AMENYEDWA NDI MBAMA YACHIKWANJE KUMALO OBISIKA ndipo zadzetsa ulumari kumaloko.

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 6. 05. 2024

Komentáře • 226

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 Před 2 měsíci +20

    Mwenye ameneyo azkpita kwawo ndiwankhaza..kukanakha kuno ku South Africa akadapanga zonthekela kuti amuyimbe mlandu..koma Malawi mmmmm sadzantheka..amasamgalala ndikuti Malawi nzawo adzivutka....zomvetsa chisoni😢😢

    • @ChilpaKamcholoti
      @ChilpaKamcholoti Před 2 měsíci +2

      Vuto ndi apolice sanagwire ntchito yawo mwadongosolo ngati anthu oti anaphunzila ntchito yawo bwino bwino.

    • @juliusnjerengo2610
      @juliusnjerengo2610 Před 2 měsíci +1

      Vuto si a police ayi, vuto ndi malamulo a dziko lathu. Zikanakhala kuti kuli malamulo kwathu kuno, kuyambira galu akumuti bwanayo ndi a police onse anapanga zimenezo bwezi pano atamangidwa onse.

    • @OwenJambo
      @OwenJambo Před 2 měsíci +2

      @@ChilpaKamcholotimbuzi zap0lice kupha mbalewanga chifukwa cha mwenye that's bullshert

    • @doralinyenga9195
      @doralinyenga9195 Před 2 měsíci +1

      Ndipo apolice akuno amadana ndi anthu oyela khunguwa sangapange zimenezi kwa munthu wakuno nzawo

    • @user-og4oe5yp4w
      @user-og4oe5yp4w Před 2 měsíci +2

      Amangidwe ameneyo

  • @mlfmalawi4393
    @mlfmalawi4393 Před 2 měsíci +8

    Let lawyer's fight for this man's justice, the foreigner and police men need to answer to the LAW. This is not acceptable, #Chakwera do something urgently. Owners of the land are suffering at the cruelty of foreigner's

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před 2 měsíci +5

    Akulankhula momvetsa chisoni kmso chilungamo chokhachokha ambuye a lowelerepo mmmmm😢😢😢

  • @DanielJuly-dj2ji
    @DanielJuly-dj2ji Před 2 měsíci +2

    Mayi walankhula chilungamo. Komanso banja iri Ambuye alikhudze mwapaderadera 😢🙏

  • @marychilima1661
    @marychilima1661 Před 2 měsíci +2

    Exodus 14 vs 14 igwira ntchito pa moyo wanu mulungu akumenyelani khondo

  • @giftchale672
    @giftchale672 Před 2 měsíci +7

    Malawians please let's help our fellow brother

  • @StelliaSangaya
    @StelliaSangaya Před 2 měsíci +4

    Police ikupanga chinyengo yasiya kuona chilungamo chankhan ikufuna ndalama mbili yonyasa imeneyo

  • @user-qu9iu7hs8k
    @user-qu9iu7hs8k Před 2 měsíci +3

    Ntolankhan ari bho kwambiri amafusa ma professional 😊

  • @janetchinga695
    @janetchinga695 Před 2 měsíci +1

    Tikuthokoza maloya ozipeleka woo mulungu asogolele zonse ❤❤

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před 2 měsíci +4

    Ulamuliro wa MCP muli nkhanza

  • @BlessingsJames-yp6on
    @BlessingsJames-yp6on Před 2 měsíci +3

    Amalawi please kaocheni company imeneyo basi thats too much 😢😢

  • @user-zy1br2fy6v
    @user-zy1br2fy6v Před 2 měsíci +2

    Ku Malawi kuno kulibe apolisi
    A Malawi okhaokha kumazunzana chinchi
    Lord have Mercy on us

  • @janetchinga695
    @janetchinga695 Před 2 měsíci +1

    Apolice njala ngaphe munthu wakwanu chifukwa cha mwenye kupusa police ziwani kuti mwenye simubale wanu ndichifukwa chake mumafa udyo muzi ntchito mulozedwa Apolice

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie Před 2 měsíci +15

    Anthu wosauka ku malawi alibe ufulu mmmm

  • @user-gx7dq1bd2f
    @user-gx7dq1bd2f Před 2 měsíci +1

    Mulungu ndiwoo khulupilika pemphelani machilitso ndikumbwezeletsa kwathupi olo mulungu apange upalechoni wakumwamba chachikulu tikupemphela moyo ambuye akukhuzeñi ambuye alimbaliyanu

  • @DanielJuly-dj2ji
    @DanielJuly-dj2ji Před 2 měsíci

    May God almighty bless Abel Zulanga. Mafunso akuya komanso kulondoloza nkhani mwachidwi.

