Achakwera Sakupanga Zinthu Mmene Adalonjezera | Wina Wazuzula Mmene Zinthu Zikukhalira

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 27. 06. 2024
  • #chakwera #chilima #malawi #trending #news

Komentáře • 58

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo Před 5 dny +6

    Mwayakhura bwino kwambiri ❤ ndipo athu awa achoke mwankhaza mademo achitike ife tikumva kuwawa amalawi

  • @user-gx5ht9gm3z
    @user-gx5ht9gm3z Před 5 dny +4

    NO PAIN NO GAIN TIYEN PASEO ON 10 JULY BASI CHAKWELA ACHOKWE BAS WALEPEL NO PAIN NO GAIN

  • @JustinLipipa
    @JustinLipipa Před 5 dny +4

    Afiti awa a Congress, Congress singasinthe ndi ng'ona zokhazokha izi aaaaaa

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y Před 5 dny +5

    Ndipo zachita kuonetseratu kuti ngozi yandege imeneyi anachita kukoza zimenezi imene taluza abale athu 9 imfa yamamgawa simasowa ayi Lazaro ndi anthu ake ndi dzigawenga

  • @TamalaSoko-vg5wq
    @TamalaSoko-vg5wq Před 5 dny +2

    Munena zoona brother ambuye akudalitsen

  • @HamidaIweni
    @HamidaIweni Před 5 dny +2

    Mwandiyankhula bwino kwambili❤

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 Před 4 dny +1

    Kulankhura mwa nzeru uku koma oipa adana nazo.Wandale amafuna atakhala zaka zochuluka paudindo yet akapeza mwai mmalo mogwira ntchito to gain trust kwa anthu onse amakhara busy ndi 'kwapsya tonola' mkumaembekezera kuti akaba ndalama ,ndalama zomwezo azapangira campaign kuti awine.Chitani zinthu zabwino kuti zabwinozo zizakupangireni campaign zokha popanda kuononga ndalama zanu
    Mwai munapatsidwa ,mukuutaya nokha

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před 5 dny +3

    Tilankhulireni anzathu inu ife atitseka pakamwa akuti tisamalankhule
    Mau anphanvu amene mwanena ndithu ambuye akudalitseni
    Ifeyo nde tikulira misozi yathu sidzatha 😢😢😢

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před 5 dny +2

    Your speech is good bro, keep it up

  • @user-rm2xv8ys1i
    @user-rm2xv8ys1i Před 5 dny +3

    Vilombo ivi

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před 5 dny +3

    This guy is saying zoona, just imagine celebration ya ku sankhidwa kwa Mr Usi ngati VP? Shame shame

  • @yohanezimba8329
    @yohanezimba8329 Před 5 dny +2

    The problem is Malawians make decision during anger, and 2025 will do the same similar choice because of anger.
    Others they are speaking as if they are wise but the true sense these people if they happen to be chosen they will also worsen this country

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Před 5 dny +2

    Ndi agalu awa brother palibe zonse analonjeza zaboza zonkhazonkha chilibe zeru iiiiichiiiii

  • @MphatsoChengetani
    @MphatsoChengetani Před 4 dny

    Very good speech

  • @user-iu6mr5xu6r
    @user-iu6mr5xu6r Před 5 dny +1

    Vc president ameneyo ngamene agulitsa Chilima amene amakonza zothetsa Tonse Aliance. Iye, pamwambo anati; Chakwera ndi wake komanso Chilima ndi wake. Kodi pamene amanena izi, Chilima ali kuti?

  • @TadalaPaul
    @TadalaPaul Před 4 dny

    Umumu muli mfundo guyz i proud for you vp

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv

    Mmmh pali anthu amene anapatsidwa luso lolankhula ndithu nkulu uyu akulankhula momveka ndipo ndutha kuona kuti ndithu dzikoli panalibe chifukwa chobwezeletsa anthu opandanzeruwa ,
    Nkulu iwe mulungu azikuteteza komanso mukhale healthy

  • @user-be3is8rc4r
    @user-be3is8rc4r Před 3 dny

    Good speech

  • @user-re7fo3be2z
    @user-re7fo3be2z Před 3 dny +1

    Poor people feel the pain right now

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke Před 5 dny +1

    Chipani ichi 🙌🙌 ndimkangomva ine

  • @user-zr7wk4oq2x
    @user-zr7wk4oq2x Před 4 dny

    Security departments kusanduka ya a chakwera aaaa zokhumudwitsa kwambiri 💔
    God knows everything.🙏

