Kodi amene adapha Orton Chirwa anali ndani?

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 14. 11. 2020
  • Orton Chirwa anali founder wa chipani cha Malawi congress Party komanso anali Mmalitiri amene anamenyera nawo ufulu wa dziko la Malawi kuchoka mmanja mwa atsamunda.

Komentáře • 67

  • @user-xq1wd6wq5h
    @user-xq1wd6wq5h Před 3 měsíci +1

    Mulandile ulemu wanu ndikutha kuidziwa bwino mcp kudzela ku Bakili tv,keep it up God bless you big.

  • @user-qm1qb2jp4s
    @user-qm1qb2jp4s Před 2 měsíci +1

    Best tv ever next time mutiuzeko yemwe anapha sidic mia mwana wa kwathu ku chikwawa😢

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 Před 2 měsíci +2

    Rest in peace Orton Chirwa Kamuzu Banda will never get peace in his grave including people who are supporting his MCP party guys

  • @josuahkachali1489
    @josuahkachali1489 Před 3 lety +3

    Kuva history ya MCP ine sizavotaso mu Dziko la Malawi basi thanks

  • @ganizaninkhambule3405
    @ganizaninkhambule3405 Před 3 lety +6

    Kamuzu Banda is responsible for poverty in Malawi by killing people who could have contributed to the economic development of the country.....May the souls of Orton and Vera Chirwa Rest in peace.

  • @adammadi9689
    @adammadi9689 Před 3 lety +3

    Thanks my brother for shading light to us

  • @richardbanda5172
    @richardbanda5172 Před 2 lety +2

    this is the real history that we should put in our education system in Malawi

  • @viktak.d.o2835
    @viktak.d.o2835 Před 3 lety +3

    i appreciate this channel.very unique content

  • @esaumwanza3524
    @esaumwanza3524 Před 2 měsíci

    Yoooo thanks brother for your information ❤

  • @user-zv3cy2xj5p
    @user-zv3cy2xj5p Před 4 měsíci +1

    He was genius

  • @TheZuluman7
    @TheZuluman7 Před 3 lety +2

    Malawi has such a sad history .Thanks for the content

  • @selinabanda8789
    @selinabanda8789 Před 2 lety +1

    thank so much, very enlightening

  • @chimwemweyomba643
    @chimwemweyomba643 Před 3 lety +3

    Rest in peace Orton chirwa it's a very very sad story

  • @isaacbanda2973
    @isaacbanda2973 Před 3 lety +5

    Mutiwuza liti yemwe anapha Evison Matafale

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p Před 3 lety +3

    Zikomo milandu yoopsa iyi. Ambiri ali ndi magazi m'manja ndipo chowonadi chiyenera kuuzidwa. Dzikoli silidzachira popanda chilungamo.

  • @user-md5uv2cg6i
    @user-md5uv2cg6i Před 5 měsíci +1

    Koma dzimandiwawa kamuzu kumene uliko mapwala ako😢😢😢

  • @benjaminkampiyon1130
    @benjaminkampiyon1130 Před 3 lety +2

    MCP will never change

  • @mrmustdeDj
    @mrmustdeDj Před 2 lety +2

    MCP ingothesedwa 🤦🏿‍♂️

  • @KhumboZimba-x1z
    @KhumboZimba-x1z Před 5 dny

    😢😢😢 kamuzu banda mulungu amukanthe ndinthu asamukhululukire coz anali devi

  • @ismailseven4111
    @ismailseven4111 Před 3 lety +1

    Thank u for lovely history

  • @ThumbikoChipofya-gq7sd
    @ThumbikoChipofya-gq7sd Před 11 měsíci +1

    Pls tifufuziren mbiri ya Amnesty International

  • @aubreywallo1987
    @aubreywallo1987 Před 3 lety +2

    Umaitha keep it up bro

  • @doreenkhembo7718
    @doreenkhembo7718 Před rokem +1

    Kamuzu ana pasa phavu ndichirwa akayazana alekeni ku mapeto kwa che ndaziona

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 Před 3 lety +2

    Channel ilbwino👍

  • @dorikakamwendo6970
    @dorikakamwendo6970 Před 3 lety +2

    God bless you my Bro.
    You are indeed a historian

  • @PeterMakwiza
    @PeterMakwiza Před 21 dnem

    That's very sad story. RIP.

  • @brunokainga6483
    @brunokainga6483 Před rokem

    Very stupid MCP the then Government,,Tembo and Kadzamira are heavily responsible for apology to the family victims

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před měsícem

    😢😢😢 Kamuzu ndi sadzakupeze

  • @rafkey-official
    @rafkey-official Před 2 lety

    you are good on history but the problem is umadana ndi MCP,ukamapanga ma stories ako just do it osati kuonetsa mbali,remember that was one party and ndizoonekeratu kut nkhaza zinaliko koma osamakolezera moto,,,,

  • @ridgemwafulirwa
    @ridgemwafulirwa Před 2 lety

    No question, Orton Chirwa is the founder of Malawi.

  • @staceycossam5933
    @staceycossam5933 Před měsícem +1

    Tell us who kill Dr chilima?

