Mcp pamoz ndi achakwera achepa there days are numbered....live long dad kaluwa and much love to fredo kiss ,,, I speak divinely protection in that family ,God be with you
Mr kamlepo kaluwa one of the greatest politician in Malawi u fought for democracy MCP is getting us backwards to dictatorship arresting and killing innocent people this is not what the voters wanted.
Well said I hope pala ni wanthu wa umunthu wawo wapulika and if they may attempt to kill Fredo this country will go beyond what happened in Kenya. We are ready
Andale amafuna kukhala pa mpando forever yet amapanga zoononga mu nthawi yochepa I don't understand then at all. Being good will not make you lose anything at all but being bad eeeh ndi izi za cheucheuzi
Our MDF and All police officers chomwe mukidziwa kumvela/kulamulidwa basi? So many things are happening in our country but why are you just watching? That's why every president chooses his own leaders in all angles right? As a real soldiers, show us kuti munasankhidwadi mwanzelu. Kapena chomwe mumadziwa kumangolandila ma order okasaka mbewa not so? Taphani wina tione ngati kadziko kathuko sikakhetsedwa mwadzi. Za ziiiiiiiiiiii
Mwachitamakola kuwaphalila unenesyo, chiuta wamusungeni dada kamulepo,we are In democracy time!!!!.
Makolawaka 😊kwalinamwe manda
6 jjjjjoo9ooj .0pll0
V
Very powerful speech.long live Mr KALUA. may God protect you from these heartless swines
Good massage Mr u are the strongest man
Mcp pamoz ndi achakwera achepa there days are numbered....live long dad kaluwa and much love to fredo kiss ,,, I speak divinely protection in that family ,God be with you
Mr kamlepo kaluwa one of the greatest politician in Malawi u fought for democracy MCP is getting us backwards to dictatorship arresting and killing innocent people this is not what the voters wanted.
Apolisiwo ndi chakwela onse machende awo fotsek...
😂😂😂😂😂
Powerful massage bwana Mr KALUA ❤🎉🎉🎉
Why not taking them (police) to court Mr Kalua?
My Land 😢😢😢our warm heart of Africa 😢😢😢😢our peace,joy and harmony county has turned into Sodom and Gomorrah 😢😢😢😢
I support kamlepo munthu wa mkulu kwambiri mumakwanila.
Ndipo ari mu history
MCP makolo amkatiuza kuti ndi chipani chakupha ndiye tikutha kuonadi and I don't think wachinyamata ozindikira bwino mkumakaponyera vote MCP....
Mvamvekatu ma words umu 🔥🔥🔥🔥🔥
Pls bring out the CCTV footage here, ASAP. It will have a heavy impact on people's minds
Konwani kamponje ndiwe opusa kwabasi ukuona ngati kamlepo kalua ndi size yako, Bwana my God protect your family,,,,,,,,
Well said I hope pala ni wanthu wa umunthu wawo wapulika and if they may attempt to kill Fredo this country will go beyond what happened in Kenya. We are ready
This man is loaded!
Wati ndigenda waponda MWALA
🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Father kamulepo kaluwa tili pambuyo panu
Powerful Papa ❤ palibe wamuyaya tonse tizafa bas
Apo ndipo wamanya kuti watumbuka wokhumba yay kuwaseweleska
What a powerful message
We respect you mr kalua we leant alot and we still learning much love...
Ayiwala zoti achoka pampando, shame on you. May God be with you Kamlepo
God is great be safe and your family Mr kamulepo
Mwayowoya bwana ndipo nakondwa nazo fundo zino zose chiuta wakuona vose
History we learn alot
100%
Thanks dada for the message
Good massage kalua
Don't worry dad 2025 mcp police tizayikhaulisa
This is very stupid insane 😠... Chakwela should resign galu wachabechabe
WE LOVE U KAMLEPO...MCP YIKUTULUKA M'BOMA CHAKA CHA MAWA...
Oh my God Malawi police and Malawi defence force are just used they don't even know what they responsibility is really shame on them
Yebo mwawanthu, don't touch Tumbuka people, we believe in Jesus
I love the the guy
Ndikukaika ngt anthu afike nthaw yovota bwinobwino ..zikundionekela ngat mavote azizizi akhoza kuchitika mu Mziko muno...
Kwabasi
Kkkkk😂
Mmmmm koma abale mpaka kukuonongerani zinthu mnyumba abweze katundu ameneyo
Good Messnge Mr Kamulepo kaluwa ❤ Chakwela you mast go watikwana
Message ya mphamvu ❤
Wise speech Honourable
*Amtumile mwenye* kwabasi nambo ngadandaula Mcp chipani changalumbana Ata panondi.
We fear God not person 💪🔥
kumpoto MCP kulibe vote
Mupheni kkkkkkk andale amwene 🤣🤣🤣🙌 atitu enawo anyumwe kkkk muphenitu akamlepo akusendeno muone
Osaopa osaopa palibe wambewu padziko pano, ndipo kalikonso kazalawa imfa.
