Tsikana wina akuganizilidwa kuti wapha mwana wa nzake obadwa kumene motumidwa ndi amponda matiki ena

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024

Komentáře • 52

  • @Greatness664
    @Greatness664 Před 2 lety +3

    These people can feel more at home in Malawi than Mozambique 😂

  • @jfj-bu5wz
    @jfj-bu5wz Před 22 dny +1

    Iwe wakamela sk ukuti chani pakamela kamelamani amafusasokodi😅

  • @michaelsportslossi9337
    @michaelsportslossi9337 Před 2 lety +4

    Ndithokoze mamuna poyankha moopa Mulungu kuti kulanga mkwamwini namalenga Mulungu.komaso mwana sanama chifukwa sanadziwe tchimo ndipo ndiye wapha mtsikanayo komaso nkutheka kuti watumidwa ndi aanthu ena moti akhale tcheru ndi mtumbirawo ngati sufukulidwa.

    • @lovebinta6863
      @lovebinta6863 Před 2 lety

      Ambuye akudalitsen abambo inu tisaname munamulandilad Ambuye kukhala mpulumutsi wamoyo wanu

  • @andersonmaster8055
    @andersonmaster8055 Před rokem +2

    Very sad story amayenera kuwotchedwa basi

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Před 2 lety +4

    Thanks I'm with you balasco semanaro

  • @lydiaamos4214
    @lydiaamos4214 Před 2 lety +3

    Azimayi Pena tizikhala serious ndi ubereki, inu zoona munthu wakusiyani Panja kulowa mnyumba inu osamusatira? Mwa njira Ina pepan kwabasi Mulungu ndamene akudziwa zonse

    • @estherdumbo
      @estherdumbo Před rokem

      Ndipo inu mmmm munthu wakudutsa osakiyakhula iwe nde pheeee osamulondola eti......... Mwina anamupha mtima make mwanayo

    • @estherdumbo
      @estherdumbo Před rokem

      Amen adad amwana Mulungu abwezera ndipo choonadi chidzadziwikaaa pangatalike pangafupike.

  • @user-vv4qk5oh4p
    @user-vv4qk5oh4p Před rokem +1

    😊

  • @dynajohn4032
    @dynajohn4032 Před 2 lety +2

    Zosayenda mm Ndimakonda kunvere zomwe matipatsira

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 Před 2 lety +2

    Timakunyadirani a Balanco semanal potidziwitsa zomwe zikuchitika

  • @carlosadelinoamor3189
    @carlosadelinoamor3189 Před 2 lety +2

    Nkhani yovetsa chisoni

  • @cristinaviagemcaundane960

    Notícias muito triste, k culpa tema criança, ela deve responder na barra da justiça

  • @user-cm4jw7hy6s
    @user-cm4jw7hy6s Před rokem +1

    Aaaaa nakubalayu chisamaliro analibe ,😭😭

    • @ellahkapuma7908
      @ellahkapuma7908 Před rokem

      Imagine mwana obwera kumene kumusiya mpaka 1hr yekha opanda munthu kulowa munthu iye olo kusatila nakubala ali very careless😢

  • @user-ng2nu6xn9x
    @user-ng2nu6xn9x Před rokem

    Koma Umboniwu mmmm penanso zitha kutheka mwina nso mwana sadaphe ndiyeyo

  • @estherdumbo
    @estherdumbo Před rokem +1

    Koma dzikoli ladikapoooo iiiii

  • @pinkeygmw8956
    @pinkeygmw8956 Před 4 měsíci +1

    Osamatchyula dzina plz

  • @josuahkachali1489
    @josuahkachali1489 Před 2 lety +1

    So sad watching live from Kuwait

  • @princeani1752
    @princeani1752 Před rokem +1

    Zosakhala bwno bwanj

  • @anamariaxadreque5377
    @anamariaxadreque5377 Před 2 lety +1

    Triste notícia 😢 💔💔

  • @franciscachapoteraelias8083

    Isso é muito triste .

  • @edwinweyers1928
    @edwinweyers1928 Před rokem +1

    Ambuye amutsowetse mtendele komwe aliko mpaka atabwela yekha chifukwa wapha mwana osaziwa tchimo

  • @mavuschitseko7757
    @mavuschitseko7757 Před 2 lety +1

    Sad story, 😭

  • @zaithwachiwaya
    @zaithwachiwaya Před 2 lety +1

    Komaso Mai wamwayu sanali serious ndi mwanayo.Aaaa kom abale Inu😭

    • @joshuamtenje1900
      @joshuamtenje1900 Před 2 lety

      Eti munthu kulowa mnyumba 12 o'clock iwo kulowamo mma 3 aaàaa

  • @promise3693
    @promise3693 Před 2 lety +1

    Mmmmh Shame on her😭😭😭

  • @bonifaciosimao8620
    @bonifaciosimao8620 Před 2 lety +1

    Isso é muito triste e sentimental 🥲

  • @saukophiri4535
    @saukophiri4535 Před 2 lety +1

    This is very sad 😔

  • @lucysimbani3971
    @lucysimbani3971 Před 2 lety +1

    Mmmmm walakwitsa kwambili

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 Před 2 lety +1

    Koma amayi awa nawo ndiwotani iwowa anangomusiya Staples muthu yotisamacheza naye

  • @victorbanda7546
    @victorbanda7546 Před rokem +1

    Kodi ku chipatala anapita naye mwanayo kuti akamupime kuti chamumpha ndi chani? chifukwa achipatala akadanena ndithu chomwe champha mwan

    • @marianyirenda
      @marianyirenda Před rokem

      Zoona akanapitadi ku Chipatala kuti akaone chomwe chapha mwana kuti ndi chani koma vuto la anthu akewa umbuli ndi wambiri kwabasi za sukulu mitu yawo wonse mulibe

  • @josephineringstone7489
    @josephineringstone7489 Před 2 lety +1

    Mukuitha mabwana

  • @edwardedwards3577
    @edwardedwards3577 Před 2 lety +1

    Sorry ku banja lonse lofedwa

  • @vincentmathews9143
    @vincentmathews9143 Před 2 lety +1

    Zovuta izi iiiii zosamvetsetseka ayiii

  • @lamackbanda6869
    @lamackbanda6869 Před 2 lety +1

    No sound guys

  • @simangodickson1794
    @simangodickson1794 Před 2 lety +1

    Chilungamo chizamutsata ,

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 Před 2 lety

    Nkhani zoyipa ngati zimenezi zikumveka ndipo zikuchitika tsiku ndi tsiku.

  • @vincentmathews9143
    @vincentmathews9143 Před 2 lety +1

    Km ndizowawa kwambili ndisaname zandiwawa

  • @frankmaluwa5120
    @frankmaluwa5120 Před 2 lety

    Tathokodza Balanco semanayo mumagwira ntchito yotamandika kwambiri pitilidzani kutero

  • @rosebonongwe8994
    @rosebonongwe8994 Před 2 lety +1

    Abale talongosolani bwino

  • @justinjason7262
    @justinjason7262 Před 2 lety +1

    Sound pls sir

  • @confidencebanda109
    @confidencebanda109 Před 2 lety +1

    Zoopsa 🤭🤭🤭

  • @lamackbanda6869
    @lamackbanda6869 Před 2 lety +1

    Sizikumveka guys