CHIPANI CHA DPP LERO CHAWOPSYEZA BOMA KUTI LITULUSE REPORT LA KAFUKUFUKU WA NGOZI YA SAULOS CHILIMA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 13. 09. 2024

Komentáře • 353

  • @husseinmponda
    @husseinmponda Před 15 dny +11

    I agree with mmwenyeyo wa BT ku 2025 kwatalika kwambiri anthuwa achoke basi atikwana chisankhoso chisakhaleko ayi chifkwa aluza kale

    • @alphonsinaphiri4679
      @alphonsinaphiri4679 Před 15 dny

      Yomweyo a DPP apa mukubwera boo
      2025 kwatalika adzipita dzikoli litha ngati ma curtains

  • @user-ml4bl2ll2g
    @user-ml4bl2ll2g Před 15 dny +34

    Ambuye alemekezeke kuti sopano tili ndi opposition ku parliament, hopefully zinthu zisintha sopano,,wow!!!am very happy for that

    • @MartinGausi-rl5hb
      @MartinGausi-rl5hb Před 15 dny

      Llg meet😮 hi bed x BBC l
      😅
      Jinx😅v😊
      V😮😢 job
      L
      🎉
      😅
      Lv😮bh.ln.😅

    • @BrightonNdalama-x2b
      @BrightonNdalama-x2b Před 15 dny

      Am happy for u all guys this is what we call patriotic leadership 💪💪💪

    • @aaronbamusi9802
      @aaronbamusi9802 Před 4 dny

      Amene amapangisa kuti opposition ikhale yofooka anali nankhumwa uja chifukwa anali mnthira kuwiri

  • @MadalitsoMtambalika
    @MadalitsoMtambalika Před 15 dny +11

    Fire fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 mademo achitidwe ndipo chikangawa aona polekela

  • @ChristopherMakamo-ky4pq
    @ChristopherMakamo-ky4pq Před 15 dny +11

    Zikatele mademo ali pafupi ❤❤❤

  • @Sofi-p1v
    @Sofi-p1v Před 15 dny +27

    Sammeeir sagawa masiwiti

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před 15 dny +7

    ❤❤ God is good bolako tili ndi anthu akutiyimilira a DPP musatope and musasiyile pa njila god bless you all

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza Před 15 dny +12

    Nanu pangani mademo mesa nawo analowela mademo omweo aaaaaa

  • @TimothyKabumbuKendrix
    @TimothyKabumbuKendrix Před 15 dny +29

    Nkhani yabwino ma MPS athu, tonse tikhala pansewu mademo basi.

  • @user-fg1me1un8p
    @user-fg1me1un8p Před 15 dny +40

    DPP congratulations apa ndiye mukuonetsa kuimila a malawi

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os Před 15 dny +3

      Ndipo apitilize a DPP adziwe kuti dzikoli ndi la a Malawi si la achewa okha ayi

    • @LukaThawe
      @LukaThawe Před 15 dny

      Palibe Za kuyimila amalawi DPP chipani choipa kwambiri

    • @JusticeNyirenda
      @JusticeNyirenda Před 14 dny

      Zako zmenezo 🥱🥱​@@LukaThawe

  • @zinenanitruwah4778
    @zinenanitruwah4778 Před 15 dny +6

    Tiyeni kumademo. Chakwera asatuluke kupita ku China.

  • @edsonkamba3170
    @edsonkamba3170 Před 15 dny +12

    Welcome Dr George Thupuwela Chaponda as leader of opposition. Your opposition leadership reminds me of the old good days of Mbuya Gwanda Chakuamba as leader of opposition in Malawi. Kudos and bravo to your team Dr George Thupuwela Chaponda otherwise we have wasted good 4 yrs of opposition duties under Kondwani Nakhumwa (from 2020-2024). The past 4 yrs was just useless and waste of time. God bless malawi and God bless the leadership of opposition in malawi.

  • @alexgweje8610
    @alexgweje8610 Před 15 dny +17

    I agree with Sameer Suleman this Manyaka Government ( Mcp) must go we are tired of this nonsense 4sec Chikangawa

    • @tasmania527
      @tasmania527 Před 15 dny

      Mwachepa , MCP is a very big party. Munachipeza chipani cha MCP ndipo muzachisiya chili even stronger. Inu muzingokhalira kulongolola ngati ntchentche zikusangalalira manyi.

