Video není dostupné.
Omlouváme se.
Ngongole za Malawi zachulukitsa. Abwana anapita kunja kopempha ndalama.
Komentáře • 168
Další v pořadí
Automatické přehrávání
Malawi Attorney general wa chinyengo; Akuchita kusankha milandu yopita ku khothi.Bakili Muluzi TV
zhlédnutí 8K
President of Malawi Lazarus McCarthy Chakwera, shares his vision for a world free of NTDsUnitingtoCombatNTDs
zhlédnutí 43K
ONLYNET Challenge s Mich Sakem a Dodem!Horis
zhlédnutí 177K
Girl’s compassion turns foul dog into cute furry friend #shortsI migliori trucchetti di Fabiosa
zhlédnutí 6M
ОБЯЗАТЕЛЬНО СОВЕРШАЙТЕ ДОБРО!❤❤❤Chapitosiki
zhlédnutí 26M
Friends Supporting FriendsRed Bull
zhlédnutí 20M
Chakwera Family and Vitumbiko Mumba; How they got richer with govt taxes?Bakili Muluzi TV
zhlédnutí 25K
Asilikali alanda boma ku Niger chifukwa chani?Bakili Muluzi TV
zhlédnutí 53K
Mpungwepungwe pa kudwala kwa Mary Chilima ''zowona mpaka 312 million''Hanifa Mw
zhlédnutí 44K
Malemu John Tembo; Tidzamukumbukira bwanji ngati amalawiBakili Muluzi TV
zhlédnutí 59K
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔Jimmy
zhlédnutí 109K
ബംഗ്ലാദേശിലെ സംവരണവിരുദ്ധ കലാപം | Bangladesh Protest Malayalam | Sheikh Hasinaalexplain
zhlédnutí 341K
ZILIPATI PA MIJ FM-KUCHEZA NDI OMWE ANAVULAZIDWA NDI NACHIPANTITicheze Amalawi
zhlédnutí 21K
Asilikali amakatani kumanda a ku Dzaleka refugee Camp nthawi ya usiku?Bakili Muluzi TV
zhlédnutí 50K
Mzibambo wina kuMangochi AKUKODZA USIPA chifukwa chogona ndi akazi amwini, Nkhani za m MalawiMalawi Page
zhlédnutí 22K
11 year TRICKS Magnus Carlsen? 😱 #magnuscarlsen #chessChessBase India
zhlédnutí 10M
Poslední Kdo Opustí CYBERTRUCK ho Získá!FIZIstyle
zhlédnutí 114K
Chocolate Screwdriver! 🔩 Always have the right tool for the job! #amauryguichon #chocolateAmaury Guichon
zhlédnutí 34M
Arianka přinesla ženichovi a nevěstě prstýnky! 😱❤️Tary
zhlédnutí 482K
Gyms in 2024☠️Noel Deyzel
zhlédnutí 17M
Eleftherios Petrounias helped by Arthur Zanetti = epic gala moment ❤️Olympics
zhlédnutí 45M
Usogoleli olilisa kwambiri wa chakwera😢😢😢 Malawi will never forget you
😢😢😢😢
Perfect
I like you Bro , you know how to analysis things . keep it up !
🙏🙏🙏 timakusangalalilani achikulire
I like you brother thanks you so much
Dr chakwera and doog aaaa
Thanks God bless you
Munthu wankulu ulemu wanu 👏👏👏
Zikumveka ndithu munthu wankhuru kumeneko ulemuwamu bwana ...ndizoona ndithu kutikodi awa analindani .big guestion sir
Big man ndinu katundu omanga ndi mawaya afukuleni musasiye tiziudziwa usiru wawo akupangawu
Bro i see you a very good analyst, kunena zoona tikifunikadi ma investor enieni kut tiseve zambiri
Boma ili nde zero pa zero.😢😢😢
Zelo pa ten
My man,,,,,,,,,,you deserve,,, much respect,,,,achakwela atipha awaa
Bwanji angotula pansi maudindo awowo tatopa nawo ife anthuwa
The king of history
Dziko lingatha zimayenda ngati Baibulo. Mwawonjezatu pamenepo
Thanks u boss
Koma iwe ndikatundu madzi😂😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉
🤣🤣🤣🤣🤣
Well conclusion bro, that is the fact and reality let's bring people who have something better not mulimi all the way from asamunda no man please Mr president
Chitini chopanda kanthu chimatsokosa kwambiri ndiye mwazioneratu nokha. Ndimayesa amanama that an empty tin makes noise.
