BON KALINDO LERO UTM YAGULITSIDWA NDI MCP 🤔🤔🙌🙌

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 12. 09. 2024

Komentáře • 104

  • @MansonNyamwela-g5r
    @MansonNyamwela-g5r Před 19 dny +6

    Mr DC, watching you live from dar es salaam, Tanzania.just wishing you a very great Sunday, keep on doing good job.

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Před 19 dny +7

    Bwanji manganya asiye utm please

  • @user-lp2sd7lt8b
    @user-lp2sd7lt8b Před 19 dny +8

    Kalindo wabalalika kuno!!!!!!! This is the game of politics

  • @JohnfosterNkusengwa
    @JohnfosterNkusengwa Před 19 dny +4

    Restening from cape Town pa boma❤

  • @GregoryMatambo-m6y
    @GregoryMatambo-m6y Před 19 dny +5

    Osasunga legacy iweyo bwa

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Před 19 dny +5

    Yudas anali ophunzila wa yesu , komanso yudas anamugulitsa yesu ,
    History is the best teacher .

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před 18 dny

    ❤❤ zomwe amayankhula uyu ndi zeni zeni and zikuchita kuwonekelatu

  • @MaryNgola
    @MaryNgola Před 19 dny +1

    Inutu ngt mumadziziwa kt ndinu a MCP ndibwino musamamvele Za born kalindo,chifukwatu tsiku lina mudzagwa ndi BP,ngt likumulephera boma nde kulibwanji iweyo????

  • @LashidMalindima
    @LashidMalindima Před 19 dny +2

    Mumakwa adala

  • @MazyYanga
    @MazyYanga Před 19 dny +3

    My president

  • @Cee-H-Cee
    @Cee-H-Cee Před 19 dny +3

    First to watch

    • @hot265.
      @hot265.  Před 19 dny

      Kukunyadilani
      Thanks 🙏

  • @yobesaikonde6166
    @yobesaikonde6166 Před 19 dny +2

    Kalindo drama amatha go ahead we will keep roughing kkkkkk

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před 18 dny

    Usi ndimuthu oyipa kwambili mm ndiapo anamupereka chilima

  • @junasssabiwa1996
    @junasssabiwa1996 Před 19 dny +4

    DC

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před 12 dny

    Mwati M C P ndi yazibekete 😂😂😂😂😂😂

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 Před 19 dny +3

    Iwe Kalindo zangokuvuta kkkk you’ve met your match in Jesse Kabwira…..munatumbwa kwambiri pakatipa nde pano mutsegula mmimba simunati 😂😂😂

  • @NoorRasheed-re5vh
    @NoorRasheed-re5vh Před 18 dny

    Ukufuna tiziyendela.maganizo ako ulapa

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym Před 18 dny

    Inenso munthu uyu ndimamudabwa akayankhula zambiri zomunena chilima pano wafa ..akuonetsa ngati iye amamkonda mmm Ada Inu mdziwen Yesu kusanade...vuto anakumanan udindo..mwamutukwana peter eeeee pano ukutinso peter ndiwabwino😮😮😮😮

  • @OnenessLestas
    @OnenessLestas Před 17 dny

    Kalondo ife MCP timayikonda enafe zokamba zako sizimatisangalatsa ai

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Před 19 dny +2

    Nkalindo bwanji mullipo mulinkut bwanj malipot andege ankushedwaso after too months guys shonde bk TV mtanyiwwa

  • @victormbewe7462
    @victormbewe7462 Před 19 dny +1

    Let's admit that politics has become a global problem

  • @daltonjafali3856
    @daltonjafali3856 Před 19 dny +1

    We salute you our president

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 19 dny +1

    Ngat utm inatuluka mu mcp pali chifukwa chani chovalirira makaka pa musonkhano wa mcp. Zimene zinapita kukalandira president ndi makaka a utm ndi zisiru zipanda zeru sizikuziwa kuti uku ndi kwa mcp uku ndikwa utm sizikusiyanisa. Or usi asavareso makaka a utm

