Boma lakuba layamba kuopseza; Akugwiritsa ntchito apolisi pobisa chilungamo.

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 28. 10. 2023

Komentáře • 339

  • @ziyaya_snr
    @ziyaya_snr Před 9 měsíci +71

    If the government arrest this guy, the Whole Malawi will undertake and action. Who agree with me?

    • @user-rl6sj4bp9p
      @user-rl6sj4bp9p Před 9 měsíci

      Where iwe Uli Phee Ku south Africa

    • @ShayibuJames
      @ShayibuJames Před 9 měsíci +3

      Tikuyenera kupanga chinachake chokozekera ifeyo tili kumalawi konkuno tikuona mavuto akulu akulu

    • @ShayibuJames
      @ShayibuJames Před 9 měsíci +4

      Tikuyenera kukhazikitsa chitsogolo chabwino izizi zatopetsa

    • @erickhowoya9894
      @erickhowoya9894 Před 9 měsíci +2

      Very true

    • @ishakatimbe7341
      @ishakatimbe7341 Před 9 měsíci +2

      I pray for you big asazakupezen

  • @user-ky1sn4uv9z
    @user-ky1sn4uv9z Před 9 měsíci +13

    Simugwidwa olo ataphenga IN SHA ALLAH mulungu akutetezerani ndithu

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Před 9 měsíci +11

    Big love brother May almighty Allah bless ❤

  • @elizamaster2168
    @elizamaster2168 Před 9 měsíci +8

    Boma ili likudana nd chlungamo, pazonse zomwe akupanga , akuyiwala kt kunjakuno kili mulungu amene amawona, brother pitilizan kuyima pachlungamo ndpo mulungu azikutetezelan palipose pamene mungayende mulungu alinanu limodz🙏❤

  • @premagswp0042
    @premagswp0042 Před 9 měsíci +7

    You're the voice of the voiceless Brother!
    May God of hope feel you with more life and blessings because you're fighting for us!
    On another way,we as Malawians we're not united as the way how other countries do.
    So mine is a request to all my fellow Malawians that let's unite and make one Malawi and fight for Malawi so that we can ease ourselves and our descendants from this burden!
    Let's develop a new type of life of fighting for our country not just stay and see corruption being done in our Country!
    The main reason is that TIMAKHALA NDI MANTHA POKUFUNA KUCHITA ZINTHU CHIFUKWA TIMANGOTI WE CAN'T PROTEST AGAINST THE GOVT KOMANSO TILINDI MOYO OSIYILANA ZINTHU!
    Ngati spirit iyi ipitilire Malawi sazatukuka!

  • @erickhowoya9894
    @erickhowoya9894 Před 9 měsíci +8

    Inu ndi big. Started following you the very first day you created this channel. Always eager for the next talk

  • @khalidwetchaua24
    @khalidwetchaua24 Před 9 měsíci +4

    Kkkkk good job Bro

  • @phillimonkhamna
    @phillimonkhamna Před 9 měsíci +6

    😂😂😂😂😂 lelotu mwalusa kwambiri

  • @professorsafuta3936
    @professorsafuta3936 Před 9 měsíci +8

    You're always wonderful and great man

  • @johnkatapeh7182
    @johnkatapeh7182 Před 9 měsíci +4

    Thanks bro, God bless you

  • @Yomweijah
    @Yomweijah Před 9 měsíci +5

    A malawi tiyeni tipangeko kathu tisasiyire muthu modzi ichi ndichilungamo tiyen i tirole chiyende ngati madzi ukatero mulungu adzakumenyera khondo

  • @user-og2qx4cq7v
    @user-og2qx4cq7v Před 9 měsíci +3

    Tell them Dr kakuba ameneyo setezake

  • @user-oy2bu8vm4t
    @user-oy2bu8vm4t Před 9 měsíci +6

    Keep up the good work sir,we are proud of you

  • @ruzuwanmoyenda23
    @ruzuwanmoyenda23 Před 9 měsíci +3

    Lero mwakwiyatu bosss😂😂

  • @user-ub1mw7ce5p
    @user-ub1mw7ce5p Před 9 měsíci +12

    Chakwera must be arrested for killing Malawians through lies. And very surprising that the opposition parties are still sleeping. Shame on you opposition sides who know how to make impossible and useless promises in rallies but do not know how to do your job. STRONG MESSAGES TO YOU OPPOSITION PARTIES: Silence does not solve problems but it sells out. Please try to serve your people not only your families because it is people who put you into that positions you are proud of.