    • @FredoAbud
      @FredoAbud Před 15 dny

      ​@@tasmania527chikangawa oyeeeee😂

  • @Jessica-pg6ep
    @Jessica-pg6ep Před 15 dny +8

    Sulemani ndi zungu musaiwale zungu amanena chilungamo koma bodza amadananalo. Ndibwino kuvomeleza kulakwa kenako anthu amakukhululukila. Well done Mr Sulemani, DPP my Vote ❤

  • @CAPTAINMPHATSO
    @CAPTAINMPHATSO Před 15 dny +10

    Chikangawa he must go

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 15 dny +13

    Good message guys Chakwela you mast go watikwana

  • @AubreyNdeule
    @AubreyNdeule Před 15 dny +14

    Kodi zikuvuta pati kunena chilungamo,kaya ndizaboza anthu adziwe choona

    • @ChikupizgaKajawaMkandawire
      @ChikupizgaKajawaMkandawire Před 15 dny

      Simunamve kuti report atulutsa ndi aku germany?

    • @dilmayankam4052
      @dilmayankam4052 Před 15 dny

      Athu akuziwa kale chilungamo kodi muthu akakhala mfiti amavomera?kuma voti basi next year

    • @Yoxym
      @Yoxym Před 15 dny

      ​@@dilmayankam4052 Kwatalika amwene tiyeni tivote next month

  • @GeorgeChitapapata
    @GeorgeChitapapata Před 15 dny +12

    Much appreciate to the leader of opposition

  • @BistonMacheso
    @BistonMacheso Před 15 dny +9

    Akuziwa kuti chilungamo chinaziweka kare kuti anachita kupha anthuwo nanga akurephera kubwere poyera bwanji anthu amatopa ndiye ndatopa

  • @LangsonNyambalo
    @LangsonNyambalo Před 15 dny +4

    Game changer,ndipamene pati paonekele khoswe pa sindwi.Opposition timayembekezela koma imeneyi.

  • @RazackMofart
    @RazackMofart Před 15 dny +9

    Ku dpp kuli ma shashanso kani,,keep it up zawavuta a MCP

  • @SiffaFrackson-c8o
    @SiffaFrackson-c8o Před 15 dny +5

    Pamademopo pali bwino 😊😊izi zikuchitikazi zopusa srs

  • @hackwellkagolo6614
    @hackwellkagolo6614 Před 15 dny +4

    We can confirm Kuti Kondwani uja watitayisa thawi Kwambiri. Kususa kwake kukanakhala ngati Kumeneku zinthu i hope zinthu zikuyenda bwino kwambiri and Malawi sakanaonongeka ngati m'mene waonongekelamu. Komano MCP they make mistake kumuhonga Kondwani kuti asamawasuse koma azingopanga zinthu m'mene angathele and the end zawagwesa m'mavuto and the result no more kulamulila they are finish!!!!!!

  • @mkandawirem610
    @mkandawirem610 Před 15 dny +10

    We need report out,,,,

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p Před 15 dny +3

    Refreshing to see the opposition at play follow through on issues to logical conclusions. Checks and balances is your duty. #Malawi 🇲🇼

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Před 15 dny +2

    Kukanika kutulusa LIPOTI LA NDEGE 😂😂😂... Afiti 😅

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 Před 15 dny +1

    Mr chaponda job well done, siza Nankhumwa zija ayii

  • @MumbasnwaMumba-ih1xi
    @MumbasnwaMumba-ih1xi Před 12 dny +1

    2025 is far guys duleni ma battery mr chikangawa yooo 😂😂😂😂

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 15 dny +1

    Keep it up ma honorable ❤❤❤❤ this is what we called opposition

  • @henryibrahimsailes4638
    @henryibrahimsailes4638 Před 15 dny +3

    Anaba boma ndi ma demo achokanso ndi ma demo omwewo ndipo masatana amenewo akazangochoka mmboma azafinyidwe mpaka azabweze ndalama za misonkho yathu ndipo azafe imfa zowawa kwambiri naonse anthu oyipa amenewa

