Video není dostupné.
Omlouváme se.
tsikana wina wabeleka khanda la galu ndipo khandalo lasanduka ntengo
Komentáře • 81
Další v pořadí
Automatické přehrávání
phuzitsi wina wa school yosula aphuzitsi wapeza nkazi emwenso ndi phuzitsi akupanga zadama.Balanço semanal CK & Govate
zhlédnutí 80K
wina waphedwa chifukwa cha pakamwa pake, kuyankhula kwambiri akamwa mowa.Balanço semanal CK & Govate
zhlédnutí 30K
ZODABWITSA MNYAMATA WINA YEMWE ANAMWALIRA WADZUKASO NDIPO AKULONGOSOLA ZONSE KU MALAWI BOMA LA ZOMBAGrant Bandah
zhlédnutí 26K
Sigma Girl Past #funny #sigma #memesCRAZY GREAPA
zhlédnutí 37M
I CAN'T BELIEVE THIS HAPPENED!!!Zhong
zhlédnutí 37M
Megaluxus PŘÍRODNÍ ŘÍZEK 🍺 #ostravskygastrošef #heřmangazdaOstravsky Gastrošef (Heřman Gazda)
zhlédnutí 128K
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔Jimmy
zhlédnutí 110K
A Commedy by Chindime and Phungwaku on prohibition of selling of vacant LandMinistry of Lands, Malawi
zhlédnutí 7K
bambo a mwana omwalila kudandaula pakuona mwanayo ali ndi moyo mu bokosi logulidwa ku dedza malawi.Balanço semanal CK & Govate
zhlédnutí 152K
Banja lina lapha mwana wake pofuna kulemera ndipo amuchotsa dziwalo ku MakwangwalaBalanço semanal CK & Govate
zhlédnutí 17K
ZAMALOVE Episode 25 FINALEMibawa Studios
zhlédnutí 36K
Tsatane Tsatane wa Nkhani ya Anthu Amene Akanilirana kwa WilisoniBalanço semanal CK & Govate
zhlédnutí 138K
Anthu awiri aphedwe powaganizira kuti anapha munthu wina wa kwansonga ku madzoziBalanço semanal CK & Govate
zhlédnutí 18K
ZAMANYAZI COMMUNITY POLICE KUBA CHIMANGA MOGWIRIZANA NDI T/A BVUMBWE AGWIDWA..KANGAUDE PA MIBAWA TV.LIKI-LIKI TELEVISION
zhlédnutí 20K
Tsikana wina akuganizilidwa kuti wapha mwana wa nzake obadwa kumene motumidwa ndi amponda matiki enaBalanço semanal CK & Govate
zhlédnutí 29K
STEP CHALLENGE🦶Celine & Michiel
zhlédnutí 3M
Comfortable 🤣 #comedy #funnyMicky Makeover
zhlédnutí 15M
How I Did The SELF BENDING Spoon 😱🥄 #shortsWian
zhlédnutí 22M
Udělal jsem si HWACHAE (špatnej nápad)MaTTem
zhlédnutí 115K
艾莎撒娇得到王子的原谅#艾莎在逃的公主
zhlédnutí 28M
VOLO VIA dallo staggio (elemento PROIBITO)😂🚀Sophialand
zhlédnutí 18M
SPILLED CHOCKY MILK PRANK ON BROTHER 😂 #shortsSavage Vlogs
zhlédnutí 41M
Box jumping challenge, who stepped on the trap? #FunnyFamily #PartyGamesFamily Games Media
zhlédnutí 28M
Ndiye Tsangano Imeneyo, Zikomo kwambili tikudziwa zithu zakumudzi mwasanga kudzela kwa inu Balanço Semanal. From Maputo
Zikomo tikuziwa nawo mmene moyo wa abale athu okuyendera madera ena pa dziko pano one love from malawi
Koma dela ili mumachitika ma story ambiri. Koma good job guys. Love here in MALAWI
thanks
Zokumva zimapweteketsa mutu , program iyi ili boh, tikumanva ndikuona mmene zikukhalira , here Durban love you guys pitilizani
Keep up the good work proud of you guys,mmatidziwitsa zambiri watching you here from South Africa Durban.
Very sad
A sing’anga Amati amachokera ku Mozambique aja mwati samachokera ku dera limeneli?
