CRUISE 5 - CHIFUNO CHIFUNDO MLAMBE - CHIPEMBEDZO CHAMAKOLO ACHIKUDA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 5. 09. 2024
  • Chifuno Chifundo Mlambe ndi mneneri wa Chipembedzo cha Makolo Achikuda. Mnyamatayu adabadwa muchipembedzo chachiKristu ndithu ndipo adasintha mipingo kangapo mpaka kuyamba u Rasta. Kenako ataphunzila ndi kuwelenga bwino zazipembedzo adazindikila kuti makolo achikuda anali ndi njira yao yomwe ankapembedzera Namalenga, ndipo kuti azungu atabwela ku Africa adagonjetsa zipembedzo za makolo athu ndikubweletsa chiKristu, chisilamu ndi zina.
    Iye adaganiza zobwelera ku Chipembedzo cha Makolo Achikuda komwe akuti tsopano wakhazikika pamodzi ndi banja lake.
    Chipembedzo cha Makolo Achikuda chimakhulupilira kuti makolo athu akamwalira mizimu yawo imapita mmwamba ndikusanduka milungu. Anthu amoyo amatha kuthira nsembe, kuitana mizimu yamakolo yi, kuipatsa nkhawa zathu kuti ikatule kwa Namalenga.

Komentáře • 42

  • @Omwale
    @Omwale Před 5 měsíci +2

    ndalimba mtima, ineso zobwera ndazunguzi aaaa mbwerera

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 Před 9 měsíci +1

    Its time to get back brothers... long live funiro❤

  • @Malani41
    @Malani41 Před 4 lety +5

    Smart dude! Philosophically and spiritually correct! Eye opening!! !

  • @amtondo1699
    @amtondo1699 Před 4 lety +5

    Joab i should recommend you for making C5 live on Facebook,as your followers we used to be left behind,now we are proud,Thank you

  • @feranjikachingwe
    @feranjikachingwe Před rokem +1

    African spirituality on point. Thank you Chifuno for enlightening me.

  • @GeoffreyYusuf-w7w
    @GeoffreyYusuf-w7w Před 8 dny

    That book is a must have

  • @user-ny6qh5if3n
    @user-ny6qh5if3n Před rokem +2

    Grand rising king's and queens

  • @fenordmachaka1736
    @fenordmachaka1736 Před 4 měsíci +1

    Apa ndiye tikumvana kwabasi it gives sense

  • @salikilinje9674
    @salikilinje9674 Před 2 lety +1

    Am a Christian but this man wayankhula mfundo zomveka bwino and a very good argument. Well spoken

  • @user-bg4ec7xz2v
    @user-bg4ec7xz2v Před rokem +1

    Your 100% brother anthu saziwa akungotchula za Jesus anazela iwowo kalelo osati pano akungosatila za zungu

  • @vidmore2180
    @vidmore2180 Před 4 lety +3

    Frank, this is different and I have liked it so much

  • @tembodavidson2640
    @tembodavidson2640 Před 3 lety +1

    Well spoken Mr Chifuno Chifundo Mlambe well narrated Africa we need to wake-up.......Vukani MaAfrika......................kudos Joab nice job.

  • @user-lz1uy7yv5w
    @user-lz1uy7yv5w Před 4 měsíci

    Ndiwe Rastar ndakuona

  • @vide2179
    @vide2179 Před 2 lety +1

    GOT U BRO LOUD AND CLEAR 🤗❤🤗👍👏👍👏

  • @ririvilla1423
    @ririvilla1423 Před 4 lety +8

    If only tonse tikanamaganiza ngati this guy Malawi will be a better place we have been brainwashed by azungu. How do we contact achipembezo cha makolo? Tingawapedze kuti?

  • @fynessgasalamu3078
    @fynessgasalamu3078 Před 4 lety +6

    So deep wow tiuzeni ku Lilongwe ulikuti mpingo umenewu?

  • @HassanBandah-wd2ox
    @HassanBandah-wd2ox Před 2 měsíci

    Ndagwirizana nazo

  • @Skasompha2016
    @Skasompha2016 Před 4 lety +3

    The spiritual awakening

  • @josephchisomo7450
    @josephchisomo7450 Před 4 lety +1

    This is heavy teaching muli uthenga omveka muchiphuziso chachikhalidwe chachikuda

  • @nditumenichagunda4192

    Ku zomba mumakumana kuti tilowe zimenezi

  • @simonijuliyo1294
    @simonijuliyo1294 Před 3 lety +2

    Umboni uwu tigawane momvesa bwino, makolo ndi mulungu wachiwiri, tikawapangira zabwino amatidalitsa, zikomo chifukwa cha program yapamwamba iyi ndayikonda zedi

  • @FatsMagalasi
    @FatsMagalasi Před 3 měsíci

    Nsalu zovala zokwela zimkuza mau zosemela ng'oma tuimbazi opanga mzungu

  • @josephsaka6412
    @josephsaka6412 Před 4 lety +2

    language yaku south africa,nzungu amati mulungu

  • @vidmore2180
    @vidmore2180 Před 4 lety +2

    So deep

  • @giftfombe873
    @giftfombe873 Před 3 lety +2

    Well spoken

  • @klemwaterman
    @klemwaterman Před 6 měsíci

    zathu zeni zeni

  • @noxiousgondwe4287
    @noxiousgondwe4287 Před 4 lety +3

    Wanditenga mtima mbaleyu komaso akunena zoona

  • @sulaylawashali4522
    @sulaylawashali4522 Před 4 lety +1

    Zimene akunenazi ndizoonadi

  • @sillahkachomoza9349
    @sillahkachomoza9349 Před 4 lety +1

    Ndazikonda izi

  • @klemwaterman
    @klemwaterman Před 11 měsíci

    Tiupeza kuti

  • @lamackbanda6869
    @lamackbanda6869 Před 3 lety

    Komatu izi ndizoona kwambiri tikuzithaya tokha chikilisitu sichatu,chisilamu sichatu ndizoona. Frank ukuyita kwambiri ukuthenga anthu oyenela ndi nkhani zabwino.

  • @EmercianahKasiku-en6hl

    Ku Lilongwe timakumana ku bortanic garden pafupi ndi parliament

  • @giftfombe873
    @giftfombe873 Před 3 lety +1

    Wachikunda

  • @lamecknjowe909
    @lamecknjowe909 Před 3 lety

    Reality talk adhawa amatha

  • @kondwanitembo386
    @kondwanitembo386 Před 4 lety +1

    Joab ndi Chiphaliwari

  • @godixjvogausi9891
    @godixjvogausi9891 Před 3 lety

    Ndizoonadi

  • @pattaika3507
    @pattaika3507 Před 2 lety

    I'm convinced,koma funso langa linali lokuti ndekuti samagwiritsa ntchito bible?kapena ili ndibukhu lawo?koma akukambazi ndikugwirizana naye100%
    where and how can I get his book lomwe analembalo?

  • @sydneysilo9396
    @sydneysilo9396 Před 3 lety

    I want that book

  • @Sebuzuna
    @Sebuzuna Před 4 lety

    Joab, zuoneka kuti akulu wo avala mtanda. Kodi mtanda wawowo ukuimirira chani?

  • @christopherkamaliza6379

    Joab I need that guys number please please