GURU LINA LONYASIDWA LAWOPSYEZA A PRESIDENT CHAKWERA LERO KUTI ACHOTSE PA MPANDO A ZIKHALE NG’OMA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024

Komentáře • 51

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 Před 28 dny +6

    Kumkuyu iwe galu kwabas iweso ukuyenela kuchoka sutha ntchito ai mbalame yenyen gwape

  • @jacomw5797
    @jacomw5797 Před 28 dny +7

    Kunkuyu amazitenga dolo poyankhula while ku immigration zinthu sizikuyenda

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf Před 28 dny +2

    akunkuyu ndi a chakwera chonde muwuzane kuti pantumbo pa chamanu zitsiru za anthu lino ndi dziko kapena mudzi wakwanu boma la zitsiru zokha zokha

  • @Yoxym
    @Yoxym Před 28 dny +3

    Achoke 💪💪💪💪💪💪💪💪

  • @user-ii2sh1mz3r
    @user-ii2sh1mz3r Před 28 dny +1

    I think the problem we have with our president is , ali soft kwambiri , and ali ndi chifundo kwa even ma ministers ,so chimene ayenera kuziwa church ndi dziko ndi zosiyana ,Iwo asamanyengerere munthu Kaya akuoneka bwanji,

  • @ChristopherMakamo-ky4pq
    @ChristopherMakamo-ky4pq Před 28 dny +3

    Apule achoke basi

  • @amosmuluwane4182
    @amosmuluwane4182 Před 28 dny +1

    Azimaywa amazipangitsa okha akasankhidwa palibe chomwe amachita mwachitsazo phungu wa ncheu bwanje North akhala paunduna zaka zonsezi koma dela lake ndilovesa chisoni pamudzi omwe amachokela mayi amenewa school idasasuka denga Chaka chatha koma mpaka panopa school iyi sinakhomedwe amene mumadutsa pamudzi wa akaiya kupita ku balaka kapena kugolomoti mundivomeleza phunguyi ndi nase chaola ndoko

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před 28 dny +3

    Ma passport a fake a Nic Chakwera

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 Před 27 dny

    Koma pamenepa pothandiza school President Chakwera timuyamikire osamangosusa zili zonse chifukwa cha ndale pena zabwino kumayamika so zonse munthu sangakhale 100%

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi Před 28 dny +1

    Chikangawah party ichoke basi

  • @BillyKalambo-jx3vf
    @BillyKalambo-jx3vf Před 26 dny

    Vuto si zikhale ng'oma koma galu uyu otchedwa Chakwera tiziti iyeyu sakuona kuti immigration zinthu sizikuyenda contract angapereke kwa mwana wake Chenjela Nick ndi makutu akowo okhala ngati bowa masiku akuthera mbuzi iwe

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 Před 28 dny +1

    Achosedwe watikwana galu ameneyo even chakwera achokeso sitifuna .. futso koma zikhale ng'oma azalola kuti achoke si nankha mcp yakwawo nankha kkk

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n Před 27 dny

    Anthu sakuziwa zimene akufuna it's straight forward isue chajwera achoke basi

  • @VictoriaWilly
    @VictoriaWilly Před 27 dny

    Kunkuyu nayenso achoke, onse achoke akuononga dziko la Malawi. Tatopa ndi boma labodza ili

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 Před 27 dny

    Apm akubwera kudzakonza dzikoli tazunzika mokwana 4yrs ngati 400 yrs?

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s Před 27 dny

    Chakwerayonso achoke palibe chichita iye panopa chilichonse ndichosokonokera

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd Před 27 dny

    Ufune oti uwapusitse Chakwela wamva

  • @DalitsoAlufeyo
    @DalitsoAlufeyo Před 28 dny +3

    Ndipo zoona

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf Před 28 dny +2

    boma la zitsiru zokha zokha ili zigawenga

  • @MosesMkandawi-e2v
    @MosesMkandawi-e2v Před 23 dny

    Palibe chomwe akuchita zikhale ng'oma pakuti iye ndi chakwela ndi zigawenga nde akuba okhaokha safusana kuti chithu ichi wachitenga kuti pomwe ose ndi akuba,,, koma chomwe amafusana ndikuti kodi ichi unakaba kuti bas,, ndee chakwela sangamuchotse zikhale ng'oma pakuti zonse zimene akupanga iye amapanga limodzi ndi chakwela Kuba kupha katangale akupangila limodzi