  • @abdulaziziislaj2416
    @abdulaziziislaj2416 Před 9 měsíci +6

    Love you bakili muluzi Chanel umatiziwitsa zobisika menemomo❤zambili timaziwa ndi inuyo abambo great job bro.

  • @user-mp7nu4oz9c
    @user-mp7nu4oz9c Před 9 měsíci +2

    Man osaopa continue giving the truth, Pompano tikhala tikukakavota nthawi yake yatha remember next year ndi kampeni don't worry Man well are following you

  • @raffickaffick
    @raffickaffick Před 9 měsíci +12

    on repeat, boss man is here, only VOICE OF A KING IN MALAWI

  • @user-nn9mx5tt6d
    @user-nn9mx5tt6d Před 9 měsíci +3

    My Allah protecte you and bless you

  • @johnsemani7142
    @johnsemani7142 Před 9 měsíci +9

    You are my voice keep it up chilungamo kuwawa 🎉

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 Před 9 měsíci +12

    DO NOT FEAR SPEAK THE TRUTH THE TRUTH WILL SENT YOU FREE

  • @ZONKEMASEKO-rm5fn
    @ZONKEMASEKO-rm5fn Před 9 měsíci +6

    Big up bro. Never give up

  • @CHINDEBVU
    @CHINDEBVU Před 9 měsíci +10

    Let's hope you must be safe my Journalists

  • @kantionsankhulani
    @kantionsankhulani Před 9 měsíci +7

    inu ndakatundu timakudyalani kwambili ❤❤

  • @MuhaKShaibu
    @MuhaKShaibu Před 9 měsíci +3

    Anthu oipa amenewa ..big up boss Man .I was not happy when someone told mi about u kut mwamangidwa

  • @user-zx1zs8el7q
    @user-zx1zs8el7q Před 9 měsíci

    Palibe zoopsezana ndikumangidwa apa,, chilungamo chiyende ngat madzi,,,ngati akufuna kumanga akamange Chakwera chifukwa walephela kupanga zomwe analonjeza
    Brother osachita mantha💪💪💪nenani chilichonse mosawopa munthu
    Chakwera ndimbuzi kwambili

  • @wilsonsawasawa3794
    @wilsonsawasawa3794 Před 9 měsíci +2

    You are number one!

  • @VioletChikopa-mx1ye
    @VioletChikopa-mx1ye Před 9 měsíci +3

    Kkkkkkk Koma apolisi matama😂😂😂😂😂😂😂

  • @user-ti2ct8ts8d
    @user-ti2ct8ts8d Před 9 měsíci +4

    More fire,ayerekeze kukumangani atiputa Ife amalawi tonse.a fisi amenewa atikwana kwambiri tikuzunzika

  • @user-vd3xy1eb2h
    @user-vd3xy1eb2h Před 9 měsíci +3

    Chakwera ndi satana Mulungu amulange

  • @christophermkhize1991
    @christophermkhize1991 Před 9 měsíci +2

    Our brother we play for you may Allah protect you komanso ndizowona big enawo sakwiya koma tambala wakuda sadzasinthanso basi mcp ndichipani chakupha basi anthu akufa m'midzimu ndinjala chifukwa cha kuyipa ntima kwa chakwela

  • @owenskabazanechiumia3543
    @owenskabazanechiumia3543 Před 9 měsíci

    Ku Malawi pakali pano kulibe Ufulu, tabweleranso mu one party system of government, timakunyadilani Brother you are true freedom fighter Almighty bless you.

  • @user-dj5hd4ys3n
    @user-dj5hd4ys3n Před 9 měsíci +2

    Kkkkkk koma nde watopatu dolo wapsa mtima umakwana

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Před 9 měsíci +1

    Proud of you Boss Man, may God bless and protect you always

  • @sulemanimatumula194
    @sulemanimatumula194 Před 9 měsíci +4

    May Allah protect you brother

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Před 9 měsíci +2

    Zoona brother chakwera watikwana chilungamo chioneka paifa yawitika

  • @SamuelNandolo-nc2mo
    @SamuelNandolo-nc2mo Před 9 měsíci +2

    Salute brother

  • @user-er1qs3zx7x
    @user-er1qs3zx7x Před 9 měsíci +2

    Am proud of u bro keep it up

  • @MwenyeCheNsoma-gb2yz
    @MwenyeCheNsoma-gb2yz Před 9 měsíci +3

    Hope Mr. Chakwera is listening to this golden voice. Munthuyu tu ndiwamisala amene anawona nkhondo

  • @allanimindozo9937
    @allanimindozo9937 Před 9 měsíci +2

    True fighter love you bro

  • @fae6833
    @fae6833 Před 9 měsíci +2

    More fire bro Apolice matama.

