Amayiwa ndi amene anapangisa kuti a Malawi asakhulupilire azimayi pa maudindo osiyanasiyana Makamaka pa udindo wa pulezidenti Kumavera za azungu, Kuba ndalama za ndege a Malawi ali duuuuu..osafusako Kaya a Malawi anapangilidwa mankhwala Kaya?
Aliyense anali wabwino munthawi yake komanso woipa munthawi yake sakhala wabwino mu zonse. Mwachitsanzo bingu amene mukumunena kuti ndi wabwino, alipo ena amkamunyoza Ali mmoyo
He is the very first thief of a president of Malawi 🇲🇼 he went to London to donate money from Indians who were kicked out of Malawi 🇲🇼 by Kamuzu Banda because of corruption. He told them to give him £2,000 each to come back to Malawi 🇲🇼
Mutharika's family is blessed with good leadership
Best of all the time Mutharika's 🇲🇼🇹🇿
Bingu was a great leader followed by his brother Peter, the family is blessed
Bingu ndi Peter sadzapezekaso
💪💪I support late Bimgu wamntharika only. Enawo nde kaya I don't know them
Number 1
Bingu ws great leader our country ever since continued rest in peace I respect n we'll never forget ur jobs.
Bingu n Peter mutharika I respect you guys❤❤
I support late Mr bingu wamutalika
Bingu a dali atate,,,,, siizi
Bingu was a leader not a politician
Madala madala , we will remember you for ever RIP
Bingu alwayz waz be legend
Bakili mbakatundu kwenitu
Bakilli ndiwe Galu kwabasi 😂😂
Wawo wachiyao
Munthu wankulu adayankhula uyu a Malawi a m'nzanga!,,,
Bingu anali anthu
He was a great man bingu
Amayiwa ndi amene anapangisa kuti a Malawi asakhulupilire azimayi pa maudindo osiyanasiyana Makamaka pa udindo wa pulezidenti Kumavera za azungu, Kuba ndalama za ndege a Malawi ali duuuuu..osafusako Kaya a Malawi anapangilidwa mankhwala Kaya?
😂😁😁😁 bingu muthalika super speech💪💪😁😁😁😁
Powerful 👊
Bakili love you
Bakili muluz my king
Ayao ngakombola basi 😂😂😂
Bingu was great leader bakili ndikayani
Kutunda kumeneko Bakili Muluzi
Wachiyawo wangalusa bulasa
The same applies to the current leadership
Bingu and Peter good speechs
Muluzi super
Mawu chair amenewo 😂😂😂
Hehehe pitala wake uti aaa nenani za Bingu osati pitala hiyaaaa musatinyase ana anjoka inu
Nice Bingu speech
Bakili anasokoneza mitu yamakolo athu
l like chair koma bingu anali katundu
Peter munthalika amathaso
Pa osewa walankhulapo za chitukuko nd Bingu mh koma zinazi
Acheya sopano zinali nthawi izo!!
😂 our presidents ...making history ...😂😂😂
Kkkkkkkk 😂😂😂😂😂I miss home
Azitsogoreri anarakhura mau abwino
Bingu was a politician..the rest just power hungry people..Peter it was his brother’s dream so had no details..but apparently second best..
Kkkkkk malawi ndimene imakhalira BINGU
Mawu omveka bwino ndithu koma anthu kusamva Brooo
koma atcheya wa ndi machine
U libo
Bingu anali akatundu.
Koma muti bakili zimayend
kkkkk kuba ma billion ndikopanda ntchito? koma awa andi opoila kkkkkk
Bingu was a man indeed
Bingu anali dolo
This last one send him back to school his chewa isnt right.
Bingu adali machine
Kkkkkkk
MHSRIP Late President Bingu Wa Mutharika. You were indeed a good president Malawi lost a lion.
Aliyense anali wabwino munthawi yake komanso woipa munthawi yake sakhala wabwino mu zonse.
Mwachitsanzo bingu amene mukumunena kuti ndi wabwino, alipo ena amkamunyoza Ali mmoyo
Apule bwaaa
At list bingu amaganiza guyz
Bingu anali adala
Chitsilu unawononga dziko
Wasalile wee ayao
Zonse ndi thawi
Bingu he was a leader others looters
Zinakukanikani 😂😂😂😂
Unali mwana sukudziwa chomwe ukuyankhula
Mayi uyu alibe zeru
I like your voice chair😂😂😂
King behavior detected
Bakili
Zoona
Makiyolobasi
He is the very first thief of a president of Malawi 🇲🇼 he went to London to donate money from Indians who were kicked out of Malawi 🇲🇼 by Kamuzu Banda because of corruption. He told them to give him £2,000 each to come back to Malawi 🇲🇼
Mami
Bingu ndi peter inuyo mulungu anachedwapo
Mulungu sachedwa, amapanga zinthu munthawi yake
Kkkkk
Mumakwana gyz
Bingu was a big not this thief the late big was very wise
Mbava zakumalawi kulankhula Ngati anjelo sorry
Super yao
Bingu was great president 😍🥰
Aq
Koma Amalawi ndife omvesa chisoni kwabasi kumangokuwa zilizonse
Big . Boos 👎
JB useless