  • @PatrickChagaka
    @PatrickChagaka Před 27 dny

    Awatu palibe chomwe akupanga boma lawoli onse ndizitsiru zokhazokha zikhaleyo sangasokoneze zinthu payekha alipamodzi

  • @user-ev4or2kg4z
    @user-ev4or2kg4z Před 28 dny +2

    A CDED please now take things seriously
    Please we are suffering like God created people from to suffer

  • @PanganoChilambe
    @PanganoChilambe Před 27 dny

    Ok, kondi munthu angapite kusuku ya ukachenjede asanate ku pulaimale? izo ndindale zaku Malawi mukafu kupitiriza kumba mumatenga omphunzira amenewa why thandinzo yanuyo siyambe muchipatara olo kundende,ku pulaimale? Osatimvetsa mutu ife Malawi timudziwa musateye ndalama zoti ana amasiye asamalike ndeye nkhumbo langa ngati Malawi. Koma ndati mudziwe kuti mawa silero.

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 28 dny +1

    Bora pamenepo achokedi saziwa ntchito amalawi tikuvutika

  • @MirriamKambale
    @MirriamKambale Před 27 dny

    Boma mpaka kumapanga passport ya feki?Nigerian mmodzi kumaposa boma la malawi?coz feki passport yopangidwa ndi Nigerian individual ilibwino kuposa yopangidwa ndi boma la Malawi.

  • @KawawaIbrahim
    @KawawaIbrahim Před 27 dny

    Kodi chifukwa chani maudindo kumangopasana anthu oti saziwa ntchito

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Před 27 dny

    😂😂😂😂 ndalama kulibe nanga zomwe akuba m'boma akuba kkuti ndalama zoooooo tatiwuzani

  • @user-fg1me1un8p
    @user-fg1me1un8p Před 28 dny

    Keep it up comrades atule pansi udindo

  • @NosparPalamelagee
    @NosparPalamelagee Před 27 dny

    Iweso kumkuyu uchoke

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e Před 28 dny

    Enanu mkumat boma nd lomweli kma likulephera kukonza zinthu shame😢

  • @MarthaBango
    @MarthaBango Před 27 dny

    Anthu amatopatu amafika poti topi 😂😂😂😂

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před 27 dny

    Ayende basi aaaa atikwan

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 Před 28 dny

    Boma la Chakwera zavuta ndithu 😂😂😂😂😂

  • @JamesGondwe-l6b
    @JamesGondwe-l6b Před 28 dny

    Boma, limapanga chidodo kwambiri, pop anga ziganizo.

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Před 28 dny +2

    Achoke kamajeketi zikhale Ng,oma foseki Thabo chakaka nayeso alibali ya MCP sakutithandiza ayi nayeso foseki

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před 28 dny +2

    Kamajekete apite 😮

  • @kingthymus4613
    @kingthymus4613 Před 28 dny +1

    makosana😋😋😋😋

  • @user-re7fo3be2z
    @user-re7fo3be2z Před 28 dny

    Achoke kumene

  • @thomasbodo4099
    @thomasbodo4099 Před 28 dny +2

    Boma lalephera so mkuyu asamati president razarus mphamvuzo tinangomubwereka osati adzitumbwanazo apa

    • @JafalihMitawa-u2d
      @JafalihMitawa-u2d Před 28 dny

      Mmmh nawesotu uzilankhula bwino wava, alindi mphanvu basi Chakwela.

  • @user-bg5oe1sl8n
    @user-bg5oe1sl8n Před 28 dny +1

    😂 ndpo live

  • @AllieJonassi
    @AllieJonassi Před 28 dny

    Achakwela awombeledwe

  • @PatrickMailos-j6u
    @PatrickMailos-j6u Před 28 dny

    Athutu amanena kuti mcp sizithu

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Před 28 dny

    Musanapange upload muzimvera kaye zinthu zanuzi, this is very unprofessional.

  • @LasieMolebatsi
    @LasieMolebatsi Před 28 dny +1

    Anyamuke

  • @adamabiyen5079
    @adamabiyen5079 Před 28 dny +1

    Bolan pamenepo