BILLY KAUNDA'S STORY

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 04. 2024
  • billy kaunda explains his music carrier and journey
  • Zábava

Komentáře • 76

  • @MonicaThocco
    @MonicaThocco Před 2 měsíci

    I'm very proud with this man and I love him so much ,samadzipanga proud ku ma social media moyo wake za family yake ayi ,komanso ngati muthu woti wagwira ntchito m'boma simudzamva any speach ina iriyonseyo ayi , amachita kukhala ngatinso ku Malawiko anachoka koma ayi ,amawonetsa kuti ziii ameneyo amakhala busy kumasamalira zopanga tsogolo la ana ake ,ndi momwe mwamvera apapa za mamphunziro awana ake ,uhule ngati anthu woyimbawa momwe timamvera iyeyu ayi ndithu ,ndimamumva kukoma mkati mwangamu koopsya ada awawa

  • @patrickkusailemp3769
    @patrickkusailemp3769 Před 2 měsíci +3

    Munthu wamkulu kwambiri , A bwana ozichepesa kwambiri . Inuyo big ,God bless you .

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Před 2 měsíci +6

    kuphudzitsa Ana mopereka chidwi kwa anthu omvera ndikutha kuona kuti palibe mphwepwa mwa Ana onse

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Před 2 měsíci +2

    Ulemu wanu Mr billy ndimakunyadirani kwambir ❤❤❤

  • @JimmyChiwaya
    @JimmyChiwaya Před 2 dny

    I like Billy Kaunda mainly the number NALIYERA

  • @ZapadzanaMuzik
    @ZapadzanaMuzik Před 2 měsíci

    I thank God I was part of your generation as well as your music, we are blessed by your art

  • @user-dd1qq5xq1k
    @user-dd1qq5xq1k Před 2 měsíci +1

    Ndine emweuja,my favorite song

  • @user-yv6ef1bo6c
    @user-yv6ef1bo6c Před 2 měsíci

    BK my legend... We love you honourable here in Zambia. Your music is so classic.

  • @PhilemonChima-jh6eg
    @PhilemonChima-jh6eg Před 2 měsíci +1

    My favorite artist n the role model himself

  • @janetchinga695
    @janetchinga695 Před 2 měsíci

    Opanda mbiri yoipa Billy kaunda pitilizani kukhala munthu wa bwino achimwene ❤❤❤❤❤ from Capetown

  • @richardsolobala7128
    @richardsolobala7128 Před 2 měsíci +1

    Ndiye emwe uja… watching in the States.

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 2 měsíci +1

    Eeee iwe phe ameneyu timadziwa kuti ndinu biggy Inu🔥

  • @starlonJames-qr4xl
    @starlonJames-qr4xl Před 2 měsíci

    onabo bile mkaunda voice very nice ❤❤ Mr. nkhumani

  • @crosbeygondwe5403
    @crosbeygondwe5403 Před 2 měsíci +3

    My favourite musician Bill Kaunda

  • @user-oh9gv8kc8l
    @user-oh9gv8kc8l Před 2 měsíci

    The old legend still lives on.

  • @evansevas119
    @evansevas119 Před 2 měsíci

    Munthu wodzichepetsa kwambli ndiyamba kumvela nyimbo za billy kaunda mucha 1999

  • @liftedphiri2735
    @liftedphiri2735 Před 2 měsíci

    Big respect to Billy kaunda 💚🇲🇼💪

  • @user-qw5ub4su4k
    @user-qw5ub4su4k Před 2 měsíci

    A classmate timakunyalani
    May God bless you all the time

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před 2 měsíci +2

    Mwacheza ndi Munthu wa bwino uyu kwambiri

  • @AndersonAnusah
    @AndersonAnusah Před 2 měsíci

    Billy u stil young boy lv ur music

  • @user-vf2fo1mb2c
    @user-vf2fo1mb2c Před 2 měsíci

    Well done Mr BK, we love you more

  • @BNDMalawi
    @BNDMalawi Před 2 měsíci

    Few seconds into the interview and yep. Great voice from the host

  • @jangiya03
    @jangiya03 Před 2 měsíci +2

    Ndangosilila maphudzisidwe a ana ooo God bless you big and humble man

  • @hawardmkandawire673
    @hawardmkandawire673 Před 2 měsíci

    ❤❤❤watching from south Africa sand

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Před 2 měsíci

    Oyimba opanda matukutuku God bless you

  • @alickmsini1931
    @alickmsini1931 Před 2 měsíci

    Ndi big man pophunzitsa Ana ake sukulu

  • @user-po6ir6eh4z
    @user-po6ir6eh4z Před 2 měsíci +1

    Zikomo kwambiri oyimba yemwe sanavekepo ndi nkhani zanyasi ndi Billy kaunda ndipo ndioyimba okhazikira pa luso lake timakunyadirani malume k

  • @petermsamariamapira8933
    @petermsamariamapira8933 Před 2 měsíci +2

    Munthu odekha ndi dzeru zache ,I really like him, with his songs too

  • @powercharios2087
    @powercharios2087 Před 2 měsíci

    I like your songs MR

  • @AndsonKadelu
    @AndsonKadelu Před 2 měsíci

    I like that guy so much

  • @samuelsergio5343
    @samuelsergio5343 Před 2 měsíci

    Ulemu wanu Mr presidente 🙏🙏🙏🙏

  • @FrankNyoni-pm3jz
    @FrankNyoni-pm3jz Před 2 měsíci

    THIS MAN IS CALM.

