ANA NDI ACHIBALE A ZIMAYI WADZUKA KUMANDA KULONGOSOLA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 24. 02. 2024
  • ANA NDI ACHIBALE A ZIMAYI WADZUKA KUMANDA KULONGOSOLA

Komentáře • 86

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Před 2 dny +1

    Ku mpoto nde kuli ufiti wa serious akapha akapha anthu aphabasi tsamauka ku manda pamene kumwela amauka kumpoto kuli ufiti oyipa!anthu ambiri kumwera akumauka ku mpoto zero🙄

  • @siskanyirenda
    @siskanyirenda Před 4 měsíci +5

    Mukamapanga zinthu please khalani serious munthuyo muzimuonetsa tizimuona munthuyo

  • @user-dk8ey5pu5w
    @user-dk8ey5pu5w Před 4 měsíci

    Mzimayi ameneyo mugwireni,mumumenye makofi auluru omwe anamutuma. Wamutuma ndi prophet

  • @SleepyAnteater-bh5zo
    @SleepyAnteater-bh5zo Před 4 měsíci +8

    Hanifa chonde uzitionetsako muthuyo ngati momwe amapangila azanu

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa5981 Před 4 měsíci +2

    Munthu wabwelayo sakufana ndi yemwe anamwalila ndiye akhalawao bwanji

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 4 měsíci +1

    Kodi ku lilongweko sanabwereko aaa

  • @user-ih3qe8ho3v
    @user-ih3qe8ho3v Před 4 měsíci

    Zonama idzi akuchita kulakatula ngat thano hiyaa 😊

  • @YONA-v5o
    @YONA-v5o Před 4 dny

    Nde inuyo aku banja munthu woti mmakhalanaye simnamu fananitse ndamene anamwalilayo

  • @gracemphande550
    @gracemphande550 Před 4 měsíci +1

    Ulendo waku Lilongwe ayendako bwanji?

  • @user-rd4ft9nd8t
    @user-rd4ft9nd8t Před 4 měsíci +1

    Kodi ku Lilongwe kwake mbali iti koma ngati zili zoona Ambuye alemekezeke

  • @BarnabeMacuane
    @BarnabeMacuane Před 8 dny

    Ndikupemba mamba ya profit ine Kuno ku mozambiaue

  • @user-co4ej4cw8r
    @user-co4ej4cw8r Před 3 měsíci

    God have mercy

  • @tiwongehojaney5873
    @tiwongehojaney5873 Před 4 měsíci +2

    Za satanic izii munthu anamwalila ndi mzimai abwera bwanji zibambo aaa komatu anthu amulungu samalani tili mmasiku osiliza 😮😮

  • @user-hx4mz9nk9g
    @user-hx4mz9nk9g Před 3 měsíci +3

    Aaa munthu wamayi kumwalira mpaka kuzabwela ngati nyamata bwino nazotu tizalandila nazo ziwanda zakomweko

    • @ChrissyChakhala
      @ChrissyChakhala Před 3 měsíci

      H😊😊😊😊😊😊😮😊😢😢😅😅😅😮

  • @selinaalufasi3150
    @selinaalufasi3150 Před 4 měsíci +2

    ine sindikumva ataa

  • @user-dh4xl3jb9d
    @user-dh4xl3jb9d Před 4 měsíci +1

    Zakumidima izi aaaa

  • @JosèFelixsailessFelixsailess

    Zoipatu zimenesi

  • @JamLifa-xz8nc
    @JamLifa-xz8nc Před 3 měsíci

    Mudzina Lamulungu wachifundo komaso wachisoni khulupilani mwa mulungu mmodzi ekha ndipo wanu sameneyoyo wanu adapita ndithu

  • @janetchinga695
    @janetchinga695 Před 4 měsíci

    Kuli profet ku Tanzania ku dasalama auka anthu ambiri pitani komweko kubuza dasalama

