Chakwera Family and Vitumbiko Mumba; How they got richer with govt taxes?

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024

Komentáře • 122

  • @mustafamaquissuel4636
    @mustafamaquissuel4636 Před rokem +2

    Kuchokera kuno ku Mozambique ndimasangalasidwa nayo program yanu❤❤❤

  • @owenskabazanechiumia3543

    Kumeneko ndi kutha kwake chifukwa mulungu si James amphawi akuvutika komano iwowa azinjoya ndikuba, sapita nazo patali mark my words

  • @user-vb5dh8ip6g
    @user-vb5dh8ip6g Před rokem +1

    aMalawi Ife ndife amene tikugona awa akuba ndalama zathu zomwe after wards akumabwera kumatiponyera ndalam zathu zomwe
    Malawian when are we going to wake-up Pano na activists akumangidwa tidzalapa liti
    My God

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před rokem +3

    A Malawi tili dyooo ngati akutimeta ntundu onvesa chisoni

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 Před rokem +2

    Tili pa mavuto kwambili AMALAWI 😢😢😢😢

  • @bayview4554
    @bayview4554 Před rokem +2

    Aziba bas Mesa tamusia DC yekha akumangidwa tiziona uku ndikuyamba

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 2 měsíci

    Amalawife ndife anthu opusa kwambili ...tikungoyang,anila chakwera akuononga ziko

  • @JacksonNdauma-yc6mp
    @JacksonNdauma-yc6mp Před rokem

    Koma kut mavuto amenewa athe nkupanga chan tsano! Chifukwa ndalama zikungopita Kwa anthu olemela kale ovutika nde kulira nd umphawi.. kuthyolo uku anthu akulira nd njala... Shaaa Malawi!!!

  • @user-gl2tj5nj8d
    @user-gl2tj5nj8d Před rokem +1

    Pena ngati ndipite ku state house komweko

  • @user-zx1zs8el7q
    @user-zx1zs8el7q Před rokem +1

    U are the best ❤ulemu wanu bg never give up pitilizan kutiziwitsa

  • @user-pt1fy3qg4u
    @user-pt1fy3qg4u Před rokem +4

    Never give up bro ❤

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Před rokem

    Uyu nde kaswiri guys respect nthawi zonse ndimakunyadilan bg mn

  • @eastergondwe5511
    @eastergondwe5511 Před rokem +1

    Team Vitumbiko Mumba pheee

  • @samuelsamirawjohns2671
    @samuelsamirawjohns2671 Před měsícem

    Bina Malawi mbwe makutu Jule busy kupulikizga utesi wadoda ili....muchali mukupusikika nividimbiko vya doda la utesi nge ni ili

  • @user-xc1xt2qd7t
    @user-xc1xt2qd7t Před rokem +1

    Keep up bro inu mumatha💯🇲🇼🙌👍✌️

  • @professorsafuta3936
    @professorsafuta3936 Před rokem +2

    You're always the best mr

  • @HunchoMgoms
    @HunchoMgoms Před rokem

    Our best Chanel

  • @user-nx7yz4qo8f
    @user-nx7yz4qo8f Před rokem +1

    Soka kwaife aphawi,mawu tilibe

  • @fefa2050
    @fefa2050 Před rokem

    Koma Bwana inuyo ay munabwera good explanation

  • @ganizaniyonam5041
    @ganizaniyonam5041 Před rokem

    Akulu nkhani imeneyi ndiyayikulu takasumani ku court tikakuthanizilani

  • @JahcureTepeka-mv7vv
    @JahcureTepeka-mv7vv Před rokem

    wasilikali waku Malawi mbambula kusambila that is main problem

  • @emanuellbanda4028
    @emanuellbanda4028 Před rokem

    Good information boss akubatu azampha anthu ngiumphawi akanganya awa amtuluse Boooon Kalindoo!

  • @innocentmanyera1861
    @innocentmanyera1861 Před rokem

    Ukatonthora umwe madzi ayise. Mtima ukuwawa kwambiri koma uchira easy

  • @bobkenneth2947
    @bobkenneth2947 Před rokem

    Ndikamuganizira President Chakwera ndi leadership yake mtima kuwawa kwambiri i think tilibe president ku Malawi kuno.

