Eti munthu uyu akutsutsa zama demo pa 10 zija kaya sanatumidwe ndi boma kaya

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 26. 06. 2024

Komentáře • 159

  • @SamuelChiwere
    @SamuelChiwere Před 4 dny +14

    Ndiye funso langa mkumati ngati tikulira maliro nanga bwanji ena mwawolilawo akumaponyedwa mundende pamene misozi yawo ikadari kutsikira mumchifuwa 😢

  • @user-kv8rk4ms5q
    @user-kv8rk4ms5q Před 4 dny +5

    Uyu alibe mfundo mwakasungura iye amamuzunza ,Bingu iye amuletsa ndani asatikwiyitse akhale chete

  • @user-gx5ht9gm3z
    @user-gx5ht9gm3z Před 4 dny +5

    NO PAIN NO GAIN PASEWO BASI AWONA WATUMINDWA AMENEO BWANJ CHAKWEL SAKHULILA OLILA NDIFE BASI BUZIWE

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Před 4 dny +1

    Ndipo mademo awawa atipatsa mangolomera ngatimomwe achitila anzathu achinyamata aku Kenya well done those Genz ndikawawa

  • @user-rv8pq8yg4s
    @user-rv8pq8yg4s Před 3 dny

    Mademo achitike,iyeyo ngati akuziwa kuti tikulira maliro, bwanji anthu ena omwewo olilawo akumangidwa, komaso kwacha ikugwesedwa,
    Pasewu papitidwe bas more fire

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g Před 3 dny

    Mumuuze mwakasungulayo Kuti ndi mbuzi 😮

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala Před 3 dny

    Amutuma

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 4 dny

    Machende ake manganya mwamulumbilisa liti musatitengele kuthako tell chakwera machende ake 😢😢😢

  • @staffordchibambo6439
    @staffordchibambo6439 Před 4 dny

    That galu is drunk demo yikhalepo basi mo faya 🔥🔥🔥

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r Před 3 dny

    Mwakasungura mariro ake ati umufuse kaye chakwera kt bwanji akumanga anthu nthawi yorira paribe zot mupusise anthu apa kenya kenya bas aporice samarani mademo awawa ndi aja anthawi ya bingu osat zoma opyezana ngat murinkanthu nanu mukuvutika masary anu onyenyekaso

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Před 4 dny

    Tikufuna ma demostration , undule mwakasungulayu wakakamba panopa alibe mzelu

  • @user-jj3oo6jh1l
    @user-jj3oo6jh1l Před 4 dny

    Sizikungwilinzana anthu tidalunza kale nde amene tili moyofe tife pawiri

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm Před 4 dny

    Koma kwamangidwa anthu ena mnthawi yomweyi yolila bwanj Sanabwere poyera kudzayakhula mbwelelazi,, zopusa zimenezo

  • @RachelLupiya-hi2pw
    @RachelLupiya-hi2pw Před 4 dny

    Akateroo amupasa chibazii,ma Demo sakulephereka , ngati tikulirabe maliro y anthu akumangidwa

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Před 4 dny

    Machende ake Galu amene apasa ndalama Galu chimunthu banda wakunamiza

  • @user-ug8rj6ut9y
    @user-ug8rj6ut9y Před 4 dny

    Akulesamademo chamba

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 4 dny

    Mademo kulibe ndipo sachitika mademo kumalawi kuno anatha ndukuzanizi ndizoona pls tikulilaso maliro awachiwiri kwa pule ndithu sachitika ndipo ndizoona

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv Před 2 dny

    Ndikape kwambilit ameneyoyo

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Před 3 dny

    Maganizo opusa kwambili ndikangati athu apita kokambilana ndipo mphindu ndichani ngati walandilla zake asatinyasepo ife iwe ndati wadananazo uzizangodya ma pwevipwevu akowo zosochelesa amalawi zithe tose tikulila iweyo wapambana chini zaziiiiiii