  • @sarahkamphanga
    @sarahkamphanga Před 4 měsíci

    Tipasileni ndithu

  • @arseniomoraisfabiao6342
    @arseniomoraisfabiao6342 Před 3 měsíci

    Tatiwuzaniko dzina lá a prophet

  • @LufanMenard
    @LufanMenard Před měsícem

    Mmm zavta kwambili😂😂

  • @WysonMpatama-cv1mc
    @WysonMpatama-cv1mc Před 2 měsíci

    Kodi a prophet amenewa anakupatsani zingati

  • @danielmaganiza
    @danielmaganiza Před 4 měsíci

    Munthu anamwalira Ali wankazi abwela bwela bwanji Ali wammuna mmm😢

  • @kondwanimalikita5604
    @kondwanimalikita5604 Před 4 měsíci

    Iya za boza izizi zakumidima basi anangotumiza nkhalambyo

  • @JasiGoche
    @JasiGoche Před měsícem

    Nafe timazisowa ndipo zachitikanso ifa yotelo

  • @user-io8ig8xm6z
    @user-io8ig8xm6z Před 3 měsíci

    Mau zitolelen muziyankhura bwno bwno man aaha

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 4 měsíci +1

    Komatu mulandira nazo mzukwa aaaaaosowa munthu wa mmkazi abwera wa mmuna bwanji aaaaakomatu

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc Před 4 měsíci

    Tangotibweleselani ulendo wakulilongwe Kuti anayendako bwanji

  • @charityamos2183
    @charityamos2183 Před 3 měsíci

    Komadi akufanana ndi m'bale wanudi kapena zauneneri zomwezi

  • @user-nr8ww2oo4w
    @user-nr8ww2oo4w Před 4 měsíci

    Aaaaah komatu anthu mudzikhala serious Pena inu bwanj sanabwele munthu wanu wen wen anafayo mutakhale ndi dziwanda dzaku satanic pa khomo mukumutenga munthu oti simukudziwa zoona zot dziko linayipa inu zimenezo simukudziwa ikanakhala nkhope ya munthu wanu yo bola Koma mukunamizanazo ndizosatheka

  • @livemonkaposka3714
    @livemonkaposka3714 Před 4 měsíci

    Number ya prophet please

  • @Khadjajemes
    @Khadjajemes Před 4 měsíci

    Mwana Wako ungasowe komatu muthetsa nazo chakudya

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Před 4 měsíci

    Zamasiku akumapeto

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc Před 4 měsíci

    Kodi video imeneyi mumajambulila foni ya tilili kapena ayi

  • @mwale1154
    @mwale1154 Před 4 měsíci

    Last day

  • @WatsonMayor-lf3ey
    @WatsonMayor-lf3ey Před měsícem

    Eeee ngat boza koma ndozona

  • @Jermah51kennias
    @Jermah51kennias Před 3 měsíci

    Sanabwelebe

  • @KennethKachokola-er3us
    @KennethKachokola-er3us Před 3 měsíci

    Zoopsatu eesh

  • @slatielchipeni-zy3wb
    @slatielchipeni-zy3wb Před 4 měsíci

    Ziwanda iziiii

  • @paulchilola5462
    @paulchilola5462 Před 4 měsíci

    Aaaa

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 4 měsíci

    Zabodza izi munthuyo ndi wina

  • @mercyphiri6867
    @mercyphiri6867 Před 4 měsíci

    Timve zosatira plz

  • @BeatriceSaulo
    @BeatriceSaulo Před 2 měsíci

    Ili ndy bodza la nyooo munthu kumwalira mximai kuzazuka ali mwamuna ndy kut chani

  • @HardyGutu
    @HardyGutu Před 22 dny

    Chipo

  • @LoveNatala
    @LoveNatala Před 4 měsíci

    Zamatsiku osiliza owerenga khala maso

  • @user-hs8vn6wc4b
    @user-hs8vn6wc4b Před 3 měsíci

    😢

  • @AmaduJuma
    @AmaduJuma Před 4 měsíci +2

    Zakumidima izii,akhristu musocherela ,inu munthu oti ndi wanu mungalemphele kumuzindikila?

  • @user-ws2xi7ch7z
    @user-ws2xi7ch7z Před 4 měsíci

    Inu nkhope take mwaiwala ya munthu?

  • @lasmoboko5989
    @lasmoboko5989 Před 4 měsíci

    Zabodza zeni zeni kulibe zimenezo

  • @ShiraSaidi-oz5mx
    @ShiraSaidi-oz5mx Před 4 měsíci

    Tionetseni munthuyo

  • @user-tj2vx2xf7e
    @user-tj2vx2xf7e Před 4 měsíci

    Koma muzionetsako akulankhulayo ndinso munthu omwalirayo

  • @user-iq3iv8tp8t
    @user-iq3iv8tp8t Před 4 měsíci

    Don't stress your self please,munthu àmene mukunenayo ndi scammer amango panga pretend ngati wa asma nditambwali ameneyo he used Kuma panga zakeko ku Lilongwe around kanengo komanso area 43 titamuzindikira maplan ake adathawa