  • @Carlington78-ql4lh
    @Carlington78-ql4lh Před 5 měsíci

    Mcp were heartless and real devil. 😢😢😢

  • @samuzymkwanya8490
    @samuzymkwanya8490 Před 3 lety +2

    Munthu woyipa kamuzu obelayu

  • @geraldnyirenda5279
    @geraldnyirenda5279 Před rokem

    Wasn't there a political party called "Nyasaland African National Congress " party in Malawi?

  • @HoseaxChidemba
    @HoseaxChidemba Před 10 dny

    Koma ya nkhazatu

  • @chimwemweyomba643
    @chimwemweyomba643 Před 3 lety +1

    Sindinkadziwa kuti chikamuzu chinali choipa chonchi

  • @ulemuchigoma4899
    @ulemuchigoma4899 Před 3 lety +1

    You will never become who you were meant to be if you keep blaming everyone else for who you are

    • @jamesgare3746
      @jamesgare3746 Před rokem

      but its important as well to know history of where we are coming from

  • @fae6833
    @fae6833 Před rokem

    Kamuzu and MCP worst Government ever in Malawi kuposa asamunda

  • @samsfrankle4921
    @samsfrankle4921 Před 3 lety

    Channel cha chibwana.time yonseyi mudali kutiko cadet uchira

  • @prosskaymw9953
    @prosskaymw9953 Před 3 lety

    Mcp nd yamagadzi mpaka kale

  • @wanangwachirwa6021
    @wanangwachirwa6021 Před 3 lety

    That was far too much

  • @alickbanda6257
    @alickbanda6257 Před 2 lety

    Akulu mumatikonza kwamiri

  • @kondwanigulupiragulupira2911

    Amalawi ambili amachita zinthu chifukwa cha kusadziwa.

  • @charleskennie9684
    @charleskennie9684 Před 3 lety

    Muma kwana amweni mutsatsiye kufukura nkhani

  • @luuu22mwanjabala79
    @luuu22mwanjabala79 Před 3 lety

    Kamuzu was a devilish mind

  • @kadzilangechiwoko1071
    @kadzilangechiwoko1071 Před 3 lety

    Kafukufuku wana penapake niwabodza

  • @kaluadavie1514
    @kaluadavie1514 Před 3 lety +1

    Rest in peace Orton chirwa.
    Mcp was more than evil. Kamuzu hell fire

  • @dorcushonda3047
    @dorcushonda3047 Před 3 lety

    Very nice story
    Keep it up

    • @dorikakamwendo6970
      @dorikakamwendo6970 Před 3 lety

      @@rossbank7248 bodza lake la kuthako kwakoko? asakudziwa ndani ku Malawi kuno kuti Orton chirwa anaona zoopsa komanso kuphedwa ndi chipani cha mcp?

    • @kaluadavie1514
      @kaluadavie1514 Před 3 lety

      @@rossbank7248 ndipo iweyo ndiwe chitsiru kwambiri. Zoona ungamayikire kumbuyo mcp mmene idathera anthu mdziko muno?
      Pamntumbo pamako wamva galu iwe

    • @kaluadavie1514
      @kaluadavie1514 Před 3 lety

      @@rossbank7248 ife tili kunja kuno chifukwa makolo athu analandidwa malo ndi kamuzu. Bullshit president amene uja akanakhalapo lero ndikanathana naye ndekha with my bare hands

  • @dennnisjames6489
    @dennnisjames6489 Před 3 lety

    I will never get tired

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 Před 3 lety +1

    Mcp ndiyimeneyi koma mulungu anatiyankha koma muluzi bingu peter joyce a mbola malawi sazasinthapo zivute zitani

    • @lucymawindo9283
      @lucymawindo9283 Před 3 lety

      Can you please exclude Bingu monga simmaona Zabwino zonwe anapangila amalawi?

  • @aubs4321
    @aubs4321 Před 3 lety

    This is new MCP not the old one, do not mix these two. Wamva author?

    • @johndulla7705
      @johndulla7705 Před 3 lety +1

      Whatever but this mcp logo is very ugly in the minds of people who suffered with this cruel kamuzu

    • @Gundasonic
      @Gundasonic Před 3 lety

      Regardless of the new mcp the damage they did is unforgivable and i will never be on their side

  • @Justman34_dislike
    @Justman34_dislike Před 3 lety +1

    Please make the channel as objective and independent as possible. It has great content. Don't favour sides please

    • @neliyachambakata8523
      @neliyachambakata8523 Před 3 lety +4

      But I think they are not taking side. They are just talking of what happened during that time.

    • @Justman34_dislike
      @Justman34_dislike Před 3 lety

      @@neliyachambakata8523 not this video. Some videos before this one. There is a clear portrayal of innocence of other regimes... and the conclusion of John Chilembwe saga is unfounded since his body was never found

    • @johnjeffrey4863
      @johnjeffrey4863 Před 3 lety +1

      @@Justman34_dislike koma zimene akunenazo ndi zabodza? Sizinachitike? Let us be serious guys chifukwa zomwe akunena munthuyu tonse tikuzidziwa kale, palibepo zabodza apa. Mukuzitenga ngati zandale chifukwa choti akutchula mcp, komano mcp inapangadi zimenezo

  • @kondwanitembo386
    @kondwanitembo386 Před 3 lety

    Iwe zimenezo amakuuza ndani mbuzi iwe