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal Před 3 dny

    ifetu osamatitengera kuntoso ngati malilo anjoka iyeyo ngati akudya ndalama si onse omwe akusangalala mzipatala makhwala mulibe mwadimac chimanga sichikupezeka kwacha ikungogwa mwa uchitsilu mwatasakotu kubomako koma lafote likukwanilani agalu inu

  • @lysonmkolongo1927
    @lysonmkolongo1927 Před 3 dny

    Aaaaaaa sizikugwilizana mgati iyeyo akutele a vise president anasakhwidwa bwanji analephelanjji kuwalesa amenewo

  • @Moses51
    @Moses51 Před 4 dny

    Mbuzi yamundu

  • @user-vv6rv4it4j
    @user-vv6rv4it4j Před 3 dny

    Akunama ameneyo Ife tipitatabe pasewuuu

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 Před 4 dny

    Undule ndi wadyera wazipakula. Ine asandiyase

  • @StevenJanuary-m8x
    @StevenJanuary-m8x Před 3 dny

    Uyu anapusa kale kale tinamudziwa pakanthawi

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 4 dny

    Msdemo kulibee ndukuzanizi muzisunge mademo panopa sangachike ai mwina kutsogoloku koma pano tikulila basi wina ali tiyeni kumademo apupuluma adikile kaye

  • @BenardMwale-g9x
    @BenardMwale-g9x Před 3 dny

    Anthu mulibe nzeru Mulimbikila kuchita ma protest chifukwa chakuti kukenya kuli ma protest kwafa anthu angati ku Kenya pitani muwapangile ndalama anzanuwo

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef Před 4 dny

    Wapatsidwa ndalama galu ameneyo

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Před 4 dny

    Amaneyu ndi galu kwa basi amakhalakuti tikamugende tikamuwotchele nyumba

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk Před 4 dny

    Amupasa ndalama a Mcp chisilu ichi muthawi ya ifayi aboma akowo apanga zinthu zingati

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m Před 3 dny

    ayi mademo achitike bwanji Boma likumanga anthu amene tikulila

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Před 4 dny

    Tikuvutika Ndife iwo akunjaya ndi ndalama za misonko yathu pamtumbo pako galu iweyo ukudya nawo ndalama zakuba za chakwela Galu

  • @user-zx3pz2wy1j
    @user-zx3pz2wy1j Před 4 dny

    Adatha ameneyu musamuvele.

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9i Před 4 dny

    Tiyeni toooooooonse......pa 10...ku mademoooooooooooooo😂😂😂😂😂😂

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Před 4 dny

    Iweyo ndiwe ndani pamtumbo pako ku Kenya wawona azako anthu akuvutika kuno Galu iweti wakumana chakwela nonse machende anu

  • @ChilangoNdalama
    @ChilangoNdalama Před 4 dny

    Pasewu bas

  • @HaroonMaundala-lg5lg
    @HaroonMaundala-lg5lg Před 4 dny

    Galu ameneyo. Ngati watumidwa utafe ndiwe

  • @ClifordBwwanali
    @ClifordBwwanali Před 4 dny

    Dont mind him. his looks have spirit of serfish akungoti bora akukhukuta alibe nao anthu ntchito anthu akuvutika dziko muno

  • @LastenWesele-wq8jh
    @LastenWesele-wq8jh Před 4 dny

    Mumuwuze mwakasungula patumbo pake

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Před 4 dny

    Inde takapangeni ma demo koma phindu lake likhala chani zonsez zitsintha chifukwa Cha mademo

  • @AllanBinali
    @AllanBinali Před 4 dny

    Mbuzi ya munthu

  • @user-bc3tx3wp1i
    @user-bc3tx3wp1i Před 4 dny

    Uyu galu kwabasi asatinyasepo ameneyi

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 4 dny +1

    NGATI AMUTUMA TIKAMUTIKITIRA PANYUMBA PAKE MBUZI YAMUNTHU AMUTUMA ACHAKWERA MUFERA LIMODZI NDI MCP YAKOYO ANTHU TATOPA ZOKAMBIRANASO PALIBE ATIZOLOWERA AGALU AWA INU AMENE MUKUMUIKIRA KUMBUYO NKULUYI MWADYA CHAMBA CHOMWE AKUMADYA CHAKWERA AKAFUNA KUPHA ANTHU NDIEKUKWEZA KATUNDU

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Před 4 dny

    Ndichifukwa kufunika ma demo, aliyese otsutsana ndi demo,ali kazitape wa boma lamulo la demo afe ndithu.