Mukapha uyu nde muyalukatu poyerayera
Ndipo kwambiri tu mmm
Andale amafuna kukhala pa mpando forever yet amapanga zoononga mu nthawi yochepa
I don't understand then at all.
Being good will not make you lose anything at all but being bad eeeh ndi izi za cheucheuzi
May God protect you and your family
Koma nde mwangoti 3stars apa pali nkhani apa tiuzeni zambili bwanaaa
What does it mean?
Mmm mpaka I know akumidima omwe mumadalila 2025 Kuli ntchito
Pathu sipadziko zoona but the voters are suffering bwana
Kuyankhula kwabwino uku, nawo apolice alibe nzeru angowagwiritsa ntchito malipiro ochepa km kumangozunza anthu
Mmmm nde afika posausano... Kupha bas!!!!! Eeee why Malawi now
😂 koma kwachema osapanga mantha aonese
Mwana wamupoka wayoghoya wa chewa mfela za Eni 😅
Rise up Kamlepo we want peace
Chakwera, don't know,do good, be good, live good, he's no good..
Tavuka na mcp onse wa mcp mavi yao (komaso inu akamulepo mukufoila kwambili mr kalua u sleep too much
Koma ndiye Kwachema
Ing'aluleni bwana Kaluwa,,,,,,,,,,,,
Chitukuko chA razalo ndikupha basi
Ngati muja Chinalilinso Chitukuko Cha Peter Mutharika pakupha Issah Twaib Njaujyu, Buleya, Masambuka, Tambala Family kutchulapo chabe ochepa
@@user-tk6qh9zs7hmuli m'bomatu. Tengerani umboniwu kukhoti tidziwe zoona zenizeni. Mwina munkapha ndinu kuti muipise mbiri yaamnzanu
Yah ndimakape
big boy ting set
Leader
30:24 my God protect you kamulepo and your family ilike what you saying
Fact
We love you Kamulepo Kaluwa
Achilundi samalani, msaone ngati mwafika. Lindani madzi achilundi apite nde mziti mwadala, nzosiilanatu izi osasimbwa.
Dadi apa mwafikapo muuzeni zoonaasiye chibwanamooto uyake asazolowele
Mwayankhula abwana
Kamulepo kaluwa mumatiyomilira munatsala nokha (RIP chakufwa chihana)
Awawa ngat ali mau awodi. Aah the Man must be suspected sure
😢 indeed this world it's not our home am crying Malawi
Afa okha
Powerful
With heavy heart
Akapha mwana inunso tiyeni tikaphe awo.
Ofunika kuyamba kubwenzera. Zatopetsa.
Athuwa akufuta chifukwa amalawi sabwenzera.
Ayelekeze 😳😳😳😳
Koma ndalama mani mmmmmh ay ndinthu mmmh anthuwa guyz samagona muja tigonera enafe
Hon kaluwa🔥🔥🔥🔥
Osapita ku khothi bwanji a Kalua? Komanso ndalama zanga simunabwenze kuchoka 2019 paka lero mumaganiza bwanji bwana Kalua? Koma umunthu mulinawo?
Panyopanu inu achitsilu
Why Mr Kamulepo want to kill his own son? Sad
Nonsense did you here him kut akufna kumupha mwana wawo
Mawu amphamvu kwambiri chakwerayo ngati kulikumva wamva dziko ndilizungulira
Ntchana asamuyese ghetto azaimva
Za phone iwalani asiyileni ikhale yawoo...
That's fact's indeed
Ndipo ndizoonadi zamawa siziziwika
Munthu wamkulu wayankhura❤
Aphe fredo awone
Komanso katundu anaonongayo abweze
Nabo bafwenge bachakwera kulije wamuyaya
Tili mukati mweni mweni
Muzazisumire zimbava izi zidzakulipireni hiyaaaaa
Mwamuyambapo kaluwa amayabwatu chwe mwana chwe
Mwachita makola mwawa phalila unenesho.
Chiuta wakudangirileni.
Chakwera pa m’tongo pa mako
Koma ndiye ndinthawiso yakamuzutu aaa
I support you
Mukapusa amupha
Fredo kiss kodi kapena Onesmus
Following
28:52
Koma z..ikoli ...Amwene
Our MDF and All police officers chomwe mukidziwa kumvela/kulamulidwa basi? So many things are happening in our country but why are you just watching? That's why every president chooses his own leaders in all angles right? As a real soldiers, show us kuti munasankhidwadi mwanzelu. Kapena chomwe mumadziwa kumangolandila ma order okasaka mbewa not so? Taphani wina tione ngati kadziko kathuko sikakhetsedwa mwadzi. Za ziiiiiiiiiiii
Ndipo kwambiri tu mmm