Nyimbo yako imene unamenya posachedwa iyi it's 100% to my side mama. ( Wolimbana ndi ine akulimbana ndi yehova) Keep it up mama God almighty must help you util forever 🎉🎉🎉🎉
Ndipo funny how some people mpaka pano amafunabe Miracle aziyimba and behave ndendende ngati mayake, forgetting ndi anthu awiri osiyana. Mwanayu pena amaziona eeeh
Nyimbo yako imene unamenya posachedwa iyi it's 100% to my side mama. ( Wolimbana ndi ine akulimbana ndi yehova)
Keep it up mama God almighty must help you util forever 🎉🎉🎉🎉
Miracle she's really blessed and she knows how to make friends with people, much love you dear Chemwaaa ❤❤❤
Beautiful and clever girl ❤you mimi keep it up. Gospel suits you
Amen and Amen , am also blessed with your story my Sister.you are blessed.
Wandiyankhulira bwino kuti sitingafanane zonse ,grace was grace and miracle is miracle
Chauzimu sichipheka.
This is a seed which God sow in you.
You will go higher Miracle
You will keep on shining
God will fight all your battles.
❤❤❤❤❤❤
Nice interview like daughter like mother God bless you miracle
Nice interview on phenomenal being miracle chinga your so courageous
This z wonderful miracla I love you...u know hw to chill❤
Welll spoken,powerful words miracle chinga
Big up Mimi.... munthu kumakhumudwa Ndrama zikasowa osati zinazi isaaa 🔥🔥🔥🔥🔥
Miracle you're such an amazing soul🥰🥰 yes you can't much everything with Grace but God uses you🎉 keep on shining girl🥰🥰
Nsangala zokhazokha.. I love her. Keep it up mamie
Miracle ndiwe ochenjera hvy, interviewer sukumupasa mpata😅
Ndipo ndilipo amene ndimamva kukoma ND nyimbo yako 🎉🎉ndmasuthik umandifikitsa kutaliii komwe maso phenya anga samafikakooo keep going zofooketsa sizimalepher mamie
Grace was good friend to me and humble lady. I still miss her. Miracle keep it up when I see you I see grace chinga
Much love beautiful mimi 💓
Mrs. Mpukunya❤
Wow like daughter like mother❤
Very clever and intelligent keep it up miracle
Very inspiretional my dear❤❤❤
God bless you Miracle
And God be with you always
Don't judge miracle coz of her looking coz God target is your and her heart
My favorite❤
Powerful powerful dear
Beautiful Mimi❤
Keep going mama much love❤❤❤
Wishing you all the best sister
Ndizoon ngakhare angakupoterez anthu kom mulungu amasithabe nyengo❤
You are an inspiration Miracle
Go ahead with Gospel my dzotsa Miracle luvs u so much
My favorite
You are smart!
Mwana ochezeka koopsa my favourite artists in Malawi
You are a star umangondikumbutsa mayako always
Amen and amen mulungu ndiwazatheka bwanji
Ur the best dea
Beautiful Mimi
Blessed from the womb keep it up girlie ❤
Beautiful mimi
Thanks ndaona ring
Amen👏
beautiful
Improve koma studio setup , ambient voice has to be faded out. Mukuveka ngati nkalasitu
You really empress me Mimi
I love u mamie❤
Ukuimilira chikhalidwe chathu Cha chimalawi 🔥🔥. Anthu ambiri oyimba samatha kulankhula chichewa bwinobwino chomchi 🔥🔥
Eeeee l salute u gal ur vele strong 😘😘
Ngolongolola uyu kkkkkk ndiye ngokokomeza bwino koma amandisangalatsa very confidence
No chance for interviewer to ask questions angolongosola ekha aaaa😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂
Miracle chinga umandiwaza❤❤❤❤
Miracle iweyo ndi wakhani, ukufunika 3 hours. Anyway your strong lady. Keep it up
Your strong mamie
❤❤
❤❤❤
Best forever
❤❤
Miracle chinga from 1 question wafotokoza interview half kkkkk
I love you girl
Ndimaona ngat ndaiona ndekhaaa😂
I see the ring is back that's beautiful ❤️
Ndi interview yakale kwambiri... Rainbow TV iripo
Beautiful miracle
❤
Amen
So sad ... but one more thing is difficult to her to explain storys because there is many storys she just cut off cut off.