Thanks bwana pakusakatula maganizidwe aa anthu
Tenaon amenyo nchewa wasiru amneyo wanonga Malawi 🇲🇼 akuyesa kuvena gule
Wa udindo aliyetse adziba,, akhulukidwa zili ku Malawi,,,pano palibe kuopa kuba chifukwa chikhululuko chilipo,,,koma tsoka ili kwamuthu ovota palibe chimene chikumukomela muthu otsauka.
😢 iiih koma ine chakwera 😢😢
Salute bro
Achakwela angogwidwa kwachotsa pa u president 90 minutes eterber wakuba
Kkk big man kutsitsa mfundo zabwino
I used to LOVE Boma ili mbuyomo koma pano..
Aaaaaaaa Zosayenda uyu or atangoyerekeza kuyenda wapasi nditha kusanduka DAVID . mwala utha kugwira ntcito
Keep it up big
Kusowa kolima chifukwa choberekana ngati ntchentche ...palibe chomwe amalawi angapange pawokha .
You are king 🤴 of history in our country 'kma chilungamo China kupweteka ndithu
Malawi tili ndi madzi ponsenponse koma boma limangoganiza zokuba ndalama zathu iwo kumalemela
Zomwe zimandimvetsa Chisoni ndizoti mtsogoleri wadziko akamalephera kugwira bwino ntchito yake pali anthu ena osaukisitsa omwe akuponderezedwa ndi mtsogoleriyo, muwaona akuimbira mmanja ndikumamuchemerera mtsogoleriyo. Ndife olilitsa zedi.
BIG 👍
Respect to you my brother
We need to vote again awa zikuoneka Kuti zawakanika basi
Komaso trip ya President ya ku Malawi anthu ambiri,there is no war on Malawi but security yambiri
Achakwela mukhululukiletso ma prison amene alibe mulandu wakupha,,ogwililila,,ndi opyanya nyumba please atuluseni
Mumatha man keep it upp
Kupempha like akupenpha chachikhumi ,he must go!!
President cakwera tidzamukumbukira kuti anali wakuba wakupha oononga.
Mupange video yoti ma donating a Cyclone freddy anabwera angati ?kikikiikiki Malawi 🇲🇼 😀 🇲🇼 wanthu akulowera ku ntchire. ♥️ Mapeto ake mitengo it itha, koma nawonso they are failing to empower Malawi 🇲🇼 😢 Shaaaaa.
Anazolowera kusonkheledwa ndi mpigo kumati zabusa kuparsidwa chopeleka kudya zachinkhumi
Well done brother koma tafufuzaniko za ma passport please malawi wawonongeka wuyu pakufunika ma demo anyone chakwera ndi mphawi wa chabe amene sangatukule ziko
Ntundu umenewu sibwino kuwupatsa u president m'malawi muno chifukwa ndidzilombo, a malawi tinapanga mistake
Always I disagree with you but now totally! totally agree with you accordingly
Bomali ndilasatanik coz ngongolezimenezo azabweza ndimagazi amalawi ndichifukwa akusowesa mankhwala zipatala ndi chakudya Kuti amalawi azimwalila azipeza ziwalo ndimagazi sure
Boma likulamulidwa ndi zigewenga chakwea ndiwakuba
Kkkkkkkkkk Eeee!!!!!! Koma ndie kwapephedwatu...kungozolowela Chachikhumi.mpaka kukapepha Company yopanga juice.
Amakakumana ndi Sattar ameneyi
Iyeyo anali mbusatu basi kenako president
Uyu mumati chakwerayu ndi chitosi basi aah!
Akhululuke ndithu Chonde mulungu dalitsani Malawi
I think in future Malawi will be part of zambia because it's too much now
Chakwela ndi mbudzi😅
Mwayi okwela ndege alibe kkkk
Respect 🙏
Tht true bro
Chakwera mtayeni opanda nzeru
Please president chakwela leave presidency and go
Mumatha abwana awa anali ndani awa😂
Mr Atupele anayankhula kale kuti lenara samupasa bus or galimoto,
Chimene tizawakumbukile agaluwa ndi kuba kowopsa basi ndikupempha pempha. Sindisintha Chichewa changa, kuti mwa Chakwera mulibemo ubwino, munthu wotumidwa ndi satana angapange zokhumba anthu? Mesa akupanga chimene tate wakeyo akufuna? Dont expect anything good from this heartles presdent.
