Vuto ku Malawi athu amene akuononga dziko ndi mitundu iwiri Malawi yonse pali (Achewa) (Ayao) mitundu imeneyi ndi imenenso ku school ndi (0-10) ndeno ndi mwambi uja amati ikaola imodzi mu bwato ndekuti zonse zaola,,ku Malawi ndi koola chifukwa cha mitundu iwiri,,tidzavutika mpaka kale or tidzagawana dzikolo.
Salankhula za mzeru awa ayi amafunika mbuli zimzawo aziwamvera mulibemo choonadi koma msanje ndi imene yakula mwa akuluwa ndi ena onse amene akuwawombera mmanja kuphatikizapo APM osewa ali ndi maloto a chumba sindingavoterenso APM 😅😅anthu anji asanje osayamikilako munthu akachita za bwino iwo zinawakanika pano aziti adzakomza iwo ndi Mulungu ayika ano ndimasiku otsiliza zambili simungakwanitse mpakana zittakwanilitsidwa andale ndi a bodza ndi ochepa amachita chilungamo koma enawo aaaaaa azipusitsa mbuli zimzawo aziwamvera amenewo ine ñdiye ayi 😅😅 bola kumavera yesu mboni yokhulupilika yopanda chinyengo nthawi zonse chilichonse, ndale basi kumangotsotsa chilichonse Ngati satana mudzakolola ndale zomwezo basi mpaka kumanda woooooo work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die 😢😢😢
Ing'aluleni Mr DC aiwala kuti tili mu vision 2020, zosankhana mtundu ndizakale 😮
God must watch over you bcz ukuchita great job ndipu akufungatire iwe dc
Ulemu wanu Mr DiiiiiiìiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiC The presiiiiiiiiiiiiiiiiident ❤❤❤❤❤❤
A DiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiC mor 🔥 fire3
Mwina adya ma Banzi ma president wa mumakwana Born Kalindo ❤❤❤❤❤❤❤❤
Bon Kalindo is good guy Zoona ❤
My president u lemu wanu a president aziko lamalawi ndinu🙏🙏
Iyeyu Kalindoyo ndi mayesa anali ku parliament komweko tinamvapo mukunena kuti salary yake imodzi atalandira tinamvapo kuti waipereka kwa osauka? Kungonena poona kuti iwo sali kumeneko ndiye kumangobwebweta basi.
Mchewa samaenda kutari, kwinaku kulibeko adazeelera kukhala pakhomo pomama
This is nothing but the mere truth Mr DC our president,, aku opposition akugonadi Kwambiri,,
We have suspended the searching until tommorrow
The only opposition
Akalindowo ngati akuona kuti ife apposition tikugona basi angoyambisa chapani chake
Aaaaaah km achewa ajaila et
Ngati a Malawi asiya kutsakha mitundu afford ndichipani chimene chikuoneka kuti chitha kulowa mu boma 2025
Big up DC
Boooon kalindo ❤❤❤❤❤
The DC your speech is pening me
Zoona zipano zinazi zikugona❤❤
Zoona osusa akugona kwambili inu mukuvutika, awu zeni Zowona
Akalindo chonde mwalakhula mwakwana tangoyambisani chanu chipani kuti mukathane ndi mabvuto please inu boni yesesani kupanga chipani basi
Eeeeee km ziliko km zochitika ku Nyasalande ai ndithu km ife ndili nanu Bon
Bro kod nanuso mwatopa ndizikoliet masiku azithamanga chochi paka kuduphisa masiku iii lelo pa 9 kkkk
Koma ndi zoonad Mr Bon kalindo
Vuto ku Malawi athu amene akuononga dziko ndi mitundu iwiri Malawi yonse pali (Achewa) (Ayao) mitundu imeneyi ndi imenenso ku school ndi (0-10) ndeno ndi mwambi uja amati ikaola imodzi mu bwato ndekuti zonse zaola,,ku Malawi ndi koola chifukwa cha mitundu iwiri,,tidzavutika mpaka kale or tidzagawana dzikolo.
Achitsilu awaa kapolo wa munthu
Za ziiiii
Zoona Big apa sono tiyamba kusapota atsopano monga inuyo ndi wina kamwana akayamba zolo zololi koma mapulezdent akalewa akukaikisa zikukhala ngati kuti akuzikaikira kuti sangaduse mfiti Chakwera basi inu yesesani mwina mulungu adzayankha kulira kwathu
Salankhula za mzeru awa ayi amafunika mbuli zimzawo aziwamvera mulibemo choonadi koma msanje ndi imene yakula mwa akuluwa ndi ena onse amene akuwawombera mmanja kuphatikizapo APM osewa ali ndi maloto a chumba sindingavoterenso APM 😅😅anthu anji asanje osayamikilako munthu akachita za bwino iwo zinawakanika pano aziti adzakomza iwo ndi Mulungu ayika ano ndimasiku otsiliza zambili simungakwanitse mpakana zittakwanilitsidwa andale ndi a bodza ndi ochepa amachita chilungamo koma enawo aaaaaa azipusitsa mbuli zimzawo aziwamvera amenewo ine ñdiye ayi 😅😅 bola kumavera yesu mboni yokhulupilika yopanda chinyengo nthawi zonse chilichonse, ndale basi kumangotsotsa chilichonse Ngati satana mudzakolola ndale zomwezo basi mpaka kumanda woooooo work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die 😢😢😢
Osawanyengelera aonjeza
Inu akukanthani ndi mulungu inu.Inu mungalongosole dziko koposa kuliononga inu?Activist behind the party. Kkkk koma ku Malawi
Namachende Bon mathanyula, kamadrama nzako pano akuyendela MG2 , iwe ulibe even njinga yakapalasa,
Panyini pamako mwana wahule iwe, zoti amalawi akuti suukuona what kind human being are you
@@dalitson3558 pamtumbo pamako, kunyelo kwamako amfumu nyini zawo
😂😂
Kodi mwalezela eti😅😅😅lero ndi pa 9?
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Komadi bwanji a opposition ali phee a dad bwanji ali pheee we are in pain