  • @user-tg7ls4vw9p
    @user-tg7ls4vw9p Před 2 měsíci

    Very inspired ❤

  • @wisdomsadyalunda2001
    @wisdomsadyalunda2001 Před 2 měsíci

    Cool man yoh ilove the personality

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w Před 2 měsíci

    Mawu a billy kaunda takumbuka amalawitonse

  • @EstherKaunda-sc3ff
    @EstherKaunda-sc3ff Před 2 měsíci

    Bless you Bro

  • @ronniemwanza9835
    @ronniemwanza9835 Před 2 měsíci

    Very humble man ❤

  • @childofgod6123
    @childofgod6123 Před 2 měsíci

    Our new MP

  • @Maponda123
    @Maponda123 Před 2 měsíci

    I remeimber when I was a kid pa chiwembe

  • @samuelchilubachisalajr7221
    @samuelchilubachisalajr7221 Před 2 měsíci

    The best

  • @rexnyalugwe4910
    @rexnyalugwe4910 Před 2 měsíci

    A humble Man

  • @samuelchilubachisalajr7221
    @samuelchilubachisalajr7221 Před 2 měsíci

    Legend

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d Před 2 měsíci

    Ati ku ndale sikoti kuli ndalama zoti ukhoza kuphunzisila ana aaaah ndie kuti zimveke bwanji? Iweyo billy anthu ambili amakuziwila mu music and umaimba bwino and kuimba uku kunapeleka chidwi kwa anthu ovutika kukuika mu m'boma ndi maganizo oti ukhoza kusintha ziko, koma anakaziwa kuti umapanga za moyo wake ndi family koma pa chilungamo ndiwe munthu oipisisa kwambili pa ndale ziko lako sumalikonda wadyela sangatukule ziko.

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 2 měsíci +1

    Aaaa nde kachepatu ka inteviewko

  • @bennytembo200
    @bennytembo200 Před 12 dny

    How can i access the book "Hills and Valleys"'?

  • @HassanJamesonni
    @HassanJamesonni Před 2 měsíci

    Uli boh bily

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Před 2 měsíci

    Humble mn ❤❤❤❤❤

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Před 2 měsíci

    Abily timakunyadirani mwasinthisa zambiri mziko muno

  • @user-xv5pr3ji6w
    @user-xv5pr3ji6w Před 2 měsíci

    Ndi oimba yemwe sayangana pansi pa nyimbo zake ,.. amatha

  • @pheterachirwa5560
    @pheterachirwa5560 Před 2 měsíci +1

    Amandidalisa kwambili wakwanthu kupoto ndine symon phetera munthu imozi amandisangalatsa

  • @benmunana5556
    @benmunana5556 Před 2 měsíci

    Ahhhh mwakafupikisatu abale

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 2 měsíci

    Cool man

  • @ZabulaServices-zh2vi
    @ZabulaServices-zh2vi Před 2 měsíci

    Awawa kungowataya basi palibe angamasule zingwe Nsapato zawo

  • @wonderfulmkhutche5422
    @wonderfulmkhutche5422 Před 2 měsíci

    Nice 🔥

  • @kingdavidmhango9511
    @kingdavidmhango9511 Před 2 měsíci

    Timati Mzimba osati Nzimba😮

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 Před 2 měsíci

    Humble man

  • @samuelchilubachisalajr7221
    @samuelchilubachisalajr7221 Před 2 měsíci

    My man.

  • @KingMasamba-iz2mj
    @KingMasamba-iz2mj Před 2 měsíci

    Zazelu basi

  • @MtenjeHassan
    @MtenjeHassan Před 2 měsíci

    50+ koma looking fresh...

  • @WisdomBanda-lu4vm
    @WisdomBanda-lu4vm Před 2 měsíci

    Wa akulu tsopano timakunyadirani mumatha.

  • @samuelchilubachisalajr7221
    @samuelchilubachisalajr7221 Před 2 měsíci

    Master

  • @bobchizaula
    @bobchizaula Před 2 měsíci

    mwimbanga makola akulu tingateta yayi

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 2 měsíci

    Ana sachuluka man🔥

  • @geofreyzulu6025
    @geofreyzulu6025 Před 2 měsíci +1

    It is his music career not carrier.

  • @user-nt4fr2le3f
    @user-nt4fr2le3f Před 2 měsíci

    Komatud makolo anu anabeleka mpaka ana 11,,ayi ntchito anaigwira

  • @listonnantapo1670
    @listonnantapo1670 Před 2 měsíci

    Nthawi inachepa koma.

  • @RodgersmungatiMoyo
    @RodgersmungatiMoyo Před 2 měsíci

    Munthu ozichepesa kwambiri komaso wanzelu

  • @masakaunga4099
    @masakaunga4099 Před 2 měsíci

    Oh koma wabeleka

  • @DeffinateKim
    @DeffinateKim Před měsícem

    Sikefa chimoto

  • @George-zd5le
    @George-zd5le Před 2 měsíci

    Billy uli ndi Ana 7 ine ndiri ndi 8 ndichitsomo cha namalenga

  • @user-nq2pm3wz9r
    @user-nq2pm3wz9r Před 2 měsíci

    In politics ku Blantyre palibe chomwe tingaloze chomwe amapanga chothandiza

    • @user-jk8sh7fh2d
      @user-jk8sh7fh2d Před 2 měsíci

      Ndietu ukayankhula amati ndiwe wa nsanje aaah zichani umakhala umakhala kuti pena ukunena chilungamo. Uyu anthu samamuziwa bwino bwino coz sanakhale nae , amamuziwila mu nyimbo and kwa ine ku nyimbo amaimba bwino mumakhala nfundo , koma kumuonesesa amapanga za family not ziko ndi munthu oipa kwambili

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 2 měsíci

    Kwabac

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 2 měsíci +1

    Koma nde unasosolatu man, ana 7 alone?, kkkkkkk

    • @geraldmtika7961
      @geraldmtika7961 Před 2 měsíci

      Amavuta kuphunzira ndi kulela osati kubeleka kkk