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e Před 2 měsíci +1

    Pepeni kwambiri Mr Felix ,Ambuye akukhuzeni ndi dzanja la machilitso....

  • @user-sz9uu2dm1o
    @user-sz9uu2dm1o Před 2 měsíci +4

    Amabungwe Ntchito yanu imeneyo

  • @officemoyenda-rj2hz
    @officemoyenda-rj2hz Před 2 měsíci +3

    I wish Bushiri could come in and assist this family for daily nsima so that the wife should not run away from this man

  • @user-ln5hn5kj8i
    @user-ln5hn5kj8i Před 2 měsíci +3

    Iphani apolice onse apanga izi zimene zikuchitikazi sizabwino abwanaonso panga nawon zinthu

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy Před 2 měsíci +1

    Ambuye alowerere ..why police nkhaza izi mukuzitenga Kuti dziko lathu la ufulu ..Koma mudzayankha

  • @JosephChitseko-ro9fv
    @JosephChitseko-ro9fv Před 2 měsíci +1

    Good work Abero❤❤❤❤

  • @enocknkhata1001
    @enocknkhata1001 Před 2 měsíci +2

    Chonde if someone can help get justice for this man, wenela police imatchuka ndi nkhani za nkhaza....

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 Před 2 měsíci +1

    plesident akutipo chani azipita amwenye wa kwawo

  • @user-zl3ne5kv5t
    @user-zl3ne5kv5t Před 2 měsíci +2

    Muthune ndikumalota ndili ku school pafupifupi tsiku lilonse Koma school ndinasiya 2019 nditalemba mayeso a4 anthu amati za school ndimadziganizira kwambiri komano sidziri choncho ndani Muthu angandimasulire maloto amenewa.

    • @marychilima1661
      @marychilima1661 Před 2 měsíci

      Spirit of demotion
      Just pray and fasting to rebuke that Spirit.
      Mapephero muli mphamvu khulupirani mutsutsane nawo mzimu obwerela zithu mbuyo

  • @chiputulaerik-nx4hn
    @chiputulaerik-nx4hn Před 2 měsíci +1

    Nthawi imakwana yomwe Mulungu amaonetsa mphavu zake ndipo zoti ndiwe wa Police sizioneka.

  • @MzatiMkolongo
    @MzatiMkolongo Před 2 měsíci

    Osauka alibe mawu 😢 ,ambuye odziwa kukhuza awakhuze Mr kachingwe

  • @yamikanifischer
    @yamikanifischer Před 2 měsíci +5

    Anthu kumeneko gwilanani manja kukaotcha shop ya mwenyeyo

  • @user-tm9ro2sm6n
    @user-tm9ro2sm6n Před 2 měsíci +1

    Ndipo mulandu uwu usaime pa njira ukambidwe ndithu ndiponso m'mwenye ameneyo anyongedwe ndithu
    sizoona katundu wake alipo okwana ndikumateronso hmmm ayi

  • @patisonlufan2823
    @patisonlufan2823 Před 2 měsíci +2

    Amwenye ndi akhaza kwambiri

  • @davismwale8602
    @davismwale8602 Před 2 měsíci +1

    Some of our police oficers are wicked..... Very unfortunate. I wonder the school they attend

  • @GiftMunyonga-ko9dz
    @GiftMunyonga-ko9dz Před měsícem

    Nanga ungasume kuti mathero ndi boma 💔🙌

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 2 měsíci +1

    Mmmm abale inu wosauka alibe mau, ndlama inamuphadi yesu, apolis akumalawi kufuna kupha malawi nzanu chifukwa chosusukira ndlama? Manyazi akugwireni ndithu ntchito yanu simukuyikwanitsa ndipo Mulungu akulangeni pamodzi ndi m'mwenye wanuyo bola zikanakhala kuti zinthu zo zabedwadi panali pombveka
    Mulungu akufungatireni bambo inu pamene mukumbva zowawazi muthawi imeneyi, Koma boma limene tili nalo panoli nde ayitu yohhh