  • @hopeskafumbi2246
    @hopeskafumbi2246 Před rokem

    koma a president amati anthu aziwauza zoona izi akudikilanso anthu zomwe mwana wawo apanga zi zamanyazi

  • @enockdaisi1306
    @enockdaisi1306 Před rokem

    Zikuoneka ngati university of malawi ikuphumzisa umbava chifukwa onse ogwila mboma from university of malawi they are thieves

  • @AustenBushiri-ti5ny
    @AustenBushiri-ti5ny Před rokem

    ALWAYS RESPECT 🙏 MR

  • @dartweedzmdawali5063
    @dartweedzmdawali5063 Před rokem +1

    Tina yimbila mfit mmanja bas

  • @fefa2050
    @fefa2050 Před rokem

    Thanks for update

  • @user-zx1zs8el7q
    @user-zx1zs8el7q Před rokem +1

    Always respect u 💪🔥

  • @user-rd3iz2ou6g
    @user-rd3iz2ou6g Před rokem

    Atifuna pompano anyapapi amenewe.
    Ndipo akupanga dara akudziwa kuti or atachoka boma akudziw kt sazamangidwa 😭😭😭

  • @bwenzkatswiri3565
    @bwenzkatswiri3565 Před rokem

    Ndiye titan

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Před rokem +1

    BIG 👍

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 Před rokem

    Abwana that's why yesu anati za kaisala pelekani kwa kaisala izi mulibe cholowa pamaso pamulungu awa alemela ndi misokhu ya amalawi away

  • @Satier47
    @Satier47 Před rokem

    Ulemu wanu big 😮

  • @dellingsmunthali2669
    @dellingsmunthali2669 Před rokem

    Vuto kuno kumalawi mantha bwanji asilikari angoranda boma?chizumayoso mmm palibe chikuchitika"

  • @hanifuyahaya9064
    @hanifuyahaya9064 Před rokem

    Ina Lillah waina lillah rajiona tamva tipasileni za Maiko ochenjera monga Gabon

  • @innocentkandulu2825
    @innocentkandulu2825 Před rokem

    kuMalawi sizilongosoka PETER MUTHALIKA NDIMUNTHU BASI

  • @Syakinongwa
    @Syakinongwa Před rokem

    Enya...tukhumba Refuge Camp ku Chitipa. Ise, musewu tikuukhumba yayi. Tiri vindere ise 😢I 😢😢

  • @bubakalimustafa
    @bubakalimustafa Před rokem

    Thanks

  • @arambicgj3524
    @arambicgj3524 Před rokem +1

    Infomartive🎉

  • @ganidaitoneairone6973
    @ganidaitoneairone6973 Před 2 měsíci

    Kuno ku mozambique timasagalalananu mumakwana

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 Před rokem

    aululeni asatanawa kukulitsa umphawi io akunjoya

  • @humairamalombe295
    @humairamalombe295 Před rokem

    Thenks bro
    Ku Gabun kod zikut bwanji kumeneku

  • @user-uw8gu4tc1y
    @user-uw8gu4tc1y Před rokem

    Big up bro! Watching from Pretoria

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před rokem +2

    Thanks but waiting for the analysis of elections in Zimbabwe, coup in Gabon and new wagner boss

  • @ishmaelmkuluma2013
    @ishmaelmkuluma2013 Před rokem

    Uhuu

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 Před rokem

    All respect

  • @user-og2qx4cq7v
    @user-og2qx4cq7v Před rokem

    Pathako chakwela ndi mwanawake mbava yothelatu

  • @CharlieJimmy-sr1ie
    @CharlieJimmy-sr1ie Před rokem

    Kodi Martha chizuma akadalipobe pa udindo wa ACB??? Nanga bwanji angoti ziiii

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před rokem

    A opposition ali busy kulimbirana ma udindo olo mademo osapanga endorse akuti koma akufuna kudzalamumulira ,adzakuvoterani ambuyanu 😔😔😔

  • @WillieMakoza
    @WillieMakoza Před rokem

    Mug cup, k25000 belt, k 75000vest, k110000....police food ration scandal, unali pheee...osaysnkhulapo apa bwanji? Anyapapi inu

  • @juniorbvumbwe9822
    @juniorbvumbwe9822 Před rokem

    respect bwana never give up

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 Před rokem

    The best of story

  • @RobertChipatala-ow9vn
    @RobertChipatala-ow9vn Před rokem +4

    Amalawi anzanga tiyeni tisataye nthawi ndikumatsatira anthu awa a ndare popeza onsewa ndiamodzi. Tisamaiware kuti dpp yomwe akumaipangira campaign akuruwa ndiyomwe ija tinaichotsa m'boma pazifukwanso ngati zomwezi. Chofunika apa ndichakuti tirimbikire pa zochita zathu kuti tipeze zomwe timazisowa pa miyoyo yathu. Tangoganizani kodi mulandu wakuba wa bakiri muluzi unatha motani? Nanga lero arikuti ndipo akuchita chani? Lets focus on our dreams plz, akuluwa mutha kuwawona ngati akutimenyera nkhondo lero ife a malawi, koma mudzavomereza kutsogoloku kuti amangofuna kukhonza tsogolo lawo.