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Před 4 dny

    Mbolo yamake galu ameneyo ndikanakhala ku Malawi ko ndikananthana naye chisilu chamunthu ichi mademo wooooooooye

  • @OliverNkhoma
    @OliverNkhoma Před 4 dny

    tilira pa masiku 21

  • @user-pl2lj6mh1z
    @user-pl2lj6mh1z Před 4 dny

    A choke amenewo zausilu

  • @DonexNasenga
    @DonexNasenga Před 4 dny

    Km iye sadave kt nthawi yomwe tikulilayi kwacha idagwaso ndiye tizingosekelela zimenezo tikamatche panseu basi

  • @JamalTambula
    @JamalTambula Před 4 dny

    Mwakasungula machende ako iweyo anthu akumudzi akuvutika kwambiri kumanena zoti anthu aspange mademo mowa umenewo wamwa kuti 3:01

  • @DonexNasenga
    @DonexNasenga Před 4 dny

    Km iye sadave kt nthawi yomwe tikulilayi kwacha idagwaso ndiye tizingosekelela zimenezo tikamatche panseu basi 3:01

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo Před 4 dny

    Tiyeni tiyeni 🔥 ameneyo ngati wamutuma chakwera zake zmenezo

  • @user-hg8zy8pt5b
    @user-hg8zy8pt5b Před 4 dny +1

    Zopusa watumidwa uyu Ife osauka ndiamene tikukumana ndizowawa tipita pansewu basi nanga Ngati tikadalila malilo ndifukwa chani a boma akumanga anthu nde iwo sakuwona Kuti tikulila malilo

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před 4 dny

    Mwadya banzi uyu

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 4 dny

    Ndiwe galu kwabasi ngati warandira ndarama ka gwere wuko nyani

  • @user-hp4rl8cv3h
    @user-hp4rl8cv3h Před 4 dny

    Efe tipita bas pa musewu

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl Před 4 dny

    Mademo akhaleko msamuvere ameneyo komano akhale a peaceful osakhala ngati aku Kenya unless apolisiwo ngati angapange za ukape then take them on

  • @paundfeston
    @paundfeston Před 3 dny

    IWE NDIWE OPUSA OKUBA IWE WAPASIDWA NDALAMA UGALUWAKO WALILA AMAKOO

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo Před 4 dny

    Akunamatu ameneyu

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal Před 3 dny

  • @user-yk5qd6sk8e
    @user-yk5qd6sk8e Před 4 dny

    tiyeni pa sewu osasekelela dzompusa

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali Před 4 dny

    Watumidwa ameneyo galu ameneyo palibe zokambilana apa

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 Před 4 dny

    Ndichisiru akumanga abwanji athu ndiwe osaganiza bwino umadya bwinotu iwe athu akuzuzika mbolo yako wadya chibazi😅

  • @OmegaMussa
    @OmegaMussa Před 4 dny +1

    Akuphasa chidadzi uphusa iweyo

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa Před 4 dny

    Mbuzi ya mcp iyi chitsiru cheni cheni cha munthu

  • @kingSoko-wf4pe
    @kingSoko-wf4pe Před 4 dny

    Amakhala mbali ya boma akulu amenewa

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 Před 3 dny

    Musiyeni umphawi wamuswa ameneyu

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od Před 4 dny

    Enawo akukwanisa bwanji kumanga andu kapena kugwesa kwacha ife tilikoko

  • @jameschibwana2751
    @jameschibwana2751 Před 4 dny

    Mkati molira momwemo mzika zili mkati mofinyidwa mopanda chifundo, ndiye zikusiyana pati?
    Adindo akuyenera kukhala osamalitsa posaonjezera mikwiyo kwa a Malawi.

  • @patassonelucaszovuta3431

    Mademo achitikile kunyumba kwa ameneyu

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 Před 4 dny

    Ma demo alipo whether he likes it or not...