  • @DannielOnions-fy3dc
    @DannielOnions-fy3dc Před 15 dny

    Nice one thanks so much keep it up please

  • @user-dw9zi6bo3o
    @user-dw9zi6bo3o Před 15 dny +3

    Let the government know that as citizens we will not sit while they are abusing our patience. we will go in the streets till the recind

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Před 15 dny +13

    Achakwera ndi munthu ouma mtima alibe chifundo ndi umphawi womwe amalawi akukumana nawo

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Před 15 dny

      Nchifukwa chake Tembo adamusankha.adamuona kuti ndi oipa mtima.alibe chifundo ndi munthu.akungoyenda opanda chomwe akubwera nacho.

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os Před 15 dny

      @@user-wx1jt5fd2j U President wu anawutengera mphuzo. Sanatengere kuti a thandize Amayi ayi. Mbuzi ya ku Kasiya

  • @AbdullahSaeed-tg1cm
    @AbdullahSaeed-tg1cm Před 15 dny +7

    Now we know that there is an opposition....thanks to all opposition parties present here❤❤

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Před 15 dny +1

    Alone gadama...dicki matenje...twaibu sangala ...achiwanga... Sadiki Miya... Albert muwalo.. Alani witika .. saulos chilima.. and 8 others...my question is..how many people did MCP killed all together?? chakwela what is your problem??😭😭😭😭😭

  • @user-zg6mn8qr4m
    @user-zg6mn8qr4m Před 15 dny +11

    Dpp my vote ❤

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Před 15 dny +3

    Waiting allowance for UTM And Dpp 🥳🥳🥳🥳

  • @MarthaManda-p8k
    @MarthaManda-p8k Před 15 dny +6

    Chichewa chikifunika, ife sitikumva

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v Před 15 dny +4

    Ndipo ku china akukapangako chani chitsiru ameneyu mutu wopanda zeruwo

  • @frankdomingo1109
    @frankdomingo1109 Před 15 dny +7

    Thanks our readers these are the checks and balances we craved for... keep up the pressure

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 Před 15 dny +2

    Powerful Powerful Powerful mgwilizano❤❤❤❤

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 15 dny +10

    More 🔥🔥 DPP kumeneko ndiye kuzuka your only hope for Malawian 💃💃💃

  • @GabrielLitete
    @GabrielLitete Před 15 dny

    Am in support of Suleiman the guy is saying the truth enough is enough

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Před 15 dny +1

    Chakwela wapha chilima ujha chifukwa Cha udindo 😢

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi Před 15 dny +4

    Madem akhalepo akuzolowela asatanic amenewa

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Před 15 dny +1

    Chakwela... silent killer... manipulator... A man with flowery speech without action is called... chakwela...Mr chikangawa

  • @martinmoyo4211
    @martinmoyo4211 Před 15 dny +1

    Andale nonse zanu ndizimodzi. Panopa kwakucherani mdziputsitsa amalawi. Nonsenu simukonda dziko lino. You are just power hungrily. Mkavoteredwa basi anthufe mwatisiya. Nonsenu ndinu akapsyala. Panopa ndipo mwaona ubwino wa Chilima ndi UTM?

  • @rennieyoublessmewiththisso4981

    Kodi akuyendetsa dziko ngati farm yake bwanji hahahahaha you beta resign Mr Pule

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga Před 15 dny +6

    Anthu angapo takhala tikudandaula nkhani ya ka sound kamamveka pansipo koma simumatimvera bwanji??munanena kut mwamva koma mpamene mwaonjezera volume,,,why?!

