Ndine Gardener Ku Statehouse - Samuel Lwara

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 20. 03. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Mr Samuel Lwara talks about Ghost workers in Government with Leah Malekano on Zodiak Broadcasting Station (ZBS) Exclusive Interview. You can Catch the Rest of the Interview on ​⁠​⁠‪@ZodiakMalawitv‬ Once it has aired.
    Pa Nyasa VoiceBox, Mr Samuel Lwara akukamba zanthu amene amalandila malipilo ku boma koma ntchito yawo yeni yeni siwoneka ndi Leah Malekano pa Zodiak Broadcasting Station (ZBS) Exclusive Interview. Mutha Kupeza Mafunso Ena Onse pa @ZodiakMalawitv Akayamba Kuwulutsa.
    • EXCLUSIVE INTERVIEW WI...
    #malawi

Komentáře • 8

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Před 4 měsíci +2

    Kkkkkkk koma ziliko🔥🔥

  • @chikukanyinji6873
    @chikukanyinji6873 Před 3 měsíci

    Zilikotu ziliko!!!!

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m Před 4 měsíci

    Misonkho yathu mama nee

  • @user-vo9ie2gv7o
    @user-vo9ie2gv7o Před 4 měsíci

    Ndichifukwa chake kwapita ndalama zambiri ku state house ati zosamalira kapinga mmalo mongonena kuti ndizopangira phwando nthata zanjala izi zikungokama yoonda kale ng'ombe

  • @user-dd1qq5xq1k
    @user-dd1qq5xq1k Před 4 měsíci

    Bargamoyo state

  • @user-ud9wl8yg1t
    @user-ud9wl8yg1t Před 4 měsíci

    Chakwela ndimbava yayikulu zedi ndi chifukwa chake chilima anati ichosedwe immunity kuti president aziyimbidwaso mulandu ngakhale akulamulila ndipo chakwela akalonjeza kuti ndikazalowa mboma ndizachosa phamvu Zina za president kuti azizayimbidwa mulandu ngakhale akulamulila atalawa Kuba anayiwalilatu nzose

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf Před 4 měsíci

    Dziko laMalawiimenero chonchi tingathkuke .Tidzingolila daily Asaaaa atsogoleri wathu Dziko mukulupititsa kuti .kuba kumeneku bwanji?

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r Před 4 měsíci

    Chakwela mbava yahikulu Malawi