Phungu Joseph Nkasa - Chikondano cha Lero
Vložit
- čas přidán 15. 12. 2012
- Enjoy! Send requests by commenting! Are you a musician and do you want to be published on this channel or do you have songs that should be on this CZcams Channel? Send a message on our Facebook page which can be found here:
/ chichewaonlinemusic
Our email address can be found there too! - Hudba
He was prophesiesing the time we are living in now hey angaimbe ngati mkasa pano ndi ndani guys
I like you phungu of the poor people. keep it up please.
Ichi ndechulungamo chenchan ulemu wanu
Nkasa uyuyu osamuphwekesa simunthu wamba
The man I love the most in music industry. pungu Joseph
Kuimba kotumidwa ndi mulungu mwini zonse uleeeeeeeeemu wanu.
Phungu is phungu
Padiwa
Chabisaladi pamakobili mpaka kalekale umakwana nkasa
chili kupansi kwenikweni kwa makobidi, kutali
Mumatikumbusa kale lokoma nyimbo zachimalawi zenizeni
2023 December 21
Nkasa Nkasa umatha heavy ndithu chilungamodi ndiiwe phungudi wa amphawife, thanks powerful message.
Nkasa mu nthawi yanuyo munalid mdolo 🙏🏿🙏🏿
phungu wa anthu osauka you are my star keep it up
Moto kuti buuuu wawoooo
Amen baba
Uyu ndi Nkasa katundu akamatulutsa nyimbo imakhala nyimbo kuswa kuswa ndipo amakamba chilungamo ndikuphunzitsa monga Phungu wa Amphwawi❤❤❤
Chikhefa chimoto
Ichi ndechilungamo chenchen ulemu wanu😂😂
uthenga wanu ukupitililabe sudzathamphamvu
nyc songs
Zowona ❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Moto kuti buuuuu
Phungu Joseph Nkasa umatha
Zeni zeni
Chabisaladi pamakobili
True issue
phungu joseph nkasa
Zoona
Kaswiri
Mabanja
.k