26 November tinanena izi koma ena anatsutsa. Mawu aakulu akoma akagonera

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 09. 2024

Komentáře • 143

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Před 8 měsíci +7

    Pa 36 mn watching from Mozambique never give up bg brother chakweratu ziko lamukanita koma kuvomeleza kukumukanika

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Před 8 měsíci +5

    Chipanda inu akulu bwezi sitikuziwa china chilichose thank you pitilizani ndithu

  • @alicehananiya
    @alicehananiya Před 8 měsíci +4

    Watch from south Africa springs, mukutimvesa kukoma brother ❤🎉

  • @user-dv7ht6vn9s
    @user-dv7ht6vn9s Před 8 měsíci

    Keep it up brother... True Malawian fighter... God bless you... Onjeza moto... Osabwelera kumbuyo...tiyenazo zigawengazi.... A Malawi timamva nkhwangwa ili mmutu.... Shame on Mcp and ur so called Tonse alliance... Dzidzete

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Před 8 měsíci +5

    You're number one channel in malawi!!

  • @ImanRashidi-so4oo
    @ImanRashidi-so4oo Před 26 dny

    Koma akulu inuyo mwandidabwisa kwabasi zikomo pondidziwusa zambiri❤

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 Před 8 měsíci

    Best CZcams channel of the year 2023 in Malawi

  • @user-zf8hx9cf7p
    @user-zf8hx9cf7p Před 8 měsíci

    My best channel ndipo Israel ndi Zigawenga zopha anthu osalakwa.

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Před 8 měsíci +1

    You're number one boss MCP boma lokuphaaa mmmmmmmm❤❤❤❤❤

  • @user-tr3wm5hb7s
    @user-tr3wm5hb7s Před 8 měsíci +1

    Much proud of you ❤ big mumakwana.

  • @marshacee8315
    @marshacee8315 Před 8 měsíci

    Timadikilira daily program yanu a Bakili muluzi TV timaziwa zambiri kudzera kwainu big up moyo wautali brother

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před 8 měsíci +2

    Bakili muluzi TV amatha lero ndi izi lero akulira Amalawi 😅😅😅

  • @kennykachamba9466
    @kennykachamba9466 Před 8 měsíci +1

    Keep it up bakili muluzi TV ❤❤❤❤

  • @hourlyview4226
    @hourlyview4226 Před 8 měsíci

    Ndimasatira nkhani yanu koma ndinu onyoza anthu amene akuzimenyera ufulu ku Gaza. Pamenepo pokha mumalakwitsa

  • @LOPEZFBINALI-wk1hn
    @LOPEZFBINALI-wk1hn Před 8 měsíci +1

    Good channel to watch

  • @yamikanichirwa9787
    @yamikanichirwa9787 Před 8 měsíci

    My best channel tv ever

  • @MathewsChitsulo
    @MathewsChitsulo Před 3 měsíci

    I wish everyone to hear and understand about MCP . May something can change in Malawi

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 Před měsícem

    I thought of going to Israel but ummm will not ndife ndi umphawi kuno

  • @SmilingFountain-ir7wb
    @SmilingFountain-ir7wb Před 8 měsíci +1

    Amene amatsusa bakili muluzi TV, ndi mbuli

  • @ibrahimmeemzy9754
    @ibrahimmeemzy9754 Před 8 měsíci +2

    Yeah iwedi ndilo kwambili palibetso wina ku mw❤❤❤❤

  • @user-xy4hq6sx7v
    @user-xy4hq6sx7v Před 8 měsíci +1

    Inutu mumayankhula chilungamo ndiso zo ona zeni zeni

  • @MoosaSame
    @MoosaSame Před 8 měsíci +1

    This my❤❤❤TV station mor fire 🔥

  • @giftmingo9293
    @giftmingo9293 Před 8 měsíci

    Koma ku Kenya akupitansotu. Koma eni ake sakudandaulatu omwe ali ku Israel.

