Koma zowona zeni zeni ayuda eni eni simpingo chifukwa iwowo aja anali ana ochokera kubanja kwa yakubu , koma lero lino chifukwa chokwatirana mmene mwalongosolera ndichifukwa chake zikumawonetsa ngati ndi mpingo
Thanks : koma yuda ndi mwana wa yakobo amati Ruben athalakwila atate ake' Yehovah anasakula yuda kuti ankhale mukuru wabanja ndi m'fumu wa ana ayaYakobo mwina amango sewenzesa zina layuda chifukwa champamvu yolamumulila ndi kutsunga chinkhalidwe chaochao chimene anapasidwa ndi Yehovah. Monga kalonga gawa mu'uchewa ndi chikulamayembe mu'uthumbuka a yuda ndi a Hebrew chilakulo Chao. Koma izi ndi zimene thimango welenga. chifukwa pali manguru a Hebrew ambiri koma lopambana ndi limene siligwededzeka ndim'banja laYudah.
The name Judah has its origins in the Hebrew Bible (Old Testament). In Genesis 29:35, Judah is the fourth son of Jacob and Leah. The name Judah is derived from the Hebrew word "yehudah," which means "praise" or "thanks." When Judah was born, Leah praised God, saying "This time I will praise the Lord" (Genesis 29:35). Thus, the name Judah can be interpreted as "praised" or "thankful." The tribe of Judah, which descended from Judah, became one of the most prominent tribes in Israel and played a significant role in the history of the Israelites. King David, as well as Jesus Christ, were both descendants of the tribe of Judah. In fact, the term "Jew" comes from "Judah," as the people of the tribe of Judah came to be known as Jews.
Koma mbili yachigawenga Muhammad munaichosa chifukwa chani,musamangonena mbili ya akhristu yokha ,muzinenaso mbili ya Muhammad , mbili ya Muhammad munaichosa chifukwa chani,
Ine ndimaziwa kut ayuda ndntundu, kuchokera pa ana ajacob,,mubwelese mbili ya Muhammad,munainenako koma munaichosa patangotha siku limozi,ambili sanaibveko,bwelesani mbili ya Muhammad chgawenga,
Truth about the Jews. But Christianity was started by the majesty Lord Jesus the messiah (All the worship goes to Him). But C.C.A.P; CFC; Catholic church; was started by human beings. I am also a Jew but a Malawian.
Zinthudi zinasitha apa tadziwa kuti muyuda ndichipembedzo osati mtundu ayi ,kwa America Ali ndi malo awo awo sukulu yawoyawo sangwilitsa ntchito ma phone 📱 📲 zamasiku ano ayi like smart phone ayi kikikiikiki.
Ukuzikola wekha iwe,nena zobveka,umakokela mbali yachisilamu koma chisilamu ndchipembezo chamafano Muhammad odyedwa ND nkhumba uja,palibe angakonde chisilamu chanucho,unachoseranji mbili ya Muhammad chgawenga,
Nkhani yoti,ma lsrael amakhulupilila zoti ndi tundu wopatulika ndi zoona koma titati tifufudze, lsrael ndi ziko lomwe timaliitana, Africa, Africa ndiye lsrael.komaso,ma yudawo, ndi chipembezo cha abraham.abraham,ndi wwakuda.mose,ndi wakuda,inu ndine,ndi ma Israel.
Malawi Police and Malawi Army is politicised by Malawi Congress Part as a ruling Party. This is a clear indication that our Police and Army is useless, we do not have security in Malawi. This report has reviled a lot of secrets about Kagame and insecurity caused by him in Malawi but both President Chakwela and the security agencies are just mute, no any statement from either the president or security agencies on the allegations. Do we really have a President, IG of Police, or Army Commander in Malawi? If we have then they are very useless or bought by Kagame.
