Sindikwela Ya Kuphwa - Samuel Lwara

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 5. 09. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara Says that what has happened in Karonga is that people have voted for individuals not political parties and that there was wide spread voter apathy. Therefore MCP should not rush to celebrate the victory.
    Pa Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara wati zomwe zachitika ku Karonga ndi zoti anthu amavotera anthu osati zipani za ndale komanso kuti anthu ambiri alibe chidwi. Choncho MCP isathamangire kukondwerera kupambana.
    #malawi

Komentáře • 24

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 Před 5 měsíci +3

    Yes,,yes, yes Lwara ndi munthu oganiza.

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před 5 měsíci

    Lwala you're a genius indeed

  • @arnoldchikopa2611
    @arnoldchikopa2611 Před 5 měsíci +3

    Lwara nd wanzeru

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g Před 5 měsíci +4

    Komabe a Malawi tsegulani moso anu zikuoneka kuti kususuka ndi komwe kutipweteketse zoona kungopatsidwa K2000 basi nkukopeka

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před 5 měsíci +3

    That's true brother

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 5 měsíci

    Good Message

  • @uchizJoelMumba
    @uchizJoelMumba Před 5 měsíci

    Wamisala uyu

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Před 5 měsíci

    🔥🔥🔥🔥

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před 5 měsíci

    Likukumwe lonse nduna,ma MP kukapanga camp ku Karonga 😂😂😂

  • @user-nc4vi1jt5g
    @user-nc4vi1jt5g Před 5 měsíci

    Alwara mboloyako chitsiru

  • @sekerakasawala9114
    @sekerakasawala9114 Před 5 měsíci

    A team wins with just one goal(penalty) even if it was in scored in extra time of the remaining 1 minute.

  • @user-lp2sd7lt8b
    @user-lp2sd7lt8b Před 5 měsíci

    Chisankho china chilichose ena samavota. Kuwina ndikuwina basi. Izizi ena apenga nazo misala. Komaso ngati iweyo ndiwa mcp bwanji ukufuna ikanaluza

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 5 měsíci

    Panopa zinatha zonyamla petro wowotcha nyumba zawanthu adpp simngawine mnkafuna kupha mtambo ndiye mngawine

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 5 měsíci

    Misala yimeneyo kuwina ndi ndiwina basi ndi chisilu awa khalani chete

  • @yunusmussa6882
    @yunusmussa6882 Před 5 měsíci

    11:29

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 5 měsíci

    Iwe wakwela yakuphwa luwali sindiwe wmcp ndiwe chichisilu kwabasi

  • @user-vu9rt8gj3o
    @user-vu9rt8gj3o Před 5 měsíci

    Apm my vote basi

  • @yunusmussa6882
    @yunusmussa6882 Před 5 měsíci

    Was 59 + 1 applied?

  • @Monalisa-yy1si
    @Monalisa-yy1si Před 5 měsíci

    DPP my vote inu mungo vutika bc😅😅😅😅

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td Před 5 měsíci

    Awa misala ikamayamba timaonera chonchi abwana akangomutaya basi arowa kutchire koma chakwera alibe Moyo oipa ngati iyeu ufuna kuwina motani garu iwe zilibwino azakowo sakukuyankha akudziwa kuti ndi misala akutaya unya

  • @amielkwalingana5979
    @amielkwalingana5979 Před 5 měsíci

    You need to study polical studies sir otherwise you are talking nonsense.