  • @AishaChipande
    @AishaChipande Před 15 dny +7

    Ndiye tamuoneni chilima pa mbalipo😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 handsome guy

  • @alphonsinaphiri4679
    @alphonsinaphiri4679 Před 15 dny

    Ankayesa zida waonekera poyera Mr Chikangawa ayalulepo watitopetsa atitha mfiti m'busa wakupha chisatana chanyanga

  • @MatildaThamando
    @MatildaThamando Před 15 dny +3

    We really needed this kind of opposition earlier on

  • @Yoxym
    @Yoxym Před 15 dny +1

    I love you mama grace kwelepeta am your child from jokala tc Zomba

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola Před 15 dny +5

    Mafuta asakwele plz ndipo anthu otsutsa m'boma musalole makina oyesela mavoti chifukwa mukangolola ndiye kut iyo akhala kut avotelatu ndiye kut mavuto amenewa atikakamila ife tatopa nawo mavuto achekwela

  • @StevenFombe
    @StevenFombe Před 15 dny +4

    Carry on guys

  • @giftkanjuchi-qm8hf
    @giftkanjuchi-qm8hf Před 15 dny +1

    Kodi maulendo chakwera opita kunja amalawi tikupindulapo chani?

  • @samsonchiphaka3536
    @samsonchiphaka3536 Před 15 dny

    Congratulations DPP, UTM and AFORD now we can confirm that us Malawians we have strong Opposition in Parliament.

  • @AnusaNkhoma
    @AnusaNkhoma Před 15 dny +3

    Akwedza bwanji mafuta maulendo ali mkati mpaka ku China and America mmmm

  • @VeronicaMatiki
    @VeronicaMatiki Před 13 dny

    Exactly this is their own problem ukukudi kuyake Moto, they are taking us for granted, ku trip kopita president koma akumachita kutenga gulu for what and which Money are you using kukusa anthu onsewo wokakwela ndege, for what, and what will some of the people going to do there,,this is unacceptable they can't embazzle our Money Infront of our nose, Enough is Enough

  • @MustafaJafali-c3q
    @MustafaJafali-c3q Před 15 dny

    Good move let's fight together

  • @EmmanuelKumwenda-c2g
    @EmmanuelKumwenda-c2g Před 15 dny +2

    Kho anatichedwetsa awa nde anthu viva opposition leader

  • @AubreyGood-c8x
    @AubreyGood-c8x Před 15 dny +2

    DPP ndi chiyembekezo cha ife a Malawi

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Před 15 dny +1

    In politics nothing happen by accident... when is happening... just know that it is well planned by the way..

  • @SuzgoMkandawire-ss4kh
    @SuzgoMkandawire-ss4kh Před 15 dny +2

    Fire up my mpe

  • @omarmussa8282
    @omarmussa8282 Před 14 dny

    This is a good opposition not that time mumangomenyana nokha nokha muja.... Apa nde mwayamba zantchito keep it up

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před 15 dny

    Apm my vote

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Před 15 dny +1

    💪💪💪

  • @FrancisSangwa-c6r
    @FrancisSangwa-c6r Před 13 dny

    Palibe president amene sanayendel
    Ko kwambiri I wish Chaponda atiuseso ,mimene adafera Buleya Lure

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r Před 15 dny +2

    Mr Chikangawa Bola akanapanda kubadwa

  • @FelixWiskesi-d7w
    @FelixWiskesi-d7w Před 15 dny

    I would like anthu monga hon :suleman,jean ansah,Mr kaluwa kuti akhale ndi ma udindo akalu akulu ku DPP party I hope anthu ngati awa they can change life of malawians including Mr president author Peter wamutharika and hon :namomba ndi anthu olimba mtima kuteteza life and situations of poor malawians anthu monga ine omwe tili kumudzi

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Před 15 dny +3

    Mesa mumazichemelela kuti mafuta ayamba kubwela pa sitima yapatunda ndiyotchipa chakwela wagwila ntchito lelo mukuti mukweze chani kkkkkk munya osalola zoputsa plz akufuna apane amphawi

    • @Yoxym
      @Yoxym Před 15 dny

      Simunali mafuta menemuja chimangoyesedwa koma amafuna kunama

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu Před 15 dny +2

    Ndipo asatuluse zosephana ndizomwe a malawi akudziwa, coz a natiphera anthu.