Mafuko 12 a Israel atagawikana pawiri, South ndi North mu nthawi ya ufumu wa Rehoboam, mitundu iwiri ndi half inatsala ku South ndipo amenewa amadziwika kuti ayuda (jews) kapena kuti the kingdom of Judah. Mafuko 9½ anali ku North ndipo amatchedwa Israel. Ayuda simpingo ndi fuko la anthu komwe Yesu (the lion of the tribe of Judah) anachokera, (mkango wa ayuda).
Long time ago, the world had greatest tribes and races more than Jews. Don't be deceived. This was changed 18th century to brainwash us. Remember, Jews were the first people who were literate and they use that chance to brainwash us through their writings in books.
The way I know about the Jews is that their religion is called Judaism and the way of life of the Jewish people. It is the oldest of the monotheistic faith in Abrahamic tradition which include Christianity and Islam. African Jewish communities include sephard Jews,and mizrahi Jews who firstly live in the Maghreb of north Africa, Libya,Tunisia and Egypt . The founder of Judaism was Abraham.
Judah was one of those twelve sons of Jacob........( Genesis 49)... So Jacob was renamed by God from jacob to Israel ( Genesis 35:10) So i totally disagree with your points sir this was a huge and complex topic for you. Go understand John 8:32 and Psalms 119:142 all together. From there you will know who you are according to the bible Its when you eill know you spent all your energy for nothing because you are a true jew my brother and them are so called devils go read revelation 2:9
Brother are you telling us that you believe that you can be a Chinese today ? Because masiku ano zithu zifasitha like for real 😂😂😂😂😂😂😂 Some topics are so better left uncovered because mwala You need to wake up my people because the real Jews ( Israelites) you are and i can prove that with bible 24/7
Thanks for the nice video its not easy to organize such pieces of data into meaningful way everytime it needs more efforts
Thanks for giving us history God bless you and your family
Mbambande bro ngakhale ineyo sindimazi vetsetsa thanks for your update bro
Mmatha Man. Keep fire burn ❤️🔥❤️🔥❤️🔥❤️🔥
Bg awa amalankhura wamvemvemve and true exactly inuyo musinda mmiyoyo anthu srs
Indeed you are king 🤴of history 'Torah this book revealed by prophet Moses Bible by Jesus 'zabura by David
Thanks brz for sharpening my mind
Mumasegula mitu ya anthu ochuluka kwambili tnx 4n dat
Big up brother ❤
Thanks my bro but don't forget about ukraine and Russia
Koma zowona zeni zeni ayuda eni eni simpingo chifukwa iwowo aja anali ana ochokera kubanja kwa yakubu , koma lero lino chifukwa chokwatirana mmene mwalongosolera ndichifukwa chake zikumawonetsa ngati ndi mpingo
Forever Muslim man mumayankhula Znthu zomveka bwno
Mkulu wa history ulemu wanu
Iweyo ndi bg mn respect forever
Bro you have talent and continue this amazing job😊
Thanks : koma yuda ndi mwana wa yakobo amati Ruben athalakwila atate ake' Yehovah anasakula yuda kuti ankhale mukuru wabanja ndi m'fumu wa ana ayaYakobo mwina amango sewenzesa zina layuda chifukwa champamvu yolamumulila ndi kutsunga chinkhalidwe chaochao chimene anapasidwa ndi Yehovah. Monga kalonga gawa mu'uchewa ndi chikulamayembe mu'uthumbuka a yuda ndi a Hebrew chilakulo Chao. Koma izi ndi zimene thimango welenga. chifukwa pali manguru a Hebrew ambiri koma lopambana ndi limene siligwededzeka ndim'banja laYudah.
The name Judah has its origins in the Hebrew Bible (Old Testament). In Genesis 29:35, Judah is the fourth son of Jacob and Leah. The name Judah is derived from the Hebrew word "yehudah," which means "praise" or "thanks." When Judah was born, Leah praised God, saying "This time I will praise the Lord" (Genesis 29:35). Thus, the name Judah can be interpreted as "praised" or "thankful."