  • @DanielMasenti
    @DanielMasenti Před 2 měsíci

    Big up bro

  • @henlyhollah-vs3cc
    @henlyhollah-vs3cc Před 8 měsíci

    Tikuonela kuchokela ku Dubai,keep up good work bro

  • @user-cb4yc1lo7t
    @user-cb4yc1lo7t Před 8 měsíci

    Nice one big brother

  • @user-mp7nu4oz9c
    @user-mp7nu4oz9c Před 8 měsíci

    Big Man mudabwera inuyo km otsutsa enawa kumangowasiya bola ife tikuziwa choonadi

  • @blessingsmasankhula379
    @blessingsmasankhula379 Před 8 měsíci

    Keep up good work madhala 😎😎mukuigwira

  • @charleschimwala8189
    @charleschimwala8189 Před 8 měsíci

    Koma tamakambaniko za DPP Kuchokera 2004 Mpaka 2012 tikusowapo mbiri yina ngati mulidi 1platform

  • @Shaabann
    @Shaabann Před 8 měsíci

    Ulemu wanu big man God bless you

  • @allanimindozo9937
    @allanimindozo9937 Před 8 měsíci

    This man it's true reporter imalaw

  • @AbuMussah-wi7gb
    @AbuMussah-wi7gb Před 8 měsíci

    100% my big boss we like you

  • @MikeChiwanda-p5l
    @MikeChiwanda-p5l Před 8 měsíci +1

    Tikudzitsata🤗

  • @user-ui6vh1ld4f
    @user-ui6vh1ld4f Před 8 měsíci

    Ine ndipitabe ndikazionele ndekha komweko, osati kumva mabodza anuwo😂😂😂😂

  • @user-xo8ms5wh2s
    @user-xo8ms5wh2s Před 8 měsíci

    Am watching from Brazil

  • @LloydJamesMlanje
    @LloydJamesMlanje Před 22 dny

    Kod kamajekete wachoka patali 😅😅
    Wakhalaposo Ku PP

  • @josephphiri4185
    @josephphiri4185 Před 8 měsíci +1

    My best TV channel ever ❤❤❤❤

  • @user-jm7dv1tb4d
    @user-jm7dv1tb4d Před 7 měsíci

    Good tv keep it up

  • @JohnHussein-yd5nc
    @JohnHussein-yd5nc Před 8 měsíci

    Ndiye kuti a dpp palibe choipa amapanga,, ma office ndi magalimoto amaotchedwa aja, nanga achina jomo aja,, can you balance the issue

    • @giftmingo9293
      @giftmingo9293 Před 8 měsíci

      He is biased. Ine I liked his articles kwambiri koma pano timangomva ya Zikhale Ng'oma basi.

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 Před 8 měsíci

    Koma please tatiuzen zoonad za president Bukina Faso IBRAHIM TRAOle the best of best president in Africa

  • @user-cp4gt4pw7j
    @user-cp4gt4pw7j Před 8 měsíci

    Ulemu wanu big boss

  • @GeoffreyLuhanga-bl8zp
    @GeoffreyLuhanga-bl8zp Před 8 měsíci

    Inenso ndili kuno ku Israel koma zimene mukunenazo ndizabodza, ife tikukhala bwino bwino