  • @user-rg9zc6eo2q
    @user-rg9zc6eo2q Před 2 měsíci +1

    Mwenye ameneyo aphedweso bas

  • @marychiwowa1759
    @marychiwowa1759 Před měsícem

    Kangaude plz help him to get his justice

  • @user-ek3tm3su3g
    @user-ek3tm3su3g Před 2 měsíci

    Nayeso aphedwe mwenye ameneyo ukuku ndikuphatu kudachitikaku malawi mmmm

  • @user-wm7vl4wp8v
    @user-wm7vl4wp8v Před 2 měsíci

    It's bad that these kind of things are too much in Malawi since it's not new issue. Ambli akulavulazidwa kwambli nd apolis I think many they are not knowing their role

  • @hopemasango1260
    @hopemasango1260 Před 2 měsíci

    Apolisi aku Malawi kuno atha kukupha eeee🙌🙌. Ku LL kuno kuli apolisi aku area 3 eeeee🙌🙌🙌

  • @user-dn6ts5xe2j
    @user-dn6ts5xe2j Před 2 měsíci

    This has moved me into tears 😭😭

  • @AkilenMussa
    @AkilenMussa Před 2 měsíci

    Mwenye ameneyo ndiwankhaza choncho shop chamwenyecho chikuyenera kuwochedwa , Allah akale nawo koma nkaz yo ndi fiti ameneyo kwambir komaso ndi hule kumukana mwamuna wake chifukwa choti mwamunayo wafulala tipatsen njira yoti titha kuthandizila m,bale wathuyu kochepa kamene tingakwanitse bon kalindo alowe pasewo please president was amphawi mwenje ameneyo azowe

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Před 2 měsíci

    Ndipo kwerekwere mwenye ameneyo achoke kwathu kumalawi

  • @user-ml3ly8hh8y
    @user-ml3ly8hh8y Před měsícem

    Anthu akuyenela kuthandizidwa ma lawyer alowelelepo apapa munthuyu munamuvulaza kwambiri chipepeso chikufunika Cha nyoo

  • @user-bw3qu2yt6n
    @user-bw3qu2yt6n Před 2 měsíci

    Justice should take it's course.. plz legal aid ntchito iyooo

  • @TadaDuncan
    @TadaDuncan Před 2 měsíci +4

    Osauka alibe mau

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 2 měsíci

    Amwetu ndi athu akhaza kwambili amachoka kwaoko alibe kalikose amalemelela dziko lathu komaso ndikumatizuza Chocho mmm

  • @esteryndau8546
    @esteryndau8546 Před 2 měsíci +1

    Kukanakhala kuno ku south africa akapha mu mwenyeyo

  • @innocentsathasteven4093
    @innocentsathasteven4093 Před 2 měsíci

    zovetsa chisoni kwambiri...Police anthu sibwino kuthamangira kumumenya munthu pa ntchito yanu...aboma chilungamo chionekepo apa dyera a Police ndi ndalama tikamakupangani chipongwe midzimu mudzitiona ngati adani anu...siose apolice magwira ntchito mwachilungamo

  • @user-kv4cs1ot3x
    @user-kv4cs1ot3x Před 2 měsíci

    Nkhani yomvesa chisoni kwambili mulungu awayanganile Mr kachingwe pa mvuto lawagwela komaso a police onse ankhuzidwa pa nkhani iyi ntchito yawo inthe alandileso zilango

  • @BethsiderTavares-ug4sv
    @BethsiderTavares-ug4sv Před 2 měsíci

    This is a very bad situation and their Asian bossis using the abuse of his power and it's a felony charges against this poor innocent man
    May the Lord heal him and have mercy on his soul.

  • @RashidiJala
    @RashidiJala Před 2 měsíci +1

    Malawi wachakwela anthu akuvutika😢😢😢

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w Před 2 měsíci +1

    Always is Blantyre why? We're tired of this please try other places gha

  • @lulumchizi121
    @lulumchizi121 Před 2 měsíci +1

    A police kukonda ndalama. Apapa Popat amutsegulire mulandu. Amwenye amazunza antchito kwambiri. This man has to be compensated. 32:38

  • @StiveMatias-yp4zu
    @StiveMatias-yp4zu Před 2 měsíci

    😢Mvuto apolisi aku Malawi ku konda ndalama kupotsa moyo wa munthu!! @meyo adzipita kwawo