The tribe of Judah, which descended from Judah, became one of the most prominent tribes in Israel and played a significant role in the history of the Israelites. King David, as well as Jesus Christ, were both descendants of the tribe of Judah. In fact, the term "Jew" comes from "Judah," as the people of the tribe of Judah came to be known as Jews.
Well explained but he is saying ayuda because he is narrating the story in chichewa, but he is talking about jews/Jewish
Thus true
I really respect you boss
Good job and good talent
Koma msilamu wina aliyese adziwa kuti chiyuda ndichipemphezo osati mtundu wa anthu Qran 2 ikufotokoza bwino .
Ndipo live
Koma mbili yachigawenga Muhammad munaichosa chifukwa chani,musamangonena mbili ya akhristu yokha ,muzinenaso mbili ya Muhammad , mbili ya Muhammad munaichosa chifukwa chani,
Ine ndimaziwa kut ayuda ndntundu, kuchokera pa ana ajacob,,mubwelese mbili ya Muhammad,munainenako koma munaichosa patangotha siku limozi,ambili sanaibveko,bwelesani mbili ya Muhammad chgawenga,
Bro thanks inu mumatha God bless you 👏
Truth about the Jews. But Christianity was started by the majesty Lord Jesus the messiah (All the worship goes to Him).
But C.C.A.P; CFC; Catholic church; was started by human beings. I am also a Jew but a Malawian.
Koma bwana inuyo tangobwelami kuno kumuzi tizizakuonelani pafupi inuyo mutha kukhala president wathu
Keep burning 🔥🔥🔥🔥
BIG 👍
Kma Adolf Hitler mbiri yake tikuifuna pano
Yuda ndi mtindu
Ayuda ndi mtundu omwe uli ndi chipembedzo ndi chikhalidwe chake chake
Chiyuda ndi chipembezo osati mtundu wa anthuyi
Ayuda ndi mtundu osokoneza
🙏🙏🙏🙏
Inuo mudabwera keep it up bro❤️
I like your job ❤
Zoonad ma book anasithidwa kwambili
But don't forget to follow and give us feedback
The Ukraine 🇺🇦 and the Rasha
Zinthudi zinasitha apa tadziwa kuti muyuda ndichipembedzo osati mtundu ayi ,kwa America Ali ndi malo awo awo sukulu yawoyawo sangwilitsa ntchito ma phone 📱 📲 zamasiku ano ayi like smart phone ayi kikikiikiki.
No1❤
Salute,, ndili ndi fuso ,pa propaganda imene idachitika posintha zimene Moses adalemba ndikuikamo zawo zokomela Iwo pamenepa sadaononge chilungamo ?potengela kuti zimene ankalemba Moses sizidachokele pa iye yekha Koma Kwa yehova
Kutsutsana ndiwe ndi mistake
Big man ulemu wanu
Kodi story yaku Russia zilipati cz panopa, Russia 🇷🇺 kwavuta ikuluza
Ukuzikola wekha iwe,nena zobveka,umakokela mbali yachisilamu koma chisilamu ndchipembezo chamafano Muhammad odyedwa ND nkhumba uja,palibe angakonde chisilamu chanucho,unachoseranji mbili ya Muhammad chgawenga,
Tapeleka umboni kapena ndi buku lanji limanena zimenezo osayankhula zopeka please zipembezo zidabwela ndi anthu osati mulungu
Mumakwana Big
Big up ❤❤❤
But where did you get this good history mr???
Right
Zoonandi malemba ambili mu Bible anasithidwa chifukwa chake Pena limazisusa lokha
Thix brother koma nkhondo ya ku Sudan ili pat
Nkhani yoti,ma lsrael amakhulupilila zoti ndi tundu wopatulika ndi zoona koma titati tifufudze, lsrael ndi ziko lomwe timaliitana, Africa, Africa ndiye lsrael.komaso,ma yudawo, ndi chipembezo cha abraham.abraham,ndi wwakuda.mose,ndi wakuda,inu ndine,ndi ma Israel.