  • @MosesTchauya
    @MosesTchauya Před 18 dny

    Ndiwe wachipani chanji iweyooo

  • @jeremiahmalikebu2393
    @jeremiahmalikebu2393 Před 18 dny

    Palibe zogulitsidwa! Zikuchitika ndi Manganya ndi propaganda ya MCP. Koma ma supporter a UTM enieni tili nganganga pambuyo pa UTM ndi Kaliati. Team iri ku MCP yo ikhale komweko

  • @MisheckZako
    @MisheckZako Před 17 dny

    Dc

  • @MphatsoMwale-it4xd
    @MphatsoMwale-it4xd Před 19 dny

    Kalulu mwale from jonz D C tiyenaoni ambalame amenewa

  • @YammsyZebron
    @YammsyZebron Před 19 dny +2

    The DC great

  • @tasmania527
    @tasmania527 Před 19 dny +1

    Aise Kalindo umandiwaza ndi nthabwala zako. Please keep up the good work ya nthabwalazo- the DC mwana oopsya kwambiri kkkk. Bwanji osangonena kuti umafuna UTM ipite kwa Adadi? Come on man be honest...kodi zakuwawa eti? Nobody should be mad at Kalindo because he's a funny dude.

  • @ChawezChinkhuntha
    @ChawezChinkhuntha Před 19 dny +2

    First comment ❤

  • @Martinmkapangakapanga
    @Martinmkapangakapanga Před 18 dny

    l like u born

  • @lyiemax
    @lyiemax Před 19 dny

    Zomvetsa chisoni kwambiri, may the spirit of SKC do something on this bad move

  • @PaulWilly-ge1tx
    @PaulWilly-ge1tx Před 19 dny +2

    Zoona

  • @JamesSingini-t4j
    @JamesSingini-t4j Před 19 dny +5

    Kupita Ku msonkhano wa MCP doesn't mean uzavotera MCP Mr kalindo aaaaaaaaahh,,,aja anapita Ku convention ya DPP ali mu makaka a utm,afford,why smunanene kut ndi a DPP??? Nde palibe chifukwa wa utm kupita kokalandla chakwera coz vote Nd mtima nde musasegule nazo mmimba..

  • @PreciousDzonzie
    @PreciousDzonzie Před 19 dny +1

    Wamisara wamisara wamisara zindikiran nose mumatsata citsiru ici kt ndiwamisala watsara pang'ono kuyamba kutora zinyatsi uyu kkkkk

  • @GregoryMatambo-m6y
    @GregoryMatambo-m6y Před 19 dny +2

    No logic why kuveka anthu ma t-shirt yet you know kuti ndi anu kale kkkkk . Aaaaa kulowerera za catholic Kkkk fotseki

  • @mthelisokadambo8895
    @mthelisokadambo8895 Před 19 dny +1

    Chapompano uyuyu uyu tipita naye ku mental
    Ndale ndi choncho

  • @kondwanivyalema9449
    @kondwanivyalema9449 Před 18 dny

    Mbava zaba Chipani cha SKC

  • @HarryThomson-n7n
    @HarryThomson-n7n Před 18 dny

    M matiimiliradi man

  • @JohnNamakonje
    @JohnNamakonje Před 16 dny

    True

  • @GodfrleyTembwe
    @GodfrleyTembwe Před 18 dny

    Akalindo agwira pambali

  • @GodfrleyTembwe
    @GodfrleyTembwe Před 18 dny

    Warira mokweza kunooooo 😂😂😂😂

  • @MercyHassan-p4e
    @MercyHassan-p4e Před 19 dny

    😂😂😂😂 mukharise a president anthu anthu aanthu osauka mumatipasa chirimbikitso ndipo timakhurupirila kuti tsiku rina tidzadyera nyama ndipo dima ungakute bwanji kunja kudzawara dzuwa ridzaomba Bon karindo woyeeeeee, timakutsatani ngankhare tiri kutari ndi dziko ra malawi🇲🇼💗