    • @wadsondickson5859
      @wadsondickson5859 Před rokem

      zoonad bosd

    • @asilamrazaq4261
      @asilamrazaq4261 Před rokem +6

      olo mutalimbikira kuchitazanu ngati boma nlopondeleza mungapindulepo chani

    • @malawsupet941
      @malawsupet941 Před rokem

      That's true

    • @DoreenKandinga-mw2vj
      @DoreenKandinga-mw2vj Před rokem

      Ndipo zoonad Broo simukunama iyi Ndi campaign chabe tisatanganidwe nazo

    • @abdulrafiquekalembo469
      @abdulrafiquekalembo469 Před rokem +1

      Komanso umbuli umene ndimadana nawo ndi omwe mwanena kuti tizilimbikira pazomwe tikuchita. Mukuyiwala kuti dziko lina lirilonse anthu ake kuti achite bwino limafunika ndi boma kuti lizichita function bwino cholinga kuti anthu asamavutikire kupeza zinthu zimene angamagwiritse ntchito pa zochita zawo.KuMalawi China chirichonse ndi chodula,Ntchito akusowa,Katangare ndi ameneyu akupanga abomayu,mzipatala mankhwala kulibe,Chitukuko chili very slow,.ndiye anthu olo akhale ozilimbikira koma popanda proper system ya boma yowathandizira anthu mukuona kuti anthu angatani??
      Muzichita search maiko ngati Rwanda,Uganda,South Africa,Botswana kumene anthu awo si otuwa ngati ife aMalawi chifukwa government systems imawachita support mu ma areas osiyana osiyana.Anthu sasowa poyambira kuti apange zinthu mwa iwo okha. Koma ku Malawi ntchito kulibe,economy ili very weak,zinthu kudula,katangale, chilungamo mma court chikusowa,anthuwo kuzilimbikira kwake aziyambira pati. Ndinu mbuzi yosaseta ikabhibha.

  • @JamesMalango
    @JamesMalango Před rokem

    Big up, timvenawo zaku Gabon

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Před rokem

    Bomali amalawi anzanga tisayembekezere kumva zokhudza chitukuko kuposa kuba HRDC inapanga.misiteki polimbana ndi boma la DPP pochosa m'boma mudzina loti zinthu sizinkayenda bwino ndikuzatenga amphawi amasikini anthu osaukisisa chakwera ndi gulu lake ndikuwalowesa m'boma lero ndiidzi akungoba ndalama zaboma sono ziserekwete zaanthu ena nkumaombera m"manja .😂🎉😂😂😂

  • @user-tw8td1om8h
    @user-tw8td1om8h Před rokem

    Fufuza iweyo umumange

  • @George-zd5le
    @George-zd5le Před rokem

    Malawi ndi anthu Ake mbuzi zeni zeni

  • @BonfaceMulera-px1jc
    @BonfaceMulera-px1jc Před rokem

    Eish 😕 zoopsa kwambiri, koma Chakwera ndi anzakewa atipha osanama🙆

  • @sungananikapira5963
    @sungananikapira5963 Před 2 měsíci

    He's an engineer. Don't expect an engineer like him to be poor aise. Aaa

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Před rokem

    Or atatuluka sazamsngidwa inu kumangidwa 1hour apasidwa bhel kumangidwa kimeneko

  • @sungananikapira5963
    @sungananikapira5963 Před 2 měsíci

    Awa ndi abodza

  • @masebermsanga7623
    @masebermsanga7623 Před rokem +2

    Big up to respect you always 💯

  • @osmandavie5528
    @osmandavie5528 Před rokem

    Musazapange mistake kupanga trust aliyese ogwira ntchito m'boma komaso andale ngati inu musali m'menemo. Ana asatana onse awa

  • @ElsonMuchokocho-zh6pc

    Why Malawi😢

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg Před měsícem

    Ndpo zoona zake bro

  • @user-fl1wt1ur3q
    @user-fl1wt1ur3q Před rokem

    Choncho dziko lingatukuke? Ku Canaan tikafika??? God have mercy and deal with this criminal gang called mcp

