COMRADE NTANYIWA CHIGAWO 6June24 KUNALI ZOKAMBILANA USIKU KU STATE HOUSE NKHANI YOWATETEZA A KALUMO

Sdílet
Vložit

Komentáře • 49

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt Před měsícem +2

    Limpopo fm mukudziwa kuti MDF imafuna kulanda dziko? Koma Achakwera atamva zimenezi mwezi wangothawu private soldier aliyense kupita mmwamba alandilatu ku account yawo aliyense Mk 1000000 cholinga choti asalande dziko ndinkona mukuona a MDF officers akupezeka ku state house ndati mudziwe zimenezo a Limpipo fm

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 Před měsícem +1

    Nick Chakwera akupita ku RSA kukawona Truck yomwe a MCP anagula yopangila kampeni ndipo ikusungidwa ku Kempton Park. Truck imeneyi ili ndima Amplifiers 30. Zambiri tikuwuzani

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Před měsícem +2

    This is why malawi is disclosed as a failed state becoz of the way how this boma is supporting anthu olephera no wonder kuti izi zikuchitika chifukwa ali pa tsogolo la anthu olephera ndi president, a malawi tikusogoleledwa ndi wa nkhungu.

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Před měsícem +1

    Powerful!!!!! 💪

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Před měsícem +1

    Chakwera mzeru za yekha,adaloweka nsima m'madzi

  • @TreverDominic
    @TreverDominic Před měsícem

    Yomweyo big man comrade Ntanyiwa ulemu wanu

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před měsícem +1

    Chuma chochionela kuukulu kkkkk. Mr ntanyiwa kkkkkk mumaziwa kuyankhula nanga chimwendo Banda waziwika liti kwao ku dowa nyumba za mauzu zokhazo muzi wonse nyumba za mauzu ....lelo wapenga ndi ndalama zokuba ....achimwendo ndalama zimene zikuoangisa kuti muzilalatazo ndizakuba .....kumbukilani mmawa

  • @user-ti2ct8ts8d
    @user-ti2ct8ts8d Před měsícem +1

    Chimwendo milomo Ngati kwankhuba

  • @John-to8gl
    @John-to8gl Před měsícem

    Mtanyiwa is Mtanyiwa more fire 🔥

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu Před 9 dny

    Mulungu azikutetezera comrade mtanyiwa

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw Před měsícem

    Oh no musamasowe pliz welcome back tinakusowani

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před měsícem +1

    Koma zilipo Limpopo woyeee

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Před měsícem

    Big up brother man!!

  • @CharlesmakveliNyirenda
    @CharlesmakveliNyirenda Před měsícem

    Comered ntanyiwa moto kt buuuu 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson Před měsícem

    Kkkkkkk Mr mtanyiwa congratulations 🎉🎉🎉🎉

  • @LamieTiger
    @LamieTiger Před měsícem +1

    Awombeledwe ma guy

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp Před 8 dny

    Amtanyiwa musamasowe

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu Před 8 dny

    Ine ndikungomva tseketseke ndikamamva mawu amtanyiwa mwamva inu

  • @CaptainNyenga
    @CaptainNyenga Před měsícem

    Ana achepa awa comrade akulira ndi nkodzo wawo palibe chinsisi pa dzikoli

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před měsícem

    Good message

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před měsícem

    Mmmmm koma kuwadyera anthu wosauka kulakwa tu kumeneku Mulungu chonde tichitireni chifundo

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g Před měsícem

    Big up big

  • @MadalitsoGeorge
    @MadalitsoGeorge Před měsícem

    Mmm abale Malawi ndi amalawi akupita kut pot Bagamoyo akuoneka kut wachepa sangapange accommodate all Malawians and its mother Malawi

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před měsícem +1

    Nyini yake monica chakwera

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před měsícem

    Ndiye aliyese amene anapangitsa ma passport mu boma la MCP apite akabweze akatenge ndarama zawo chakwera ndi gulu lake ndi mbamva ya president Yopanda chisoni ndi anthu

  • @LethubuhleSibanda-ed8oi
    @LethubuhleSibanda-ed8oi Před měsícem

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Před měsícem

    More fire 🔥 ❤❤❤❤

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před měsícem

    Bwana Ntanyiwa amenewo mumakwana kwambili

  • @user-sb4om5pw2h
    @user-sb4om5pw2h Před měsícem

    Mupwetekana ndithu

  • @NahwaalPalmer
    @NahwaalPalmer Před měsícem

    Good news

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa Před měsícem +1

    Kkkk

  • @dhis2iom109
    @dhis2iom109 Před měsícem

    Malawi wanga watani?

  • @AnnoyedCheeseBoard-sm5nn
    @AnnoyedCheeseBoard-sm5nn Před měsícem

    Anthuwa akungofunika kuwachosa by impeachment

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga Před měsícem

    💪💪💪💪

  • @user-bg9hx7lb8q
    @user-bg9hx7lb8q Před měsícem

    Comrade mntanyiwa sopano 😂😂😂😂

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa Před měsícem

    Chimwendo ndi mbuzi waphula njwerwa za moto nthawi yaitali makobiri owapeza okula kula masikini wachabe chabe

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Před měsícem

    Malawi 🇱🇾sachosoni🤔

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před měsícem

    Komatu mbwiyanga chakwerayi sakuphani mbwiyanga ......Boma lankhanza

  • @user-wl4nd7ic1s
    @user-wl4nd7ic1s Před měsícem

    Koma zilikotuhhh!!

  • @user-ky2fs3zr8y
    @user-ky2fs3zr8y Před měsícem

    Ife kumtima mbeeeeeeeee

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l Před měsícem

    Chimwendo azafa ngat galu azisamala kuchikamwa

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Před měsícem

    Amalawi zofuna izii tiona zinthu

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e Před měsícem

    KkkkkkkMpaka Nyawu?

  • @user-ti8ds7iq8z
    @user-ti8ds7iq8z Před měsícem

    Malawi Watani mpaka fake passport

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence Před měsícem

    Wakupha chakwela

  • @SameKaposa
    @SameKaposa Před měsícem

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Mcp vs afford ntchito ilipo

  • @YamikaniKaliyati
    @YamikaniKaliyati Před měsícem

    😂😂😂😂

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před měsícem

    Komatu mbwiyanga chakwerayi sakuphani mbwiyanga ......Boma lankhanza