  • @GraceMbwana-y8d
    @GraceMbwana-y8d Před 19 dny

    Amene mekuyankhulanu mukungofuna ndalama ife anatinyasa kale mtambo

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka Před 19 dny

    Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxiwa pa ifa ya chilima

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings Před 19 dny +1

    A DPP adadi Anu amene ananena kuti ovotera MCP amwa mutnjani KOdi amawauzao ndi a Malawi?olo ndaku Mozambique?a Kalindo misara yakulisa yendani ku Mental

  • @BoscoKalua
    @BoscoKalua Před 19 dny

    a DPP UDF UTM AFORD ndi onse enanu tengani zimene akune bon kalido seriously if not then you are finished completely and forget to be in government in 2025

  • @LindaLimbe-fo1oy
    @LindaLimbe-fo1oy Před 18 dny

    Ulemu wanu bwana Kalindo

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Před 19 dny

    Tge DC booooon kalindooooooo mwana owopsyaaa kwambiri

  • @GraceMbwana-y8d
    @GraceMbwana-y8d Před 19 dny

    Choti muziwe adale simuzatheka mpakana kalekale ifetinakuziwani

  • @AnnieJutta
    @AnnieJutta Před 19 dny

    Mr DC sizokanika kung'alula apa ai popeza ndimzanu manganya nenani kuti manganya wagulitsa chipanichi ku MCP ndipo akunama kumwamba Mulungu aliko angoutsa mkwiyio wa Yehova chabe mapangano akeo ndiopusa akuganiza MCP ingakamupatseso u vice president 2025 ndi munthu omvetsa chisoni betrayer

  • @user-ml2vw1dc9c
    @user-ml2vw1dc9c Před 19 dny

    Kalindo wayamba kulila kuno imeneyo ndiye politics kkkkk

  • @kingsleyhopematchaya5184

    Iweyo mesa chili a umamunyozaso lero ukhale ngati umamukonda chili a wosokoneza iwe

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f Před 19 dny

    Mmmm zabodza izoo

  • @MoreenSemu
    @MoreenSemu Před 19 dny

    Aliyese akunena zakuti awina wabalalika kalindo😅😅😅

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 Před 19 dny

    Dziko kuwonongeka chifukwa cha dyera, ndalama.

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e Před 19 dny

    This. was already planned before. chilima was killed

  • @Paworo-h5r
    @Paworo-h5r Před 19 dny

    Awuzeni anthu azipita kumunda si nthawi yochemelela zipani iyi. Inu ndi amene mumabweletsa njala every year

  • @user-zg9se4rw6v
    @user-zg9se4rw6v Před 17 dny

    Kalindo, you don't have evidence you are just making pipo to fight

  • @worldamazingvideoz9416

    Wamisala anaona nkhondo

  • @TamikaKaponya
    @TamikaKaponya Před 19 dny

    No ways....anthu ogulidwa ndi Manganya amenewo not real SKC followers

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness Před 19 dny

    Koma akalindo pumani kaye pathe mwezi umozi nkhani yikuwoneka kuti yatha mumutumo ndiye mukhale kaye cheti muzitipasa nkhani zanzeru ndiye kuti aroma alowelerepo kodi UTM ndiya roma koma munthu uyu

  • @ElesonChalemera
    @ElesonChalemera Před 19 dny +1

    A Mr kalindo ingojoinani ndale chifukwatu mmm zomenyera ufulu zakukanilani ndithu sizikuendapo

  • @ephraimkadamika
    @ephraimkadamika Před 19 dny

    No utm singathe utm yeni yeni tikuyidziwa

  • @StephenPrinceScale
    @StephenPrinceScale Před 19 dny

    The DC😂😂😂

  • @macchitsulo2986
    @macchitsulo2986 Před 19 dny

    Munthu amene angavala zovala za utm koma ali wa chipani china magulu ake ali ngati iweyo the DC