  • @mercychinji3417
    @mercychinji3417 Před 2 měsíci

    This is sad...chilungamo chiyende ngati madzi

  • @user-bq1mb4fk1b
    @user-bq1mb4fk1b Před měsícem

    Mmmmmm kma gyz eshiii zamasiku itsilidza

  • @user-ch3eq9yx5w
    @user-ch3eq9yx5w Před měsícem

    This is sad😢 Amwenye nd anthu opoila 😞😤

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Před 2 měsíci +1

    Amalawi okha okha kuphana cz chaminthu obwera ai zikomo ndithu

  • @dicksonmwale8617
    @dicksonmwale8617 Před 2 měsíci

    Mbale wanga pepa koposa,zikoli silibwino.Boma liyenera lilipire

  • @user-ce6hy6tp7e
    @user-ce6hy6tp7e Před 2 měsíci

    Km abale zamasiku omaliza sizoona kumupanga munthu choncho mpaka kumuwononga munthu kumoyo zosakhara bwno ndpo inuyo apolice mulungu akukanthen inuyo musadzafe mulungu akuoneni poika kuvulaza Mala
    WI nzanu inuyo muli ndi nsambi

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft Před 2 měsíci +1

    Mayi inu musadandaule za mnyumba kuti muzitani kuchipinda dandaulani zamoyo wa amunanu lungalunga nkubadwa mayi

    • @NedsonBilly
      @NedsonBilly Před 2 měsíci +1

      No sister amaiwa akuyankha funso momwe awapatsira not kut iwoo akuzifuna zakuchipindazo

    • @VictoriaWilliam-ms2ft
      @VictoriaWilliam-ms2ft Před 2 měsíci +1

      @@NedsonBilly owoooo ndimaona ngatitu chabwino ndakumvani ndithu brother

  • @EreneoMchenga-ly5vq
    @EreneoMchenga-ly5vq Před 2 měsíci

    lawyer apapa agwire ntchto mwachilungamo mmwenye uyuyu adzipita kwawo

  • @user-nn9bg3ve3g
    @user-nn9bg3ve3g Před 2 měsíci

    Madhara wa amakhalaso ghetto yopoyira bwezi titakawontcha kampaniyo ndikapolice komweko tsiku lomwelo anthu wopusa kwambiri 😹 😂😂

  • @symonmajir9470
    @symonmajir9470 Před 2 měsíci

    please tiyeni amalawi tikondane tokha tokha munthuyu ndi osalakwa nanu a polisi mmmm ayi musamatelo please

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson Před 2 měsíci

    Koma police yathu ya Malawi simukukhoza choncho sibwino tosefe ndife athu.ndikupepha mulungu wakumwamba alowerelepo mbali zose ziwili.inu a police officer munagwira tchitoyi yakumuvulaza muthuyu ambuye akudaritseni 😂

  • @user-cw5pl1hq5f
    @user-cw5pl1hq5f Před 2 měsíci

    😢😢eish koma zomvesa chisoni

  • @marianamwanje8968
    @marianamwanje8968 Před 2 měsíci

    Anthu amenewa ndankhaza koopsa vuto amasekeleledwa ineyo ndiye nsaname ifeyo ndopusa kwambiri amwenye wo apolice wo ayankhe, justice should be saved, kukonda ndalama apolicewa

  • @user-nb7dp6pr9n
    @user-nb7dp6pr9n Před 2 měsíci

    Kumuononga m'Malawi mzathu chonchi a Police ndinu zitsiru kamba ka ndalama🥸

  • @JustinLigomeka
    @JustinLigomeka Před 2 měsíci

    Koma a Malawi tokhatokha tizizunzana chonchi? we are very vulnerable ku Malawi kuno mmmm Ambuye atithandize

  • @user-nm7mv3wr1s
    @user-nm7mv3wr1s Před 2 měsíci

    Amabungwe loweleranipo apa sizoona izi chilungamo chiyende apa

  • @mariamwandwanga3035
    @mariamwandwanga3035 Před 2 měsíci

    Amabungwe athandizeni anthuwa ndithu ali mu ululu oopsa ndithu

  • @user-lx8ow6ek6k
    @user-lx8ow6ek6k Před 2 měsíci

    Amalaw mmmm kukonda ndalama ngat salandila salary

  • @user-jp9sw8sl7p
    @user-jp9sw8sl7p Před 2 měsíci

    Poor policing. Machende amayake mmwenyeyo ndiapolisi. Chakwera mboliyamake

  • @DoriccahPhiri
    @DoriccahPhiri Před 2 měsíci

    Iih ndanva chisoni 😭😭😭

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Před 2 měsíci

    Futi si yoopya pofuna, chilungamo,apa pali njila ziwili,amalawi,tiime kuthetsa, nkhani iyi.apolice,akayankhe,komaso,mwenyeyo atseke company yacheyo.waputa,kudabwe.