  • @Satier47
    @Satier47 Před rokem

    Koma eshiiii😢

  • @khadijailiyasa5315
    @khadijailiyasa5315 Před rokem

    Zachisoni ziko lathu ndindani azatiombole kumavuto amenewa🥲

  • @bobkenneth2947
    @bobkenneth2947 Před rokem

    Zinthu sizili bwino kuno ku Malawi

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Před rokem

    Eish

  • @madaritsoreis-ip3qr
    @madaritsoreis-ip3qr Před rokem +1

    Ulemu wanu. Km zikuti bwanj? Za ma drone ku Russia airport

    • @user-go4tu1fg5p
      @user-go4tu1fg5p Před rokem

      Naweso ilibize kufusa zamademo aku Russia malo moti ufuse zamadema amene smafuna achitike kumalawi kuno ndiwe galu kwabasi

    • @madaritsoreis-ip3qr
      @madaritsoreis-ip3qr Před rokem

      Zakuno ndidangofika pozizolowera. Palibe chachilendo Kwa ine bro

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Před rokem

    Akulu dziko ili lozatheka pezani Zina zotiwuza.. Mitima imatiwawa

  • @osmandavie5528
    @osmandavie5528 Před rokem

    Mulungu azalanga onse andale nthawi ikubwera tizuzeni momwe mungathele ndi nthawi yanu iyi, misozi ya anthu iyi tsiku lina muzazuzika nayo

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Před rokem

    Big up my brother!!

  • @fefa2050
    @fefa2050 Před rokem +1

    Athu ndi maso bas

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Před rokem

    Chakwela ndi ng'ona yoopsa kwambiri tikapusa amalawi atita pyiti

  • @gabrielmaluwa1038
    @gabrielmaluwa1038 Před rokem

    big up my brother....umayitha... koma amalawi tikugona osaotcha nyumba zao bwanji?

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před rokem

    Kkk

  • @JohnMilo
    @JohnMilo Před rokem

    Chakwela ndi okhumudwitsa kwambili. I can't believe kuti izi akupanga ndi iyeyu. M'buss.
    Komabe tiwuzenkoni za ku Gabon. Akuti asilikali alanda boma?

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev Před rokem

    Ai zao zkuyenda kma kumwamba kulibe sankho akalangidwa

  • @KanyengaMatress-kg4wt

    Malawi okomela anthu ose ameneyo🤣🤣🤣🤣

  • @MussaChitimbe-xq2dm
    @MussaChitimbe-xq2dm Před rokem

    Nthawi yao aziba

  • @user-dt8nr1zx6e
    @user-dt8nr1zx6e Před rokem

    ❤❤❤

  • @imanidennis6806
    @imanidennis6806 Před rokem

    Zomvesa chisoni ndipo
    ndi zowawa ndithu

  • @lawrenceblacktealyson8015

    Tikonze rand to kwacha ili pa 96

  • @user-go4tu1fg5p
    @user-go4tu1fg5p Před rokem

    Timfomeleze basi kuti amalawi ndife zisiru

  • @gracetjomane-jj3ib
    @gracetjomane-jj3ib Před rokem

    ❤❤❤❤🎉

  • @daudmasikam
    @daudmasikam Před rokem

    Chipan chikutilamulilachi chatayimusi billion katangale chichoke chitiphatose

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Před rokem

    Koma amalawi tavutika ndipo tidakali kukhala akapolo mumaiko a eni

  • @user-zj2dr2rp1e
    @user-zj2dr2rp1e Před rokem

    Boma ili latitopesta ndi zochita zake, akuchoka posachedwapa.

  • @husseinmoffatt
    @husseinmoffatt Před rokem

    Guys chitsiluichichitizuza m bomaumu mwachuluka umbava kobas zamanyizokhazokha zikuchitika m bomaumu

  • @madaritsoreis-ip3qr
    @madaritsoreis-ip3qr Před rokem

    Nanga ku Gabon zikut bwanji?

  • @user-nx8gy8lq4q
    @user-nx8gy8lq4q Před rokem

    Poor governance

  • @KingsleyWakusa
    @KingsleyWakusa Před rokem

    Tchana

  • @giftmasenti5732
    @giftmasenti5732 Před rokem

    Amalawi ndi atulo azitibera choncho

  • @tingo3155
    @tingo3155 Před rokem

    Mbamva

  • @user-vb5dh8ip6g
    @user-vb5dh8ip6g Před rokem

    Malawi army Kodi Nanu mwagoma chonchi zoti armies other countries their are took over you don't hear or c on social media
    You are busy with charcoal to the poor Malawians who are trying to earn a living
    Shame on guys arm😢😢😢😢😢😢

  • @laddinshaibu6932
    @laddinshaibu6932 Před rokem

    Tilipama Vito akhulu