Velikost videa: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Zobrazit ovladače přehrávání
Automatické přehrávání
Přehrát
Amen 🙏 father God bless you all the time
Amen father.Mulungu aike dzanja lake pa dziko lathu.
Amen father, powerful msg
Amen father
Amen 🙏🙏 father mthalika alapedi anthu amenewa aziwe chowonadi
There is Lack of Philanthropy and Patriotism in political and even in religious gatherings.REASON? Leaders' cupidity.
Mulungu atikhululikile ndikutipulumutsa ndithu ❤❤ amen 🙏🙏💪
Amnuye atiyendere,ayenderenso dziko lathu
Koma uthenga umenewu wakutumani ndani?Chifukwa uwu siwochokera kwa mulungu!!
Amen father Tinasowa uthenga wanu
Amen
Amen amen father🛐
Amen father Mtalika
Amen Father
Episcope vade confuzaye!
Amen father🙏
amen farther
Zikomo kwambiri mabishop chifukwa zinthu zikamasiya Kuyenda bwino mumaunikira ndipo pitilizani. Dzikoli ladzadza ndizosangalatsa Mulungu.Ziphuphu zachuluka.Anthu ambiri akungosaukirasaukira ndipo ochepa akudyelera chifukwa chammene dzikoli likuyendera.
Amen❤
🕊️
Mawu mulungu sazapita pachabe ku aheberi amanena kuti mkoopsya kugwa mzanja la mulungu wa moyo aprezident segulani kutu la kuweluzika
MCP yayambaso nkhondo ija ya 1992 ndi ma bishop,
Emen emen
Kopepesa koyenera anthu kupita ndikukapepesa ndi kunsipe komanso kumabanja ena. There is no business kuti ma Episcope sakuyenera ndikulora komwe kupita ku state house. People should not get money through the death of chilima and other people.
🙏👋😭
Azibusa osavutika kumpempherera chakwera azakumangani
Komaso lalikilani uthenga wachipulumtso siuthenga umene anamutumani ayi phepani
Inu ndiosokoneza acatholic mukhumudwa zeni zeni osangoyambisa chipani chanu bwanji
awa ndimlomwe asaname apa akuona ngati boma lidzabwelelaso Kwawo akunama zazii
Zikungwiridzana bwanji ndi alomwe iziiiii????
Tangoyambisani chipani musatinyasepo
Mwaiwala mayitanidwe anu mwalowa ndale mulungu akuyendelen mabishop simulungu mulungu amene ine ndikumziwa siinu ayi
Amen 🙏 father God bless you all the time
Amen father.
Mulungu aike dzanja lake pa dziko lathu.
Amen father, powerful msg
Amen father
Amen 🙏🙏 father mthalika alapedi anthu amenewa aziwe chowonadi
There is Lack of Philanthropy and Patriotism in political and even in religious gatherings.REASON? Leaders' cupidity.
Mulungu atikhululikile ndikutipulumutsa ndithu ❤❤ amen 🙏🙏💪
Amnuye atiyendere,ayenderenso dziko lathu
Koma uthenga umenewu wakutumani ndani?
Chifukwa uwu siwochokera kwa mulungu!!