😂😂😂😂😂😂😂 Bhima nditambwali mumatha guys mwatipatsa ka film komaliza chaka chino kanali bho heavy hana Mbambande selina befiya mlonda wadyela ankolo abima a Dc makwana guys nose mwatenga mbali mu ma film ose achakachino ya zama love❤😂❤😂😊😊😊😊
Eeeeh koma ma series amenewa taphunzira zinthu, tadzudzulidwa, tadziwa, takondwadi kwabasi, aaaayyaa ambuye akudalitseni a Selina, Obethia, Obima, Odankeni, and everyone of you.
A MC ati mindipatse ndalama zanga 😂😂😂 this was really nice guys thou mwatisiya mmalere koma woow it has been a nice episode since day one ❤ Selina umakwana
Koma musalekere pomwepatu, kungoti mwina tidziwe ngati muli ndi account special for such series, mwina mkumaponya limodzi limodzi kanganyase, just thanks giving and pushing such works ahead. Put some details please.
Mmmmm koma guys it must have been tiresome, but you made our days. It's a masterpiece. Can't wait to see you guys in anything you are planning to do, bravo guys!!😊
Eish .... Iliyonse mumahita ma guy.... Mwandisangalatsa from the beginning ... Where did u get this courage Selina😂... Bhima umatha.. Koma berthia iweyo mkatundu eishh
You've had a very good run guys, and I've been glued to this CZcams channel not to miss an episode. But, are you really impressed with the ending? Ndikuona ngati mukaipangenso bwinobwino
Komaso, bwanji tisamanene finale, mwina we could leave some room for continuation subject to whatever factor. Ndiye ofunika kuyesa kumapeza mawu ena oti yatha but...anything can happen....may continue or not. Kaya tiphunzitseni zimatani pa point imeneyiyo.
😂😂😂😂😂😂😂 Bhima nditambwali mumatha guys mwatipatsa ka film komaliza chaka chino kanali bho heavy hana Mbambande selina befiya mlonda wadyela ankolo abima a Dc makwana guys nose mwatenga mbali mu ma film ose achakachino ya zama love❤😂❤😂😊😊😊😊
😂😂 I love it you guys you make my evening amazing. Watching form Vaal University of technology
Hanna you are so smart I love it
Berthia's voice 🔥🔥
She has singing Voice indeed 🔥🔥🔥🔥
Yeah she has beautiful voice
Amatha
The whole serie was a package thank you for entertaining us
Wow thanks ❤
The effort was massive from everyone. Rashley on point.
iyi yandkomera hvy❤
So good to see Mr. Wellington Kuntaja
Looking forward for another series guyz ❤ Ur the best to be honest
👍👍❤️
Thungululu za nice km gyz keep it up l love all
Za kmatu mmm gyz munafasa srs 😊🎉❤😂
Wow i have enjoyed and learned alot. Keep the 🔥🔥🔥burning
This is beautiful, kuyambenso ina😊
Guys u r so wow😚
Very very best lesson Hannah God bless you Hannah ❤❤❤
Koma MC 😂😂😂😂 ati musammenye Bima ndimamuna okongola 😂😂😂😂😂😂 I can't stop laughing😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Sizinabebe 😅😅😅😅kodi bhima wafa ndichibagela
Eeeeh koma ma series amenewa taphunzira zinthu, tadzudzulidwa, tadziwa, takondwadi kwabasi, aaaayyaa ambuye akudalitseni a Selina, Obethia, Obima, Odankeni, and everyone of you.
Hope and believe that come 2024 will bring us more enjoyment
Bwanji yibwere kawiri zabeba dzedi love you guys
Koma ankhoswe a kuchimuna wo ngotengeka😂
Kwambiri
Ma guy munali serious.. bg up mesa
Zamuonekela bhima anawonjeza kwambiri amuna ena mutengelepo mphuziro kkkk selina ndi befiya and zana mumakwana kkk😂
Keep up Selina and Bethia 🎉 I love you guys
Tadala in a dress😂😂😂
I quote " inu msamumenye bhima ndi mwamuna wokongola" 😂😂😂
Apapa ndinaseka osati sewero kkkkk
it was nice series
Wow !!!!!Koma zokoma zed
Bhima ❤❤❤❤❤❤ I love you guys so much
Ndipo machita kumumvela Chison selina like it’s real,
Heart break osazaiphwekesa
Kudos guys,,, To more years for massive entertainment. Congratulations for the milestone.
Beautiful
I like your seriousness in your acting, big up
A MC ati mindipatse ndalama zanga 😂😂😂 this was really nice guys thou mwatisiya mmalere koma woow it has been a nice episode since day one ❤ Selina umakwana
this was so serious episode I like it
best from the best team love you guys you are so talented i just love everything in this episode big up to Selina Dumbula you are best sister
Thank you🎉
Live from HARTBEERSPOORT SOUTH AFRICA KEEP IT UP GUYS
Koma musalekere pomwepatu, kungoti mwina tidziwe ngati muli ndi account special for such series, mwina mkumaponya limodzi limodzi kanganyase, just thanks giving and pushing such works ahead. Put some details please.
