Kalindo is trying his best,chikufunika osusa agwirane manja!,ku UTM apereke mpata kapena position imene Mary chilima angatenge icho chiperekeranso mphanvu ina yapadera muchipani.
Mayi chilima to be president, braund banda,mwana wachilima awa kaliyati, awa musankhemo mumozi ankhale president mwana wa chilima anyamata ose ankhala ndi chidwi
What if mrs Chilima is not a politician? Komanso akuti anthu azilowa kuchipinda ndi candle nkumakatchula dzina la Chilima kodi Chilimayo wasandukano mulungu?
Koma Mai kaliyati ndi kagulu kanu choonde nvelani kulira kwa anthu ngati ku UTM kuli anthu olimba nde ndinuyo mumakhala chifupi ndi Chilima musakomedwe ndi ndalama mukwiitsa anthu ochuluka nthawi yatha kale iyi musanvere MCP kukunyengeleleni ndi ndalama misozi ili manso ndithu mutenga tsoka
Brayani Banda ndimunthu wa chikondi ndi ziko Lake mayi cilima tiwona ngati chilimayo alipo anthu tivota ambiri mwana wachilima anakonda achinyamata ndiye achinyamata ose ali ndi ife
Bon kalindo amalankhula zoona zokhazokha koma anthufe timangoti ndi wama comedy let's support him as malawians
Ati amakutengan ngat manyi😂😂😂😂 chi booooniiiiii kalindoooo
Thanks sir for ur update
Kuyankhula mopanda mantha ngati wakhalira mfuti Bon kalindo 😮😮
Ndpo inu
Your the best the DC bon kalindo❤
Wamisala anaona nkhondo,,lero Bon kalindo mukumuyamikila koma mmene munkamunyozela siizi😂😂😂😂
Kalindo amatha kwambili❤
Uyu ndiye activits yemwe timamudziwa, Bon kalindooooooo!! Mwana owopsa kwambiri.
Good advice sir.
Always your the best all the time mr president Bonie Kalindo
Yomweyo fadaa🎉
Uyu ndiye ❤
God bless you Kalindo
Umakwana
I love you so much
🎉🎉🎉 following
Born kalindo🔥🔥🔥🎷🎷
Utm siingatuluke mugwilizano ngakhaleso atatuluka palibe chazelu chomwe angapeze
Good advise Mr born kalindo thank you 😅
Salute
Good advice
Komatu bon kalindo amayakhula ngati wamisa koma ndizoonadi zimene amayakhula anhtu inu muzichenjera
Kulankhula mwachilungamo. UTM tsegulani maso. Tulukani mu tonse alliance monga akunenela Bon Kalindo please.
A MCP asakupusitseni ife tili mbali yanu ndi SKC osaopa, osatopa, osafooka 💪
Mr Kalindo mukutitsegula mmaso kwabasi keep it up
U always stand in true mr Bon l love u more than
The DC🔥🔥🔥
Chilungamo chimamasula go ahead the DC
The DC mwana ohopya kwambili
Zikomo bwana DC UTM yitulukedi kumeneko iyime pa yokha basi
Mumaitha bwana d c ndi more pachilungamo😊
The DC
True
Bwana DC mumatiimilira
Kalindo is trying his best,chikufunika osusa agwirane manja!,ku UTM apereke mpata kapena position imene Mary chilima angatenge icho chiperekeranso mphanvu ina yapadera muchipani.
Like this guy or not , but he is very sharp
Big up to you 🎉🎉🎉🎉🎉 umatha kung'alura
Kalindo amalankhula zoona uyu ndi mpulutsi.
Umaitha bon
Bon kalindo akunena zowona lelo muchoke ku mcp mukapitiliza ndiye kuti mukusangalala ndi ife ya chilima chipani chimene chingawine ndi UTM kampeni wake zikolose lapasi lipanga saport
Khan nd yoona
President wathu wathu,Mr Kalindo lero ndilomwe tidziwedi kuti UTM ipitilira ndipo SKC waphera chilungamo.
Mbambande Bon Kalindo
Mr DC 2025 woyyeee.