Keep it up good work I like this channel
This Chanel is working .thanks
Zochitika mmasiku otsiriza, love this channel
Koma mayi amenewo saanabe malo ena ake ?komanso kumeneko kwa angonia nkutheka kuti aanthu aufiti akupanga izi pofuna kutchuka komaso kuyesa matsenga kuti aone kuti zikutheka.Nkhani Ina aanthu akumeneko bwanji sakutchuka ndi ulaliki? nkuti aanthu akumeneko sakonda kupemphera chifukwa izi zikuchulukira kwambiri.May almighty God show powerful below this
Keep it up guys.... watching from Durban
Ineso poganiza pa ine ndikuona ngati ndi mkazi nzakeyo olo amacheza ndi pamaso zamumtima ndi za wenkha eyetu
pepani
Life yaku Mudzi ndiyovuta eeesh
Zovetsa chisoni . Koma akuyenera apite ku chipatala kuti akawapange check . I love your Chanel. From 🇲🇼
Very very sad news
Mmmm dzikoli ndithu langotsala pakaphindi chabe mwini wake akubwela atenge ake oyera m'tima
Kwa Angonia ni koipa , kuli nfiti olo atafuna ukussandutsa Ka mbalame ni mpompo , hmmmmm
& tikuthokoza channel iy ikumatiziwisa zambri
iiii mulungu amusungolele nsikanai 🙏Kuno ku guruwe Zambézia ine dakumudwa Izi zamasiku osiliza 🙏chomfunika tilimbike kumpepera usiku ndiusana🙏
Muzimayiyo wataya mwana kapena analibe mimba amanama
Keep up the good work guys informing us what's going on there
Mmm mulungu sizoti wangokhala chete ayi
Vuto lokhala ndi akazi 2 azibambo
Ine Friday kuno ku South Africa a Malawi chepesan uthakati schupit
Koma kuli anthu omudziwa mulungu ukuuuu kumango chitika zinthu zopanda umunthu ukuuuuu
OMG 😳 what plz anthun mudziweni yesu komazoona nkumuika nzanu chinthu Ngati in cho mmimba .Koma Choti mudziwe mfiti yozafaso
Keep it up
malodza nkhani yovetsa chison ambuye alowerelepo kuti zoyipazi zisamachitike
Dziko lafikapo ambuye bweraniiii
Pepani mai wanga mulungu akudziwa zonse imani Pamanso ake komanso ndimayamika kwa inu amene mumatipatsira nkhani zonse ambuye azikudalitsani nthawi zonse
zikomo
Zosakhala bwino
Zosakhala bo
😂😂😂
zomvetsa chisoni mutengeleni ku chpatala please..komanso upeze wako mamuna mitala ndi umfiti...
Eeee😱 koma dziko abale anthu saopa kumwamba hmm ayi Ambuye aweruzepo ndithu.
Sim boca ,essas mulheres
No good
Mmmmhhh pitani naye kuchipatala please before is too late
Mmhhh koma zoopsya
Eshiiiii but govati u're trying the best really appreciate u
Zoona zake ufiti ulipo
Ayi ndithu zoopsya kwambiri.Malodza saposa apa.
Munthuyu anachira bwinobwino koma mwanayo amafunika kukangaroo coz of kuchepa weight koma poti mkumudzi asowetsa mwanayo nkulenga nkhani yoti wachira mtengo nde poti mumakhulupirira changu mwavomereza mukafufuza mkhaniyo muzingonva kuti aliyense ananva
Kulakwirana uku 😭😭 munthu kutenga mimba nukachira mtengo Mmmh shame
zochttsa matha
Maloza awa eish
Nkuthekaso kuti mwina zikuchokera pakhomo pompo komaso mwina ndinkazi nzakeyo amangomukonda pamaso koma muntima sasangala naye awo anali maganizo anga chabe
zoona
Mmm kom zoopsa apite kuchipatala kma mmm
Kulakwatu uku
Apite kuchipatala akamuone mmimbamo
Very sad.matsiku osiliza
Mmm this is very sad eish
Is this moshiko?, mumakwana guys
Koma ndiye
Mmm koma abale kkkkkkk koma zoopsya
Eeeeeeeeish koma anthu mmmm
mmm zovuta zoopsya
Nde mwati mtsikana osati mzimayi
Dzaka 17
Ufiti
Eish 🤔
Kusatira mwachete chete
zilibwino malume
Koma !!!
Thawizina mitalayiso siyabhoo.
zoona zeni zeni
Mmmm soo sad.
Mmmmmm km ufiti uliko mmmmm
yaaa
Komatu anthu amuziwe yesu Mmmm ayenjeza
Uuuuuuhhhh very sad may God bless her life in the name of Jesus Christ.
Angónia assusta hiii
Mm zosakhala bwino mmmm
Mmmm zoopsa ndithu koma apite kuchipatala akamuone mzimayi ameneyi
A sing’anga Amati amachokera ku Mozambique aja mwati samachokera ku dera limeneli?
Zosakhala bwino
Very sad