Wow what a casting shoot out. Keep it up guyz
Koma kwakoma ❤❤😂😂😂😂 iyambileso 😂😂😂😂😂 nice Ending you deserve more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kkkkkkkkkkkk km Guys mumakwan bigups 4m cape town 🇿🇦 .....Celina iwee waonetsat manyau no tears .
So beautiful yatha ikukoma
Iove Selina
Nice job silelina umatiimilir
Final yokomaaaa inuyo mwafika iyiyi nde eeeeee nduchita kusowa chonena koma bigup guys ❤ waiting for onother one
Mmmmm koma guys it must have been tiresome, but you made our days. It's a masterpiece. Can't wait to see you guys in anything you are planning to do, bravo guys!!😊
Lots of ❤❤❤ to you all.
Acting on point even one hu doesn't have any idea of ZAMALOVE he can hv a feel of reel life situation more than acting
Guyz keep it up kakukoma
Kkkkk km ukwati umenewo yooooo ndaukonda ine 😂😂😂😂😂😂😂😂
Wow beautiful kwa ine yatha bwino
Mmmm so nice
Anthu munafatsa ndipotu well done
Only two much chipwilikiti on last part
Koma ndi 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kumenekuja kunali kwachipwilikiti kumene
Bhima udzangosowa ngati eliya wamoyo komaso Selina upole 🔥🔥 😂😂😂 mpakana kukayimba komweko zoona oky good job guys and god bless moseee
Musammenye bhima ndimamuna okongola kkkkkkkk mwabhebhetsa guys❤
Best stunt ever
😂
Dunken wapanga chani😢😅😮😂
Wonderful guys
🔥🔥🔥🔥
Eish .... Iliyonse mumahita ma guy.... Mwandisangalatsa from the beginning ... Where did u get this courage Selina😂...
Bhima umatha..
Koma berthia iweyo mkatundu eishh
😊
Ndaionela mochedwaa bwanji nankha mwana mbuya uja bwanji anagwa nayo kkkkk Kom mwana baaa
Waoooo
Thanks guys mmativetsa kukoma❤❤❤
Bhima 🔥🔥🔥🔥🇲🇼
Bhima jeketelo koma munavala ku Limbe cathedral lija ndilomweli kkkkk
😂😂😂😂😂😂 km selina ndiwe odekha kwabasi ine nde ndingamumenye mamunayo mwa nyoooo apongoziwo kuwapatsa mawaizi azelu anyoooooo , muli bho kwambili ❤❤❤❤
Koma plan ya ukwat eeeee apopo munakwanira ndithu😂😂😂😂😂
Koma selina amatha kuimba kunena zoona
Koma guys mumativesa kukoma osanama❤❤
Beautiful episode ❤❤
🔥 🔥 🔥
❤❤❤❤❤
Superb
Nice
Not tadala drinking fanta as the whole drama gets juicy 😂😂😂😂
Love it😂 lover boy watisiya
Komatu sellina wabhebhesa mopanda nsanje😂
Keep it up guys. Selina and Bethia mumantha inuyo
Too much mphokoso ine sindnamvesese😂😂😂
Kumangoyenera mapokoso kumene
Wow! Nice guys😂😂😂😂😂
Guys ai munachedwapo zili bho ❤
😂😂😂😂😂😂
Dj Kweza volume IZATHERA MAPENATE
Nice mwamaliza bwino😂
Mwatisiya mmalele,ndikusowan magaye zamalove 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
I love you guys
You've had a very good run guys, and I've been glued to this CZcams channel not to miss an episode. But, are you really impressed with the ending? Ndikuona ngati mukaipangenso bwinobwino
Yatha imeneyo basi😂
😂😂😂😢😢😢😢 Zovuta khan zake izizi 😅😅😅😅
😂😂😂😂😂 guys mumakwana 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nice ❤
Komaso, bwanji tisamanene finale, mwina we could leave some room for continuation subject to whatever factor. Ndiye ofunika kuyesa kumapeza mawu ena oti yatha but...anything can happen....may continue or not. Kaya tiphunzitseni zimatani pa point imeneyiyo.
Kkkkkkkkkk koma ndiye mwaipatsa moto
Abambo ake aBhima mwachedwatu kumulangiza mwana wanu
Selina ndiwe olimba mtima😅😅😅😅
Mumatha guys love you❤❤❤😂😂
Hanna u look beautiful ❤
Good reason guy's
Hanna to her best 💥🔥
😂😂😂 yatha bho
😂😂😂😂😂 guys muli fire ❤❤❤❤❤❤
Kom Hannayi ndiwokwatiwa nankha chebimawa Kom ngat nchoncho eeee nkaz ndimamunawo ndiopilila