  • @AuffiPillo-cf9rn
    @AuffiPillo-cf9rn Před 9 měsíci +3

    Bwana osanyumwa tili pambuyo pano ❤

  • @ickbwoy6123
    @ickbwoy6123 Před 9 měsíci +1

    big up boss mn tilipambuyopo

  • @margetjustin7170
    @margetjustin7170 Před 9 měsíci +2

    Mmmm zomvesa chisoni boma lankhanza

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 Před 9 měsíci +1

    Thanks again big man

  • @chipiliromalola6380
    @chipiliromalola6380 Před 9 měsíci +2

    Always reality brother

  • @StevenAjusugama
    @StevenAjusugama Před 9 měsíci +1

    Keep it up more videos

  • @KENETHMAJASA-ud5ee
    @KENETHMAJASA-ud5ee Před 9 měsíci +2

    You really stand for us

  • @ishmaelmkuluma2013
    @ishmaelmkuluma2013 Před 9 měsíci +4

    ❤Ndikhale oyamba ine kupeleka comment boss tinakusowani kkkk inuo tikukupephelelan Inshaallah mutetezedwa

    • @user-hy5fm1ph7f
      @user-hy5fm1ph7f Před 9 měsíci +1

      Nanga simukunena kuphedwa kwa a stambuli u don't talk for that matafari Ana akupoly simukunena bwanji

  • @farookousmane715
    @farookousmane715 Před 9 měsíci +2

    Long live Bakili Muluzi TV.

  • @giftrichard8562
    @giftrichard8562 Před 7 měsíci

    Your true story my brother go ahead lonjezo linadulitsa mutu wayohane pazimene analonjoza chakwera zilibe thandauzo kwammalawi.

  • @HajimaKhalid1714
    @HajimaKhalid1714 Před 9 měsíci +1

    May Almighty Allah bless you abundantly

  • @juniortsegula3847
    @juniortsegula3847 Před 9 měsíci +2

    Mumatha boss man. we are with u

  • @CharlesEliyas-do1ec
    @CharlesEliyas-do1ec Před 9 měsíci +2

    ❤❤❤ number one boss

  • @DicksonBlack
    @DicksonBlack Před 9 měsíci +3

    Ulemu wanu bigger ❤🎉

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 9 měsíci

    O yes wafika bro wanga

  • @sharlifcassim6591
    @sharlifcassim6591 Před 9 měsíci +2

    Tili kumbuyo kwanu big boss and we will not allow the government to arrest you tiyeni amalawi tipitirize kumufunira ntchito yabwino munthu ameneyu

  • @Yabwata
    @Yabwata Před 9 měsíci

    So touching, this bakili muluzi channel is the best amd truth, tell them the truth, .. chiuta wamudangilileni akulu , ivo mukuyooya nivakusekeska yayi kwe nivachitima according ivo wakuchita wa mcp . 😢 wathu wakukavuka dele dele kumalawi uko , njala , ifa daily. Shameful..

  • @Shaabann
    @Shaabann Před 9 měsíci +3

    Ulemu wanu big man timakunyadilani kwambiri

  • @StevenAjusugama
    @StevenAjusugama Před 9 měsíci +1

    Wel done tell them one is one

  • @ibrahimjackson-cg6tc
    @ibrahimjackson-cg6tc Před 9 měsíci

    Big inshAllah inuyo Allah akutetezeni basi timakukondani

  • @rechealbracia-vk7np
    @rechealbracia-vk7np Před 9 měsíci +2

    Mulungu apitilize kukudalisani big man

  • @mikechapondapo1213
    @mikechapondapo1213 Před 9 měsíci

    Umandisangalatsa ase may God protect you

  • @ThokoMaggie
    @ThokoMaggie Před 17 dny

    It's my prayer kuti peter azawine mu 2025 adzakupatsen something for this job

  • @MuhaKShaibu
    @MuhaKShaibu Před 9 měsíci +2

    Koma l think do not say that .some gyz a m 'boma mu akukuuzan zambir za ma gyz WA ...coz zitha kuwapanga impower , and anthu omwe akukuuzaniwo anthu kunkhala ndi Mantha ndiye aziwopa kukuuzan zambir

