Vendor Ndi Munthu Ofunikila Pa Chuma Cha Dziko - Bon Kalindo

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 3. 07. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo talks about the importance of the government creating an enabling and business-friendly environment in Malawi to boost the country's economy and development.
    Ku Nyasa VoiceBox, a Bon Kalindo akukamba za kufunika koti boma likhazikitse ndondomeko zabwino zochitila bizinesi m’Malawi kuti atukule chuma ndi chitukuko cha dziko lino.
    #malawi

Komentáře • 2

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 10 dny +1

    Mukhale ndi moyo chikhaleli Mr boni kalindo tsoka kwa iye amene amamunyoza boni kalindo ife timamulekeza chifukwa timamutenga ngati Tate wathu mulungu adzikhala nanu thawi zose ❤❤

  • @CaptainNyenga
    @CaptainNyenga Před 10 dny

    Yehova azikusunga ndi moyo born kalindo andalewa chikondi alibe ndi a Malawi komaso nkhalamba za MCP zatizolowela kwambiri