Iwe bro uwerenge deuteronomy 28 ndiye uzaziwa kuti amene amkazunzika ndi Adolf Hitler ndindani komanso Genesis 25 :25, malachi 1 ukatero psalms 108, uziwa kuti myuda ndindani
Man izizi simuzidziwa mukafufuzeso kapena mumangowada ma Jews
Big mn ugu
Ulemu wanu big
Kodi braza ya macholowe bwanjii?
Ayuda ndi mtundu
Good history next story hindu people
He did that
Tadzatipatsaniko history ya Titanic inamila bwanji ship imene ija???
Anamiza ndi satana imene ija
Malawi Police and Malawi Army is politicised by Malawi Congress Part as a ruling Party. This is a clear indication that our Police and Army is useless, we do not have security in Malawi. This report has reviled a lot of secrets about Kagame and insecurity caused by him in Malawi but both President Chakwela and the security agencies are just mute, no any statement from either the president or security agencies on the allegations. Do we really have a President, IG of Police, or Army Commander in Malawi? If we have then they are very useless or bought by Kagame.
Zikugwirizana pati ndi nkhani za ayudah ndi malawi police umbilical suzakutherani m chifukwa msonda akukutengererani ku court umbuli
Mafuko 12 a Israel atagawikana pawiri, South ndi North mu nthawi ya ufumu wa Rehoboam, mitundu iwiri ndi half inatsala ku South ndipo amenewa amadziwika kuti ayuda (jews) kapena kuti the kingdom of Judah.
Mafuko 9½ anali ku North ndipo amatchedwa Israel.
Ayuda simpingo ndi fuko la anthu komwe Yesu (the lion of the tribe of Judah) anachokera, (mkango wa ayuda).
Long time ago, the world had greatest tribes and races more than Jews. Don't be deceived. This was changed 18th century to brainwash us. Remember, Jews were the first people who were literate and they use that chance to brainwash us through their writings in books.
The way I know about the Jews is that their religion is called Judaism and the way of life of the Jewish people. It is the oldest of the monotheistic faith in Abrahamic tradition which include Christianity and Islam. African Jewish communities include sephard Jews,and mizrahi Jews who firstly live in the Maghreb of north Africa, Libya,Tunisia and Egypt . The founder of Judaism was Abraham.
😅😅😅
other people called jews by faith aren't original jews it's by faith similar to biologiacals!! Juda (son of jacob)is a tribe& judaism religion
Zoonadi kuti chiyuda ndi mtundu
anthu onse amene mwawatchula kuti ndi ayuda pomwe makolo awo si ayuda, makolo Awowo akumakhala mmodzi muyuda wina simuyuda that's why they are Jews
Siungakhale muyuda pomwe makolo ako simuyuda choncho chiyuda ndimtundu
Kometi yoyamba wowonela oyamba zwambino bwanji
Judah was one of those twelve sons of Jacob........( Genesis 49)... So Jacob was renamed by God from jacob to Israel ( Genesis 35:10)
So i totally disagree with your points sir this was a huge and complex topic for you.
Go understand John 8:32 and Psalms 119:142 all together.
From there you will know who you are according to the bible
Its when you eill know you spent all your energy for nothing because you are a true jew my brother and them are so called devils go read revelation 2:9
You research is very shallow on this subject I can give u books to read on this subject
Very true, his research is very shallow, I can agree with you.
Brother are you telling us that you believe that you can be a Chinese today ? Because masiku ano zithu zifasitha like for real 😂😂😂😂😂😂😂
Some topics are so better left uncovered because mwala
You need to wake up my people because the real Jews ( Israelites) you are and i can prove that with bible 24/7
Mukuva apolice ndati mwava apolice ndati mwava apolice ndi zikhale ngo'ma wava zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ngo'ma police udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndi apolice ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ngo'ma wava zikhale ngo'ma wava zikhale ngo'ma wava zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice ndati udziva zikhale ngo'ma wava zikhale ndi apolice