  • @SurprisedDriftwood-ef3lc
    @SurprisedDriftwood-ef3lc Před 4 měsíci

    Bodza mukufuna ma comment 5:25

  • @user-hp8du2lx3z
    @user-hp8du2lx3z Před 4 měsíci

    Zaziii

  • @user-dk8ey5pu5w
    @user-dk8ey5pu5w Před 4 měsíci +1

    Munthu amene anabwera kunamizira ku wa esthma uja ndi mmene ndi amene anadzafufuza maina anu

  • @EvansKatambo-hi3sr
    @EvansKatambo-hi3sr Před 4 měsíci

    M'bale wako oti wamwalira angabwere akuoneka ngati munthu wina mkumati ndameneyo zoona?guys come on come on,these so called prophets asokoneza anthu Kwambiri,

  • @DauglassNkhoma-dj9lp
    @DauglassNkhoma-dj9lp Před 2 měsíci

    Mukuti pano alikutoti ifeso kuno tili

  • @user-ju3kj9vy9e
    @user-ju3kj9vy9e Před 4 měsíci

    Za ziii

  • @osbornleman2500
    @osbornleman2500 Před 4 měsíci

    mmmmm profit wanama apa

  • @andrewmwachande7612
    @andrewmwachande7612 Před 3 měsíci

    😂😂😂

  • @BenfordChuzu
    @BenfordChuzu Před měsícem

    Zoopsatu

  • @DolineDalison-br1et
    @DolineDalison-br1et Před 2 měsíci

    😂😂😂😂

  • @user-ky4nh4wg7y
    @user-ky4nh4wg7y Před 3 měsíci

    Koma zikoli

  • @user-kn3ym1zf3m
    @user-kn3ym1zf3m Před 4 měsíci

    Zabodza

  • @user-ln7wg9jn4x
    @user-ln7wg9jn4x Před 3 měsíci

    Kkkkk

  • @augustMag
    @augustMag Před 4 měsíci

    Funso langa ndi Ili kunena kuti koyamba kunabwera mnyamata amene amaonesa kuti Ali ndithenda yomwe amadwala m bale wanu asma eti? Ndipo abusa anakuyimbirani phone munthu mukamufuna uja anabwera simunamusama pamene wanu yemwe anamwalira ndi mkazi sichoncho tinene kuti athufe tikamwalira timakasitha matupi anthu? Muthu oti anali mzibambo kudziko lapansi pano ndiye bambo uja mwalira pozauka Kwa akufa azauka ndinthupi la mzimai? Koma anthu amene munakhala busy ndi azibusa musamale inutu ameneyo simunthu amene mumamuyembekezera ai ndichiwanda chimenecho chochokera Kwa busa pofuna kuti atchuke ku dziko kuno

  • @AnjelinaKasowanjete-fo8it
    @AnjelinaKasowanjete-fo8it Před 3 měsíci

    🤣🤣🤣🤣🤣koma athu muri ndichibwana muthu waikidwa manda kumati wabweraso tangomvomeredzani muthu akamwarira

    • @mphatsomonjeza4371
      @mphatsomonjeza4371 Před 3 měsíci

      Zina ukamva 😅😅😅kambanga mwala munthu okhala wawo kulephera kumudziwa😂😂

  • @ThomsonNyirenda-df9io
    @ThomsonNyirenda-df9io Před 4 měsíci

    Wasting time for nothing I can't believe that

  • @Allieshaibu8612
    @Allieshaibu8612 Před 4 měsíci

    Malawi ❤❤❤❤❤

  • @ZefaniyaWelios-e5y
    @ZefaniyaWelios-e5y Před dnem

    poop?

  • @fredlemani
    @fredlemani Před 12 dny

    Anali yemweyo kapena ayi? Nkhope imasiyana bwanji? Mprothet ameneyo anamutumiza Mulungu kapena ndani?
    You and your prothets are fools and you don't know God.

  • @YONA-v5o
    @YONA-v5o Před 4 dny

    Nde inuyo aku banja munthu woti mmakhalanaye simnamu fananitse ndamene anamwalilayo

  • @JosèFelixsailessFelixsailess

    Zoipatu zimenesi

  • @EmmaRichard-hr7jj
    @EmmaRichard-hr7jj Před 3 měsíci

    😭😭

  • @DauglassNkhoma-dj9lp
    @DauglassNkhoma-dj9lp Před 2 měsíci

    Mukuti pano alikutoti ifeso kuno tili