Phungu Joseph Nkasa - Mose wa lero
Vložit
- čas přidán 15. 12. 2012
- Enjoy! Send requests by commenting! Are you a musician and do you want to be published on this channel or do you have songs that should be on this CZcams Channel? Send a message on our Facebook page which can be found here:
/ chichewaonlinemusic
Our email address can be found there too! - Hudba
Anaiwala kuti Mose ndi mtsogoleri analeledwa ndi Farao. 🔥🔥🔥🔥
(Kuganiza mwakuya)
I love that song ever nkasa continue release a good more musics
Mkasa my favorite local musician ❤
Koma nyimbo iyi eeee muli uthenga oti Malawi sadzaiwala
Can't we turn this song into National Anthem 😊
We are here 2024 remembering Bingu the real leader of Malawi
Dear God may give us another leader like Bingu Wa Munthalika
Pa no tuguladi 40 pin Thumba😂😂😂 we miss you bingu MWeh😭😭😭
Mwai sufanana. Listening now 11th -03-2024
Mose msogoleri adaleledwa ndi Farao. I love this point ❤
This song hits different
Uyuyu anaona utsogoleri way back
Ku Malawi sikuzapezekaso President wamasophenya ngat Late Bingu Wa Muthalika...RIP Bingu🇲🇼🔥🔥🔥🔥
My days were funny!❤️😂😂😂
Ur the best Joseph mkasa
Kkkkkkkk koma Nkasa. He has the talent. This guy can sing nonstop.
Bring back Mose😌
2021 we here
Nkasa your the best singer bcoz your always put the truth openly, your the greatest musician and may God bless you.
30-october-2022 this song still Hot 🔥🥵🔥🥰🥵 oyimba akwathu
One of my best song.....kip resting well Mr President ...kufunika kwanu anthu akudziwa pano
Rip Mr President🇲🇼😭😭
Ndi Mutharika yekha amene amadziwa kutsogolera dziko komaso kumva chisoni ndi anthu Ake osati enawa anaferanji Mutharika mtsogoleri wacifundo mzimu wace uuse mumtendere amutharika mwasiya dziko likulira anthua Ali mmavuto mkasa nice song
Best song ever Joseph produced
mose wa muntharika RIP ntchito za manja ako zikuchitilabe umboni
yes u are right
Music with a lot subtance and meaning....
Nkasa akanati tisankhe muntu wamuyaya mkuyimba nkanayamba Kamakoko ne, kenaka nkumati mofuwula Phungu Phungu Phungu!
Sad that he wasn't recognised by the president for creating this masterpiece 😢
Apapa nde tadziwa😂ehh simmene kulili
Politicians finished this man otherwise he is the best 😊😊
All the malawians who uses their brains and who knows the truths, will like this song, and your the best singer Nkasa bcoz the late Bingu wa Muntharika he was best of the best president not in Malawi only but the whole Africa, and we will never have a president like Mose Wa Lero guys. Thank you so much Nkasa for your powerful song.
❤
❤❤❤
Just corrupt as other Malawian leaders.
Pa zaka zonsezi nyimboyi ndayimvetsetsa relo 🫂
😅
🤣🤣🤣
Lovely song
I like this song
Koma Akanakhala amadzukaso. Dr bingu tikanapempha abwerereso tachilapa
Bingu wa muthalika he was a great reader with vision
Nyimbo ya bwino kwambiri
Kuvera, kuonera ndikuwerenga ma comments 2019 press like
I will neverr forget Mr Mose Bingu his soul may rest in peace
Nkasa timakunyadila koma ndiwe thila kuwili baba
Kkkk koma guys
Nkasa nd legend mmmm❤❤
Phungu Nkasa!! aba ndiwo amuna
Bingu takusowa Ku Malawi kuno
The best lyricist
The best storyteller
Watching from mwineriwa vg mulanje
Nice guy good music
I like the music
Taimbani zafikapa mwina ava 11 November 2023
R . I . P #Muthalika pumzika kwa amani 😢😢😭
He is a creative mn kkkkkkkk bravo Nkasa
Heve
komabe tidzamkumbulkila moses wa mkasa
Bingu ehh tizamulira mpaka kale
I love his creativity
Continue resting in peace mr president
Zabwino kufulumira kutha!
very nice song I like it
Good music with meaning
Nice song phungu mkasa
big Captain on music
R.i.p father of the nation
😂😂😂Josephy Nkasa munthalika
Muntharika was the best leader
Nkasa ndidolo Eeeshiii
Nice movies
ulemu wanu mr mkasa mumadziwa kupeka nyimbo
Pano ndiye dziko lalowanso njala ija chakwera panyapako zedi
Kkkkkkk timakufila mkasa ...nyimbo iyi ndiyakale koma imandiwaza mpaka pano eishiiiii muli uthenga umu....
Zoona Mr
❤️❤️❤️
masida akuti yomweyo
Zonse ndi nthawi
K kkk east or west mkasa is the best
Eeeeshiiiii
❤❤❤❤🎉
Zoona ankasa zikuveka bwino
Umatha mkasa
🔥
Thanks God that devil is gone
PLEASE CAN YOU UPROAD LAWLENCE MBENJERE TITLE[UMPHAWI SIKANYAMA KOSEWELESA} IF I M NOT WRONG ABOUT TITLE
5:30 verse anakwapula apa si yamasewela
kodi amayimbila bingu eish chozaziwa ndintu
classic song
Hello a Malawi! i am Zambian.Can you please upload that one in which he sings about a president promising him a vehicle for the good songs but it turned out that the president didnt fore-fill the promise.
I can send for u the title is Anamva
Drimu
Nayeso anali wachaba
mMkasa ndi akatundu
Matafale
Kkkkkkk
munangobetsa man
Kkkkk koma nkasa ndikatundu akut chimanga chomwechi ndichomwe tikawonetse ku mzimba kuhora
Nice message but bad readership the whole Africa nations
Nice movies
Nice message but bad readership the whole Africa nations
Nice message but bad readership the whole Africa nations
Nkasa mwina akanati tisankhe anthu okhala muyaya padzikopa nkadayamba kusankha ndine kuti Nkasa Phungu, mumakazinga!