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w Před 19 dny

    Or atagula sitingavotele awa akanganya awa

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 Před 19 dny

    Ndare ndi Mabozatu

  • @ChicoBanda-kq7py
    @ChicoBanda-kq7py Před 19 dny

    Pitilizani bwana

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Před 19 dny

    Inu munapenga palibe zazelu mungakambe

  • @HarrietSainetStone
    @HarrietSainetStone Před 19 dny

    😢

  • @TaweniChavulaKamwendo
    @TaweniChavulaKamwendo Před 19 dny

    Eee

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před 19 dny

    apita okha ku chikangawa ife tidangoyikonda utm but the moment they join mcp ife tonse ku dpp basi or atangura anthu 200 ife tikukawinisa dpp

  • @xinalungu9616
    @xinalungu9616 Před 19 dny

    UTM and Kaliati has no money to run the party.
    If MCP is funding UTM, let them help UTM an alliance partner.
    Dr. Kabambe has 50 followers in Thyolo, considering his last rally. He doesnt have money either.
    Its Utsis camp through MCP n Mary that have money.

    • @mzeewandembonyirongo2972
      @mzeewandembonyirongo2972 Před 19 dny

      Kabambe has money...only that is relatively new in politics and giving out money is not his taste. In UTM Kambala is doing everything by himself. Imagine the whole top guys beg fuel money from him. Money as less than 300, 000 kwacha. They want him to pay. They the rest are not contributing to the party. And seems Kambala is tired. He is being told kuti zabwino zikubwera soon😮

  • @xinalungu9616
    @xinalungu9616 Před 19 dny

    Bwanji tinene kuti IWE CHILUNGAMO NCHAKUTI ndiwe munthu WA NSANJE kwa anthu amene si a Ku Mulanje or Thyolo.
    Correction.
    Iwe SI PRESIDENT WATHU ayi.
    I we ndi president was anthu 50 amapanga ma demo timawaona aka. Kkkkk
    NSANJE.
    KKKKKK

  • @GiftMaiden-g5w
    @GiftMaiden-g5w Před 19 dny

    Live show

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings Před 19 dny

    Akalindo zipitani chabe ku DPP uko

  • @JimmyMhone-b5p
    @JimmyMhone-b5p Před 19 dny

    Manganya wagulisa chipani cha UTM kung'ona

  • @moseskapelekeza8849
    @moseskapelekeza8849 Před 19 dny

    Mukuva kuwawa man

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e Před 19 dny

    ❤❤❤❤

  • @sauuladi6753
    @sauuladi6753 Před 19 dny

    Zakeyo

  • @RobertMisheck-w1v
    @RobertMisheck-w1v Před 19 dny

    Awanso mutu wamaminawo

  • @TelinaNjanje
    @TelinaNjanje Před 19 dny

    ⁱᶠ ⁱᵗ ˢᵒ ᵗʰᵉⁿ ᵗⁱᵏᵃᵛᵒᵗᵉʳᵃ ᵉⁿᵃ

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 19 dny +3

    A MCP ndi mbulidi zoona, sasiyatsa za boma ndi chipani, mai awa azitengela pa mgong'o.

    • @ziyamporoma377
      @ziyamporoma377 Před 19 dny

      @@user-pv9uk6sc3w Inuyo mukamayankhula ntudzu mumasiyanitsa ?

    • @LukaThawe
      @LukaThawe Před 18 dny

      Ndipo mbuli ndiyeyo

  • @isaacybanda-s6e
    @isaacybanda-s6e Před 19 dny

    Mumatha inuyo bwana

  • @ChilindeHarry
    @ChilindeHarry Před 19 dny

    Za chamba zokhazokha.

  • @Cee-H-Cee
    @Cee-H-Cee Před 19 dny +2

    First to watch