  • @HalimaShafie-q9k
    @HalimaShafie-q9k Před 15 dny

    DPP yayamba kuonetsa kwaimilira amalawi dzikomo dad❤❤❤

  • @JustinWBanda
    @JustinWBanda Před 15 dny

    Sitikusewela kumene 💪💪💪

  • @kenmasta
    @kenmasta Před 15 dny

    Chi Nankhumwa uja ndamene amawononga dziko,lero mcp yakumana ndi opposition leader yeni yeni

  • @LucyKulemeka
    @LucyKulemeka Před 15 dny

    This one is really an opposition leader

  • @LushaWalance
    @LushaWalance Před 15 dny

    Please mukalowa boma groom Denis Mahata aswell he is king game changer

  • @DavidMtambo-e3b
    @DavidMtambo-e3b Před 15 dny

    Amwene please tiyen tipange mademo.koma apapa ndiye chaponda ayi takunyadiran zedi osusa, pitilizan kuimira amalawi osauka.

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf

    Tazimitsani motowo tikupysa Kono Inu wolemekezeka athu. Tikukutsatirani mwachidwi❤❤❤❤❤❤🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼

  • @MumbasnwaMumba-ih1xi
    @MumbasnwaMumba-ih1xi Před 12 dny

    I'm here for suleman

  • @patrickmuronya7486
    @patrickmuronya7486 Před 15 dny

    Sure Sulyman

  • @chrispinechirwa2655
    @chrispinechirwa2655 Před 14 dny

    Yes please zigawenga izi za mcp zisowe basi

  • @EnockBanda-r8k
    @EnockBanda-r8k Před 13 dny

    Bon kalindo Ali it agwirane nawo mania anthuwa😢😢😢

  • @glochilangwe936
    @glochilangwe936 Před 15 dny +1

    Ya asilikaliyo to DRC......ndi fuel from DRC yabaya koopsa

  • @DavidMtambo-e3b
    @DavidMtambo-e3b Před 15 dny

    Yes 2025 kwatalikadi, kodi inu osusa munali kuti inu tavutika nthawi yaitari opanda kutiyankhulira ku parliament.

  • @DavieKumbanga
    @DavieKumbanga Před 14 dny

    Oposition ija kuno yayamba kuwanvetsa nyunyunyu😂😂😂

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 15 dny

    Keep the fire burning Suleyman, 2025 kwatalikadi, tiyeni tiwachotse m'boma asatanawa before 2025,

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k Před 15 dny +2

    Akanakhala nankhumwa bwezi akungosekelela izizizi

  • @user-le3lr6jn7g
    @user-le3lr6jn7g Před 15 dny +1

    Panopa yayamba kuiwona opposition osati za Nankhumwa zija

  • @MarcFelson
    @MarcFelson Před 14 dny

    Chakwera kuyendayenda ndi m'mene ziriri kumlw sikoyenera
    But I don't blame him coz he do knw what he's doing and he is the state president without knowing the meaning 😢😢😢

  • @austinmussa6957
    @austinmussa6957 Před 15 dny +1

    we had a dead opposition..for 4yrs....thumbs up akamuna inu

  • @user-yh3dw6qu7z
    @user-yh3dw6qu7z Před 15 dny

    Nkhani ndi mademo adatenga ndi mademo,achokenso ndi mademo.achoke administration ya boma alinayo kutali.

  • @glochilangwe936
    @glochilangwe936 Před 15 dny +1

    Koma ndiye achoke pa 2530.00 kwacha ........ndiye tilire bwanji abale

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 15 dny +2

    Mudziyankhula chichewa kuti anthu ena adzimbva mawo

  • @MDKwinja
    @MDKwinja Před 15 dny

    Salaimana is the best fighter

  • @MorganMwikhala
    @MorganMwikhala Před 15 dny +5

    I like mkaladi uyu chilungamo chimamupweteketsa mutu kuchisunga

  • @aubreygrant99
    @aubreygrant99 Před 15 dny +2

    Appaa ndiye opposition yabwera

  • @muhabaulen7912
    @muhabaulen7912 Před 15 dny

    Ooh allah protect and guide all leaders how stand with Malawian peoples 🇲🇼🤲

  • @TshepangThabo-c4j
    @TshepangThabo-c4j Před 15 dny +2

    Chakwela apha anthu ndithu

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Před 15 dny

    l can't wait chakwera you can go

  • @maulidjames8542
    @maulidjames8542 Před 15 dny

    Apapa ndipamene mwayamba kuwa imilila a Malawi Dpp🤞