Mumatiimilira a bon
Kmat uyu tiyen Tzimuvela zimene amayankhulaz
Mayi chilima to be president, braund banda,mwana wachilima awa kaliyati, awa musankhemo mumozi ankhale president mwana wa chilima anyamata ose ankhala ndi chidwi
Tiyeni tiyeni tiyeni Mr DC
❤❤❤❤❤❤❤
President wathu Mr DC
My vote kalindo umatha umatiimirila
Bon kalindo umakamba zoona
Na pa Bone Kalindo palibeso same same Mtanyiwa anthu awa amanena chilungamo chokhachokha
What if mrs Chilima is not a politician? Komanso akuti anthu azilowa kuchipinda ndi candle nkumakatchula dzina la Chilima kodi Chilimayo wasandukano mulungu?
kalindo umakwana ase
It's true bwana president woyamba wa anthu osauka muno Malawi
😹😹😹 iwe umakwana aaa nilinje mau
Powerful spetch
Chilungamo ndimwano❤ The DC pick up man
the dc
In short Utm ibwerere ku DDP....tigwetse vinyau tikinze dziko
Sanena boza uyu
Musapusisidwe a utm mcp sichipani .muzifunse kuti kodi chilima chamupha ndichani kodi mukugona a utm, tsegulani mumaso
Umakwana winiko
A UTM uthenga ndiumeneo zili ndiinu kunyalanyaza kapena kutengapo kanthu km mawa pangatalike muzawakumbukira mau a Bon sadutsa pachabe
DC Huma kwana
A UTM mukapanda unvera za bon kalindo muzalira moyo wanu onse
THE DC PANGOLINI 💪💪💪💪💪
Big up de DC our pool p
Kalindo more 🔥 ❤
Tidziwe basi.
Ma traitor tiwadziwa lero
Wise man
Nice
Koma Mai kaliyati ndi kagulu kanu choonde nvelani kulira kwa anthu ngati ku UTM kuli anthu olimba nde ndinuyo mumakhala chifupi ndi Chilima musakomedwe ndi ndalama mukwiitsa anthu ochuluka nthawi yatha kale iyi musanvere MCP kukunyengeleleni ndi ndalama misozi ili manso ndithu mutenga tsoka
Zoona mb'ale
The DC kkkk konda u ife
Ndipo a mcp ndi athu ochenjela ndi kuipa komwe ndipo chilima amusasa lelo akuyanja otsalao mukapusa akumezani
Our freedom fighter ndiwe kawawa ndithu
The DC ,lankhula chilungamo bas
Kalindo good advice
The DC mwana oopsa kwambiri satekeseka ndi Uniform ya a police,ingankhale Unyolo. Tell them 😅😅😅😅
Very true
The Dc bon kalindo 🎉🎉🎉
Usazafe kalindo uzangotsowa ngati eliya
Tikumupemphani a Born kalindo bwelelani ku UTM please
Ndipo president akakhale iyeyu ndimunthu wamaso mphenya❤❤we love him❤
Good Good news
🎉More fire!!!!!!!!!!!
Ah b
boooooon kalindo!
Mumatha
The Dc bon kalindo ❤
The DC mulomwe wathuwathu odziwa zinsinsi
Brayani Banda ndimunthu wa chikondi ndi ziko Lake mayi cilima tiwona ngati chilimayo alipo anthu tivota ambiri mwana wachilima anakonda achinyamata ndiye achinyamata ose ali ndi ife
The DC agogo anga akufuna azakuoneni
Amakwana koma ❤
Makwana mr keep it up
The problem is anthu akumudz unthengawu suwapeza cz of social media
Mzimu wa bwana Chilima uwavuta.mukaone maruwa ngati akukanika kufa .musamale kwambilitu.
My vote umakwana
Za manganya ku mcp palibe chimene mukunena akalindo
Koma manganya asamuwelengele ndiwa MCP kuyambila kale
The Dc mawu ako a koma akagonela
Kaya tidzasegula liti maso, kumva ndiye tikumva ndipo tikuziona🤭