e1n Před měsícem

    Iii akut mpakaana ma interview uphumzitsi

  • @DavieDavie-o4k
    @DavieDavie-o4k Před měsícem

    Koma chakwela

  • @SameSamliu-u7h
    @SameSamliu-u7h Před měsícem

    🎉🎉🎉🎉🎉

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft Před měsícem +1

    Mumatha A Bon Kalindo tiyeni pansewu akatiuze zenzeni kutu ndrama zomwe zinapezeka Ku Zambia komaso zomwe zapezeka ndi minister zinali zandani

  • @godfreyamos7452
    @godfreyamos7452 Před měsícem

    Iyiyi yolipilitsana in dollars sizoona , kaya who is setting this rules and regulations, kwacha now is becoming useless how will people cope ....

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 Před měsícem

    anthu inu phuzilani yesu chithyola mkunenayo ali bussy campain moti zulo anali ku BT inu mkuti agidwa ndindalama pa air port