Zomwe Wakamba Lero Bon Kalindo | Nzeru Zilimo Umu

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 2. 07. 2024
  • #malawi #trending #viral

Komentáře • 21

  • @LekkttarKhembo-or1tx
    @LekkttarKhembo-or1tx Před 3 dny +2

    Zoona kalindo awuuze mbuzi za chakwera ife ahlomwe sianthu opusa tu uziona.

  • @shotsfired588
    @shotsfired588 Před 2 dny +2

    Koma amalawi, munapanga ma demo nkhani zazing’ono, mademo mukulephera pano zinthu zitayipiratu. Mwagonanso amalawi, mademo akufunika

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před 3 dny +2

    Zokha tikuchita dziko lamalawi mulungu alekelera'zoon lelo UDF lelo yakhalaso yazelu lelo DPP lelo yakhalaso yazelu chomwe tikufuna amalawi ndichan mfziko mwathu momo ndiuzen

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Před 3 dny +1

    We're behind you the DC

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 Před 3 dny

    The DC mwana owoopsa kwambiri,we are behind you

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx Před 3 dny +1

    Zinthu zake dziko muno nsaname zafika poti munthu ukumazifusa kuti koma anthu opanda ma lawyer fe tili ndikoti tikasume????

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před 3 dny

    Chinthu chikafa ndieno chizikhara chazelu kapena boma likatuluka ndipomwe lizikhara lazelu

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před 3 dny

    Booon kalindo usasochelese amalawi

    • @PempheroMoleni
      @PempheroMoleni Před 2 dny +1

      Kkkkkkkkkkkkk inuyo mukuti Malawi Ali bwino et ????

  • @user-mf5ce9wj4m
    @user-mf5ce9wj4m Před 2 dny

    When This Chakwela is out of power him and his whole cabinet minister they must be arrested and all state money they stolen they must pay back

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před 3 dny

    Iweyo udzafera anako osati amalawi aliyense pano wadziwa kt iweyo ukupanga business pabuyo pamalawi uzisochelesa machota omwewa

  • @berthamigodi6529
    @berthamigodi6529 Před 2 dny

    Vuto takutulukilan kut siinu omenyera ufulu koma cadet wa dpp kkkk vote ndmutima ukunama iwe

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před 3 dny

    Munthuyu kumutengera ndiekut wasatira Misara yake palimbepo chazelu akuuza amalawi

    • @user-bn8ci6vx5c
      @user-bn8ci6vx5c Před 2 dny +1

      Wamisala ndi iweyo ife tiri pa mbuyo pa DC.

    • @ChrifordBiziel
      @ChrifordBiziel Před 2 dny

      Ife palibepo tikuchiwona chovuta inumukudya ndrama zaku opposition ndinu mukunjoya

    • @ChrifordBiziel
      @ChrifordBiziel Před 2 dny

      @@user-bn8ci6vx5c DC waboma lanji'?

    • @SameKaposa
      @SameKaposa Před 2 dny

      Osati ife uziti iwe

    • @user-gx8or3yz9u
      @user-gx8or3yz9u Před 2 dny

      uli mgulu lofuna kuononga malawi nde unyatu Born kalindo akunyeletsani mukalaka kulowa pansi

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před 3 dny

    Azathuwa akupangatu business mwina simukudziwa munthuyu akudya ndrama za opposition mwina simudziwa mukupanga ma moment azanu zikulowa Inu mulichete ndinakholowa kumudz