Kudzavuta kumuyiwala chakwera ndi team yake wagwiritsa a malawi mafuwa a moto kudzera mu bodza. Ndithu anthu awa palibe choti angapange choposa kupemphetsa nkumagawana ndalamazo mu team mwawo
Kodi awa anali ndani?😂😂😂😂 Yankho mulipeza nokha😂😂😂😂
Sibola atsamundawo asatenge malo anga 😢ndikuopa
Big mumakwana koma ndaseka mpaka nthiti kuwawa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 ndiye mwati chakwela amaganiza bwanji???? Eeeeeee
Mmmm inupenapake paja
Ndinu audf
Atsogoleri a mu africa lero ayamba kutseka zitseko za atsamunda ndipo ali pa mgwilizano wochotsa US dollar mma bank mwao. Pomwe President wa Malawi Ali busy kupempha kwa ma oppressors. A disgraced man. Experience alibe zoona.
Koma nkhawa zanga ndi ndani yemwe angatipulutdr
Program iyi imandisegula maso, ndikunditsuka ubongo
Anali mkulu wampingo uyu apite akatumikile nkhosa zake
kutipweteketsa basi olo misewu ya mamidzimu osapalanso yakumbikakumbika nde ndalamazo akungodya kwawoko ayiwala kuti adzafunaso anthu
Chakera awononga ku malawi bwanji mulungu tutandizen tuuu koma ndalama zimenez abweza ndan kod 😢😢😢😢😢😢😢😢😢
Chakwera asiya dziko la malawi lili pamoto
Is true he think like mana like time of Moses
Koma ndiye Malawi tifapo 2 chifukwa anthu amenewa akungoba ndalama basi
anyway big timakunyadirani
Kwathu kuja amene anatiloza akanatikhululukira 😢
nothing to say you man you deserve medo koma ndimafuna nditakuona uli ndimawu aboh
Ine sindizabweraso ku malawi kulimose kulimanda ku malawi ndizataniko ndizafe. Ndi njala ine ayi Malawi 🇲🇼 anavunda kwambir chakwara zeru alibe wawononga malawi
Simumati mukufuna kuona zina ndizimenezotu
Ichi ndie ayi chichoked 😢😢
I wish to have chakweras number so that I can send this to him, # this is the most corrupt government in Africa
Tcheya mani wa anthu ovutikaa kkkkkk
Mkulu uyu ndi wa BaBulo basi 😂😂😂😂😂🤣
Chekwela ndi mbudzi yamunthu mutu wake sumakoka mutu mwake mawaya anaduka
akungofuna ma angodya ndalama basi
Kkkkkkk koma ndasekaa kkkkkkkk
Kodi iwowo anali ndani kikkkkkkk
Chakwera why 😢😢😢
Ubulutu wa chakwera suzatha hahaha
Kulimbana ndi chakwera bola kumwa temeki
Muyimbireni salamba nyolonyo uyu muzimuona nkhope yake nyau yeniyeni.
Chakwera ndi anthu ake nzeru alibe ndipo kaya ndinene bwanji?pena ndimalakalaka ntakhala ujeni ndikuthana nawo andale opusawa
Mnyamata wamzeru uyu, ulemu wanu
Kkkkk k zoopsa abuse opanda nzeru okuba cisiru mbava yachabe chabe mbuya wakumidima okumwA MAGAZI
Kkkkkk km man mwayakhula masikini aulesi kkkk ndie mwat chakwela al mgula lamasikini kkkkkkk
Ndinanena kale kuti mmutu mwa mkulu ameneyo muli mamina okhaokha komanso okuba ndalama za a Malawi
Kungopha basi chakwelayi
Amalawi zafika posauzana
Muluzi anali makina mseu wathyolo mulanje its like built yesterday
Kmans mumamunyoza kut sangapange kanthu koma mwamva lero zimene muluz anapanga ķwa anthu amene amazitsata
Kuipa uku ndithu zapanda ubwino uliomse