  • @AfredMbeta-pk1cn
    @AfredMbeta-pk1cn Před 8 měsíci

    Please go ahead I always to listen it

  • @longimtimabii1017
    @longimtimabii1017 Před 8 měsíci

    More appropriate my dear brother

  • @EdsonRufeyo
    @EdsonRufeyo Před 8 měsíci

    You're number one

  • @frankcholimbirapo262
    @frankcholimbirapo262 Před 8 měsíci

    Vto nd uphaw k malawi.. bola tizingotchona komkuno k south Africa

  • @TONYJUSTIN-cx7yt
    @TONYJUSTIN-cx7yt Před 8 měsíci

    My best tv 📺 ❤

  • @user-tn4xm2dc2n
    @user-tn4xm2dc2n Před 8 měsíci

    Akutitenga ngati zinyama agalu amenewa

  • @patriciacraiton-sf5vu
    @patriciacraiton-sf5vu Před 8 měsíci +1

    Much love 🎉

  • @ashikalam8616
    @ashikalam8616 Před 8 měsíci

    Big up Big man

  • @PaulMvuma
    @PaulMvuma Před 8 měsíci

    Give us ur solutions bakili muluzi

  • @user-xr3ty6qq5o
    @user-xr3ty6qq5o Před 8 měsíci

    Watching live from johannesburg

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 Před 8 měsíci

    Munasowatu big man takufiran

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780 Před 8 měsíci

    kupusa chakwela osaganiza mbudzi ya muthu

  • @nyararaishumba9288
    @nyararaishumba9288 Před 8 měsíci

    Ulemu wanu bigy tiuzen zoona bas ayaluke chakwera

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 Před 8 měsíci

    Best channel

  • @JohnChibanda-h6b
    @JohnChibanda-h6b Před 8 měsíci

    Watching live from Israel in the Jerusalem city

  • @chikumbutsonsanga418
    @chikumbutsonsanga418 Před 8 měsíci

    kod nkhani ya anne rwigara ikukhala bwanji

  • @StanielMarius-es3gp
    @StanielMarius-es3gp Před 8 měsíci +1

    Ndinu dolo kwambiri

  • @staubioxygensensor559
    @staubioxygensensor559 Před 8 měsíci +1

    Dolo

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k Před 8 měsíci

    Kkkkk....aaaaa...wapanga chani ..chanzeru....inflation akuchita kuikonza ...mitengo ya zinthu ikungopweteka anthu kunjaku

  • @JemiMangani-if6wt
    @JemiMangani-if6wt Před 8 měsíci

    Proud of u boss makwana

  • @musaphiri317
    @musaphiri317 Před 8 měsíci

    Inu amene mukupasiwako kenakake mumakanira inde sanachitepo chabwino tiuzeni ndinu chabwino chimene anachitako muchiziwa ndinubasi

  • @patrickjaenda8288
    @patrickjaenda8288 Před 8 měsíci

    Your #one brother

  • @soxdososola2937
    @soxdososola2937 Před 8 měsíci

    😮😮😮😮,,osaukafe tizingosaukabe basi

  • @gaddiemkandawire6436
    @gaddiemkandawire6436 Před 8 měsíci +1

    Kodi Inu mukunduza kuti sanapangepo chabwino munthu uyu?

    • @kasupeowenpaul
      @kasupeowenpaul Před 8 měsíci

      Can you mention only 1 thing that chakwera has delivered only 😅

    • @LoydMcheleka-uq3ix
      @LoydMcheleka-uq3ix Před 8 měsíci

      palobe chimene wapangapo

    • @Lizzie-h1k
      @Lizzie-h1k Před 8 měsíci

      What has he done??.... he's eveb failling to handle inflation...nduna zikulephera, but the man os incharge??

  • @abisalomchunga6695
    @abisalomchunga6695 Před 8 měsíci

    Zoona bwana mumatiimila amalawi

  • @georgechikafutwa1334
    @georgechikafutwa1334 Před 8 měsíci

    Your number 1

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Před 8 měsíci

    Zoziyamba dala

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Před 8 měsíci

    Pano tikumva kuti sanawagulilebe ma phone kkkkk komaso sanalansile ndalama 😅

  • @user-yp8zf1wz5c
    @user-yp8zf1wz5c Před 8 měsíci

    Bakili Tv forever

  • @wilsonsawasawa3794
    @wilsonsawasawa3794 Před 8 měsíci

    Mumatha big

  • @MuhamadiIbraima-dr3lz
    @MuhamadiIbraima-dr3lz Před 8 měsíci

    Allah bless you

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 Před 8 měsíci

    U r my hero

  • @user-tq8xi4jg7x
    @user-tq8xi4jg7x Před 8 měsíci

    Komatuu Zina mukunamatuuu 😢

    • @uthmanalex
      @uthmanalex Před 4 měsíci

      mbuz palibe chomwe mukuziwa

  • @user-sh4jz7hs3x
    @user-sh4jz7hs3x Před 8 měsíci +1

    Love you so much boss❤

  • @alexlowe192
    @alexlowe192 Před 8 měsíci

    Information yomwe imapelekedwa ina yasathandiza kwenikweni , anthu ena ali pa south Africa pompa adapita okha koma akuvutika kwambiri ndiye ife tisanamvere chisoni anthi omwe adapita ku Israeli iwo eni ameyenera udziwa kuti akuvutika