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Před 4 dny

    Ndi galu ameneyo wapasidwa chi banz

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Před 4 dny

    Napanyelo amei Galu vuto lake chakwela ndi osamva za anthu amei kumunyala mademo azione ruto ku Kenya

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr Před 4 dny +1

    Ngati amalawi akulila makiro nanga anthu akumangidwa bwanji?

  • @JossamMalon
    @JossamMalon Před 4 dny

    Mumuuzekuti asatiphuzitse kutukwana enafe tinazolowela kupeleka ulemu

  • @EnerstNtchefu-nk9gf
    @EnerstNtchefu-nk9gf Před 4 dny

    Ife kuno ku lilongwe tinamaliza mademo mwina kimwera kwanuko

  • @JosephChikabadwa
    @JosephChikabadwa Před 3 dny

    Akufuna akawadyetse bans ma representatives wo basi end of story

  • @ChimzyGwadira
    @ChimzyGwadira Před 4 dny +1

    Tiyeni Tiyeni Tiyeni pa sewu musamumvele wamisalayo

  • @phillgatoma4857
    @phillgatoma4857 Před 4 dny

    Walandila Ndalama ku MCP AkusakupusaniMbuzi Yamunthu

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg Před 4 dny

    Galu ameneyo siyen palib akuziwa

  • @johnmsona8845
    @johnmsona8845 Před 4 dny

    Ma Coward remember JB

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 Před 4 dny

    Akudya limozi ndi chakwe lol a

  • @ChimzyGwadira
    @ChimzyGwadira Před 4 dny +2

    Amupasa ndalama zambiri ndichisiru ameneyo

  • @JimmyMatope
    @JimmyMatope Před 4 dny

    Akunama ameneyu

  • @DaveSitolo
    @DaveSitolo Před 4 dny

    Angophedwa basi munthu olesa mademo

  • @IssahBannet
    @IssahBannet Před 4 dny

    Mboliyake iyeyo anthu akulila ndeno bwanji kwacha ikungogwa daily

  • @ClemenceDanielChinkono

    Uyu anagulidwa kale ndi aroma and there is nothing chanzeru chomwe amalankhula

  • @EyobeAyala
    @EyobeAyala Před 4 dny

    No sitimva zimenezo takwiyatakwiya bas..kumanga president wathu Bon Kalindo ife tikuona..no sorry 😢😢

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn Před 4 dny +1

    Pajatu abambo awa ndiopanda phindu kuyambila kale za ziiii

  • @DennisDonework
    @DennisDonework Před 4 dny +1

    Malilo talila kwakwana sangadzukeso Basi tiyeni ku mademo

  • @kaungabondera892
    @kaungabondera892 Před 4 dny

    Give me his name

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Před 2 dny

    Ma demo ndiye kulirako

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda Před 4 dny

    Vilekeke

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn

    Ndi galu ameneyu anthu asamvere galu uyu

  • @JimmyMatope
    @JimmyMatope Před 4 dny

    Pantumbo pake pamakeso ife pa 10th July tipita pansewu bas

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI Před 4 dny

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @AllanBinali
    @AllanBinali Před 4 dny

    Bwanji ena akumangidwa ena akulira??

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před dnem

    Ndichitsiru ameneyo wadya bazi let's go guy's apa ndi Kenya Kenya fire all idiots

  • @user-yi4bs3cd7w
    @user-yi4bs3cd7w Před 4 dny

    Akati mpala ngati?? Chende zako

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx

    Ndigalu kwambiri akuletsa mademo yoo.
    21 days yolira ikhala itatha podzafika pa 10 July.
    Akumanga bwanji ngati akudziwa zoti akulira.
    Asatichimwitse mayankhulidwe

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy Před 4 dny

    Amutuma ameneyo mbuzi yamunthu.. Bwanji Ngati tikulira maliro why akumanga anthu osalakwa .why akugwetsa Kwacha nthawi yorila .Mr kasungula kagwere uku mukupita Ku mademo siinuyo mwadya baz