  • @Mrskasambala-nc4ux
    @Mrskasambala-nc4ux Před měsícem

    Very bad mulungu awakanthe onse atengapo mbalipa nkhaza iyi

  • @yanoh-hk5fe
    @yanoh-hk5fe Před 2 měsíci

    a mabungwe please lowelelanipo po thandiza felix kut mwenye ameneyu amuliupile ndithu ndipo ndalamazisakhale zochepa chifukwa uku ndye ndikuphana komaso a police wo alanbdiole zilango

  • @RobertGoliat-gt2qh
    @RobertGoliat-gt2qh Před 2 měsíci

    Mbudzi za apolice akumalawi pansi pa achakwera kudzunzana okhaokha nkhani ya anthu obwera eeshhh chilungamo chiyende ndithu

  • @makomberodgers3791
    @makomberodgers3791 Před 2 měsíci

    😢😢😢 dziko lanthu lomwe kumazuzika

  • @PatriciaFast-gf7fc
    @PatriciaFast-gf7fc Před 2 měsíci

    Km apolice aku malawi mukuwonjeza kukonda ndalama ,bwanji kd sizabwinitu izi akhala bwanji muthu pa ziko lapasi mutamunga khaza conci

  • @ConnexMakande
    @ConnexMakande Před měsícem

    Kumalaw kulibe mtendere tikuphana chifukwa cha ndalama

  • @CikumbutsoCitokire
    @CikumbutsoCitokire Před 2 měsíci

    Umphawi sizinthu abale munthu walumala okula Kula abale 😢😢

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 Před 2 měsíci

    😢😢😢 zachisoni kwambiri

  • @user-dx1ic4ij1v
    @user-dx1ic4ij1v Před 2 měsíci

    Police yanji yokomedwa ndalama choncho 😔😔

  • @user-rg6hn7mt6w
    @user-rg6hn7mt6w Před 2 měsíci

    Eshiiiii 😢😢😢

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 Před 2 měsíci

    A police amaikilana kumbuyo ipangeni follow up nkhaniyi please munthu wamwamuna nkumusi ndikutha kuona ululu omwe akudutsamo bambo athuwa

  • @kennedymakhula1203
    @kennedymakhula1203 Před 2 měsíci

    People are wicked, ntha kuwalodza ine apolisi amenewo

  • @user-kk1pi7ng8u
    @user-kk1pi7ng8u Před 2 měsíci

    Abuye alowelelepo

  • @lillahnmahuzahshabah5883
    @lillahnmahuzahshabah5883 Před 2 měsíci

    Awalakwira abambo abale ,a police akhaza amenewo

  • @CostanceChibwato
    @CostanceChibwato Před 2 měsíci

    Ammmmm too bad😭😭😭😭

  • @lillianmwanza4218
    @lillianmwanza4218 Před 2 měsíci

    #timothy mtambo ...mmwenye uyu nde ofunika mademo ajA

  • @shepherdmaseko3561
    @shepherdmaseko3561 Před 2 měsíci

    Uyutu ayiphula

  • @PreciousChipolopolo
    @PreciousChipolopolo Před 2 měsíci

    Khaza kwa osauka koma ambuye muchitepo kathu chilungamo chiyende

  • @user-rl2ow2qk7k
    @user-rl2ow2qk7k Před 2 měsíci

    I even crie 😢😢😢😢

  • @EuniceBanda-pu6qp
    @EuniceBanda-pu6qp Před 2 měsíci

    Mmmmm kulakwa

  • @GiftMwasauka-uv6ql
    @GiftMwasauka-uv6ql Před měsícem

    Mtendele si Nsima #Malawi🤔.

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 2 měsíci

    Amabugwe ntchito iyi ndiyosavuta akuyenera chithandizo

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 Před 2 měsíci

    AmaBungwetu apa zikanali zandale mukanaona kumachita kupikisana kuyankhula kuti atchuke ndicholinga chakuti apeze cholowa kuchokera kwa ndalewo.Koma apa zamunthuyu kuli Ziiiii.Akuti omenyera ufulu wa anthu bwanji osanena kuti omenyera mimba zao bwanji

  • @PiterDeleza
    @PiterDeleza Před 2 měsíci

    Malawi Police sinasinthe olo amakamba zoti inapanga reform koma sizoona .

  • @user-xw6rr9gm1z
    @user-xw6rr9gm1z Před 2 měsíci

    Eishhh

  • @kasupeowenpaul
    @kasupeowenpaul Před 2 měsíci

    Osauka alibe mau.pamene chilima amukhulukile ma billion