    • @darlingtonbarhazanhie6830
      @darlingtonbarhazanhie6830 Před 8 měsíci

    • @user-rf4br1fv2z
      @user-rf4br1fv2z Před 7 měsíci

      Amenewa akufuna kumachititsa ulesi anthu Kodi ifeyo kuno ku South Kodi ntchito timangeilazi ndi za ma office basi tizikhalila kupepha ulakwa uku

  • @georgechikafutwa1334
    @georgechikafutwa1334 Před 8 měsíci

    Malawi wafika pomvetsa chisoni

  • @user-km3ek5pl3p
    @user-km3ek5pl3p Před 8 měsíci

    Kuva zenizen ❤

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 Před 8 měsíci

    Congratulations

  • @issabwanali29
    @issabwanali29 Před 8 měsíci

    Amalawi ku samva

  • @LoydMcheleka-uq3ix
    @LoydMcheleka-uq3ix Před 8 měsíci

    ine ndimafuna kuti mufufuze za ndalama zimene natasidwazo popeza kuti a mozesi nkunkuyu anati zithandiza zina ndi zina pa chitukuko za dziko! sopano afotokoze

  • @timothymhone2340
    @timothymhone2340 Před 8 měsíci

    Futso kumati mwalankhula bwino ndie inuyo mwathandizapo chani anthu ali pa u mphawi inu mkugwira tnchito

  • @user-iq2un8ix2g
    @user-iq2un8ix2g Před 8 měsíci

    Timakunyadilani abwana koma osamachita kunena kuti ku BIBA ai instead use mau otikudzithandiza
    Please I beg

    • @felixharry3117
      @felixharry3117 Před 6 měsíci

      Kubiba ndi mawu abwino kusiyana ndibkunyela

  • @musaphiri317
    @musaphiri317 Před 8 měsíci

    Bwana mulipo ndinushabe tiuzeni zoona vuto makani azaziona

  • @user-yk9ib1bg2b
    @user-yk9ib1bg2b Před 8 měsíci

    Akuziwa kuti zonse alinazo sizawo koma Ali Olanda, awa si ayuda ayi koma m'bado wake wa Satan

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 Před 8 měsíci

    ❤❤❤❤

  • @user-rk3kq9fn6p
    @user-rk3kq9fn6p Před 8 měsíci

    😂😂😂😂 akuti ndi good development chifukwa anakwera ndege..

    • @user-pn7cj9hb3t
      @user-pn7cj9hb3t Před 8 měsíci

      😂😂😂 Brother umbuli uli kwathu kuno ngati wolodzedwa

  • @mastermindmanyozo5853
    @mastermindmanyozo5853 Před 8 měsíci +1

    Fist to comment

  • @user-hr8xk6of5z
    @user-hr8xk6of5z Před 8 měsíci

    Big up

  • @peterparkergondwe4142
    @peterparkergondwe4142 Před 8 měsíci

    Following kut ndiziwe zambiri

  • @ShaqraWakusa-pe9ne
    @ShaqraWakusa-pe9ne Před 8 měsíci

    My brother

  • @PeaceAli-t9e
    @PeaceAli-t9e Před 9 dny

    Mbambande

  • @gracetjomane-jj3ib
    @gracetjomane-jj3ib Před 8 měsíci

    Dolo wanga

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před 8 měsíci

    Lero anthuwa akuti azilandira 150 USD(=250,000 MK) yotsalayo ikupita ku MCP ya campaign.

    • @Lizzie-h1k
      @Lizzie-h1k Před 8 měsíci +1

      Kkkkkkk...aaaaa. US 150...ndiye bolanso kumudzi komweko😂😂😂😂😂😂

  • @Yabwata
    @Yabwata Před 8 měsíci +1

    4th comment

  • @user-pn7cj9hb3t
    @user-pn7cj9hb3t Před 8 měsíci

    Ena adzatsaladi popita kumwamba

  • @mavutojackson9264
    @mavutojackson9264 Před 8 měsíci

    Umakwana

  • @IssaKakowa
    @IssaKakowa Před 8 měsíci

    Best

  • @user-zm5ho6wh1e
    @user-zm5ho6wh1e Před 8 měsíci

    More 🔥