  • @FrankAdonis-zl6qc
    @FrankAdonis-zl6qc Před 5 dny +1

    Ulamuliro upusa even mwana wachichepele sangaganize mopusa ngati chakwerayu

  • @FrankAdonis-zl6qc
    @FrankAdonis-zl6qc Před 5 dny +1

    Chakwera achina zikhale ng'oma and other team opusa zitsiru za anthu oma ankhula America English koma athu opusa ngati nsima

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před 3 dny +1

    Yonseyi ndi mission ya chakwera, koma iye akutsogoza anzake iye azamka kuti sikumanda basi a chakwera be careful pple we watching you 🖕

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před 5 dny +1

    Akulephera kumanga kumkuyu okupha Allan witika koma kulimbana ndi bon kalindo mcp ndi ya satanic

  • @PetroMatias
    @PetroMatias Před 4 dny

    👍👍👍👍👍👍👍gud

  • @CHIWSABINYAMBOSE
    @CHIWSABINYAMBOSE Před 5 dny +1

    Alibe nzeru awa

  • @hussenadam3786
    @hussenadam3786 Před 5 dny +1

    True Malawian

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před 5 dny +1

    Muone ma tie amene ali pakhosi atau afira magazi okhaokha. Onani chithunzi chili pa video imeneyi.

  • @OwenNyangu-nv1yt
    @OwenNyangu-nv1yt Před 4 dny

    Adafa pa mdipiti wopelekeza maliro aja samalawi? Kodi Malawi ndi anthu amayina okha?

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op Před 5 dny +1

    Kuyakhula kwa bwino

  • @leviefeston7626
    @leviefeston7626 Před 2 dny

    Apolice ndi opusa kwambili
    Amalavula chingamu ndi mtegmdza olawa
    MCP ichike

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Před 5 dny +2

    Chakwera sangarire ayi chifukwa iye.niamene.wapha.chirima kkkkkkkk mubusa kumuchosa ku mzuzu.kukamusiya.ku lirongwe amafuna kuti akamuphe.ndipo akamudwe ku nyanja kuribe magazi ndeno amafuna magazi kkkkkkkk koma chakwera sataniki

  • @user-um6ob9sf3g
    @user-um6ob9sf3g Před 2 dny

    Achakwera ndi gulu ace wakanika

  • @EssaPindani
    @EssaPindani Před 5 dny

    Koma walephel kuyendesa malawi unku uyu achoke

  • @GrolyGondwe-e9s
    @GrolyGondwe-e9s Před 5 dny +1

    Zilombo zimenezo

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Před 4 dny

    Namu bwana mukuyangu rabwinino man big

  • @WisdomBlack-uu7zt
    @WisdomBlack-uu7zt Před 5 dny

    Za kugwa kwa ndege akudziwapo kathu awa ndichifukwa bwana aja anauzidwa kut ndege malo

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Před 5 dny

    Tiyeni Amalawi tigwilizane anthu awa achoke basi

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela Před 2 dny

    Mukuyankhuladi chilungamo zaonjeza

  • @Uncle_B265
    @Uncle_B265 Před 5 dny

    Malawi tinagulisa uyuu

  • @DavieChiwale
    @DavieChiwale Před 5 dny

    Sitikusowanso zabwino kwa afiti amenewanso atsala ndi masiku owerengeka

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx Před 4 dny

    A nkava kuwawa mu mtima ankangonena zimenezo koma sakugona asiyeni azuze anthu tsika mu mtengomo a tipeza a Malawi pansi pano

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před 4 dny

    Munthu asanafe mumayamba kugontha nimukhutu

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 Před 2 dny

    Zowona alimife tili mumavuto

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona Před 5 dny

    Evil men,Greedy, Jealousy men. Wait for your judgement day. Mulingati abwino popeza nyansi zanu zabisika

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa5981 Před 4 dny

    Mfiti za anthu izi

  • @raphaelfanuel4608
    @raphaelfanuel4608 Před 5 dny

    Inu simunalemekeze maliro asanachitike bwqnjiii

  • @KhalideNerve-mu1eq
    @KhalideNerve-mu1eq Před 5 dny

    😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @AckimMhango-v1x
    @AckimMhango-v1x Před 5 dny

    You are talking

  • @FrankAdonis-zl6qc
    @FrankAdonis-zl6qc Před 5 dny +1

    Democracy will never demolishe we are in new generation

  • @user-wb9ji3oe5o
    @user-wb9ji3oe5o Před 5 dny

    Yankhulani tikumveni