  • @chippiephiri4505
    @chippiephiri4505 Před 9 měsíci +1

    Osaopa bro

  • @sugarboynine9270
    @sugarboynine9270 Před 9 měsíci

    Watching from rsa ❤

  • @lusolawo73
    @lusolawo73 Před 9 měsíci +1

    Big man ndinu 1

  • @IbrahimMatias-te1kc
    @IbrahimMatias-te1kc Před 9 měsíci +1

    My Allah bless you

  • @Goliath461
    @Goliath461 Před 9 měsíci +2

    Abwana chilima pamenepajatu anapepera akanaziwa sakadamuthandiza gwape ameneyu

  • @sebi2439
    @sebi2439 Před 9 měsíci +1

    😂😂😂 I love this guy

  • @StevenAjusugama
    @StevenAjusugama Před 9 měsíci +2

    Nthawi yomwe Chilima akanaima ndi ino

  • @Innoh_1979
    @Innoh_1979 Před 9 měsíci +1

    This guy doesn't deserve arrest

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 9 měsíci +1

    We have been waiting for this video

  • @blessingsmasakala3285
    @blessingsmasakala3285 Před 9 měsíci +1

    Koma mwana iwe umatha kuyankhula chokhacho bas timakukondela kupanda kumva zaiwe timadwala ndithu 😆😆😆🤣🤣🤣

  • @Maklanalfredo
    @Maklanalfredo Před 9 měsíci

    Waitha and i have strong massage for you *please don't fear nobody* stand on justice and Almighty God 🙏 always with you

  • @joekawenga3163
    @joekawenga3163 Před 9 měsíci +2

    Big man wathu tsopano.

  • @user-ki4bl9mm1h
    @user-ki4bl9mm1h Před 9 měsíci

    You are the voice of the voiceless malawians. Ndipo chakwela mliska pooo! Aaaa that's why I don't trust these so-called pastor 😒

  • @HopeChembe-lx1wm
    @HopeChembe-lx1wm Před 9 měsíci +1

    Never give up bro

  • @loxydickson5045
    @loxydickson5045 Před 9 měsíci

    Love u brother man

  • @user-dk6yc8pl2m
    @user-dk6yc8pl2m Před 9 měsíci +1

    Timakunyadlan bwana ana achepa

  • @mastermateyo9533
    @mastermateyo9533 Před 9 měsíci

    Great voice and well said

  • @HycithMakina
    @HycithMakina Před 9 měsíci

    Ee koma wakwiya muthuyi kopsa koma umakwana bro 🔥 🔥 🔥 🔥

  • @harrykhomera-qq6ww
    @harrykhomera-qq6ww Před 9 měsíci +1

    My Malawi shaaaaa !!! Pali nkhani apa

  • @user-su2uz4yu4j
    @user-su2uz4yu4j Před 9 měsíci +4

    Zoonad mumanena chilungamo osaopa 🇲🇼🇲🇼

  • @Hendersonspoon
    @Hendersonspoon Před 9 měsíci

    You are doing great job man

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Před 9 měsíci +1

    🔥🔥🔥Respect you boss..

  • @kassimumar6421
    @kassimumar6421 Před 9 měsíci

    I wish you should've teach me and if they arresting you as they looking for you this channel should continue to tipitirire kuwayalusa mbava za anthu
    Ulemu wanu boss

  • @petertukula1649
    @petertukula1649 Před 9 měsíci +1

    need to support you bro know that tili pambuyo pako

  • @user-bx8qr9lt2n
    @user-bx8qr9lt2n Před 9 měsíci

    Watching from Chipata Eastern province republic of Zambia

  • @adamdiverster6127
    @adamdiverster6127 Před 9 měsíci

    Your the pearls of Malawi

  • @tonemuyaya6284
    @tonemuyaya6284 Před 9 měsíci +1

    Matama bwno mn😂😂😂😂😂

  • @patiencetchapo803
    @patiencetchapo803 Před 9 měsíci

    Voice of my boss

  • @user-ye3uu1jd7r
    @user-ye3uu1jd7r Před 9 měsíci

    Go deep brother

  • @user-dl8yg8cj8z
    @user-dl8yg8cj8z Před 9 měsíci

    I love bakiri muluzi tv

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w Před 9 měsíci +2

    Guys let's protect this man

  • @OMARISHUAskimu-hd3zd
    @OMARISHUAskimu-hd3zd Před 9 měsíci +1

    Ife tinakhulupilira zoti mwamangidwa

  • @ekarimanyalo5234
    @ekarimanyalo5234 Před 9 měsíci +1

    So emotional. We’re with you bro

  • @Atatere
    @Atatere Před 9 měsíci

    Apa ndiye bigy mwabwera ... mulipo respecct

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 Před 9 měsíci

    Thanks brother