Miracle Miracle
Nce
Miracle wayankha ma funso onse kudzera mu funso number one loti "kodi miracle ndi ndani ?"😂
She needs counseling eish I can feel her
Ndimaona ngat ndaona ndekhatu 😅😅😅😅
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk koma ndaseka
This is nice❤
And plz subscribe
This woman inspires me so much
dope
Miracle wasanduka interviewer😂😂😂😂😂
Miracle wanduyankhulira bwino God bless you ❤
Mklass mwathu muli winawake funso limodzi amayankha zambiri chonchi nkumadabwa kuti bwanji walephera😮😮
Ooh my God😂😂😂😂😂 this is so funny kkkk
Indee kumankhumudwa ngati ndalama yasowa ,umakwana Mimi
Kuli party kwa adani akumwa musonzi yanga mmmmm, rest well Grace
Iiiiiii Miracle mwerani madzi...
Hahahahahah
😂
😂😂😂😂😂😂😂 koma kumeneko
Kkk
Your mother was like my late mother she was working hard for the children to survive
I like u mama oh yes .......mamvuto amapanginsa kuti muthu ufike pana pake
Ndipo mavuto ndie mulato wathu owolokera Chemwaaa
Ndipo funny how some people mpaka pano amafunabe Miracle aziyimba and behave ndendende ngati mayake, forgetting ndi anthu awiri osiyana. Mwanayu pena amaziona eeeh
Mrs mpukunya
I see ring🎉🎉
Ine ndasilila kwambili ndithu mmm mulungu anakudalisa kwambili komamulimbikile kwambili osafooka mama ambuye akudaliseni
lne mulungu andipase mtima olimba ngat wa miracle
Miracle akuti ndine miracle chinga mpukunya
Amalawi kumanama kuti Banja lake linatha mmmmm Malawi a.sitizatukuka ndithu pakamwa too much mmmmmm
Awa ndakatundu
Much ❤️ love from zim miracle ❤
Zandinkhuza😢
Improve on your sound recording
Mavuto!
Akuyenela ma seweloso miracle😅
Mafuso wayakha bwino koma ali ndi nkhani zambili Mwanayu ndiposo ali ndi uthenga wa mbali wa Mulungu
Mayi Mpukunya tatumizani chipewacho chonde kuno ku Jozi Pretoria
😂Mpaka chikwere bus 😂😂
@@user-oi7wm4td7p eya plz tichilipilira bus basi
Mimi uli ngat ine makhumudwa ndkakhala maluz😂😂😂😂
Hahahahaha mastern koma afusaso fusolina kapena mafuso onse miracle wayankhiratu
Kkkkkk ndipo
Koma iiii kuchenjera mama
Akufunika interview ya 3 hours uyu interview yokoma kwambiri inachepa ndi nthawi 😂😂😂
Nde ena azit banja latha eeh 😢
Kodi ndiyaliti interview yi?
Yakale
Ineso fuso langa linali lomweli
Komaso ubusa ungakukhaletu😊
Miracle ndi one 😅😅
Ndi chifukwa anthu timalephera mayeso, funso limodzi koma kuyankhula zonsezi aaah
U deserve secular music to match your life style
Kodi a gospel ndi Angelo? Eeeh eeeh
Are you God? So long as she has never mentioned your name in her music then just shut up.
@@paulinechirwa7582 truth pain pain
Who are you to judge her
@@stellasapakudwe3061 pain pain
Miracle you're beautiful ❤❤
Eish girl you can talk,1 question koma answer 10 pages essay